The Nkhotakota first grade magistrate court has fined a man for encroaching into Nkhotakota Game Reserve and cultivating cannabis Sativa locally known as Chamba.
According to Nkhotakota Police Public Relations Officer Sub Inspector Williams Kaponda, the man, Bernado Mikayele, 32, has been convicted and ordered to pay a fine of K40, 000 or in default to serve two years imprisonment with hard labour for illegal entry into the game reserve.
He has also been sentenced to pay a fine K200, 000 or in default to serve 6 years in prison for cultivating Chamba.
If he fails to pay the fines Mikayele will go to jail and serve the sentences concurrently.
The convict hails from Kapelura village, Traditional Authority Kapichira in Kasungu.
Zopusa
Kod boma limalimbana ndi chamba chifukwa chani?azilimbana ndi zinazo kom mbali yokhayi ndiy ai xiku lina tizaukura ndithu ngati oxazitenga bwino coz tinatopa nanu a boma mukumva!!!
Achamba ndefdilu ndi kunena pano ndapangakale 500.000 odana ndi chamba ali forkolo farken labch
Achamba ndefdilu ndi kunena pano ndapangakale 500.000 odana ndi chamba ali forkolo farken labch
Rasta man food
sanalakwe chamba ndi game ndipo ndindalama iiiiii kusiyana ndikuba aaaaa!!!! Walakwa chani?
sanalakwe chamba ndi game ndipo ndindalama iiiiii kusiyana ndikuba aaaaa!!!! Walakwa chani?
Chamba ndi deal heavy fodya sakuyambapo let us try season ya mawa alimi a fodya asalimeso 4dya insted alime Ganja ucan see dora zomwe Mw ingapeze bt government kukhomerera……… work up just legaliz it Mulugu sanalengepo chinthu chopanda ntchito. muli chuma mu Chamba bt we cm like we r short sighted
nde chamba chokhachokhacho ine ndalima changa mubwere muzaone Kasungu panoso chidayamba mphonje
May be he want to recoved our economy for the next season kkkkkkkk
May be he want to recoved our economy for the next season kkkkkkkk
nde yake
nde yake
high grade.
hahahahaha so funny why but why MALAWI GOVERNMENT TARGET dem idreans ahh guh plant da seed fi de healing nation ? malawi nuh guh stop yeye water
High grade forever even or you stop it
High grade forever even or you stop it
Penapake inesindimamvesesa kusowa ntchito mkumalowa mnkhalango kumakayang’na olima chamba kodi mikango inali kuti imaleka kukuphani,ndiye mutiwuze chochita ndi judge wanuyo kapena tiziba kuti tizipeza ndalama?

Ndidilu kusuta ganja kupha khawa komaso ndichuma
Ndidilu kusuta ganja kupha khawa komaso ndichuma
chamba chilimidwe bas
Buzzy Fining Jah Pipo Leaving Pipo Wth Murder/corruption/defilement/criminal Cases.Say YES to LIGERIZATION OF MALIJUANA CANNABIS
What f*ck are you arrest this man he jst try the life he want….
What f*ck are you arrest this man he jst try the life he want….
Come and arrest me too, have a 50 hacter ting!… Yall blood_crat popo!!!!!!!
Mbuzi za Mano kusi Inu Mukulephela kuteteza Chuma cha Boma Mukumanga olima Chamba.Nkhota kota nde Sitisiya Apolice mupeza polekela tiwonana ndi Magogodera
Ndunena pano ndili ndi njele zokwana 25kg ndukafesa kamvula kakangowaza…..ndiphe makwachaa nane
Opusa aku court walakwa chani ameneyo
chuma chamalawi chili muthaka ife timadalira ulimi,ndiye tikalima mbeu zathu mukutijataso #shutupit #police

Chaka Chino Inenso Ndilima Muzandimange,ndipoison Kuti Apha Anthu?Mesatimapangira Mavuto,ndimomwe Timapezera Ndalama Komanso Kuparliament Anakambirana Kuti Chiyambe Kulimidwa Ndemukuwagwira Anthuwo Kuti Atani? Ndipo Pamlando Wanji?
I think he was planting trees in game to reserve it why being fined?
I think he was planting trees in game to reserve it why being fined?
mubwere muzandimangenso ine!!
Bora kulima chamba
Kkkkkkkkk
Alakwisa kumumanga becoz chamba ndi dilu kuno ife timangomenya
Cannabis………..kkkkk
achinyamata mbiri tilibe zocita boma likudziwasi za izi.inde xul tidalephela koma 4m 4 lidafika ndipo tsamba ambiri lilipo ndithu zocitazo ndie palibe umphawi. ndie mukuti titukula bwanji miyoyo yanthu o tizingokhala popanda cocita cazeru? bola chambacho pot akadatha kugulitsa ndikupezapo kenakake. fuck all the pipo who arrest and fine him.go to hello coz mmafuna ife tizingotuwa inu mukungoba ndalama zathuso nbomamu pa……….. pan_!!!!!
tizilima
A police ambiri school feed bamboo ako amalima chaba .tamusini muthu wamba akufunanso kulipila school ya ana ake azakhale ngati aja ananwelirs ndinjala chifukwa anakumba okha manda pamseu
Asiyeni anthu azilima Chamba.Ulimi wa fodya ukutha.Ngati kuli kumanga inu aPolice kamangeni anaba ma Tractors,Kamangeni Mcheka Chilenje ndi Chiwaya anaba ndalama zamalendi
Plz reagalize it
This particular judge here has committed a sin & will answer before The JUDGE. His brain need a medical check up. Legalise weed today so I can advertise it.
mukachigwira chambacho mumasutaso ndinu nomwe mkumamanga anthu osalakwa poti mwasuta chambiri.
Kwa ine ndi maluwa
Chamba is not a drug its a plants like Nkhwani,Bonongwe,Mpiru.Munthu adule mtengo wozara yenkha amangidwe eeeeeee ,
Odana ndi chamba ameneyo ndiye ndiwachamba weniweni
Chaka chamawa ndilima changa, I didn’t know kuti it’s big money. Enafe kuba ndikupha ayi; tidzilima whatever can give us cash.
Iyi ndi deal ya boo
mlekeni munthu sanabe koma kulima chamba bwanji inu apolice akumalaw mukufuna muzititapa khamwa bwanji
Jah is Big
Mangani aliese amene wapezeka ndichamba,,,muendeso mmakampumu aliese mukamupeze pa kampu mangani,,,sitikufuna kut anthu apenge kuno amene akufuna kupenga asamuke apite ku USA aadzikasuta mwaufulu kuno tikumangani chabe
Akanapezeka Ndi Ziwalo,kapena Mafupa A Alubino Mukanammanganso Apa Walima Mukummanganso Kkkkk Akabe? Akangokhalanso Muziti Wa Ulesi Hahahaha Nde Mpatseni Chochita Bola Azidya Pakhomo Pake Ndi Ana
NO ZERU #Apolise Mkulemphera Kugwira Ogura Fodya Akubera Alimi Koma Ku Limbana Ndi Anthu Kumudzi Zausirrruu!!!.
Uku ndiye kudya kwathu.
Ma men ndi ma ledies tonse amene timawaza ganja tiyeni tipange ma demo coz apa a boma akutikhomelera fosek
Amangidwe chamba chikupangisa kut anthu mitu yawo isagwile bwin ntchito,ana ambiri asiya sukulu chfukwa cha Chamba
Zoonadi Kuno Wina Adapenga Mwezi Watha, Wa Form 3, Chifukwa Cha Chamba.
Kuthana ndimavuto amendwa ofunika kulimbana ndi amene amalima ndi ogulisa Chamba chamba chisamapezeke
Ku malawi kukhomelerana 3 much cfukwa chake dzko silikutukuka atsogoleri athu amafuna zonse zkhale zao
Uchisilu umenewo mxiew
Uchisilu umenewo mxiew
Muzimanga andale ndi ogwira ntchito mboma aba mabilion ambirimbiriwo osati alimi ambeu yabwino ngati iyi ayi

Zauchitsilu basi…chambacho kodi chinalakwa chani
Zauchitsilu basi…chambacho kodi chinalakwa chani
Zauchitsilu basi…chambacho kodi chinalakwa chani
Let him focus on his buisiness
Let him focus on his buisiness
Let him focus on his buisiness
nosense ife timasuta mukutiphera ufulu.
nosense ife timasuta mukutiphera ufulu.
nosense ife timasuta mukutiphera ufulu.
Mtengo wamdaliso uwu. Plz mmasuleni
Mtengo wamdaliso uwu. Plz mmasuleni
Mtengo wamdaliso uwu. Plz mmasuleni
thanks to see our dailiy meal tree 4 life Amen
thanks to see our dailiy meal tree 4 life Amen
thanks to see our dailiy meal tree 4 life Amen
Anthu mukungowamanga osalakwa apa muwapatsa chakudya chalero inu
Anthu mukungowamanga osalakwa apa muwapatsa chakudya chalero inu
Anthu mukungowamanga osalakwa apa muwapatsa chakudya chalero inu
aletseni osuta ndionse omwe amagula ndupanga ma chemical mkatero anthu azasiya kulima chamba without that mwauponda

uyuyu sanalakwe .mukufuna tidzipha alubino kapena
uyuyu sanalakwe .mukufuna tidzipha alubino kapena
uyuyu sanalakwe .mukufuna tidzipha alubino kapena
Jah creation! Amazing tree
Jah creation! Amazing tree
Jah creation! Amazing tree
Kusowa Zochta Chan? Tamangan Anthu Olakwa Not Ma #WEEDFARMERS, Bwanji Kd Umbuli Makape Inu? #TEAMWEED.

Vuto sindikuliwona apa, he was just trying to plant more trees in the forest
Vuto sindikuliwona apa, he was just trying to plant more trees in the forest
Vuto sindikuliwona apa, he was just trying to plant more trees in the forest
Ka high grade kabwino
Ka high grade kabwino
Boma ili lau siru bwanji
Boma ili lau siru bwanji
Osamumanga Munthu Chifukwa Choti Walima Chamba, Zikhoza Kutheka Inu Mudaphunzira, Makolo Anu Amalimaso Chamba Nkugulitsa Kenako Kukakulipirirani School Fees. Mukumva Bwa?
Osamumanga Munthu Chifukwa Choti Walima Chamba, Zikhoza Kutheka Inu Mudaphunzira, Makolo Anu Amalimaso Chamba Nkugulitsa Kenako Kukakulipirirani School Fees. Mukumva Bwa?
Green stuff but dry. I like it (y)
Mikhobwa tikuibala ife musawamange anthuwa
Mikhobwa tikuibala ife musawamange anthuwa
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.
Tsopano mukufuna tidzitani,tikulima chamba kukana kuba olo kupha ma arbinho,aaaaa mulibe pabwino munthu azilimbikire mukummanganso apa ndiye payelepayele chabadwa chafa sichiopa kuola olo kununkha dziko lopusa ngati ili sindinalionepo
Tell dem man
Pano waliona

Komatu chilimidwe ife mgodi wathu ndiomwewu
Government dem nuh care about we
High grade ikutisowa kuno ku joz imeneyo nde ndikamaiwona chonchi, shaaaaa! maaaaa
High grade ikutisowa kuno ku joz imeneyo nde ndikamaiwona chonchi, shaaaaa! maaaaa
Koma nde mulitu ndi sanje apolice osakama a k577 billion ya cash gate muzamange ine muzaone ndizakuyankhulanu pa public mu court aliyese akuva
Koma nde mulitu ndi sanje apolice osakama a k577 billion ya cash gate muzamange ine muzaone ndizakuyankhulanu pa public mu court aliyese akuva
Koma ichi ndiye changabandetu
Koma ichi ndiye changabandetu
walakwa chan rasta…….
walakwa chan rasta…….
Better to arrest gays, the guy has family to look after.
Better to arrest gays, the guy has family to look after.
Khobolaa !
Khobolaa !
Cha green bwinoto
Cha green bwinoto
Nde Chambacho Achitchetcha??
Nde Chambacho Achitchetcha??
Kkkkk koma kumeneko
Kkkkk koma kumeneko
Chamba nd diil