Bad news for DPP:Chakwera, Kaliwo, Msowoya are burying hatchet

168

Months after Malawi Congress Party (MCP) leader Lazarus Chakwera and Secretary General Gustave Kaliwo clashed, reports reveal the two had a meeting on Friday to map the way forward for the party.

According to sources, among the members that attended the meeting on Friday included Richard Msowoya who is Chakwera’s first vice, Tony Kandiero, James Chatonda and MacDonald Lombola.

DPP: Clashed

Reports reveal further that the meeting was scheduled to look at positions like of Secretary General and Spokesperson which the party is operating without due to internal political squabbles.

However, when Malawi24 contacted MCP second deputy secretary general Eisenhower Mkaka to confirm the reports, efforts proved futile as he did not respond to questions sent to him.

Kaliwo and other MCP members have been expressing discomfort with Chakwera’s leadership saying he was becoming a dictator within the party.

He later called for emergency party convention so that members should elect new leadership for the party.

Share.

168 Comments

 1. Davison Wa-Dolie Phiri, Clara Banda, Bridget Gama, Victoria Pretty Bandah, Mercy Mzembe, Gloria Lingani, Jestina Nga’andu I thank God 4 u

 2. Posachedwapa ayambanaso ku mcp dikilani muone akazapanga convention yawo . Kukhala kukanganila maudindo pakati pa mia,kaliwo njovuyalema ndi msowoya . Chakwela alibe luntha lausogoleli , amafuna kutenga chipani ngati farm yamakolo ake .pomwe ayiniwake achipani cha mcp ndi akaliwo ndi njovuyalema enawa angovala ngati malayi ,kuti azpeza podyela .

 3. Zotsatheka amcp sakuonapatali akuyanga,ana zapopopo aluza afufuze chithu chimenene amaluzira akanchipeza agwiritse nchito chimenecho

 4. Malawi24 mwatidabwitsa. Anthu amakangana muchipani chawo lero alumikizana nanga zikhumudwitsa chipani chachikulu cholamula boma cha DPP? MCP is MCP. DPP will remain the same

 5. Mwamuona anatitu dziii kutinkhani yakuba Ku waterboad ija iszidzileko ,panopa wayambilanso?Munthu ameneyi ndiotani ,uyutu ndi dzaya kunkhongo basi
  .

 6. Kodi kaliwo watuluka dpp kulowa mcp?makape amalawi 24 mwakhuta msima watininkha chauta yi kudxera mwatsogoleri wathu wamasomphenyayu adakakhala chakwera wanuyo atagulitsa chimanga chonse mukulira mayi kokoko bwenzi mukusowa mphamvu zolembera dpp ndimoto kuti buuù

 7. Kuvotera mcp kuligati mkhuku oti inanyera manyi nde kumakadyaso yokha kapena kuti munthu wansaza nde akufuna kudyanso mansazi akeyo
  Ndimalira ambuyaga ine ndichipani chibwenechi

 8. You have used’ bad news for dpp’ inorder to attract readers.Thats good style or introduction.The opposite is the case.The team mentioned were intact when the party mentioned made successful stories.One may ask what each of the members mentioned did good to dpp for the party to lamment for their reunion.This is how dpp do well on such issues.Already Mr Mia has an asignment on how he will cope up with this reunion.Will he feel comfortable?How about if he also feels of going back to dpp for reunion? Time is up for roundabout politics.There are still many influencial mcp members who need this unity and should better be done massivelly versus piecemeal type of reunion.Its not bad news for dpp but an awakening message.Dpp should start identifying their members including Sidic Mia.I can suggest one for you to find.Dr.Lucious Kanyumba.

 9. Ine Ndimadabwa Nd Munthu Osapota Dpp Kkkkk Ine Sndngankhale Buzy Nd Chimunthu Cholankhula Zosanvekacho Ayi Ife Nd A Chakwera 2019,bomaaaaa!!!!

 10. Comment reserved because I don’t know who will win the 2019 Mcp convention, Chakwela? Mia? Kaliwo? Mind you if Chakwela will lose then the party will completely lose direction

 11. We are Mighty Dpp,not kamlepo kalua…za tambala sizitikhudza ataaa…and tukhonzetsera kudzamupikulanso tambala….biggest ruval wa chakwera ndi Jessie Kabwira..nde ask urself some sirus questions thwre..not this silly stuff

 12. Hahahahahaha bad for DPP kkkkkkkkkkkkk…mwachepa nazo,,even our president APM akaona Post Iyi akhoza kukomoka ndi kuseka kkkkkkkkk…still end still fan for DPP.Thus a fake story u have posted here..kma 2019 muzakomokadi ndi kukuta mano
  mafana nose odelera APM akulumbulitsa kachikena.

 13. hw is that bad 4 dpp,,are those people from dpp? i can’t understand this..chakwera is a cruel leader. just see from these examples within his own party,,so how can we trust him to run the government? no no no,,no need to waste my vote on the person whom i already know his true colours.

 14. hw is that bad 4 dpp,,are those people from dpp? i can’t understand this..chakwera is a cruel leader. just see from these examples within his own party,,so how can we trust him to run the government? no no no,,no need to waste my vote on the person whom i already know his true colours.

 15. Ngati mukufuna kuziwa zambiri za usogoleri wa chakwera mfunsani ma members a Malawi assemblies, mmene anawuwonongera mpingo umenewu, nanga munthu woti anayamba ndale ndikumalandirabe 6 million pa mwezi Ku chokera ku assemblies, ku mafunabe kumagwira ntchito ngati mbusa pomwe ndi tsogoleri wazipani zosutsa, munthu wadyera ngati uyu, wakumva zake zokha. Mmene akuchionongera chipani cha MCP ndiye kumati bola Tembo. Munthu ameneyu kukhala President wa Malawi? Then he will be the worst President in the history of our nation. Angakhale Tembo sananyozepo mtsogoleri wadziko mu Parliament mpakana speaker kulowerera. A Malawi chakwera asatipusitse.

 16. That’s democracy and good leadership that Mr chakwera has shown to the country, where ever is disagreement we need to sit down and discuss, I know Mr chakwera and MCP,in MCP people believe in negotiations because MCP is not a family party or regional, or Tribe party,MCP is a national party.we are proud of you Mr Chakwera.secondly I would also give thanks to Mr Kaliwo and Richard msowoya for being so humble,together we can build,fight for the better of our nation.

 17. All DPP Cadets here pretend not to understand this post. Zakuwawani, DPP was funding Kaliwo to disorganize MCP. Now that they are reconciling, DPP has lost their dirty game. Shame!

 18. Mgwilizano ku mcp sizikugwilizana ndi Dpp.Ndizofunikira ku mcp ko zamgwilizano wawo,komano musayembekezere kusintha kwazinthu kuti mcp ingalamule zikoli ayi.Munthu wamzeru salolanso kusewera mmadzi pamene akuziwa kuti analumidwapo ndi Njoka mmadzimo.Mcp tinayiwala kale zakulamula zikoli,ndipo sizalamulanso ngakhale dzuwa litasintha kotulukira kapena kolowera.Apa pakufunika chipani chasopano osati Mcp.Zipani ziyenera kupanga mgwilizano mmaundindo awo kuti ziziyenda bwino komano sibwino kupanga zazipani zina.

 19. People you your desperate for change but you don’t see the true colors of the leader chakwela is a short tempered man he don’t deserve to rule the country

 20. Ngati chipani anthu ayenera kugwirizana ndipo pamenepa zinthu zilibwino koma vuto ndi Sidik Mia ,kodi a Msowoya avomera kuti aMia azakhale wachiwiri kwa a Chakwera?

 21. Its not that bad news, have you forget we are in a multiparty democracy? The DPPs should not be annoyed when they see MCP members; The same applies to MCP members when they meet the blues.

 22. kd mumakamba za mcp mukuti izalowa mmboma boma lake liti ayambe. kaye akamfutse. mkulu wawo john ungatenge tembo kt wakhala zaka zingati pa mpando wa upulezidenti mpaka walema ndikusiya yekha. chomwe mungaziwe ndi ichi muli ndi mbili zoiiipa kwambiri ndiye anthu sanaiwale ai makolo awo omwe munawapha aja alipo. ndipo amakumbukila mpaka pano. mukalamulira kumanda

 23. Is that a bad news 4 Dpp? uchitsiru popanga post nkhani FB pano bwanji? ine I love Dpp not mcp becauz in mcp most of member r full of rudnes,jelousy and provocation (4 eg) chakwera

 24. the point here is that anthu a dpp amasangalala kuona kuti ku mcp kuli kusagwirizana,tsopano popeza chakwera akufuna kuthetsa kusamvana komwe kudalipo its a bad news to ddp chifukwa mcp yathetsa kusamvana,am not apolitician but thats the way i understand the post

 25. It is not bad you forgate one thing. you fogate the poor citizen of Malawi. stupied Goverment. ask Dr Bakili Muluzi what we has been fighting in the year 1993 to 1994. come out you peoples.

  • Mmmmm amalawi kukonda kusekaba mzanu akalakwitsa ka chizungu.Ndichifukwa chake anthu amalephera kuyankhula English chifukwa choopa kutsekedwa.Chikhalilenicho omwe akusekawo they are just good for writing but coz u can rectify your mistakes before you post but when it comes to spoken eeesh mavuto

  • Zapafoni simungamuseke nzanu chifukwa iwe umati ukulemba bwino pomwe fon yazilemba zake nde olemba uja amakhala ngati samatha.sibwino chomcho.After all mukuseka koma mutanva kuti munthuyu amati chani

  • This happens only in Malawi when you write or speak broken english, people will take those mistakes as their topics of discussions. English is there for communication nothing else that’s why is called first international language. Honestly this is not out mother’s tongue we all know that. But you will see a professor who is very intelligent person but finding it so hard to speaking english whilst seeing someon with no school papers but speaking as if there is no tomorrow. Nicholas Dausi is my good example, the guy who speaks as if tomorrow will not speak again. And not only that Peter Mutharika does speak as if he is holding a frog on his mouth yet we all know about his vast school papers. Putting political aside Chakwela speaks as if he is pure white guy we all know about this. Even in our own mother’s tongue we do make mistakes, what about this? When you see somebody teasing his friend due to english problems just know he is a barbaric person.

%d bloggers like this: