Malawi Government bans Tikuferanji on MBC TV


Tikuferanji

Government has directed top management of state owned Malawi Broadcasting Corporation (MBC TV) to stop broadcasting Tikuferanji soap, over what reports site the play as being ‘too critical’ of it and the Peter Mutharika led regime Malawi24 can report.

Confirming the development, Tikuferanji Producer Michael Usi said the producers of the play have received a letter from MBC TV management that the program will not be shown.

Tikuferanji
Usi in one of the episodes with his wife.

“We have received a letter from MBC TV top management that the show has been deemed to be offensive to others, but discussions are underway and we will fight that the program is there for Malawians,” said Usi.

Earlier, Usi blasted MBC TV director general Aubrey Sumbuleta for blocking the latest ‘Tikuferanji’ episode.

According to Sumbuleta, the episode was deemed to have content not favorable to the Democratic Progressive Party (DPP) led government.

Tikuferanji was initiated by Adventist Development and Relief Agency (ADRA) as an advocacy program and it addresses issues of human rights, gender, democracy and other issues.

In 2008, the radio version of the show received the radio play of the Year Award at MBC Entertainers of Year Awards, and it has been voted the best advocacy program in Malawi.

1,404 thoughts on “Malawi Government bans Tikuferanji on MBC TV

 1. Peter Mutharika panyapako and Albert Mungumo panyapako. Nonsenu simukudziwako komwe kudachokera TV imeneyo, and it comes to Malawi for Malawians not for you. We are tired watching your ugly face.Kodi mukudana ndi chilungamo? A Malawi adachenjera pano simungapusitse. We can’t be silent watching justice is taking out of power!! We should never watch. TIKUFERANJI was only program that was entertaining people,educatimg and transforming our minds, therefore we are apeal to you,bring back Tikuferanji.ANTHU OPUSA INU…Manganya hold on fight.you are Malawian and you have rights to express your concern behalf of your Malawians.WE BEHIND YOU!!!

 2. I alwys laughing when I see my fellow Malawians blaming Peter coz he didn’t put himself on that position.You are the one’s who voted for him.Galu wako akakuluma timamugulitsa.

 3. Ena ayitenga kale lamulungu ndi lachinayi 7:00 PM Pa M tv ngati muli ndi Decoder ya digintal. Izo za Awelesikizo zitayeni

 4. mbuz imeneyi ndie itengetu mbc tv yakeyo ikakhale nyumba mwake tisadzaioneso pot sitimayisowaso chimunthu chopanda chitukuko tidzionera ma station enawa ubwno wake si mbc tv yokhayo zilipo zambr chilungamo chmawawa zoonadiiiiiiiiu

 5. Hard to solve Noah open the door and allow us to enter

 6. kodi mexa akuti ndi omphuzira? koma zikuwakanika pano akulimbana ndima plogram apa TV malo mulimbana ndimamvuto Azachuma.

 7. The Government Must Learn All Democracy Kod Z This Who We Are Going To Live If They Have Issue Why Cant They Talk Lets See

 8. koma tinasankhadi olakwika ndithu ndikanadziwa ineeeeee aaaaaaaa mayo my vote vuto ndichani kodi anthu inu ? mxiiiii tiziyionera kwinako hope akalipilaso maka kukhale ku Times or ZBS

 9. Ndizopanda dzeru mokuti adzipanga za barget akulimbana ndi tikuferanji,,,,anangowona kukabweza card yake iija koma azipita tiribe ney dicam

 10. Ndizopanda dzeru mokuti adzipanga za barget akulimbana ndi tikuferanji,,,,anangowona kukabweza card yake iija koma azipita tiribe ney dicam

 11. Ndizopanda dzeru mokuti adzipanga za barget akulimbana ndi tikuferanji,,,,anangowona kukabweza card yake iija koma azipita tiribe ney dicam

 12. Ndizopanda dzeru mokuti adzipanga za barget akulimbana ndi tikuferanji,,,,anangowona kukabweza card yake iija koma azipita tiribe ney dicam

 13. Mmmmh…manganya’s play of tikuferanji was drop dead off~track…he overcalculated and substituted his creativity to political attacks…the program was a deal back then when mch of its focus was on social issues…az mch as the move to terminate the prog iz politically motivated, tikuferanji organisers were off track dats y they kept repeating the same program a countless times…it was easy to see that manganya had lost the creativity track to soup up his prog…bon vogage..the civil society wil do your job Mr coz its so strong now…..

 14. I saw this coming from very far. Malawian “ndale” (politics) we’ll not grow. Where shall get our checks and balances if we use cheap propaganda like this?

 15. Mbuli zandale pa Malawi zikuchulukirabe,kodi mesa munali ndi Green card,Ku Americako munaphunzira kutsutsa ndi chilungamo? Panyero pa mako Peter kachibwibwi Mutharika.

 16. Achita bwino ku banner..aaaaa Programme imabowa iyi…kukamba za HIV and AIDs anasiya kumakamba za chipani ndi za tchalitchi lawo.aaa shupit….Thumbs up Govt

 17. dzuka malawi iwe!!! kuti kwaaaaachaa!!!! limeneli ndiye boma la matchona they have failled and they just barn anything shameooooo!!

 18. Ndiye Boma La Pitala Limenero . A Malawi Azigwira Sanati 4 Only Single Yr The Malawian’s Out Cry Hs Been Heard Wth A Full Voice Already.Everything Is Hiked.Talk Abt Xul Fees,prices, Taxes Wat U Mention.But No Hiking On Salaries.The Lemons Are Stl Squized Till They Dry Kkkkkk.Tizigwirenge.Com

 19. mbc tv kuyambila mapresentr a ke onyasa .maprogram onyasa ,zochtika zonyasa nyasa kgweleni uko ife tikuwonela times tv zot kuli mbc tv ndamva kwainu a k24

 20. Its mbc not dpp tv mean ndiya amalawi ngati mufuna tsegula yanu monga olamulila dziko zamkutu basi ndiufulu wao atikufelanji kuyakhula zomwe akufuna dont hate the game hate the prayet

 21. Its ” THE LOSER FLAMES FOMBONI MALAWI UNITED”KUMENYA NDI SUDAN PA ETHIOPIA LAND TODAY MONDAY 23RD NOVEMBER ”KOMA ALIMBA AKATUMBU AMENEWA???

 22. T.v m ndayakubanja kwa bingu siyadziko timkati mudzaziwona mumkati ndalama fisi sangabeleke mbuzi zoyamwira kwa mkuluwake uja adziwekuti imfa ikafupikira sumamva

 23. Fear of the unknown- Still in a one party state? Whats wrong with Tikuferanji? Amalawi dziko likupita kuti: Mungaletse sewero loti llmawunikira anthu momwe zinthu zikuyendera mdziko kupatula kuphunzitsa za edzi? Asiyeni tiziwonera pa Luntha TV ndi pa Zodiak nkhalani ndi MBC yanuyo muziwonera nokha:

 24. Ndi kuti kuyambila mulonda wapa gate kumalizila bwana zeru mulinazo koma zochepa kwambiri tv yotsalira muno mu Africa senseless Malawi Boring Conquered tele vision

 25. ku malawi kulibe ufulu olakhula zakukhosi shhhaa Mr president mwatani kodi

  Bamusi mesa ndiwe mulangizi wa presdent y this time u r so phee akutafunitsa chisikono eti usadalowe m’boma umkatimilira kutiyakhulira lero ukungoyang’ana chonsecho mlomwe yo wayandikana naye eti okay

  muzatifuna DDP ikazagwa mukazatipeza ku ma NGO’s

  case closed

 26. Athu kudana ndi chilungamo A DPP mukwie ngat mukufuna mukakolope nyanja ndi pantie aseveth dae atan? ngat mukulakwitsa asakudzudzuleni bxi kumasogoza kunena kt ndi aDRA ndi bungwe la seveth dae fuck u ndipo mukhaula ndi apeter anuo muona kt mupanga bwanj??? makape achabebe inu mxxxxx

 27. mmmm ife banja lakwathu lonse timakonda mbc coz of tikufelanji ndie mene mwaicotsamu.. mmmmmmm il switch to times tv basi.. i hop kumeneku ayamba kuionetsa tikufelanji..

 28. Iwe #Kettie ukanakhala okongola sibenzi ma profile pic ako unachita upload ali ndi ma LIKEs 5 and 6 respectively.Kuonda kosakukhalako wamva!

 29. Peter mutharika is a stupid guy,ine singamvotere ataa!!!! Tizaoneranso Joyce Banda akazatenganso boma,ali busy kulimbana ndi zaziiiii inorder to fight with hunger,very stupid

 30. Eish! After all ADRA was paying money to MBC and that doesnt mean the very same ADRA can not afford to pay that to Private televisions like Zodiak tv, Times tv and others.

 31. Magetsi akazima ndi za normal, akayaka ndikumada nkhawa. Kuti mwina ndekuti ku chipatala, kuprisoni ndi kumortuary azima chonsecho kumeneko sikoyenera azizima. Chonde mnyani wa kunkula iwe uzizimitsa ku chanco, kupoly , kunyambadwe ndiku sunside koma kuchipatala asamazime chonde.

 32. Ambuye munakangomutengaso uyu, ngati momwe munamtengera bale wake uja akutizuza uyu. Ngati alipo yemwe amakoza tamkozani uyu mwachangu asowe watisautsa kwambiri. Iwe peter iwe samala upita watsala pong’ono mtundu wa anthu tonsefe sitingamakudandaule iwe minyama ilinawe londilondi ndithu upita iwe mwachidule ngati bale wako uja.

 33. Ine ngati nawonera MBC tv ndikuonera Tikuferanji basi…. Chifukwa sindimawonapo chaphindu chomwe amawonetsa kma ma tv omwe anthufe tikukonda kuonera ndi Zodiak tv,Times tv,Joy tv,Luso tv and Matindi tv.Timawakonda ma tv amenewo Chifukwa amawondetsa programme aBwino zedi en zimaonetsadi kut ali pa digito.Kma MBC tv,Ine sindiona Kusitha kut ili pa digito ndimangoona kut ili pa analog popanja… MBC tv is not tv but……….Kkkkkk…hahahahaha

 34. Tathokoza pot patsa customer ife a ZODIAK tizionetsa musaone ngat MBC nd yakwanu,,,Zapaphata nde chan?i dnt thnk its soon 4 malaw to develop if wi continue ignoring critisim

 35. Tathokoza pot patsa customer ife a ZODIAK tizionetsa musaone ngat MBC nd yakwanu,,,Zapaphata nde chan?i dnt thnk its soon 4 malaw to develop if wi continue ignoring critisim

 36. Freedom of xpresion without responsibilities then its total mess than message conception!mind people have the right to make and publicise plays on air or any media platform bt they have the role also to check on the responsibilities behind the message on delivery.so if the target was changed from public to a grouping of politicians then thats it.after all the play lost direction before already!!

 37. Asowa chochita eti!!!!???? Fix probz ther wil b no such critics!!!!!! Wat dey r tryna do z tell dem dey hav 2 speed up!!!! So dey ban tikuferanji, its naht solving de prob!!!!!!! I tink if dey negotiated probz it wud b beta coz sizikanadziwika!!!! Kma nw wen pple ask y it ended every 1 wil kno!!!!!!

 38. Tizionerabe ku ma Tv station ena,Tikuferanji amalawi chilungamo chilipo,amene adayambitsa tikuferanji,sanyambize kuti iziphunzitsa anthu za edzi zokha komanso Zomwe zikutipangitsa amalawife kufa tili maso,a adra musasiye kutiphunzitsa,timakunyadiran,big up to u manganya and your clue,mumatiyimirira..Aids is not the only thing killing us malawians,kmanso kusadziwa,poti the words of God say my peaple are dying because of kusadziwa,nde a adra amatiunikira zinthu zmene zikutipha tsiku ndi tsiku.thank u adra

 39. The goodness is that we are now having alot of Malawian television stations so guys let’s chose another tv stations to watch

 40. Why removingTIKUFELANJE?tikufelanji was one of the best program on TVM&it was moving with justice&reality&remember tikufelanji was a private program.no wonder we r in last days indeed therefore!opresing this lovely program is not amazing thing.

 41. Ineyo imene mmati MBC TV ndimaonera ndikapita kuchimbudzi/toilet basi kodi imeneyinso ndi TV station? asa nyasiiiii zokhazokha MBC TV ndi tissue hahahahaha azionetsapo Mr and Mrs Ibu basiiiii

 42. just go to vuclip.com and write tikuferanji on search u will watch all series from last month to I don’t know,stupid MBC,Malawi bingu corporation..

 43. galu ameneyu akuFuna tisamawonenSo anyooo [winiko] akhale ndi macommunity college akewo. mbc tv wayileS ya anthu akufa

 44. Ngati MBC imakoma chinali chifukwa cha tikuferanji.. Tsopano mwachotsanso nde mukutino tidzionera chani..poti Mabodza Broadcasting Corparation (MBC) YANGODZADZA NDI ZANDALE ZOKHAZOKHA….Thanks to new channels mwina tizipeza kothawira.

 45. ine ndi apabanja anga tonse tinasiya kuwonera MBC TV pa 20 may 2014 pamene Judge Mbendera analira he knows chomwe amalira look to day what happen

 46. Weak in mind….i guess malawi wil wake up nw…ar we nt liviin in aworld ov democracy….ppl shud hv avoice…u jst hv 2 accept 2 b criticized…..uyoooooo

 47. koditu akakhala pa u president MBC TV sikuti imakhala yake kapena ya DDP ayi sichoncho, ndi Television yathu amalawi. iyeyo ngat program imeneyo ikumunyasa simply because guy talks nothing but the truth asamaonele basi tilibe naye ntchito!

 48. There is no Democracy in Malawi instead we are under autocratic system, but why TIKUFERANJI akutaya nthawi pazinthu za ziii m’malo moupanga barn umphawi m’dziko muno mukulimbana ndiku barner ma program amene akumaphunzitsa,kusangalatsa ndi kuchenjedza anthu, is there any logic there??? Dont forget that 2019 is just around the corner we shall respect the principle of elimination!!

 49. Ua o fuz hu supot dix idea.y stopng dx nyc progrm?w@ av w lft wit apat 4rm tkufernji?y u fuu pple show a smle on dx?ngat zkuvutn jst get a rst.du u wnt dx angr Malawianx 2 fre u?stop w@ ua caling econmic n let us 3r.foolx.wyz wordx 4rm wagwaan.gambuxii

 50. Ndemukudandaula chani? Tv ndiyokhayo m’malawi muno onseonsewa kuli Luso, Luntha, Zbs, Timveni, CAN, MDBN kungotchulapo ochepa chabe. Tidzionerabe zimenezo

 51. sanapange bwino, ukamalakwisa anthu asakunzunzule? akufuna tizingoombela mmanja n,kumasekelera zilizose? ngati zikumuphweteka asinthe osati kuletsa prog. ayi.

 52. Ngati mwachotsa tikufelanji ndi chiyani chidzasangalatse TV? Kapena mlako wa lomwe? Ineyo ndimakhala ngati ndikuwonela generation kodi ameneyi mudakamutenga kuti?

 53. And Xo It Begginz Buh Itx Ending Soon,,, Hahahahaha Mr A.P.M Wer Z Ma Freedom Ov Press,, Liberties Led By Democracy I Hat It

 54. Inu ili ndi sewero, a MBC ndi Pitala mukuopa chani? Manganya(Michael usi) museweromo mkazi wake amakhala make sikono(Ruth simika) sindinamvepo kuti mkazi wa manganya(winiweni) akudandaula kuti Ruth simika amulanda mwamuna, chifukwa amaziwa kuti ili ndi sewero chabe. Nde ndikudabwa kuti zamusewerori a MBC akuti akunyoza iwowo pamene ili ndi sewero chabe lofuna kuphunzitsa.

 55. Mapulani anu onse mituyonse yomwe mumayidalira after kufunsira zeru kwa anzeru ena mwaganiza zochotsa chomwe chikusangalatse aliyense mdzikomuno,mwapanga chani aapa!!? any way ishall stop watching your TV iwill be watching other TVs like RV TV(the misser),E SPACE,MONDE you are chasing us thanks

 56. Ine ndinasiya kalekale kuonela usilu wanu umene mumautcha kuti TV malawi, zauchifwenthe zanuzo ine ai, shupiti!!!!!!

 57. Is MBC a DPP sponsored radio and TV or it’s sponsored by our tax? Why is this party trying to gag people who to tell Malawians the truth. Osamusiya choncho, azolowera. Amayesa utsogoleri ndi phada eti…

 58. Manganya ngati ukundimva bungwe la Adra ndilomela u can manage kutsegula Adra Televition mosavuta..ma company adzachita malonda awo pa tv yomweyo,,mudzakhalanso mukuzisaka uku tikumakuonelani pa Tikuferanji … Tayesetsani piliz ma donors ndiwosayamba inu aaaaaaaaa!!!

 59. Who said APM can lead this country? People in DPP as whole wanted him in because the party belongs to the Muthalika family. “Anyone can steer the sheep, but it takes a leader to chart the course” (Dr John Maxwell). Awa atigwetsa ku phompho awa…

 60. Ili ndi dziko lodana ndi chilungamo koma boza peteryu eeee wandiopsa kenaka tizamva kuti aliense ozuzula presdnt amangidwe tithamanga

 61. Basi ndasia kuonera mbc ma tv masiku ano achuluka komaso adra yalakwa cha? Tikuferanji imazuzula aliense ndie ok ndinaziwa ine kuti peteryu amakana kuzuzulidwa tikuferanji silitathauza kuti tikuferanji ku matenda a edzi okhaokha ai pali zinthu zambiri zimene amalawi timakhala moyo okusadziwa ndie ok basi tasia kuonera mbc.

 62. Nzeru zopusa zimenezi nyapanu kwambiri nose opusa mwaganiza bwanj?kapena amalakwitsa? mtima ngti chiwala wamanyi pa khosi NYAPANU muyakhe changu ndat NYAPANU koma

 63. this shows that the regime of peter lacks political tolerance which is one of the fundamental pillars of democracy. If there was one thing that malawians ever wished to continue viewing MBC was tikuferanji not its news which personalizes the ruling govt. and banning tikuferanji shows that the peter’s regime is a coward one not able enough to face the real situation but viewing any criticism as opposition. To make it even much funny, MBC uses taxpayer’s money and not only DPP members pay tax but all malawians of different parties do that and tikuferanji has the right to be beam on the Tv. Let me remind the president that he is in bad books with many malawians and this issue might even worsen that relationship.

 64. Mukhale nayo TVM yanuyo.Dont you know kuti you are now making Manganya more famous?Bwezani ndalama zomwe anakulipilani to air the programme.Ndale penapaliponse even in Church,Hospitals mmmm

 65. Moyo onukha ngat manyi umeneu tikufelanj yalakwa chan dis is a stupid goverment mbc tidzingowonela proferser dis profesor dat instead of being entertained to hell with u zandinyasa

 66. Mukuona ngati basi mangayo afa kapena azilira? ma Tv ndi ambiri, ndiponso ma Tv station enawa amaoneka bwino kuposa kumene amulesako. More fire Tikuferanji.

 67. Koma chimakhala chani amalawi kodi amafuna anthu azisekerera zinthu zikuonongeka? Malawi pano anthu anachangamuka sizotiphimba mmaso apa. Munthu ukamauzidwa choona mtima umawawa. tsalani ndizimaprogram zanu zonyasazo.

 68. Dikira pang’ono Manganya chakwera akawina 2019 your programme will be back on mbc tv,tikamati atsongoleri opanda masophenya mumaletsa,akuchotsa programme pa mbc pamene amalipira ndalama zambiri zomwe zimathandizira amalawi ovutika, lero akt ayi lekani kkkkkkkkkkk zili kumawi

 69. Bambo Asikono munalowa mkati,Zakazonsezi amakulolani bwanji,munaonjeza,konzanizolakwikazo,Sinkhani kapepeseni basi mwalakwainuyo,Timba sachepandimaziraake mumateropaja mwaganizabwanji bwana Manga?.

 70. Sindiku kulupilila ngati a DPP akudziwa kuti mbc tv imatanthauzanji,kapena inayamba chifukwa ninji?ngati sakudzi wa mwina chifukwa chakuti ppm sanakulile ndikukhala Malawi muno,ngati sangadziwe zonsezi mumumva akuisintha dzina kukhal DPP TV

 71. winiko umandiseweresa,winiko umandiseweresa,.koma winiko nde waziwa2!! Aaaaaa n’gooooo ndizionerabe pa JoYtv,iyaaaaa

 72. Kkkkkkkkk, #Malawi24 inayesa kuuza anthu kuti kwabwera investor ndipo wapereka kalata yachilolezo. Nkhaniyi yalembedwa maola makumi awiri ndi anai apitao, ndipo yakomentedwa ndi anthu anai okha. Pano akemba nkhani iyi koma nthawi yomweyi ili ndi makomentioposa 200. hahahaha, koma Malawi……?

 73. tikuferanji is not only matenda ai
  komaso zomwe likupanga boma anthu ambirife tinanthawila kuno ku South Africa tikuphedwa kuno ife a Malawi chifukwa cha boma lamalawi likutiphetsa kwambiri kandala ka misinkho kaathu kaja agwilitsa ntchito kumulakho wa lomwe shaaaa tikuferanji
  More fire manganya N Nyoo never give up

 74. Chifukwa cha ufulu sikuti tiziphwanya malamulo kenako ndikumanyoza Boma palibe alipamwamba pa malamulo ngati anapezerapo mpata ophwanya malamulo Boma yachita bwino kuyimika sewero imeneyo p

 75. Amalawi ngati zithu sizikuyenda mulodzeniso Piter amwalire ngati kuluwake fokofu we are tyde with him n tell him this is not her mother’s hole that he can play
  Please malawi ngati akulephera kupanga zomwe tinawasakhira angonena kuti alephera

  Ine Mwana Wa kanada zandikhuza becoz all of Malawian they like Tikufelanji
  Tikufelanji ndi mene ambiri tikuphuziramo zambiri

  Malawi mfuko langa ulipamavuto ndi Olamura

 76. Amalawi ngati zithu sizikuyenda mulodzeniso Piter amwalire ngati kuluwake fokofu we are tyde with him n tell him this is not her mother’s hole that he can play
  Please malawi ngati akulephera kupanga zomwe tinawasakhira angonena kuti alephera

  Ine Mwana Wa kanada zandikhuza becoz all of Malawian they like Tikufelanji
  Tikufelanji ndi mene ambiri tikuphuziramo zambiri

  Malawi mfuko langa ulipamavuto ndi Olamura

 77. kod paja #Tikufelanj amkaonetsa pa mbc??ndimkangooneratu sindimkadziwa pot ndinalumbira kut sindidzaoneranso #mbc aah!!palibexo chamzeru chomwe amapanga

 78. kod paja #Tikufelanj amkaonetsa pa mbc??ndimkangooneratu sindimkadziwa pot ndinalumbira kut sindidzaoneranso #mbc aah!!palibexo chamzeru chomwe amapanga

 79. chilungamo chimawawa kaya ife hatingaleke kuonera kamba kot mailesa kuli zodiak aziponyeza,,,,,,tsono boma mufuna tikuferanji lidzikuyamikirani pomwe muchita zoipa?????????kkkkkkkm mwalemb mmadzi achule awelenga,,,,,

 80. chilungamo chimawawa kaya ife hatingaleke kuonera kamba kot mailesa kuli zodiak aziponyeza,,,,,,tsono boma mufuna tikuferanji lidzikuyamikirani pomwe muchita zoipa?????????kkkkkkkm mwalemb mmadzi achule awelenga,,,,,

 81. Successful people look at life from the other perspective. Why? Because u will understand the otherside of your self from what people are talking. Don’t forget that mbuto ya Kalulu imakula ndi tadzawonani, if its true then what are going to replace that 30 minutes with? The soap has been there for years and it has helped you mbali yina yake…… Eish to sum it up ndi zomvetsa chisoni kwambiri.

 82. Successful people look at life from the other perspective. Why? Because u will understand the otherside of your self from what people are talking. Don’t forget that mbuto ya Kalulu imakula ndi tadzawonani, if its true then what are going to replace that 30 minutes with? The soap has been there for years and it has helped you mbali yina yake…… Eish to sum it up ndi zomvetsa chisoni kwambiri.

 83. Lest u 4get, we hav so many TVs in malawi. Tikuferanji yisadande……kuli times, zodiak, joy,luso n many more. TVM nkachaniso apart frm being the president’ diary. I stopped watching tvm smtym bak. Thanks to the numerous alternatives available

 84. Lest u 4get, we hav so many TVs in malawi. Tikuferanji yisadande……kuli times, zodiak, joy,luso n many more. TVM nkachaniso apart frm being the president’ diary. I stopped watching tvm smtym bak. Thanks to the numerous alternatives available

 85. Kodiso kuli MBC TV ine sindimaziwa, ndimangoziwa kuti kuli tikuferanji loweruka haf 7 ikatha basi kuseka. bcz mbc kulibeko zopindulira anthu koma chipani.

 86. Kodiso kuli MBC TV ine sindimaziwa, ndimangoziwa kuti kuli tikuferanji loweruka haf 7 ikatha basi kuseka. bcz mbc kulibeko zopindulira anthu koma chipani.

  1. When Shall we learn to accept constructive criticims?Should one rejoyce when things r not for fear of greedy politicians?NO!

 87. As an ADVENTIST, I am happy with this development because to me, that program lost direction way back and that was only misuse of my offerings.

 88. As an ADVENTIST, I am happy with this development because to me, that program lost direction way back and that was only misuse of my offerings.

 89. As an ADVENTIST, I am happy with this development because to me, that program lost direction way back and that was only misuse of my offerings.

 90. As an ADVENTIST, I am happy with this development because to me, that program lost direction way back and that was only misuse of my offerings.

 91. As an ADVENTIST, I am happy with this development because to me, that program lost direction way back and that was only misuse of my offerings.

 92. As an ADVENTIST, I am happy with this development because to me, that program lost direction way back and that was only misuse of my offerings.

 93. tikuferanji ndi programme yokhayo yabwino yoti ukati sudawonere umawoneka kuti siudapange zabwino . amadzudzula onse awiri amene amatisusa ndi otidambulawo.

 94. tikuferanji ndi programme yokhayo yabwino yoti ukati sudawonere umawoneka kuti siudapange zabwino . amadzudzula onse awiri amene amatisusa ndi otidambulawo.

 95. tikuferanji ndi programme yokhayo yabwino yoti ukati sudawonere umawoneka kuti siudapange zabwino . amadzudzula onse awiri amene amatisusa ndi otidambulawo.

 96. tikuferanji ndi programme yokhayo yabwino yoti ukati sudawonere umawoneka kuti siudapange zabwino . amadzudzula onse awiri amene amatisusa ndi otidambulawo.

 97. tikuferanji ndi programme yokhayo yabwino yoti ukati sudawonere umawoneka kuti siudapange zabwino . amadzudzula onse awiri amene amatisusa ndi otidambulawo.

 98. tikuferanji ndi programme yokhayo yabwino yoti ukati sudawonere umawoneka kuti siudapange zabwino . amadzudzula onse awiri amene amatisusa ndi otidambulawo.

 99. Walesayo apange dziko lake lomwe azikakhalamo moyo umenewo akufunawo.akuona ngati iye atapanga sewero ife tingaseke kapena kuonera

 100. Walesayo apange dziko lake lomwe azikakhalamo moyo umenewo akufunawo.akuona ngati iye atapanga sewero ife tingaseke kapena kuonera

 101. Walesayo apange dziko lake lomwe azikakhalamo moyo umenewo akufunawo.akuona ngati iye atapanga sewero ife tingaseke kapena kuonera

 102. Walesayo apange dziko lake lomwe azikakhalamo moyo umenewo akufunawo.akuona ngati iye atapanga sewero ife tingaseke kapena kuonera

 103. Walesayo apange dziko lake lomwe azikakhalamo moyo umenewo akufunawo.akuona ngati iye atapanga sewero ife tingaseke kapena kuonera

 104. Walesayo apange dziko lake lomwe azikakhalamo moyo umenewo akufunawo.akuona ngati iye atapanga sewero ife tingaseke kapena kuonera

 105. ndy who z going 2 advice govt in chining’a way …..? tulusan modz mwa ife ndpo osalafe tzatengela phunziro….skrrrr we love dr #manga

 106. ndy who z going 2 advice govt in chining’a way …..? tulusan modz mwa ife ndpo osalafe tzatengela phunziro….skrrrr we love dr #manga

 107. ndy who z going 2 advice govt in chining’a way …..? tulusan modz mwa ife ndpo osalafe tzatengela phunziro….skrrrr we love dr #manga

 108. ndy who z going 2 advice govt in chining’a way …..? tulusan modz mwa ife ndpo osalafe tzatengela phunziro….skrrrr we love dr #manga

 109. ndy who z going 2 advice govt in chining’a way …..? tulusan modz mwa ife ndpo osalafe tzatengela phunziro….skrrrr we love dr #manga

 110. ndy who z going 2 advice govt in chining’a way …..? tulusan modz mwa ife ndpo osalafe tzatengela phunziro….skrrrr we love dr #manga

 111. akuluakul choti mudziwe ,nkhani iyi ndiyosavuta ,mutu woyamba ku nyumba yamalamulo ,nkhani. yoyamba ndi tikuferanji program ,komanso program imeneyi muli uthenga wofunikira kwa achinyamata onse osati akuluakulu,nsanje. siumuna man,komanso tikuferanji yatha zaka zambiri ndiye takhuta. matowo basi timvekere kuti yatha .wanama

 112. akuluakul choti mudziwe ,nkhani iyi ndiyosavuta ,mutu woyamba ku nyumba yamalamulo ,nkhani. yoyamba ndi tikuferanji program ,komanso program imeneyi muli uthenga wofunikira kwa achinyamata onse osati akuluakulu,nsanje. siumuna man,komanso tikuferanji yatha zaka zambiri ndiye takhuta. matowo basi timvekere kuti yatha .wanama

 113. akuluakul choti mudziwe ,nkhani iyi ndiyosavuta ,mutu woyamba ku nyumba yamalamulo ,nkhani. yoyamba ndi tikuferanji program ,komanso program imeneyi muli uthenga wofunikira kwa achinyamata onse osati akuluakulu,nsanje. siumuna man,komanso tikuferanji yatha zaka zambiri ndiye takhuta. matowo basi timvekere kuti yatha .wanama

 114. akuluakul choti mudziwe ,nkhani iyi ndiyosavuta ,mutu woyamba ku nyumba yamalamulo ,nkhani. yoyamba ndi tikuferanji program ,komanso program imeneyi muli uthenga wofunikira kwa achinyamata onse osati akuluakulu,nsanje. siumuna man,komanso tikuferanji yatha zaka zambiri ndiye takhuta. matowo basi timvekere kuti yatha .wanama

 115. akuluakul choti mudziwe ,nkhani iyi ndiyosavuta ,mutu woyamba ku nyumba yamalamulo ,nkhani. yoyamba ndi tikuferanji program ,komanso program imeneyi muli uthenga wofunikira kwa achinyamata onse osati akuluakulu,nsanje. siumuna man,komanso tikuferanji yatha zaka zambiri ndiye takhuta. matowo basi timvekere kuti yatha .wanama

 116. akuluakul choti mudziwe ,nkhani iyi ndiyosavuta ,mutu woyamba ku nyumba yamalamulo ,nkhani. yoyamba ndi tikuferanji program ,komanso program imeneyi muli uthenga wofunikira kwa achinyamata onse osati akuluakulu,nsanje. siumuna man,komanso tikuferanji yatha zaka zambiri ndiye takhuta. matowo basi timvekere kuti yatha .wanama

 117. Should we say criminals are more organized than govt or govt is more organized by criminals? Enafe tinaiwala ma program amene amakhala pa MBC TV… Jst twice in a week timaika mbc pa nthawi ya tikuferanji… Take the progrm to Times or Zodiak TV…

 118. I know the person who has influenced the ban of Tikuferanji.
  Ngati siibwelera pa MBC ndibwino MBC ithesedwenso bcoz yakhala ikuphwanya ma ufulu a anthu enanso.
  DZUKA MALAWI CHONDE AMZAKO AKUPITA KU NTCHITO.

 119. Komatu zimenezi musamale nazo inu a DPP, musaone ngati zikutisangalatsatu ife zomangodzipangila zinthu mwakufuna kwanu mwamva! Tizaonana 2019!

 120. ife anaziwa mwayamba ndale chifukwa chani ? tikuferanji n ndale zikugwirizana? off target!!!!!!!! I support the motion 100% right.

 121. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

 122. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

 123. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

 124. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

 125. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

 126. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

 127. That’s the good idea. Adra imalandira thandizo ku NAC ndi cholinga chofuna kuphunzitsa a Malawi zokhudza HIV ndi matenda a Edzi. Koma zomwe zikuonesedwa zikusiyana. Komanso ADRA ndi bungwe la mpingo wa Seventh day Adventist kodi zimene amaonetsa zimagwirizana ndi chipembedzo?

  1. Bambo,cholinga cha tikuferanji sikuphunzitsa za edzi,pepani,ndipo bungweli sililandila thandizo kuchokera ku NAC. Ka fusensoni kwa amene anakunamizaniyo. Bwanji osapita ku adra kuti mukawerenge nokha cholinga chatikuferanji kusiyana mkumalemba za mabodza omwe mwauzidwa kapena maloto omwe mwalota!

  2. Ine ndi kuziwa za Adra kuposa inuyo. I don’t need to disclose my position zimene mukunena simukuziziwa. On Tikuferanji Adra receives donations from NAC and from Denmark. Adra is a humanitarian organization of Seventh day Adventist Church. Its a charity arm of the church. But Tikuferanji has lost the path. REMEMBER: I KNOW ADRA THAN YOU

  3. Of course zoti primary aim ya Tikuferanji ndi HIV/AIDS and related issues ziliso work plan ya ADRA ndipo DANIDA imaziwa zimenezo. Much as sindkusekerera zobana seweroli pa MBC koma generary speaking Tikuferanji lost its glory long time ago! Hope sindinatukwane munthu apa eti vuuu

  4. Ine ndinamva kuti .Manganya ndi amene amasayinira Aid ya unicef kuti ibwere.ngati ndizowona ndiye kuti Manga akhozanso kukhaulitsa peter

  5. komanso nthawi ina tikuferanji anadzudzula ana asukulu aphunzitsi ,water board ,Escom ndiye pamenepa muzitinji? amazuzula boma kapena anali mbali yaboma?

  6. akulu ngati muli ndi EDZ tangoperekerani umboni wanu pompano musalimbane ndi ADRA, zimaphweka mzako akamavina koma akati nawe vinako nde…..

  7. Mphatso Tibula zikuoneka kuti nkhani imene ukunena ndi ina. Iwe ukunena ena za edzi pamene Iweyo sunakayezetse. Pitani mukayezetse kaye.

  8. Let us build anew Malawi so that our children should behave as ahuman being not danger as lion,clever as goat & quit as a snake.so Tikuferanji was changing our direction.

  9. Mukamati Adra ikumayenera kukamba za Edzi zokhazokha ndiye simukuziwa chimene mukukamba, ADRA ili ndi ntchito yaikulu yophunzitsa a Malawi zimene zimawakhuza pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku, ndiye ngati Boma likukwiya nazo lingofuna kusamazuzulidwa likalakwisa, and kuipanga ban sikuti pangavute ma Tv ali mbweeee masiku ano

  10. Angobweza ndalama for breach of Contract a MBC.Ever since it started to air programmes,Palibe cha nzeru anaonetsapo.Picture quality Nyasi,Sound balancing Nyasinso.To hell with TVM.

  11. wosadziwa ndinuo mani ndipo musalimbane ndi adra ngat zakuwawan pamodzi ndi apeter anuo mukakolope nyanja ndi pantie kwinako muona kt mupanga bwanj we chizemphano uweh

  12. zilipano ndi zokhudza adra ndi mbc atumbuka mukayankhula zotukwana ngati pano ndatukwanapo munthu. ngati muli ndi vuto ndi president izo ndi zanu ndinamuika pampando siine mukafunse a MEC. Nkhani zanu zandale musatukwanire pa comment yanga. Ine ndapanga comment direct ku Malawi24 nanunso mutha kutero. ADRA is an organization of SDA CHURCH and am a worker of that church and I know what am saying.

  13. Koma pena imaonjezasi sukunama Mc not zandale zokha koma even ma cases ena mmene amapangira tackle. Zimalowa chibwananso pena reality imawathawa nthawi zina………….

  14. Ndiye ngati tikufelanji sikuchita bwino kulibwanji kungowauza kuti akumbukile ntchito yawo nanga kubanaku zitanthauza zanji poti kuteleko nkuwonjezela nkwiyo

  15. UKAMATI IMAKONDEDWA NDI ZIKO LONSE UKUPHATIKIZA NDI INE NDEMWE? INE SINDIMASATIRA ZA MANGANYA MASIKU ANO ANALOWESAMO ZA NDALE .

 128. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 129. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 130. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 131. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 132. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 133. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 134. Kkkkkkkk…moti mudziganiza zothetsa Mavuto azachuma avutawa, basi Nkhani ikhale yothetsa tikuferanji program pa TV. Kkkkkkkkkk… ithetseni mwina chuma chisakuyenda bwinochi ndi program imeneyi.

 135. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 136. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 137. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 138. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 139. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 140. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 141. amenewo ndiye manyaka.tizionela pastation ena.mukakhala pa pando mutivute .kumangositha zithu basi .zafika povita

 142. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 143. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 144. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 145. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 146. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 147. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 148. koma mudzionetsa nsokhano ulionse wa DPP live plus usiku mkubwerezanso eti??? zimenezija ndiye zaziiiiiizo.. bola kumaonera manganya ndi NYOo (mr i need my money) osati kumangoonetsa dzimisokhanozo..

 149. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 150. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 151. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 152. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 153. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 154. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 155. #Aubrey_Sumbuleta Kuchotsa #Tikuferanji pa TV cholinga adziikapo Ma #Blowjob omwe akupanga iyeyo ndi ma secretary ake mu office yake ndani sakudziwa #Mwachotsa Luso langa pa kanema inu muikapo ma blowjob anuwo tikumana ku #kachaso

 156. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 157. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 158. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 159. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 160. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 161. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 162. Manganya Ndi Ovaya Simungamuthe!Akangopita Ku Zodiac Kapena Ku Times Muli Mmadzi Guyz!Kumeneko Nde Kukakhala Kunene Zenizeni!Freedom Of Expression!If U R Rullin This Country And U R Expecting Pipo To Stay Quite 4 Eva That Is Completely Maloto!U R Dreaming In Black And White While Other Wea Dreamin In Colorz!

 163. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 164. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 165. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 166. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 167. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 168. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 169. Ufulu uja mwatilandanso, unali wa ngongole kodi? Agalatiya mwataya chipangano!!! Its just 1yr and 4 months, kuthere 5yrs ma Nyasa tili mu lake Nyasa basi.

 170. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 171. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 172. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 173. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 174. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 175. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 176. akeee so wakukhumba kut or wakunangiska mbwe wawabekenge waka wan2 sono wakumanya about uful n democracy so ivo wakupanga wakunangiska pala wavuka wajale waka vmastation vawo ivo even radios vatkwana ivo

 177. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 178. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 179. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 180. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 181. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 182. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 183. akhale nayo tvm yaoyo.more fire manga mupite ku times kapena ku zodiak tv.timakufilani GRACE,MAKE SIKONO,AZAKHALI,PAULO,A CHISI,A WINIKO,AMULELEMBA,ABUSA,PITILIZANI MUSASIYE AI,

 184. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 185. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 186. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 187. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 188. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 189. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 190. Akanaziwa number ya anthu amene amakonda kuonera MBC TV chifukwa chatikuferanji,sakanapanga mistake imeneyo.Mukaimaka kwambiri MBC TV anthu ambiri aluza nayo chidwi

 191. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,

 192. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,

 193. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,

 194. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,

 195. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,

 196. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,

 197. This is just rubish ,so u don’t want to be castigated .what kind of readers we r having in Malawi? JB am at azungu andituma koma anaonga zinthu,so Iwe peter ndan ,