Ukali wa malamulo a pamseu amene aopseza oyendetsa minibus wayamba kuoneka.
Bwalo la Milandu mu boma la Mulanje lalamula dalayiva wina wa minibus kuti alipile chindapusa cha K180,000 kapena akagwile ukaidi wa kalavula gaga kwa miyezi isanu ndi inayi.
Malinga ndi malipoti, bwaloli lapeza Bambo Ellias James olakwa pa mlandu oika moyo wa anthu pa chiopsezo atawapakila ngati nsomba mu minibus.
Apolisi ati Bambo James anaimitsidwa pa Mkando mu boma la Mulanje ndi mlandu oti anapakila anthu ambiri zomwe zinali kuika moyo wa anthuwo pa chiopsezo.
Iwo ati anawauza Bambo James kuti ulendo wathela pomwepo ndipo iwo anjatidwa. Koma atamva izi Bambo James anayamba kuchita mavuvu.
Apolisi ati pakuchita mavuvu paja, a James anang’amba yunifomu ya wa Polisi ndi kuwathotholela ena awiri zizindikiro pa zisoti zawo. Komabe Apolisi anawagonjetsa ndi kuwathila unyolo.
Atapita nawo pa bwalo, a Khoti anawapeza olakwa pa mlandu oika miyoyo ya anthu pa chiopsezo ndi okana kumangidwa.
Pa mlandu oika anthu pa chiopsezo kamba kopakila ma folo folo, Bambo James analamulidwa kupeleka K150, 000 ndipo pa mlandu okana kumangidwa, analamulidwa kupeleka K30, 000.
A bwalo anaonjezelapo kuti akalephela kupeleka, akatsekeledwe kwa miyezi isanu ndi inayi.
Vuto ndilakuti zimene akuchitana zukathera pamunthu amene ndi osauka akakwera amukwezere mtengo zimene zikutanthauza kuti akuchita dala zonsezi ndicholinga choti pokana zimenezi madriver azingowapatsa zammanja kuti aonjezere pazomwe alinazo kale.
The rules are not observed in Ntchisi to Mponela road and vice versa. 4-4 is still observed by minbuss operators.
Hmmm!!! Bolaso Okupha Alubino Anakat Adziwapatsa Cilango Chotele Ndiye Kt Dziko Lili Bo,
Well-done our law enforcers. Musabwelere mbuyo ndi malamulo amenewa alipilitseni kapena kuwakwizinga akanganya amenewa anationjeza kutiphwanyira ufulu okwerafe. Psya! koka! luma!!!!
Mwina asiye kutikwezeka ngat mbatata
Iya ife atumbuka tikut zipitirire
Ok
Its unfortunate that zotsatira za Virgil ija ma min bus anakwezedwa mitengo chimene anthu tinagwirizana ndi ganizo loti tizikhala atatu atatu pa mpando koma lero zokhala 4 pampando zabweleranso n tikulipilabe mtengo okwerawo. It’s unfair kuti ma fruits a virgil ija ovulala ndi ma passengers and yet some one claims kuti Passengers Association mdziko muno
Ndizine ndimafuna makondakita ama onjeza amatinyamula ngati matumba!
Malamlo awa apanga ndi anyani okonda zimphu andi alibe maminibasi, 1 salunu imapanga ngozi mli farmily,lole imapanga ngozi itanyamla matabwa, fodya, chimanga or ilibe katundu imagwa waminibasi walakwa chani kuno kujoni ngozi pamwezi anthu amafa kopitilila 400 koma misewu ikulu ikulu fork akhwangwala
Nkhaniyi ndiyomveka komano , eni minibus atsitsenso ma target omwe amapereka kwa ma drivers.
Sikuti akuluma mumbuyomu amanyamula bwino bwino 3 3 3 4 uku ndikuwaputa a Police
Muziona berewanu akamangidwa ndemune nekutimaramuloayamba kungwiranchito panyapaanu
Kma ndi apolice akumalawi zitheka izi???
oky
guyz munakweza mtengo multiply by 2ulendo wina uliose ndemukufuna chan kulemer nd nthaw2
Kod a malawi munakhala bwanji u always react whn thing r getting worse kod mesa zot pampando tizikhala 3-3 zinanenedwa kalekale ? Now u hav seen it very important coz more lives hav been perished just like that? Shame to u mai malawi and ur foolish rules! Mxiiiiii
Aaaa wiyez yokhayo? Awapanga bwino pokwela bwana khalaniapa posika asetapanga fast
kma nanga oba chimanga uja mukumuopa????
zilibwino TB ichepe kufala. Naomi amenewo asiye zibwana
Achita bwino okwerafe ufulu amatilanda wokhala 3-3 ukati ukane amati sikani pamenepa aziopa lamulo sopano munthu aziopa lamulo ndemunthu amene
anchita bwino
Gud idea ama minibus amawonjeza kukonda ndalama not munthu
Nkasa ananena kale kuti lamulo limaposa mphavu ndiye mwina akafuna awone akayesa masewela
Exceeeeeeeeeeeeeeeeeding bt kuchisapo czinathe kma ma price ndi a3 3
Yes they should continue doing that we r not goods!
Akamawamanga ine kuva kukoma ndichipongwe kumatipakila ngati matumba a kabitchi
Nonse Muthoka Zopusa, Galimoto Ngakhale Zelu Nulibe Komaso Simudzagulapo.
akukweza mtengo in the name of three three and akufuna kupakila 4.eish.thats public stealing and another case levelled against him and stealing z has nothing to do with fine but jail term
Boma likungofuna kuononga business ya minibus linazolowera kupondeleza a Malawi 4 4 4 palibe cholakwika coz 3 3 3 mpana wina umatsala
Kwasala ku Machinjiri / Luwanda Nkhama road mubwere
Sziwona zmenezo muganize bwino
Mavuto apanseu sazatha vuto ndlot mmalaw muno ndalama mulibe ndye mukaletsa anthuwo azdya cha?
Shaaaaaaa!Wakundende basi,angaitulutse K180000 driver ndi conductor?
Wake up minibus ass of mW,we need modern minibus terminals in all our cities and towns!
Times and things have changed don’t politicise these issues,that’s the betterment of passenger welfare!we are in the 21st century!we want that to be adhered and nomore standing passengers in big buses!
Opusa ndife Ma passanger nchoncho mkumalola kukwerra osakana bwanji us ur freedom. Malawi plz don’t sleep
Malawi dzuka zoona anthu 4 4 mkumalola ndalama ndi nzako mkumakweratso ngati madengu ansomba osakana bwanji
Boma Lakuba Ili! Mpaka 180? Tionana 2019!
Kkkkkkk lakuba chan zoziputazo yachepaso imeneyo
Ah Akawadyera Kt?
INE NDIMADABWA DIRIVER ALIBE VUTO KOMA ANTHU OKWERAWO. KODI AKATI FODYA AMAONGA MOYO , IWE KUGULA FODYA. DIRIVER ALIBE PROBLEM M’MASULENI MWACHANGU.
Bola pamenepo
A court agwiritsa ntchito lamulo lanji? Was the constitution amended?
Kujon tex umachita kuyinjoya ukakwela usati zakumalawi tex kukwela posika thupi kumapweteka ngati unakwela hachi
#DPP government yur doing agood job law it must work nw and itwillbe taough ngozi zapanseu zikanachepa
If u say kuti 4-4 imapangisa ngozi nde nanga mchifukwa chani galimoto imachita ngozi even driver alimo yekha? just find other solution not this or else u should focus on speed osati zamkutu zanuzo
That’s true
ngati achita ngozi atapakira 4-4 afamo ambiri ngati achita ngozi atapakira 3-3 afamo ochepa chiwerengero chitsika osati amati singapange ngozi ‘funso lina bwana
Akakhala mmodzi ikachota ngozi angafe atatu????????
Mmmmmmmmmm Koma Malawi Watenthe Bwanji,
Good job
Goooooood job
2019 ineyo boma ndipo boma langalo siilizamanga muthu kamba koti akusaka ndalama
ngat malemu bingu ankakwera chibasi chija okhaokha,nde ifeyo tizikwera anthu mpaka 20 mukabongo??? zausiru amene sakufuna 4 4 akagule yake….
Zili bwino koma pena athufe tili ndi ufulu cz tiona kut minbus yazaza atatu atatu ndiye timapira pompo ndachedwa sindingakhalepo apo ndiye pameneponso tisamale
Good development keep t up police we need an accident free country. Some accidents r caused by neglegency of drivers so deal with them. Palibe samadxiwa how reckless minbus drivers r.
Mark Zuckerberg
Mark Zuckerberg
Watani?
At [4:0]
asaaa iye anali kudedela malamulo amboma anayishosha dala munthu ameneyu ati
Driver ameneyo ndioumira samafuna kudisha ife tikumakwera 4 bola ya maUnits
Mitanga yamangonso ichoke mmini bus
NDE kunalitu chichewa, ‘,minbus sidzadza’
zake zimenezo
That is not a severe punishment they must pay K200 000 and beating the driver
And conductor 200 hot sticks at the same sport. They never do that again.
Zoona guys wazgowera gud……
KODI MIN BUS IKANYAMULA ANAYI ANAYI NDIPAMENE IMAPANGA NGOZI?..DIS IS MAN MADE ACCIDENT
Lamulo liposa mphamvu ife timalamulidwa kuti tilipire zokwanira akweza mtengo we pay!! Nayeso alipire ndithu ngati ayi akalowe
kkkkkkkkkk mwakalipa chayiko apo cc
Palibe chinthu chimandiwawa ngati driver ndi conductor kupulumuka pangozi yapamseu,mbuzi zimenezi zinakati zizifa nao ndikukhulupilira kuti ngozi zapamseuzi ili mbiri yakale.Bravo police.
Mukanakhala kuti inuyo ndi mulungu ndibwenzi zikutelo koma sizingatheke chifukwa iye amakonda aliyese
Ukunenawe or ndichokwela chomwe ulibe umadalura minibus kut upite kuntchito
Zitsiru inu,mumasogoza ndalama m’malo mwa miyoyo ya anthu,pamene tulankhula pano ena ndiamasiye ndipo ena analumala chifukwa chakusasamala kwanu.
Makape inu,mumatsogoza ndalama m’malo mwa miyoyo ya anthu,pamene tulankhula pano ena ndiamasiye ndipo ena analumala chifukwa chakusasamala kwanu anthu mwapha aja akwana pano lamulo lithana nanu ndibwelezenso kuti pangozi zomwe mumapangitsazo inuyo munakati muzifa nazo,sibwenzi tudandaula.
bravo..now you are talking
Nawonso kumawa ………………
achita boo nanga si mitengo yokwelera anakweza,keep it up police.Komanso apolice ayenera kuyamba ntchito 3am mpaka 10pm kuti asapeze mpata wa ma 4×4
ndimomwemotu moyo bola osamaumila ndalama zapamalawi nd zogawana bas
to all tax drivers ,tomorrow start loading 5-5 as u are aware of the fine,before it goes up to K350,000(yr jail term),becoz u aren’t satisfied with the capacity of ur motor vehicles.welldone to those who are respossible for the fiines.
kodi inu ama Min-bus mukufuna chan?….munakweza mitengo kut tizakhala 3-3 koma mukumatiyikabe 4-4 … Koma mukhaula Coz boma silikusiyani
Usaumire, kuwafumbatisa iwe, ukaumira, uzaziona waona tcheleman. Anaumira sakanamugwira achina JP akupakira 4_4 onse achina langabwai akupanga zomwezo Sunday < Sunday 1<30 jenorobia < December koma samagwidwa chifukwa saumira ko drink onse achina Thom mufunse Vic.
Ngati zili choncho ndie tikweza ntengo
Adziweso Amenewa! Mitengo Anakweza Kale And Kutsitsila Amakana But Kungodusa Roadblock Akumayamba Kutisanjikiza Madengu, Abakha Yet Akuti Lamulo Linati Tizikhala 3,3. Anya Aona.
Ana a Israeli kuphula njelwa za moto. Umphawi sudzatithera.
Utakhala iwe magastrit sungapeleke ndalamayi ndiyochuluka mawa ndiwe ogamulawe
Vuto ndinu okwela mtengo wa kwa mkando ndi 1000 munthu mmodzi mumalephela kulipila mumafuna 500 ndinu anthu oyipa inu
Thats good mwima nkusitha!!!!!
Thats good mwima nkusitha!!!!!
Rude to passengers and don’t bring all the moneys to the owners. Serves them right
thus totally stupid, are they saying all the accidents that have been happening it’s cause of 4 4? This government is full of shot.
Dziri bwino mayiko adzanthu mipando amankhala atatu ndipo anazoliweranso osati kumatifinya
Amuchita bwino mwina enawa atengelepo phunzilo amapachila ngat khun kut akukangulisa kw mayaka.
Za boma zatha mukufunano mudye za anthu a business mbuzi za anthu agalu inu
shaaaaaa
Good
Very good
Malawi dzuka, minbus mpando wakumbuyo sakhala anthu, amakhala 3. Apapa akukamba zamipando inayo. Maiiko anzathu ixi sidxichitika. dxuka Malawi, 53 yrs u a old.
Zofuna Zmenezo
big up @ #Rod_traffic moyo ndi mphamba ofunika kumawukonda………ndinapita ku Mozambique last week koma kutipakira kwakweko mu minibus mmmmmmm anthu 5-5 pampando ine kudabwa buss sikunyamuka,, kudzafusa Y akut sinadzadze ena amayimirira ine shaaaaa better @ my home MW kuli malamulo amzeru
Amuchitabwino azichangamuka
Uona anyamula 3 -3 akayenda kuyambanso kupakira 4 4
Inensotu zimandinyansa zimenezi umapezeka kuti wakwera bwinobwino muli pakati pa ulendo akangouzidwa kutj kutsogolo komwe akupitako kuli a traffic amakutsitsani mkukupatsanso ndalama yosakwana akuenera adzipeleka K500000 akagwidwa nonsense
Angoyika lamulo la modzi modzi basi. azitambalala anthu kapena kugona pa mpando wonse
Kkkkkkk eish mn Astings Gondwe muli super mukupha english yabwino kwambiri….mpakana acar…ifill
Mmmmmmm yachepa ndalama aonjezere chifukwa timazuzika papando ngati sitinalipile kkkkkkk
Amaminibas Avomeleze Chifukwa Minibas Anayaba Kale Kunena . Zimatheka Kupakila 4 4 Ena Kuyima . Makamaka Mseu Wa Mulanje Zapabana Mgati Akuwona Kuti Minibas Akatenga 3 3 Sikuwonesa Akasiye Minibas Kwabwana .
Bwanji osamangonyamula mwa lamulo bvuto nchani please olakwandioyendesayo amafuna kuba 4-4 its over loading
Lamulo ligwile tchito basi.
Boma laganiza bwino chifukwa tikachulukanamo timapumilana mpweya woipa
Wait and see what will happen towards mid and end of the month!!
It pains indeed and they must be punished more than that. Passengers are being loaded like lifeless things despite having paid alike. Life is not buyable and must be treated accordingly especially when we come to using road tranportsr
It pains indeed and they must be punished more than that. Passengers are being loaded like lifeless things despite having paid alike. Life is not buyable and must be treated accordingly especially when we come to using road tranportsr
Nnkhaza izi..ife tizipereka ndalama aziba zopusa
Andalamazachuluka Tsitsakoni K5000 Yokhapasi
I accept ena mwa malamulowo koma enawo i don’t. Zoti ma bus asamayende usiku ndiye fodyayo. Zoti mpando wa mmbuyo wa anthu 4 uja azikwela 3 ndikudananazo ngakhale ndilibe minibus. Malamulo awa atipweteka okwelafe chifukwa anthuwa akweza mitengo kuti azichita cover pakupelewelapo. Koma zoti no standing passenger komanso zoti 3 seat for 3 i salute that.
Koma zimenezi ma 500mk tikulipirawa tilimba salary tikulandirawa?
Zautsiru
Nkhani yokoma
Aaaa hahahahahaaaa
Muzimaliza nkhani mukangoti ukayidi wa kalavula gaga,ife ndiye tiziti bwanji? Watani driveryo?
Yeah amatifinya ngati matumba mukuwachita bwino
Akhaule amenewa kusava!
Komaditu amaminibusi amaonjeza
Malamulowa ngabwino we want sanity on our roads
So nice!
amangwe basiii kusakhutitsidwa ndi capacity e same atakhala waudindo angakhale wadyera ameneyo osamakhutitsidwa ndikumapondereza amnzake ngat awowo awo……
Its Simple, Anthu Amenewa Amafunika Adzilipilipira Ndalama Yocholuka Kuposa 180,000.Amangotipakira Ngati Mitembo Kumotchale,akapezekaso Oteloyo Lamulo Limugwire TChito.
Amchita bwino
Nde Ifetu Kuno Kwa Manje Mpando Umodzi Timakwera Anthu 5,,,kutsogolo Kwa Driver Timakwera Anthu 4,,,malamulo Achan.
I love that, don’t favor anybody who is wrong otherwise they will take advantage over that.
TAMABANI NDALAMAZO,athu opha malubino nde kumangowabisa osatengela ku court.
Ineyo ndinakhulupirira kuti zomwe adapanga ma driver a ma minibus ziwatsata.Panopa ziziti ka mulandu kakang’ono pa court pomwe mmbuyo muja amangoti ife ndi amalawi tasiyeni.Koma kukawotcha ma police units amayoooooooooo.
akulipisa mtengo odula ati chifukwa ndi 3 3 3 ,,kuyenda pang’ono uwona mukukhala 4 4 4 what’s that????alangidwe kumene,,bongo mpaka 4 4 4???
Malamulo amenewa ndiabwino akuthandiza ifeyo ngozi zikuchitika chifukwa chosasata malamulo aziwona maminibas
Boma ndi Boma basi
Mighty Beforward Wanderes fc 2-1 Red Lions fc
Haaaaaa kaya kumeneko
dic gvt dey ar under money nt kukoza zithu
One of bad laws of DPP government let wait and see in 2019
One of bad laws of DPP government let wait and see in 2019
Ndie angokweza ntengo coz pa 3 3 azituluka ndindalama zingati pa day
Anakweza kale two weeks ago
Aaaa Zoona ndie akulakwadi azimangidwa
Anthu aziyenda wapansi
Nice job
ACHITA BWINO
Very very good and please don’t go back they must pay heavily to save lives
lives are not lost by packing 4-4 kuipa kwa misewu yathu nkumene kukuchititsa ngozi, boma lilibe ndalama angofuna kukama zoonda kale, amalawi osaukafe tikhale migodi yaboma?
Ayi pepani ndithu ma minibus amathamanga zosowa zija ngati kuti sananyamule miyoyo ya wanthu ndalama zilibe kanthu apa ofunika awonjeze punishment kuti oyendetsa ndi eni a ma minibus asinthe kayendetsedwe
Komatu somewhere tiziganizira miyoyo and safety. The seats in a minibus are designed to accommodate three persons period!!!
this is totally nonsense akanamugamula life imprisonment agalu amenewa akujaila kwabasi 4 4 kt chani ma driver nonse a minbus lisani lalikululo mwamva pa ujeni panu axikumangani kumene
Kkkkk
Good teach them to respect the traffic rules
Ku lilongwe kuno akunyamulabe 4 pa one seat so pathetic . Kodi a police bwanji sapanga patrol mainly pick hours ? Please police help us we beg you stop this malpractice in our city lilongwe .
Zoonadi ineyo on sunday 9 july anatipakiranso 4-4 ndipo titawapeza apolice pa centuary tinauza and zotsatira zake anapatsana ndalama tikuona ndipo anangoti musamatero malu
Mostly ma bus amenewo Eni ake ndi a Police omwewo. Ndiye ndipovuta kuti minibus yawo yomwe isapange business.
A police ndi a road traffic officers ali ndi ma minbus that’s why vuto limeneli silikutha.
I sappprt de movie
Iye amafuna ayese zda waziona
Lamulo liposa mphamvu amalawi timakonda zomapanga unkhutukumve chenjezo lita pelekedwa yachepaso ndalamayo amatilongeza ngati madengu ansomba anthu amenewa
More fire
Eeeee! Koma tikudya pambar
Ameneyo amchinyila
ukapolo still exist in Malawi
Bambo Elias yaakhakilatu apa
Bodza ili malamulo ameneyo adapangidwa liti? Ku nyumba ya malamuli sikunavomerezeko malamulo otero inali chabe presidential directive during Bingu administration.
The driver can challenge this through an appeal. Ndizoona amalakwitsa koma likhale lamulo through parliament.
Enemies of progress! Yamikani poyenera kuyamika osamangothamangira kunyoza boma pachilichose!
Izi sizikugwirizanaso ndi ndale
Acar or minibus has capacity, ie 15 exceeding the recommended capacity it’s wrong, bt miniming it’s capacity is evn awfull
Chilichonse aphungu? Malamulo a mumpingonso ku parliament. Anyakwawanso malamulo a mmudzi mwawo azikapangidwa ku parliament. Ali ndi zambiri zochita aphungu ku parliament kuja.
Tiyeni tikafuna kutsutsa development iliyonse tizibwera ndi mfundo yozibakilila. Tisamangolowesa ndale pa chilichonse.
Amenewo simalamulo adziko laMalawi lokha it is supposed to b world wide pipo u just surport things which doznt even favour or cover us during accidents,n we r used kuyika umoyo wathu pachipyinjo tikunziwa kuti siziti thandiza
Kukonda kusutsa basi
muzikhalako ndimanyazi akulu tiyeni tisithe maganidwe ndi machitidwe athu
Ukawerenge road traffic act about Minibus capacity
che Richard Mphande Lyson apa bwanji manyadzi mulibe aliyense akukusutsani zinazi tamavomerani anthu afa mminseu aja 4 akanakhala ma brother ndi sister anu bola tikanaona kuti ndale zanuzo zithera pati ndangudutsamo….
Ukumasangalala anthu akamafa pa nseu eti? Iwe nkhululu eti
Not every goes through parliament.. For the constitution a law passes thru parliament laws for some government agents such the road traffic doesn’t necessarily need Parliament to deliberate.
highway codes do not need parliament
wadya chamba iwetu. zomwezi mpaka Parliament. tiziti ngozi zikuchitikazi sukuziona. its a morden world now.wake up broo…
Malamulo anapangidwa kalekale alipo ngati uli real driver kapena minibus owner pita ukawerenge RTA (Road Traffic Act) chinavuta pakatipa enforcing the law sinali pa 100% panopo angoonjezera ma fines komanso milandu ina izipita ku court
guuuuuudu akhaule baxiii
Kkkkk 1) Tchoveli, 2) 2 Psngrs Kutsogo Then 3+3+3+3+3 Yili Booh Mwina Ntchentche Nkumapezako Mpata Woulukira
Achita bwino amayelekedwa pamsewu kkkk
aaaaaaaa GOD iz near juxt b cloze 2HIM rather than b bzy wth de world
Kkkkkkkk more fire bungwe ,
Kkkkk 1) Tchoveli, 2) 2 Psngrs Kutsogo Then 3+3+3+3+3 Yili Booh Mwina Ntchentche Nkumapezako Mpata Woulukira
Wamva kuwawa mphwanga,hehehe ukagwire ukaidi wakuba iwe.
Congrats muziwatero atikwezera mitengo kumatiikanso 4_4 nde ife a Malawi ndikupusa kwathu sitimalankhulanso nde nkamanva zimenezi Ai ndithu zilibwino pitilizani kuwamangako alipo ambiri
Tione ndi mmene zithere.
Ma minibus achulukirenji,tengani atatu atatu basi muzipita,enawo asiyireni anzanu, nawo anyamule.
Zilibwino
Zonvesa chisoni,koma lamulo ndilamulo basi
Tiona komwe zithere anayamba kuletsa kale. Ine ndinapakira 4 -4 popita kumangochi ndakumana ndi atraffic muzombamu mpaka lionde timangowaweva pobweraso ndapakira 4 4 plus matumba ndakumananawo ali busy pa whatsap ndangowapatsa moni zatha
ngunda 2much!
ine ximandinyasa bwanji zomakwera ngati chimanazi
uzasiya ukazachita ngozii.pitiliza
180,000 that’s too little
Big up packing us like tinned fish.
Great news
Lamulo liposa mphamvu
Personally, ifill it’s nt the way it should be, considering the fact tht a car has capacity, exceeding the capacity it’s a crime bt saying, a 4–4-3-3 should carry 3-3-3-3 it’s nosence. Iwonder hw did the authority reach on tht. Plus saying no acar aftr 10 it’s jst pathetic.
Go back to school
Wolf,go to hell wth ur unpleasant hole.uknw nothing. Tsek
Azimva anthu amenewa mamulo ligwile ntchito
zikatelo zibwino tizikwela mwaufulu mabasi
Koma Ndalamayo Yachepa Bola Inakakhara MK500 000 Koma Akagwire Ntchito Ya Kalavula Gaga Kwa Zaka 5.
Nice
munthu osamvera lamulo amayenera kulangidwa
Silamulo koma ndimene zimakhalila since kwa amene amapanga ma minibus ngati mipando yili 10 muyenera mukhale anthu 10 koma amamibus anali kutitenga ngati zisilu okwelafe mupando wa anthu 3 kupezekapo anthu 5 ndawi zina minibus kuzaza mpaka pakhomo komanso pomwepo papezekenso space ya condactor chonchi ngozi zapamsewu zingathe
Amuchita bho akuyenera kulemekeza malamuro ,
bravo for the judgement!!!!!
Chilango chidzikhala choletsa osati kulimbikitsa. Tima K3000 timachepa
THAT’S a lesson tobe learnt.Fuel prices are still constant,but they are exploiting (plundering us
Ofcoz he is guilty but the fine its too much
Driver yo wamwano onyasa and anang’ambira apolisi uniform and analedzera kwambiri
Thats good even here in RSA minibus singanyamule anthu odutsa muyeso ngati chimanga
bodza*jubeg yake it:->
Town, nde kuti iwe umadziwa itiyo pot joburg ndiyose, mwina iweyo umakhala ku Binoni
@ Julio dnt tell pple lies, a minibus has capacity of either 15, 14 or 16 ihv bin in SA thr is no such a thing tht a minibus should carry less thn it’s capacity,dnt misslead pple
I dint get her saying:less capacity,what she said is:over capacity or overload.she wrote in chichewa even.
@ Nkuna its true
The lady says “siyinganyamule anthu odutsa muyezo…” So are u saying she’s lying?
Julio akunena zoona kapena ine sindikutha kuwelenga. Please read before comment
Jorberg Ndi Ma Quantam Kuno Ndi Ma Vanette
Ku SA amanyamura,4-4 -3-3 pamene kumalawi,akuti or mpando ukhale,wa 4 inyamule,3, thus y enafe,we are saying tsidzoona,cz the issue here is the new law says every minibus should carry, 3-3-3-3 or itakhara,ya 4-4-3-3,same wth ma bus thy are allowed to carry standing passengers bt the the new law says no,let’s b honest here, acar has capacity, exceeding it its a crime, bt minimising it is awfull too
Mwina anthu ena kuvetsa nkovuta, zomwe ine ndanenazo
Lembani Chichewa Julio Nkuna kuti give bwino bwino
SA yakuti nanu mukunamidza wanthu ine ndili kuno ku CAPA anthu timakwera mothinana 4-4 plus oyimilira aaa
Aaaa nde mwina Komwe mumakhalako amwene ndi ku ma farm wot apolice kulibe ndinkawona mumakwela choncho
Kkk koma anthu ena ngoduka mutu ma reply awo sakugwilizana ndi comment eish kodi mwalemba chizunge #Julio kkkkkk auzeni awelengeso
anthu ena anangozolowela ntima wa John Tembo wongotsutsa zilizose
Asisi inenso ndili komkunotu koma minibus imadzadza mkupezeka ena oyimilila. Ndipo ma driver ambiri a kuno ndi ampwesa kuposanso a kumudziko. Ambirinso opanda ma license.
Tiyeni tingokamba za kwathu tisafanizile ndi mayiko ena mapeto ake tisiya nkhani ili apa mkuyamba mtsutso wa ziii.
Next time ukadzafuna kutchura dzina la a Tembo udzatchule mwa ulemu komanso udziwona ndinkhani zake zokhuzitsa anthu akulu-kulu ulemu ndiofunika
Local zimanyamula 4,4 nanga si mitunda yake ndi yayifupi
Komatu apa Julio Nkuna ukunena zowona..ndankhara ndikukwera from pretoria to randberg..taxie imanyamula exactly anthu ofunika kukweramo.ndipo pamakhara anthu owonera amene akukwera .koma kukwanthu mmmmm aima njira yonse kuzaza anthu ngati matumba achimanga..koma even ma bus akwanthu kuzaza kwambiri ndichimene chimapangisa kuti driver agwese galimoto .
Komaso kuno ku joni ma taxie ake no conductor..
Let me repeat what Julio Nkuna said: Thats good even here in RSA minibus singanyamule anthu odutsa muyeso ngati chimanga. Translation: A minibus cannot load more people than it’s capacity like bags of maize. Mwina simunamvetse. She didn’t say kuti minibus imanyamula anthu ochepera muyeso. Munakhalika bwanji anthu a mpanje. Jo’burg yake iti yomwe munaona minibus ikupanga overload anthu? I think mukunena mmene amakunyamulurani ngati matumba achimanga mukamapita kodyetsera ma horse mma farmer mwanumo…case closed. Julio Nkuna is right amene ukutsutsa izi joburg umangobwerako umakhala either ku Mozambique or Congo ndikomwe mukuchokera. Osandikwiitsapo apa….
Maujeni anu palizotsutsana apa!!!.mbuzi za anthu.
Ngakhale kuno ku ma farm ku Brits ma minibus sanyamula modusa muyeso. Ndiye enanu mumakhala South Africa iti?
Anthu akutheba mumatiimilira. @Patrick its “Taxi” and not Taxie Thank you.???
ndiekut chifukwa choti munapita kukagwira ukaidi Ku Jon mpaka mwaiwala chichewa eeeh koma aMalawi,mzanu walemba bwino Chichewa inu mukut simukumvesa
Kkkkkkk koma!
hahahaha mvuuuuu ndadusa
Kodi apa khani ndiyotiziwasa kuti muli ku RSA, kapena chani? Nyali ? Usilu ife ayi
pachuluka anthu aku Theba apa, nkhaniyi yalakwika basi……
Hey one ndimayendetsa taxi paweekend kuno kulibe 444. Quantum back sit 4 then ena 3 then yapafupi ndiye driver 4. That is 15 passengers and driver 16 no conductor.
Harold phiri amene muli kundende ndinuyo kaya manyasa dziko lomvetsa chisoni ngati limenero sindidaliwone chakudya chomvala pogona zomvutikila kunyasalande ndikugahena
Killy Az-nature aaaa koma iwe mpaka ukufuna ndipange edit zomwezi..but you know what we are talking about here eish…
nah bra u don’t have to edit . zangotanthauza kuti ndili ndi chidwi ndi comment iliyonse aliyense akukamba….lol pa low
kwaeni kulibe mkuo muzatipeza
kkkk apa pali nkhani….
Even here in RSA ngati ndi kwanu….
OMWE MUNATHAWA KU MALAWI MUNALIBE POGWILA IFE KONKUNO TIKUPHAKA LIFE NO CHEU CHEU ZENOFOBIYA IKAYAMBIKA MESA MUMALILA INU KKKKKKKKK
Kkkkk! Amene akuphaka life kumalawi ndia cashgate iwe usatinamize
Kkkkkkk
yeah big up, zanyanya heavy.
Kaya zawo izo omwe ali ndima minbus wo ine ndilibe galimoto yonyamula wanthu.
Nsete zawo ndithu. Adyeletu ma K180 000 wo komaliza poti nthawi yatha tikufuna kuona zina ife. Bullshit gvt
U ishu Kaliasi I think u r out of des issue so u just keep queit ok.
Out of order
W@ da fuck u can tell me to keep qiet? U wanna tell me dat accident happenz only in a9t? Accident happens any tym day or 9t boss so there is no need to fine some1 so much money jst becoz of dat silly nonsense @ mac henz t banda,what ever u call ur self ok?
Eish!…?…
mmmmmmmmmm
This is out of context!!
Musiyeni mumthuyi mwina ndi minibus driver kkkk eish capacity ili bho koma mesa akweza ma minibus
zimapanga prevent zinthu zambiri osati bgozi zokha. wise up man
English yakenso ma adverb okha okha
Ena atengerepo phunziro Mesa anakweza mitengo
Akaseve basi ameneyo
amuchita bwino lol
Kkkkk koma iwe kkkk
kikik amatiwonjeza akanganya amenewa
Mwinadi ngozi zapa msewu nkuchepako mmm coz zaonjeza
zosabwino
amuchita bwino asajaire metsa mitengo anakweza nde nkumapaliranso 4 four
Malamulo adziko la Malawi amapanga Ku Parliament nanga zimenezo anavomereza Ku Parliament?
Amwene apo zingoonekeratu kuti lamulolo linabwera kalekale simungavutikeso ndikufusa nokha mmaziwa kut galumoto imakhala ndi mlingo wakanyamulidwe ka anthu nde sizingafuneso paliament izi zimapangidwa pomwe galimotolo likupangidwa
shee!!