As Malawi’s economy continues to evolve, more entrepreneurs are exploring various investment opportunities to grow their wealth and secure their financial future. Two prominent options have emerged: traditional investments and cryptocurrency. Each offers unique advantages… ...
Articles By Lindiwe Sambalikagwa
Bwato la ulendo wa ku Kenani lakumana ndi mafunde, ndipo ena adindo ayamba kuzitaya. Nduna yoona za ntchito, mayi Agnes Nyalonje, atula pansi udindo wawo tsopano. Izi zachitika patangodutsa tsiku limodzi zotsatira za kafukufuku zitaonetsa… ...
…boma lawaonjezera malipiro ndi 41%…aloledwa kuitanitsa galimoto osakhomela msonkho Akakhala oweruza milandu zawo zoyera, za kukokanakokana timaziona ndi anamwino kapena ena oyendetsa galimoto zikulu-zikulu sizinaoneke kwenikweni. Ngakhale iwo eni oweruza milandu ayamika ndi kusintha kwa… ...
Poyenda mtaunimu kumayenda osamalitsa, penanso olo mutatsinzina kumene. Pali chiopsezo choti amayi a chipani chotsutsa cha DPP tsiku lina mutha kukumanizana nawo adakali chibadwire. Amayi otsatira chipani cha DPP ndinso mtsogoleri wakale a Peter Mutharika… ...
Photo by Maxim Hopman on Unsplash The sports betting industry has used innovation to cultivate a better environment. As we progress it's very important to understand the trends and innovations that shape the landscape of sports betting. Digital… ...
Image Source: Pexels Over the last decade, the gaming landscape around the world has changed. Once upon a time, video games ran on hardware like bulky, pricey consoles and professional-grade computers and laptops. PC and… ...
Ngati wina kundendeko amakonzekera kuti tsiku lina adzakhala mesho wa a Saulos Chilima asiyiletu. Milandu yawo yonse ija a boma aithetsa. Tsopano ndi mfulu. Bwalo la milandu lero pa 6 May lavomereza pempho lochoka kwa… ...