Malawi akulowera ku chigwembe – Kafukufuku
...DPP idzapambana pa masankho... Malinga ndi kafukufuku wa AFRO-Barometer yemwe wavumbuluka pa 06 December wawonetsa kuti Malawi akuyenda mchizilezile ndipo akulowera kolakwika. Malinga ndi kafukufuyu anthu 76 pa handede aliwonse (76%) afotokoza kuti Malawi akulowera… ...