Kamuzu Academy students in a terrible accident

An Axa bus was today involved in a terrible accident at Zalewa in Blantyre today.

It is reported the bus had Kamuzu Academy students on board.

Thus far, unconfirmed reports say one person has died.

We have more to come.

Advertisement

95 Comments

 1. Atate mu dzina la mwana wanu yesu tikudza kwa inu mogonja ndi mozichepetsa,musalifulatire dziko lathuli chonde tichotseleni mphanvu za kumidima zimene zakhazikika! Tumizani a Mngelo anu akerubi ,Gabriel aka the kutiteteza ife ana any tathodwa!

 2. Consider only three things when a traffic accident occurs; Road conditions, vehicle condition and vehicle control by the driver!!! One or a combination of the three could result in an accident. Stop blaming unknown things (like satanism) for our own carelessness and mistakes.

 3. Tiyen tizingovomereza zikamachitika ndimthawi yake chachikulu tizongopemphera bas kut nyengo zimenez mulungu atichotsere ovulala onse tikuwaikiza kwamulungu kut awapase machiliso mokwanira

 4. The problem its not about the roads of malawi neither the vehicles clashing but stanic attacks..many claiming to be men of God are the ones who surrendered themselves to illuminat..ambiri akulemera ndi magazi a amalawi osalakwa, amane mumati wa mkulu wa ma prophet ndi wamkuluso kumidimako,thats why simudzamva akukamba zokhudza ngozi or rebuking the spirit of accident because a devil cannot cast another devil..

 5. These buses fly they really drive like mad wen l visited Malawi took this bus to Mzuzu yooh was just praying too much speed I am not surprised get well soon victims

 6. Enanu kaya mukana koma dziwani kuti atsogoleri tili naowa akulora ziri zonse kudza dziko mwanu kamba ka dyera la ndalama,mukulowa anthu adzithandiza osadziwa kuti phindu lawo mlotani,ndiangati amene akupanga izo amene ali ndi mbiri yabwino munzochita zawo? Chachiwiri ma Pastor anthu amene tili nao si ake aMulungu,akupanga zinthu mumdzina la Mulungu koma siali ake a Mulungu,mwina nkumadabwa chuma chawo chonse ali nacho kuti amapatsidwa kuti kapena chopereka cha Sunday chingafike ku ma 10million dollars????? Mupaonetu apo iwo akudya ndalama zochita zizichitika M’malawimo, Evison Matafali,anati,ufulu si nsimatu,chenjera posaka iwe malawi,nyama yako ikhoza kukhala nyambo. Malawiiiii,Malawiii iiiiiiiihh

 7. Gloria Munthali…..I’ll miss you may your soul rest in peace …..

 8. Jx to comment on the like button. Sikutizawasangslatsa but they would like to follow the developments through ur posts the news it’s incomplete. Malawians please let’s learn to be humble.

  1. Kuganiza kopusa uchitsiru these buses r new mumakhalakuti osamayankhula zinthu zene simukudziwa kulibwino mukhalechete kupusa

  2. Ngozi ndi ngozi. Olo ikhale galimoto ya new one,msewu wabwino,zimachitika. America ili ndi the best roads but people are dying in road accidents day in day out. Osamaledzera ndi ndale pliz.

  3. but some ngoZi can be reduced through good roads infrastructure though its unexpected thing,,, dont just oppose cause you want to say something…..misewu siyabwino

 9. ah..just an accident,you dont know how many lost their lives,how many injured and what caused an accident? dont be fast in publishing please

  1. Information has to be posted for people to get updated! U can’t get all the info from one source, as it is happening updates will fly in. This is not wrong it’s called breaking news

 10. Kodi ma Admin mulipo angati kumango poster mkhani imodzi since morning koma ma results njeee tili now why my Malawian madias akanakhala a BBC news bwezi atatiuza kale anthu ovulara + omwalira zachamba izi damn

 11. Sizinakhale bwino kwa oonse ovulala tingoti pepani kwambili kukufunilani kuchila kwa mnsanga. koma ikanangokhala minibus eeee eeeee, mmmhu kaya zikanatha bwanji khaya pano ilipokopoko.

Comments are closed.