![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2022/09/The-photo-shows-people-doing-business-as-usual-at-the-Limbe-market-in-Blantyre-235x176.jpg)
Kuchepa kwa malipiro kukukolezera mchitidwe okuba mu ma kampani a amwenye
Ogwira ntchito mu ma kampani a amwenye mu mzinda wa Blantyre akuti akukakamikizika kuyamba mchitidwe ozembetsa katundu m’malo ogwirira ntchito ndi kumakagulitsa chifukwa cha kuchepa kwa malipiro. M’modzi mwa ogwira ntchito wina yemwe anati tisamutchule… ...