An Axa bus was today involved in a terrible accident at Zalewa in Blantyre today.
It is reported the bus had Kamuzu Academy students on board.
Thus far, unconfirmed reports say one person has died.
We have more to come.
An Axa bus was today involved in a terrible accident at Zalewa in Blantyre today.
It is reported the bus had Kamuzu Academy students on board.
Thus far, unconfirmed reports say one person has died.
We have more to come.
Comments are closed.
Copyright © 2024 | Malawi 24 - Latest News from Malawi and Around the World
Sory wish you a quick recoverly
But seems to be a bus we only talk of a single person? Not even the one who was driving
IT’s time guys
Ambuye tioneni sitikulamula ayi koma tagwada pamasopanu
Whyyyy
Atate mu dzina la mwana wanu yesu tikudza kwa inu mogonja ndi mozichepetsa,musalifulatire dziko lathuli chonde tichotseleni mphanvu za kumidima zimene zakhazikika! Tumizani a Mngelo anu akerubi ,Gabriel aka the kutiteteza ife ana any tathodwa!
Shaaa Malawi watani keep kodii
Pakufunika mapephero apadela ngozi zanyanya eshiiiii
Shaaa God have mercy on us!!!!
Eish why God alwayz Malawi ??
Sukunama Ziezwa chirwa usatanic is ruling pa Malawi
Consider only three things when a traffic accident occurs; Road conditions, vehicle condition and vehicle control by the driver!!! One or a combination of the three could result in an accident. Stop blaming unknown things (like satanism) for our own carelessness and mistakes.
I advise everybody to pray before,during and after the journey to conqur the demonic accidents
Usatana wavuta pa Malawi
SOO SORRY
oh god help those victoms
No much about happieness
Oooh my God
koma mwapuluka anthu umu ?
Tiyen tizingovomereza zikamachitika ndimthawi yake chachikulu tizongopemphera bas kut nyengo zimenez mulungu atichotsere ovulala onse tikuwaikiza kwamulungu kut awapase machiliso mokwanira
They want to pass pa bridge 140km /h. .mw drivers
akut ndnaponda latalata!!! these drivers I don’t know which kind of driving did they go to learn latalata on a bridge
Kkk..ali ndi B class ameneo
The problem its not about the roads of malawi neither the vehicles clashing but stanic attacks..many claiming to be men of God are the ones who surrendered themselves to illuminat..ambiri akulemera ndi magazi a amalawi osalakwa, amane mumati wa mkulu wa ma prophet ndi wamkuluso kumidimako,thats why simudzamva akukamba zokhudza ngozi or rebuking the spirit of accident because a devil cannot cast another devil..
That’s true
These buses fly they really drive like mad wen l visited Malawi took this bus to Mzuzu yooh was just praying too much speed I am not surprised get well soon victims
So bad
Very sad but zalewa os bad road in this country
Bad hey
Just next to my house eiish
I hope the kids are ok.
Zalewa isn’t in Blantyre,it has never been and I believe it will never be.zalewa is in Neno district
SAD
Enanu kaya mukana koma dziwani kuti atsogoleri tili naowa akulora ziri zonse kudza dziko mwanu kamba ka dyera la ndalama,mukulowa anthu adzithandiza osadziwa kuti phindu lawo mlotani,ndiangati amene akupanga izo amene ali ndi mbiri yabwino munzochita zawo? Chachiwiri ma Pastor anthu amene tili nao si ake aMulungu,akupanga zinthu mumdzina la Mulungu koma siali ake a Mulungu,mwina nkumadabwa chuma chawo chonse ali nacho kuti amapatsidwa kuti kapena chopereka cha Sunday chingafike ku ma 10million dollars????? Mupaonetu apo iwo akudya ndalama zochita zizichitika M’malawimo, Evison Matafali,anati,ufulu si nsimatu,chenjera posaka iwe malawi,nyama yako ikhoza kukhala nyambo. Malawiiiii,Malawiii iiiiiiiihh
Gloria Munthali…..I’ll miss you may your soul rest in peace …..
Jx to comment on the like button. Sikutizawasangslatsa but they would like to follow the developments through ur posts the news it’s incomplete. Malawians please let’s learn to be humble.
Eti mziwiseni thandauzo la like
“An AXA bus was TODAY involved in a terrible accident at Zalewa in Blantyre TODAY”
A traffik salimbana ndi ma bus koma ma minbus basi.shame!!.
Thats sad may God be with the families of the student in this diffigult tome
am seeing some are pressing the like button nd am wondering
Dpp Tikhululukiren Mwamwako Magazi Aanthu Akwana,izitu Zodabwisa
Try to buy new buses and construct good road’s those buses too old pa msewu #dpp be serious with people.
gud roads doesnt mean anythng lets put GOD of all mighty to be de first than anythng then we wil never suffer
Kuganiza kopusa uchitsiru these buses r new mumakhalakuti osamayankhula zinthu zene simukudziwa kulibwino mukhalechete kupusa
Ngozi ndi ngozi. Olo ikhale galimoto ya new one,msewu wabwino,zimachitika. America ili ndi the best roads but people are dying in road accidents day in day out. Osamaledzera ndi ndale pliz.
iwe be serious. ngozi ndi ngozi amwene. yo point has indicated the level of your stupidity. shame on you.
but some ngoZi can be reduced through good roads infrastructure though its unexpected thing,,, dont just oppose cause you want to say something…..misewu siyabwino
Those buses are not old…do ur research well. And u sayin the road is in a bad shape? I wonder if u travel man
Iweyo ngat concerned citizen osamanga miseu yabwinoyo bwa??
Chilichonse kumangolowetsapo ndale basi. Umbuli?
iweyo jojo osamanga bwanji ngati good citizen?
ndale ndingozi kikkkk koma
That’s bad
very bad
Too bad
Ma bus amenewa anatha
I thk ndi ma guys amapopa magazi aja angosintha system ….so sad everydae Helps us God…
AMBUYE NGAT ZILI MPHULUPULU ZATHU TIKHULULUKIREN!!!
Xorry very bad!!!!..get well soon cctrs ….
GET WELL SOON!
ah..just an accident,you dont know how many lost their lives,how many injured and what caused an accident? dont be fast in publishing please
Information has to be posted for people to get updated! U can’t get all the info from one source, as it is happening updates will fly in. This is not wrong it’s called breaking news
u whare expecting to hear how many died??
Atleast we know about an accident we hav been updated
Guess ur really lucifer’s son…..heal in the name of the almighty God
Guess ur really lucifer’s son…..heal in the name of the almighty God
kakaka
Satana uyu
akufuna kuwelengela mitembo mzanu kkkkkk
kikkk
Koma dziko likupitadi kumapeto eti?? Smh
Shaaaaa
I pray in the name of Jesus the son of living God ! the evil spirits must stop now to our country
Amen
Kodi ma Admin mulipo angati kumango poster mkhani imodzi since morning koma ma results njeee tili now why my Malawian madias akanakhala a BBC news bwezi atatiuza kale anthu ovulara + omwalira zachamba izi damn
All the children have survived the hostess Munthali died
Alemekezeke Yehova
that’s good to hear that Thanks Heaven & all who living There
R.I.P to all who dies
Koma too much mayn.. everyday eish
hw many died? very bad
The hostess Gloria Munthali
Ndipo sindikuziwa abale mulongo wanga junior lunjikani chirwa
Wamwalira mmodzi
Shaa! Komansotu ma bus awa ndosalimba eti? Kuphwanyika choncho ngati chitini aaah!!!
5 hours ago.
Koma abale malawi ai sizikuchita bwino tidzingomva ngozi dily.
How many died??
Kwamwarila Anthu Angati?
Mmodzi at the mean time,Gloria Munthali the hostess the children have survived
Sizinakhale bwino kwa oonse ovulala tingoti pepani kwambili kukufunilani kuchila kwa mnsanga. koma ikanangokhala minibus eeee eeeee, mmmhu kaya zikanatha bwanji khaya pano ilipokopoko.
sad,koma ma guys a malawi24 mumalemba zingini mochedwa
amadikira ena apange post iwo kuzitenga kukupatsani
Mmmm whyyyyyy this mmm eish word is coming to an end sure
so sad