A Malawi ndi kutheka tipeza msika wina oti utenge malo a malonda a fodya akuvutavutawa. Mmalo mwa fodya, mwina tizingogulitsa ng’ona za mphongo basi.
Malipoti ochokela mu dziko la Egypt ati ng’ona za mu dzikomo zili pachiopsezo pamene anthu ayamba kuzigwila ati ndi cholinga azigulitse.
Malipotiwo ati ng’ona zazimuna ndizo zili pa chiopsezo chachikulu ati chifukwa anthu atchukitsa kuti maliseche a ng’onawo akawasakaniza ndi uchi ndiye kuti basi ndi gondolosi kale, alingati nkhondo ku bedi.
Ndiye ati malonda a ng’onawa afika pa mponda chimela chifukwa alenje a ng’ona amatha kupanga ndalama zoposa K70,000 iwo akagulitsa ng’ona imodzi yokha basi.
Ndipo ati ng’ona zina ena akumagulitsa kunja kwa dziko la Egypt chifukwa anthu ena amaiko ena amagula kuti azikaweta basi monga ena achitila a mphaka ndi agalu.
ndilinazo plz chikho chimenechi chisandiphonye
Guys samalan ,maka inuyo otengeka pofuna kulemela nsanganu , akufuna mupotele ( yakwiya ndimizimu ya allibno ) kkkkkkkkkkkkkkk
Zimenezo ndiye zibwana ndithu inu a Malawi24 Ng’ona mumaidziwa bwino?
Kkkkkk kusawuka ndi mavuto akulu or sibwino. Poti fodya sakuyenda bwino ndiye mukuti ng’ona ndiye zithese mavuto aku Malawi that is not true chifukwa palibe amene amapanga ulimi wa ng’ona m Malawi ndiye boma izakhala busy kusaka ng’ona mu shire kkkk mavuto kwambiri tiyeni tingovomereza kuti zativuta basi
Visit nsanje and kill as many as you can
Vuto ndi umphawi
ng’ona ili ndi maliseche?
Heee ndie ndimmene ndiidzila ng’onamo tiyeni nazo pano nazo zili mma meeting kukambilana mmene zikuvungileni..ine kumangoonelerako bwaa
Kkkkkkk zovuta kwambiri. Kenako timva kuti nsato ndimankhwalaso shaaaa!
Kkkkkk koma kukhala kuphana kuti udziwe kuti iyi ndi yaimuna wina atakhaka basi.Admin nkhani iyi yokha waikocha boo.
mwamuna nzako mpa chulu, angakaishoshe ng’ona ndani ooooo zanu izo
Panja Mcp imaweta ng’ona ndiye ipanga ndalamatu apa kkkkkk
kkkkkkkkkkkk koma zinazi kkkk ndakomoka.. gondolosi yemweyo 2017 boma
Zazii!!
Amalawi we always talk ngini yosatheka maloto osatheka ng’ona ungakaitenge kut munthu?zachamba izi
zilibwino, angozimaliza zose ng’onazi zanyanya kupha anthu,
koma ng’onayo si phada osayiwala, imapha samalani
Kkkkk
Kulamula bvumbwe nkulinga uli ndi nkhuku,ndiye amene angabvomele kuononga moyo wake kung’onazo ndi ndani?. Pa anthu 100 aliwonse mudzapeza kuti olemera ndi mmodzi,ndipo 99 ikhala mitembo .
Zalowa chibwana
Ndiye imaziwika bwanji ya mphongo
gondolosi ndi chani?
‘dept of parks’ should declare ng’ona endangered species
KKKKKKkoma,ndemukazimariza munyanjamo ndesikuthaso kwa godolo yo
Dilu yalowa bwemba
Mwina Anthu Adanzi Angamayende Mwantendeld
stupidity at its best, combined with foolishness plus those mentally retarded can believe this myth
Kumbukani Jimu
Komatu ndiye umphawi sizinthu utha kumupengesa misala munthu, Nanga anaganiza bwanji ameneyo kuti ng’ona ingathandize kkkkklkkkkkkl koma ziliko
Mwina albino apumeko iii
anafufuza zoti maliseche ang.ona ndi nkhondo kubedi yo ndendokwiya tu mmmmmmmm tipapa sana ulendo uno Ku nbedi ko
Kkkkkk shaaaa
?????
Kkkkkkk
Kkkkkk koma mavuto alipo
kkkk koma yah
Odya ndalama akhala ochepa koma olumala ndiamene achuluke.
Ibange will do
Kkkkkkkkkkkk
Moziwona
kkkkkkkkkkk
Wat is gondolosi?
Its African medicine that makes men’s be stronger in bed
OK thank u.xul does not end
KKKKKKK KMA GUYS
Mmalo moichotsa muchosedwe ndiinu malisechewo kkkkk!!! Koma ndiye!
Kkkkkkk kayaaaa
Mmmm abale
ok man mwna zthandzad
Ndili nazo zoweta 12 koma aaa zokuphazo nde ayi ndimakagula mitembo kuchipatala yosowa aniwake kukadyetsela ng’ona zanga nde kupha iwe wamalawi 24 ndizakakuponya mudziwe limeneli ukamakamba za bodza
Dilu Yokanika iyi
kkkkkkk zovta iz..
Hello everyone my name Thandi Daniel, I was once an HIV/AIDS patient, but today am negative with the help of Dr Abuu and God who made it possible, i suffered from depression since the day the HIV/AIDS test shows am negative although i was on drugs but i still felt uncomfortable with the unwanted visitor in my body, only those with virus understands the pains, getting a good job was a problem because of my status no friends, i thought it was the end of the world, i was just waiting for my death, i was losing weight rapidly, i was unable to get married as i don’t want to effect an innocent soul or spread the virus, and i have spent a lot money because i was very desperate of doing any thing to get rid of the virus but all effort seems not working to the extent i was conned, until i met Dr Abuu who gave me the chance to be alive today, i told him i would commit suicide if it didn’t worked out because i was tired of living and my death seems to be too far, but he told me not to worry that his medicine has healed a lot of people and it will definitely work for me too, but to me it was just words of mouth, to cut the long story short i was cured after taking his medicine, today am strong and healthy, are you living a positive life like i was before? and you want to be cured from the unwanted virus? if yes contact Dr Abuu on his email address [email protected] or you can call or whatsapp him with his number +2348066454364.
anthu adazi mwina angapeze mtendere kkkk
Kikkikikiii koma kuti uyigwila ng’onayo…sheeee mpaka wina atataya moyo ndithu
olo zitatha zonse, nanga zili ndi phindu lanji kupatula kutidyela asena kunsanjeku
kwavutadi basi jkkkjkk
Kwavuta nanga hippos
haha
koma ayi iesh