
Kukanakhala kuti pachiweru kunali mwambi, kaya a Chilima akanagwilitsa uti kaya? Koma pomaliza kulankhulapo pa mwambo odzodza ansembe a chikatolika pa Limbe Cathedral a Chilima anatsindika kuti kunalibe mwambi. Koma ngakhale panalibe mwambi ochoka kwa… ...