He may have fired blanks in the 3-0 semi-final defeat to Big Bullets but Mafco’s Richard Mbulu has managed to win the 2016 Presidential Cup golden boot ahead of Moyale Barracks’ Khuda Muyaba.
Mbulu, who finished with more than 15 goals, scored eight goals against Masendesende FC in his club’s first 2016 Presidential Cup game.
The striker has broken the record for most goals scored in a single Presidential Cup tournament since the cup’s inception in 2009.
On Sunday, during a Super League match at home against Blue Eagles, Mbulu who is the current Super League top goal scorer was on the score sheet again as he helped his side to go second on the standings after beating the Area 30 Cops 2-1 at Chitowe Stadium.
Congrats our own son… The fighter and the protector of our nation Malawi.,our true soldier and footballer… We love you soldier!
respect mbulu u hav made it
Osamu fanizila ndi matchini chiukepo?chifukwa muphonya, yamikilani koma musalowelele
Amatha Koma Uona Coach Kutenga Sulumba Mmalo Motenga Ameneyu Chinyengo Basi
Koma iwe wanoma magayu akumpha tazinena zako osati za ena
Congrats
Hahahaha osati Wadabwa?
chipukuta misonzi! Komano kuchoseredwa penot ndi Kankhobwe eeeeh?? Sazaiwala kkkkkkkk
Dzulo watimwensa wa mkaka pa chitowe stadium ameneyi osati mbuzi ya Chingambwe Fc Chiukepo.
Satha mpira mbulu inu thats why ku frames cump anamubweza amatengera zaku balacks
mmmmm mavuto sanje bwanji. afanawa panopa palibe akumaka pama striker tili nawo ku malawi kuno. ndiuzeni tipange compare
Olo mutasinjilira chotani komano Mbuluyo zamukanika kupatisa prezidential ku Team yache basi thus it
Uyu nde ndiweniweni, osati nkhalamba zinazi. ayi, Big up man.
tikuziwa kuti chikho ndi chimene chikukupwetekani inu! Lirani basi mukatopa mutonthola
Wa Noma wawinako chani? kkkkk mbulu amaöneka kuma smal teams like Bane
Mbulu ali booo…flames apiten bs chukepo watha bs
Mwanayu! kunena ngamo Akutha! than Chiukepo next tym in, mu sqard ya Flames Chiukepo of.
Koma golden boot yaku Malawi imakhala ya gold weniweni?
uyu nde striker wabwino osat zinazija ka mumazit uchiuchulukepo ka chuluchaphepo ka chulukepo sndkusamala. Ndatukwana ngati???
cnt stop laughing kkkkkkk…….
sinakha anthu akumangochemelera manyaka ati chifukwa ndi player wa team yawo
mwaiwala champhepotu abwana… ndinena sukumba ndatchula munthu ngat?
Ayi bwana kkkkk
Dolo ndiyemwe amatengedwa ku frames cump.wanuyo azatengedwa kukazafunika watchman mwavep yake.now we need players
Kunyoza plyr wa team ina pomwe akukamba plyr wa team ina nkulakwa, Chiukepo sangapite yekha ku National amachita kuyitanidwa choncho ngat kuli kulakwa amalakwa ndiwoyitana komanso kuli konse si ma star wonse amene amayitanidwa ku National team ,tiyankhure molemekeza ufulu ndi ulemu wa anzathu. Zikomo mpira ndi macheza.
Khuda muyawa sitidzamuiwala ife anoma coz adatichita chipongwe chachikulu
Kochi ndi Afam ndi olakwa kumamusiya Ngwazi Prof Richard Mbulu kukasewera nawo national team
My frend dd u 4 de spots?mesa anawutenga koma anamubwezera komko kamba kosatha mpira an luck of dspln.kkkk kumazitsata man osamangotengera
@Mavuto, ukuyankhula chiyani?wadwala kapena?kapena kupenga?bola chilungamo wachimva.
15 goals
koma kubwela selection ya flame Mr Mbulu ku dropedwa mbuzi za FAM
congratx mbulu
Congrats Mbulu
Big up bro,,proud ov u