
Masikono atsike mtengo – Chithyola
Nduna ya Zachuma, a Simplex Chithyola Banda ati boma lachotsa msonkho wa 16.5% Value Added Tax (VAT) pa buledi (bread) ndi ma sikono (buns) ndipo akuyembekezera kuti mitengo ya Bread ndi mabanzi zitsika. Izi zadziwika… ...