Nsanzurwimo Ramadhan

Ramadhani wazidomoka

Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Mukuru wanderers Nsazurwimo  Ramadhani wazisiya, watula pansi undindo wake  patangotha myezi yosaposa inayi chibweleleni ku timuyi. Mphunzitsiyu yemwe watsogolera masewelo asanu ndi atatu okha (8) watula pansi udindo wake… ...