Fischer will not hang up boots

Advertisement
Fischer Kondowe
Fischer Kondowe
Fischer Kondowe: Am not retiring.

Nyasa Bullets veteran player Fischer Kondowe has refused to hang up boots saying that his age cannot stop him from playing top level football in the country.

The player who has played for Nyasa Bullets for many years claims he is strong enough to continue playing for the people’s team.

According to Anong’a, supporters should expect more brilliant goals from him and the people’s team at large.

Anong’a, who was recently given the long serving player award by league sponsors , also expressed satisfaction over Bullets’ performances in the 2015 Super League.

He said the team will continue working hard so that they should win more trophies in the upcoming season.

Meanwhile, the league sponsors  have also pledged to continue supporting Malawi football.

Nyasa Bullets were previously known as Big Bullets but they changed their name after securing sponsorship from Nyasa Manufacturing Limited.

Advertisement

114 Comments

 1. MMMM! KAYA MAJELASI NDIYE MWANYA MUSIYENI NDI PLAY WATHU IFE ABB TIMANKONDA KWAMBIRI PLUS YEKA AKUONA KUTI ADAKALIPO!!!!!

 2. sizampira izi kma nanga akanatani popeza iye sanakwatile ana alibe akasiya mpira azikacheza ndi ndani pa den. Musiyeni bola azicheza ndi maplayer anzake ku ground basi, i am NOMADS FANS

 3. Ndamaliza Kuwerenga Makometi Anu!!! Apakhani yavuta siyopuma mumpira Ayi,koma yokhala ndi ka MWALI.ndiyeno timupephe M’baleyu kuti Abwere Poyera Anene Njira zake zozitetezera ku zachilengedwe chikamusawusa.koma ngati sichimusawusa ndiye Pavuta penapake Apite ku Mens Clinic.koma ngati Chimamusawusa ndiye Akuyenera atiwuze njira zake zomwe Amazisata Monga Anachitira M’thumwi PAULO Woyera waku Akorinto.

 4. Amene Safuna Kuona Kumva Za Jahman Mu Mpira Wa Ku malawi Muli Ndi Mwai Osankha Masewera Ena Osata. Kodi Munamuuza Ndinu Kuti Ayambe Kumenya Mpira?

 5. am a nyasa Bullets fan continuing playing doesnt matter bt my concern is at that age bwedzi pano tikumva kt ja man junior akubvuta ku BB youth bt nothing at 45 what is wrong may be he needs civic education so that he shld knw important of ana.Atenge ntchito zake za ground akapanga retire ndindani plz dont be selfish

 6. gents let’s be civilised on this am afun of nyelele but age is nothing as long as he is able & marrying is person choice when u feel like. more fire jah man

 7. Mulungu polenga anthu awili adali ndi colinga ndiye e e e kutheka mwina ali ndikamvuto kenakake munthupi lake anene anthu amuthandize chuma cimakoma ukamadya ndi ana ndiye anong’a mwanyanya kwambiri ndine wa nyelele

 8. Akufuna akwatire mpira womwewu popeza kufunsira kumamuvuta

 9. INE NDIWA NOMA KOMA NA FISHER AMATIVUTA KWAMBIRI PA GROUND KOMA ALI NDI UFULU TISAMPANGIRE ZOCHITA YANJIRU SIMASWA

 10. Am nomads fan but Jahman has right to continue playing & to marry or not long live Jahman & 2 more year in field of play Jah bless ine wa nyerere

 11. Am nomads fan but Jahman has right to continue playing & to marry or not long live Jahman & 2 more year in field of play Jah bless ine wa nyerere

 12. kkkkk amakakamizana kukwatirako nkaziyo muzimudyesa inuyo muziwa bwanji mwina iye amapulumukira kammanja ena amati kubunyula kkkk musiyeni akatenganso matenda muzimunena kuti ntchito zamuchitira umboni zonyenganyenga munthu alibe pabwino ine sindinakwatire zaka 54 bwa

 13. Pamoyo wa munthu aliyese amakhala ndi chisankho chake malingana ndimomwe ukuganizila. Chocho tonsefe sitimaganiza mofanana..Ndikutha kuona anthu akulowa m’banja ali ndi Zaka 45…ndiye palibe amene angamupagire zoti akwatire ichi ndi Chisankho chake basi.Wenanu munakwatila koma mukukanika kusamala Mabanja anu mukungomuzuza mkazi.Zikusiyana bwanji ndi Kusakwatila????

 14. Ubwino wake zakazo ndi nambala ndiye palibe vuto olo mukanati 70 pitilizani madala mutimwetseso mkaka chaka chino

  1. Mulungu sakalanga munthu coz sanakwatle iwe wakuvuta ndumbuli wamva kumango ganiza zaukwatla bas kma akhafili ndemukhaula ndiya nkhalamba njoma wamva sungununu

  1. achimwene fischer ndiolemela simungafananize ndiplayer wina aliyense mmalawimuno ndipo olo atasiya lero apeza udindo onona muexecutive

  2. achimwene fischer ndiolemela simungafananize ndiplayer wina aliyense mmalawimuno ndipo olo atasiya lero apeza udindo onona muexecutive

  3. Does he own any company or estate in malawi?, what is its name? what is his salary tht makes him a top player? I dont hate fischer his is one of my favourite players. Palibe akulemera ndi mpila ku malawi kuno infact thats what i was trying to drive at. Komano you are misinterpleting my point. Anyway, you win fischer is a millionare

  4. Does he own any company or estate in malawi?, what is its name? what is his salary tht makes him a top player? I dont hate fischer his is one of my favourite players. Palibe akulemera ndi mpila ku malawi kuno infact thats what i was trying to drive at. Komano you are misinterpleting my point. Anyway, you win fischer is a millionare

 15. Only in Malawi grandfathers are still playing football chfukwa kulibe achinyamata ena oti mkutenga malo awo, in Europe players kufka zaka 36 -38 wakula koma ku Malawi at 45 no purobulem

Comments are closed.