![Michael Usi](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/12/Michael-Usi-235x176.jpg)
Zilipo 2019: A Usi alowa ndale, a Chilumpha ayambitsa chipani
Kuli kanthu konthula nchala chaka chamawa pomwe zikusonyeza kuti dziko lino labadwitsaso chipani china pomwe a Michael Usi alowa ndale. Lamulungu lapitali pa 7 Januwale, m’modzi mwa anthu odziwika bwino pa zisudzo, a Usi analengeza… ...