Police in Blantyre on Sunday evening arrested a 39 year old man for cutting down an electricity pole.
According to Blantyre police publicist Augustus Nkhwazi, the suspect Focus Billiati who is a resident of Manase township in Blantyre, at around 7pm, was found felling the Electricity Supply Corporation of Malawi ( Escom) pole at Sunny Side in the city.
Sub Inspector Nkhwazi said well wishers tipped the Police about the incident and the law enforcers rushed to the scene.
When the Police arrived at the scene, Billiati whose accomplice managed to escape was found with a bow-saw and panga knife which the two were using to cut the pole.
He was later taken to police where he is being held.
He is expected to appear before court soon to answer charges of tampering with electricity apparatus (pole) contrary to section 45 as read with section 46 of the Electricity Act.
Focus Billiat hails from Ndelemasi village in the area of Traditional Authority (TA) Mabuka in Mulanje district.
paja alomwe!!!!!!!!!!!!!!!!
Alipitsidwe ma pole asanu chifukwa wachita zinthu akudziwa kuti mtengo wa magetsi ndi wofunika.
Alibe mlandu ameneyo Escom idatha kale
Kkkkkkkkkkkkk always blackout kkkk
With no electricity he thought it was just a wood
Mutayeni ndiosalakwa moreover Magesi kulibe ka
ngati chiwalo chake chikumuchimwitsa kulibwino kuchidula basi
Wat ‘kungochidura’ Kkkkk Koma Nde Yake.
mtengo osabala zipatso kuudula basi ulibe ntcho.what is use of having poles standing when they are not doing their job.release that man now he is of no sin
Chamba mukusutacho sichabwino bwana.
Pezani zochita zina basi
Kikiki watopa nazo zima loadsheddings. Mwina amafuna akapangire makala
Zinazi nde zoziyambd dala
Lomwes’ behavior, strange……..
Olo ndikadakhala ine ndikadawaza kumene ndikhuphikira.
Ma pole sakufunikanso kumalawi magetsi ake ali kut?zachamba eti!!! Kudula zimenezo basi
Dulani zimenezo sizikugwra ntchito pano kkkkkkkkkkkkk
Anamwa midoli yayambikai,Ukaziona kundende konko.
Ndiwamisala munthu ameneyu amuwone bwino
Achakwera akuti ameneyu anatumidwa ndi DPP
Even Mchere in smouldering charcoal he was angry over the rat which was responsible for troubles in his family,,same the man Hes angry with Escom vicevesa
Iv remembered those early dayz at senkhwa… achna ntolo osayiwalanso nambe…
Hahahaha……really bruh people are mad and angry with ths govt
Kkkkkk maluzi!!!!!
anaona kuti sichikugwira ntchito sinanga magetsi sakuyaka inu mumati atani munthu
He was cutting for what…..?
kupangira nkhuni kkkk
Mbuzi ya munthu, kudana ndi chitukuko
Pano nthambo ndiyimoz ya geniset mapole sakugwira ntchito
uku ndie kuziputa! magets akuvuta ndie wna mkumapanga izi? aziwona! kaya ndi fodya,athera ku jere.
Kkkk Sinanga simunauuze pamene mwayika magetsi ama generator ma Pole azigwilabe ntchito
Wausilu ameneyo