Thieves have stolen cables at a transformer in Zolozolo location in Mzuzu.
The incident happened on Sunday night.
According to nearby residents, they saw two vehicles and people in Escom uniforms at the transformer on the night.
“It was around midnight when we saw two vehicles with people in uniforms, we thought they are Escom officials who come and give us power since the area had no electricity, but surprisingly there was no electricity till morning when we discovered that some things are missing at the transformer,” he said.
Escom officials failed to comment saying the matter is in police hands for investigation.
People are taking advantage of load shedding to vandalize transformers and steal cables.
Two years ago, thieves also stole some copper cables at the same transformer forcing residents to have no power for almost two weeks.
Kkkkkk koma
I think it was easy ,cause it had no power on the cables
Kkkkkkk finish up kkkkk
Which cables?you might be joking!kkkkkkkk. For solar Escort?Escom moved long time back to Mozambique
Galimotonso kuwabera
Ahahahah ok…zikanakhala za ntchito sizikanabedwa
Nanga mesa mulibemo moto nde nanga nza cha??
Keep the city clean,well done thieves.kkkkk osamasunga zinthu zomwe sizimagwira ntchito.
OKUBAWO NAWO ALI PA FB CHONDE MUKAIONA COMMENT MUPITENSO KU MKULA FALLS MUKABE ZOMWE KUNGAKWANISE KUBA ,IFE ZATIKWANA ZOMWE AKUPANGA ANYANI AMENEWA ,
kkkkkk koma nde action yabhotu.
Kufunika kwberanso mapolo ndi ma wire basi tatopa nazo. Ma powerbank alowe m’bwalo.
koma kodi kumalawinso kuli escom??? kkkkkk
Vima black out mulengesesa navu My MALAWI lekaso ayamba kukubiyani vipangizo asani monsi mwa EDUCATION chalucho chakutodani kwendesa andipaseni ine ndamthu wabura school ndeyedesepu waka 2 years muwonivo wadichitiyege YESU pawutsongolere wangu nokubayana nochimoloko noblack out love One another like JESUS
achitabwino mwina zikagwire mtchito zixingokhala
Thanks
nde yake ngat mukufuna nuzyatsa kut aziopa shoko iban dzmenedzo mahanger
Mwina zingakagwireko ntchito, mesa zikungokhala.
Kkkkkkkkk…what a gud news !!!!!
no security,if i was there i would hv been joined….
Good job mukabenso ku mkula
kkkkkkk zibedwe basi, mlandu palibe apa ,blantyre ,lilongwe ndi zomba, wake up
U must also remove these poles and use them for fire wood, we don’t have electricity in malawi!
Weldone
I think most of Malawian we are educated savages why comenting well done , good Job to criminals?. Whose tax has been stoled ? When Escom will be purchasing other cable which where do you thing it will come from? Learn to be patriotic and love your country .i cry for my country
inu ndie abwino?
cable wamagetsi washock uja kubedwa? nde kut samagwira ntchito bwenzi atafa amabayo
kukhala nazo kapena ayi ndichimodzimodzi no electricity in Malawi
Kunoso taba
Abe zopanda ntchito
Zikutheka bwanji anthu kumasula transform yamagesi kodi magesi kulibe
Eeeee nanga angobaso malawi yenseyi sitiwulula ayi
Mhu amalawi ndife anthu onvetsa chisoni koma!
Congrats to the thieves!!!!
Kkkkkkkk
Better
choncho magetsi akamavuta aziti boma??
Mmmm,,,,not stealing but “taking.”In fact,they r of no public use.Had t bn dat they r of any use,hopefully there couldn’t b blak-outs!! Thumbs up Mzuzu men!!
A Chitabwino or mapoloxo azigwetsa chifukwa tinalimba mtima opanda magetsi tazolowera
Achita bwino nzachaniso rather use it mnjila ina yochangu make quick cash
Achita bwino nzachaniso rather use it mnjila ina yochangu make quick cash
Mmmm otumidwa inu
Zisiru inu anthu obwezeresa chitukuko mmbuyo mnaba ndinu? Ife timavutika ndi mdima anamaliwongwe inu bwanji azakubereni inu kunyumba kwanu ,osati zonse mzitengera ntabwara
Job well done, thumbs up ma boyz, kip on hassles mpaka tiphana nawo
Good use of resources,bravo thieves
Mundibwereke makwerero aatali bwino ndigwire ntchito imeneyi basi ndipo mudzindiuza kofunika kukaba ko koma mukandiona ndikuba osakuwa
Kwasala kungoba abwana aku escom
Akubawo aziba mmene akufunila kuti a escom azipsa mtima More fire criminals u are Malawian not only for escom
achita bwino aba mwina ndalama zamisonkho yathuyo mkumagwira ntchito yoyenerera kumagula ma cable ena kusiyana ndikuti zidzingolowa mmatumba awo abomawo
Chifukwa chopanda moto anthu akuzipezelelano
sanalakwe chifukwa palibenso chodzisungila
Mmmmmm mwztero inu kkkkkkk
kkkkkkkkķkkkkk nice
Awope chani ngati mmacablemo muli moto..
Eish poor Malawi
Malawi muno umbava oba mafuta atransformer adathadi ,zoona magetsi sakuyaka osatsitsa bwanji dzimatrasfomer dzi
Ndipaseni nambala zawo kwachisapo so dzilipo dzamagetsi dzikungokhala olo kuzula transformer sungapse mulibe moto
Aba chamagetsi ,oti magetsi akuyaka
Nawonso kungoba ma cable okha?ine ndikanaba ndi tranfomer yomweyo,ndakwiya nao anyamata amenewa
Ubwinowake aba zithu zopanda ntchito.
Typing………………………………………….
Hahahahaha koma abale
Sanabe koma atenga…ndizinthu zopanda ntchito
aba zimakebo zotha ntchito,anyamata inu,mubenso ma galimoto a ESCOM,
That’s gud asala mapolo titenganso jst wait we hate nonsense
Well done guys
Yaa because they know its alwez off !
ZODABWITSA NYESI ILIKUTI LOVE OUR COUNTRY
Musaanamizile anthuwo Sanabe, angotola zot zidasiya kugwira ntchito
Escom munali kale
SEE ABOVE
The hub of criminal activities called Zolozolo township.
Ine ndikufuna mafuta atransformer. Or 300lts ndigula
BT,LL,Zomba and other area please wake up steal more cables of ESCOM so that they must have real excuse for black out
GOOD NEWS
They must steal more cables please
Achita bwino paja kundende masiku ano ndi ku Gelli zowopa kundende ndizakale!!! keep it up! kundende masiku ano ndi konjoyetsa malamulo anakalamba.
Is Escom Stil Existing,,?
ma cable okha bas ? ameneo ndithu abwerexo
KKKKKK THUS BETTER..
Anatumidwa ndi a opposition amenewo
mutengeso transformer,coz the ESCOM z mis using the resources
Angaleke kuba magetsi ake apinyolowa oyaka 6 18 black in ha
Anatumidwa ndi a opposition amenewo
Good Idea! Dats Wat We Need For De Sereous Cetzens Nt Escomshit, Let Dem Come Here 2continue Deir Tramendas Work. Proud Of U Thivies
Achita bwino paja kundende masiku ano ndi ku Gelli zowopa kundende ndizakale!!! keep it up! kundende masiku ano ndi konjoyetsa malamulo anakalamba.
Kkkkkkkkk
Since there no electricity their is no use.sell them to scrap yard.people from north they don’t deserve electricity.
keep it up
Hahahaha!! I was revisit all the comments posted here but No one is behind Escom so I don’t think Police will take any action! rather than support these thieves!!
atumbuka kupusa..
guys osaululana…
they are jst taking them away coz they are not working anymore. Its better to throw them away. Wats the use of keeping them?
Kusazgilako masuzgo ….sinanga mulibe moto
THHUMB UP MATSOTSI!PITILIZANI
Chonde ngati aba zochepaaa auzeni adzabesooo zinazoooo iyaaaa
inde aziba zonse mesa zopanda moto
its useless anyway…
Sadalakwitse nanga ndidzachiyani dzimenedzo.Dziko lama GENERATOR ngati linooo
Kaili de cables av no live power.there are useless so let them b used by serious citizens. Actually, they are not thieves but rightful owners .unless gotten by foreigners..
A country of which her majority are agents of Satan
your not using them, so why worry! . ?
Akamangire bafa
Kkkkkkkk‼ Akufuna akapange magetsi awo chifukwa a escom sakumayaka.abe kwambili
zinthu zingokhala asiyeni anthu akazigwiritse ntchito
ACHITABWINO ES COM INGOBERA ATHU MABILU NDIZIPANGIZOZAWO ZINAWOLA
I will not surprise to hear that it has been apprehended but are same Escom employees who stolen it
RIP English
kkkkk
Huh??
5
yap, no matter hw u can oppose but u 4 sure knows that its true!
since we are the only country without electricity they have seen that its a waste of resources for the cables to be there for nothing. They should even steal the whole mkula……n we are not going to report them.
kkkkkkkkkkkk koma guyz hahaha kukomenta mwamwano kt ma awoo azipsa.mtima akamawekenga…
KKKKKK akungoyenera kumaba bas,kip on guyz
kkkkkk palibe moto wa magetsi eti, wina adzafela pompo⚠⚠⚠⚠
Thax they have done well done job. …come and steal here too
Number 1
haha achita bwino
Mau amenewa akanamveka bwino mukanati Atumbuka aba ma cable amagetsi Ku Mzunzu………
Waziwa bwanji kuti ndiatumbuka?
Kkkkk ndimwana ekha emwe sangapange recognize kuti abawo ndiatumbuka sure!
kkkkkk ndye atumbuka siamalawiii
Kkkkkk aiii ndima foreigner
why u hate us the tumbuka
Apitilizebe kuwabelako koz tikungosunga zinthu zopanda ntchito
Ngat muli ndi nambala za mbavazo plix share.,azabeso kuno ku lilongwe ku chilinde A21. Sangayatse magetsi 12:58pm ndikuzimitsa 01:30pm. Just fo 30min. Fon osalowa or ndi 20% yomwe.
Kkkkkkkkkk
Ama Betha Betha simukunama ndakwiya nao. Ine ndi ku typa mayeso Ana akalembe mandeli iwo mkumazimitsa ? Ndakwiya
Andikwana ndisaname. Zochitika kaye kuchuluka zofuna magetsi lero
Hahahaha
And chodabwitsa ine mchoti akungoyendera dzimagalimoto dzabwino a Escom…pamene anthu tikuvutika. Abe ndithu dzimakhebodzo.
Pakufunlka kukazulaso zlma Gen set zlja tlpange athu magetsl, akuba anzeru awa kkkkk
With Long Blackouts All Over Country, Electric Cables Can Really B Stolen.
Ibani!!! ibani!!!! Moto mulibe m’menemo musawope mupange zimenezo
no street lights… No lights in homes…. This country is going darkness by a minute
zopanda nchito asiyeni azikapangila zawo
Atha kubad mesa sizku gwira ntchito magesi kulibeko ku malawi???
kkkkkkkkkkkk
Yaaaa lero mumalidzits dzatsalaz palibe vuto
achitabwino!
Valani sapato mukamayenda usiku
Kkkkk.Kd ESCOM ilipo? enafe tinaiwalako,aaaa zawo zimenezo aisova awona kt apanga bwanji.
Mukatha kumeneko muzatengenso ku bt kuno zilipo zambiri zongokhara
No problem nkofunikaso kuzula zimapolo zaozi zilibe ntchito anthu amphikile basi
Kumeneko sikuba, mexa ndizinthu zoti sizikugwira ntchito!!!!
FLAMEZ SIDZAVA
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk on my way haa haaaa haaa ndikufana ambili ndayamba Ku panga ma hang’ala kkkkk
Pitilizani musasiyile pompo zilibe ncto zimenezo ibani ndithu
good news en am encouraging them to go en tak a remaining transformer bcoz it is out of use
Zilibwino cz zikulephera Ku gwira ntchito yake yoyenera
nkhan yazana munena lero mmmm
A Egenco ndi a Escom opuma
zili bho mesa zikumakhala zopanda moto
Escom is steal ALIVE ?
ayamba kuba pot sizikugwra ntchto
kkkkkkkkkkkk achita bwino…akusule makasu ndizidebe…mesa sizikugwila ntchito….thats what i call recycling of product’s
Kkkkkkkkkkk yaaah koma kumenekoooooo…..
kkkkkkkkkkkkk nanga zizionongeka pomwe zitha kugwila ntchito zeni zeni
Kkkk
hahaha lovely comment
hahhahahha malawi sadzatheka kkkkkkk sanalakwitse madoloo
Cable yamagetsiyo, mpaka akakhometso makasu heehe zovutatu izi. Cable ayi ndithu, mwina ndiwerengenso ndimvetsetse.
pa nthawi yomwe timakhala tikukoza zina zinthu zina zimaonongekanso. so abawo akukakonzera magetsi ena nde a ESCOM asadandaule kwambiri sinanga zipangizo zimangokhala osagwira ntchito.
#Jafale Tambala zoti transformer achosaso simuziwa?
Kkkkkk
Make use of what is wasted!!!!!!!!
Kkkkkkk akanabasoo transformer
Kkkkkkkkkkk
Recycling….zigwire ntchito yina Kkkkkkkkkkkkk
Achita bwino…next akabanso H.E.P.S ya nkula sinanga imangokhala kkkkk
Akanangoiba yonse kkkkk
Bola Pamenepo