
Anthu a ulumali akukanika kuwulura nkhani zokhudza nkhanza—FEDOMA
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu a ulumali la Federation of Disability organizations in Malawi (FEDOMA) lati anthu ambiri a ulumali m'dziko muno makamaka amayi ndi atsikana amakanika kukanena kwa adindo za nkhanza zomwe akukumana nazo.… ...