![Unima Malawi](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/12/UNIMA-corridors-373x280.webp)
Ambiri mwa ophunzira omwe ali pangongole yaboma pasukulu ya ukachenjede ya UNIMA ati alipachiopsezo chosiyira maphunziro awo panjira kaamba kosowa ndalama yogulira zakudya komanso kulipilira nyumba zomwe iwo amakhala ngakhale kuti anasayinira ndalamayi ndibungwe lopereka… ...