Mzimba District Commissioner Rodney Simwaka has written to all directors at M'mbelwa District Council to sit down with their staff in their directorate on "The issue of theft among the council staff." In a memo… ...
Articles By Ephraim Mkali Banda
Mzimba South children have today commemorated the Day of the African Child held at Eswazini community ground in Traditional Authority Kampingo Sibande under the theme ‘Promoting Quality and Inclusive Education for All Act Now.' Speaking… ...
Khonsolo ya mzinda wa Mzuzu yavomereza kuti yakanika kuchotsa anthu ogulitsa malonda m'malo osavomerezeka. M'neneri wa khonsoloyi, McDonald Gondwe, wati khonsoloyi yalephela kusamutsa amalondawa, ndipo wati anthuwa, omwe amachitira mabizinesi awo m’malo osaloledwawa mu mzindawu,… ...
Achinyamata m'boma la Mzimba akhudzidwa ndi chiwelengero chokwera cha matenda opatsirana pogonana komanso nkhani zochotsa mimba mwachisawawa pakati pawo ponena kuti izi zikusokoneza maphunziro awo. Izi zanenedwa pomwe bungwe la Mzimba Youth Organisation, mothandizidwa ndi… ...
Police in Mzimba have detained Acha Msukwa, 35, an Assistant Information Technology (IT) Officer at Mbelwa District Council, in connection with a housebreaking and theft incident involving electronic devices. According to Mzimba police spokesperson Sub… ...
Matimu omwe sadzaiwala Mighty Mukuru Wanderers mu chaka cha masewero a mpira cha 2024 afika pa awiri tsopano. Matimu onsewa ndi akuchigawo cha kumpoto kwa dziko lino ndipo ndi a Baka city komanso Mzuzu city… ...
A choir called 'The Redeemed Family' from Zimbabwe and another called 'Sovereign Chords' from Zambia both arrived in the country on Friday. The two groups have jetted into the country following an invitation by a… ...