
Kwanu kwanu m'thengo mudalaka njoka. N'kutheka a malume kapena azakhali adatchona mu dziko la Amereka lija ndi kuwaona tsopano. Tsache limene anyamula bambo Trump lokonza mu dziko la Amereka likhudza mzika zina za dziko lino… ...