Nyasa Bullets veteran player Fischer Kondowe has refused to hang up boots saying that his age cannot stop him from playing top level football in the country.
The player who has played for Nyasa Bullets for many years claims he is strong enough to continue playing for the people’s team.
According to Anong’a, supporters should expect more brilliant goals from him and the people’s team at large.
Anong’a, who was recently given the long serving player award by league sponsors , also expressed satisfaction over Bullets’ performances in the 2015 Super League.
He said the team will continue working hard so that they should win more trophies in the upcoming season.
Meanwhile, the league sponsors have also pledged to continue supporting Malawi football.
Nyasa Bullets were previously known as Big Bullets but they changed their name after securing sponsorship from Nyasa Manufacturing Limited.
Amalawi uchtsiru kulimbana tokhatokha mmalo molimbana ndi manigeria akugodzadzana kwathukunoa
MMMM! KAYA MAJELASI NDIYE MWANYA MUSIYENI NDI PLAY WATHU IFE ABB TIMANKONDA KWAMBIRI PLUS YEKA AKUONA KUTI ADAKALIPO!!!!!
Chisankho chabwino Jahman ndi weniweni player and supporter wa Bullets
Anong’a z old enough ,siyilani ana
Apume wayigwira ntchito!
sizampira izi kma nanga akanatani popeza iye sanakwatile ana alibe akasiya mpira azikacheza ndi ndani pa den. Musiyeni bola azicheza ndi maplayer anzake ku ground basi, i am NOMADS FANS
Last yr was 40,this yr 45? zaka zao zikuthamanga
Akatundu omanga ndi mawaya machine let him play
Ndamaliza Kuwerenga Makometi Anu!!! Apakhani yavuta siyopuma mumpira Ayi,koma yokhala ndi ka MWALI.ndiyeno timupephe M’baleyu kuti Abwere Poyera Anene Njira zake zozitetezera ku zachilengedwe chikamusawusa.koma ngati sichimusawusa ndiye Pavuta penapake Apite ku Mens Clinic.koma ngati Chimamusawusa ndiye Akuyenera atiwuze njira zake zomwe Amazisata Monga Anachitira M’thumwi PAULO Woyera waku Akorinto.
Eeeeh koma Jahman mumalimbana naye
Zovuta
Amene Safuna Kuona Kumva Za Jahman Mu Mpira Wa Ku malawi Muli Ndi Mwai Osankha Masewera Ena Osata. Kodi Munamuuza Ndinu Kuti Ayambe Kumenya Mpira?
Jah man ali bho Ryan Giggs retired at 43 so y not him Bravo Anong’a i salute u
Jah man ali bho Ryan Giggs retired at 43 so y not him Bravo Anong’a i salute u
When did Paul Scores retired, Gatuso,Sibusiso Zuma,Nomvete,pliz I leave him alone.
When did Paul Scores retired, Gatuso,Sibusiso Zuma,Nomvete,pliz I leave him alone.
When did Paul Scores retired, Gatuso,Sibusiso Zuma,Nomvete,pliz I leave him alone.
Akufuna new salaries
Akufuna new salaries
Akufuna new salaries
Akufuna new salaries
Akufuna new salaries
Chenjezo: “kusuta kumaononga kumoyo”.
am a nyasa Bullets fan continuing playing doesnt matter bt my concern is at that age bwedzi pano tikumva kt ja man junior akubvuta ku BB youth bt nothing at 45 what is wrong may be he needs civic education so that he shld knw important of ana.Atenge ntchito zake za ground akapanga retire ndindani plz dont be selfish
Onse alibe ana mu dziko muno, sakalowa kumwamba?.
Onse alibe ana mu dziko muno, sakalowa kumwamba?.
Onse alibe ana mu dziko muno, sakalowa kumwamba?.
Onse alibe ana mu dziko muno, sakalowa kumwamba?.
Onse alibe ana mu dziko muno, sakalowa kumwamba?.
Hiz age doesn’t matter, what wr want iz bola akuchita bwino mu ground ife a Nyasa Bullets mkumamwa mkaka basi
What i know football has no age limit provided you are playing well,so let Fisher play until he say he tired in football.
gents let’s be civilised on this am afun of nyelele but age is nothing as long as he is able & marrying is person choice when u feel like. more fire jah man
akufuna adzafere mu ground adzampase u Hero. wosawasiyira anyamata achisozera atenge malo anuwo bwanji. Nga nga nga ngati John Tembo
Wachambatu uyu anamala ganja
Shaa!!!kkkkkkkk.
Mulungu polenga anthu awili adali ndi colinga ndiye e e e kutheka mwina ali ndikamvuto kenakake munthupi lake anene anthu amuthandize chuma cimakoma ukamadya ndi ana ndiye anong’a mwanyanya kwambiri ndine wa nyelele
Ine Paul Mpandason Ndikut Jahman Mafuta Mu Tank Akadalimo Pitiliza
Akufuna akwatire mpira womwewu popeza kufunsira kumamuvuta
apanga chani akasiya izi munthuyu.azingobandatu.sos yopezera dolla ndiyomwdyi
Komadi atani musiyeni apanga history
Musiyeni jahman apitilize kodi akasiya mpira mumulemba vep ? Chifukwa umu ndiye modyera mwawo more fire opples team
amene mukuti akwatile inu mmesa amayi anu ndi bambo anu ukwati unatha ndiye mumuwuze jah man akwatire amayi anuwo
amene mukuti akwatile inu mmesa amayi anu ndi bambo anu ukwati unatha ndiye mumuwuze jah man akwatire amayi anuwo
Jarman apitilize kusewera mpira
INE NDIWA NOMA KOMA NA FISHER AMATIVUTA KWAMBIRI PA GROUND KOMA ALI NDI UFULU TISAMPANGIRE ZOCHITA YANJIRU SIMASWA
Auze jahman asakupangile zochita
Amatha i like the guy,he is so special
Kk. Jahman
msien azafera mground ameneyu
ZIKUTIPEZA TITAKALAMBA
ZIKUTIPEZA TITAKALAMBA
mpatseni azimanu awakwatile simukufuna akwatile
mpatseni azimanu awakwatile simukufuna akwatile
Kapumeni.Miyendo imeneyo yauma.Simunamange nyumba kapena?
Kapumeni.Miyendo imeneyo yauma.Simunamange nyumba kapena?
Am nomads fan but Jahman has right to continue playing & to marry or not long live Jahman & 2 more year in field of play Jah bless ine wa nyerere
Am nomads fan but Jahman has right to continue playing & to marry or not long live Jahman & 2 more year in field of play Jah bless ine wa nyerere
kkkkk amakakamizana kukwatirako nkaziyo muzimudyesa inuyo muziwa bwanji mwina iye amapulumukira kammanja ena amati kubunyula kkkk musiyeni akatenganso matenda muzimunena kuti ntchito zamuchitira umboni zonyenganyenga munthu alibe pabwino ine sindinakwatire zaka 54 bwa
Kkkkk madolo
kubunyula too much
kubunyula too much
Gear up jah man
Enanu mukuopa kuti akapitiliza kusewela muvutikanae
Kodi ma friendlies bwanji Maule?
Pamoyo wa munthu aliyese amakhala ndi chisankho chake malingana ndimomwe ukuganizila. Chocho tonsefe sitimaganiza mofanana..Ndikutha kuona anthu akulowa m’banja ali ndi Zaka 45…ndiye palibe amene angamupagire zoti akwatire ichi ndi Chisankho chake basi.Wenanu munakwatila koma mukukanika kusamala Mabanja anu mukungomuzuza mkazi.Zikusiyana bwanji ndi Kusakwatila????
Nkhani sikuti akasiya adya chani ayi,Fischer zake zinayela kale komanso mpilawo amaukonda komanso amatha.
Ubwino wake zakazo ndi nambala ndiye palibe vuto olo mukanati 70 pitilizani madala mutimwetseso mkaka chaka chino
Big up Rasta!
Koma zake zikuyenda
Alibe kolowera uyaaaaaaaa
Matatizo kkkkkkkk
wakalamba jahman akwatire
Kkkkkkkkkk koma sakwatirayu atisautsa zedi.
nkhalamba za chingabwe bullets FC kkkk
generally,but he suppose to marry koz his stuff is growing old now.
Mulungu sakalanga munthu coz sanakwatle iwe wakuvuta ndumbuli wamva kumango ganiza zaukwatla bas kma akhafili ndemukhaula ndiya nkhalamba njoma wamva sungununu
ineyo nd mbuli kma iweo nd mbuli mapeto
kkkkkkkkkkk Aaaaaaa!!! Stuff ikukalamba???kkkkkkk ndiye iti imeneyo.
kkkkkkk,ndyonvutilapo kuinena.#THOXY
He continue to play not becoz he like bt akakhala pasi adya chani ku malawi kwathu kuno
achimwene fischer ndiolemela simungafananize ndiplayer wina aliyense mmalawimuno ndipo olo atasiya lero apeza udindo onona muexecutive
achimwene fischer ndiolemela simungafananize ndiplayer wina aliyense mmalawimuno ndipo olo atasiya lero apeza udindo onona muexecutive
then why is he still playing in his granny age
Kufuna. Chisankho chake basi.
Kufuna. Chisankho chake basi.
Kufuna. Chisankho chake basi.
Kufuna. Chisankho chake basi.
Kufuna. Chisankho chake basi.
tell me exactly what fischer has tht can define him as a wealth player in malawi

Inu ndiolira kwambiri
Inu ndiolira kwambiri
Inu ndiolira kwambiri
Inu ndiolira kwambiri
Inu ndiolira kwambiri
Does he own any company or estate in malawi?, what is its name? what is his salary tht makes him a top player? I dont hate fischer his is one of my favourite players. Palibe akulemera ndi mpila ku malawi kuno infact thats what i was trying to drive at. Komano you are misinterpleting my point. Anyway, you win fischer is a millionare

Only in Malawi grandfathers are still playing football chfukwa kulibe achinyamata ena oti mkutenga malo awo, in Europe players kufka zaka 36 -38 wakula koma ku Malawi at 45 no purobulem
kkkkkkkkkk koma ang’ona kaya mukuti anong’a azafenta mu ground amenewa
Mungofuna kukafela mu ground
Keep on strong jahman
Mwini wake anati chilapondwa wapuma inde,,,koma iyeyo pasapezeke omfusa kuti asiya liti kkkkkkk
Kodi akumenya kuti amenewa pano?
big vomelezani tchito mwagwira
Brave
Makina
Makina amwene
more fire anong’a wakalamba wafuna
Tikadali kumukondah!
True
he’s gat the energy