Malawi’s former Police Inspector General (IG) Peter Mukhito has exchanged wedding vows with his new wife Chance Mwale.
Mukhito who is State House chief of staff officially married Chance at St Patrick Parish in Lilongwe on Saturday.
The former police boss, Mukhito, 58, and Chance, 26, later had a glamorous reception at Bingu International Conference Centre (BICC).
Malawi’s First Lady Gertrude Mutharika who attended the wedding gave a fridge to newly wedded couple as a gift.
According to reports, Mukhito has been married before and Chance is his fifth wife.
Mukhito was Police IG during late Bingu wa Mutharika’s administration when a Chancellor College (Chanco) lecture was summoned by the police for giving an example that did not favour the Mutharika government.
Alomwe kukonda kukwatira ana..paja malemu aja anakwatiranso mwana..
musavere za anthu bola chikondieni akenu basi
Za ziii
People should learn to leave alone anything which doesn’t concern them.
If the man marries a young woman so what????
I got married to a eighteen year old young girl recently as a co-wife! “So what??
Mind your own business
Actually it’s better for a man to marry a virgin [if they still exist] young beautiful woman so that you should play with her and most importantly enjoy in the bedroom.
As a man you need a woman who is beautiful young and fresh otherwise you’ll have no erection [feelings in the bedroom] if you marry someone with no chemistry.
“Chemistry” means physical attraction.
The main purpose of marriage is for you to satisfy your sexual desires [sex] in a lawful way and this the most powerful desire [natural instinct]
Mkazi sachepa Chaka chamawa pezani wina wazaka 24 bola agwira bwino zofuna zanuzo. Means ndi amene amaziwa bwini kuchosa oyilo oil GO AHEAD MR
Mukafika nazo kuti mwakula.
Congrats mr mukhitho.wishing you all the best.although i dont know you it was a.colourful wedding.tsekani makutu bwana oyankhula sanati .ameneyo ndiye m’malawi ndimamudziwa ine nsanje number one.mrs mukhitho njoyani banja lanu.All the best
Good that Mukhito has cemented ubale with us up north. NyaMwale, remember Esther!! But also be a Naomi.
Azitsogoleri a Mipingo nowadays too much corruption. Wealthy pipo r heard in all evil decision by breaking malamulo a mpingo. Ndiphunzitseni, ndidziwitseni mwina Vatican idapanga amend lamulo la ukwati kachikena. Am not Jealousy of the wedded couple, koma kukhudzidwa ndi mchitidwe omwe atsogoleri a mpingo wanga wa chikatolika mukuwonongera mbiri ya bwino ya mpingo. Mumatiwuza momveka bwino kuti banja limatha pa zifukwa ziwiri izi, imfa kapena wina mwa mmodzi akachita chigololo. And more worse, mumakana kulumbiritsa ukwati kachiwiri kwa osawukafe ngati mkazi or mamuna yemwe anali pa banja kale anasiyana ndipo onsewo ali moyo. All in all corruption is spoiling good image of my church ndithu
Vatican changed the rules my brother nowadays it’s possible to Wed again even though your all alive
Congratulations.
Peter Denis Mandebvu appears more aggrieved. His contributions are full of emotions. Peter Mukhito indeed married and divorced his first wife long time ago. He engaged Chance Ndida Mwale in 2010 at a function that was held in Area 47. It was a public function. By then, Peter was the Police Chief. In 2012, Peter was sacked by Joice Ntila Banda. Peter stayed with Chance in their nice home in Rea 43 until he was appointed as the Director General of State Residences. Mind you, Peter is not a pushover. He is a level headed person that even Joice Ntila Banda failed to nail him down when she was in power. What Peter has done is to formalise his second marriage in his original, Catholic church. Chance Ndida Mwale is clocking her 40 years on 29th May. They both have three lovely kids and continue to enjoy they flambayount life. The problem with Malawians is poverty and mental mulfunction. My humble request is Malawians, avoid to hurt others and mind your own business. Avoid poking your noses where they don’t belong.
This is not a new wedding amangodalitsa they have been married for so long
Wife looks 20
ziko lafikadi kumalekeleke mpaka mwana kukwatira ndi size ya Bambo ake Mmmmmmmmmmmmmmmmmmmm shame
Mwana ameneyu waganiza bwanji ?,waiwala kut akulu anapha chasowa ndi chigawenga eti ?zake izo.
Mudyereni ameneyo akapusa….chemwali
Kukwatira Nkazi Amene Ndi Mwana Kuyelekeza Ndi Iweyo ,pa Chizungu Imatchedwa #mukhitorisation
Malawi is full of haters! Definitely the woman is old enough to make her own mind and her own choices, why all this venom? Let God judge him if he is in the wrong.
Iweyo zut mamunayu ndi manthu sukuwona Kapena sukuziwa mwana ameneyu oyenera atatengana ndi misinkhu yake kut azakamukwanisa koma madalawa si pa weak izikamunyenga masiku atatu Kapena awiri koma round imozi tangoganiza
Nde iwe chikukukhudza ndi chani olo atakhala kuti sakupanga ndi komwe? None of your business, pangani zanu!! Stop poking your nose in people’s affairs and start doing your own things! Uyu mukulimbana nayeyu si size yanu, zake zinayera kale kale, samakupemphani, samadya kwanu, koma inu mulibe zochita mmalo mopanga zotukula myoyo yanu muli busy kupanga za ena. ….njala, nthenda, NSANJE…. Si inanane national anthem yathu
Tell them…..I have a handful of poky ppo too…..just get a life ppo….
Vuto lanu ndichani nsanje basi.wakuwuzani kuti mkaziyo ndimwana ndindani?mufune musafune akwatilanabe asafuna aziphe.congrats mr mukhitho.inu ndiye ndani kupanga judge anzanu.the wedding was massive.
Ngakhale Atakwatira Wa 20years A Police Salakwitsa,
Chikondi sichiona kut uyu ndi wamkulu.Nanu bwanji mukusilira kapena? Kkkkkkk
Sitikusirira koma ndi size ya Bambo ake imeneyi komaso bamboyu anakazipatsa ulemu Nanga zoona azikamuvulira mwina ngat ameneyu manyaz alibe
Kkkkkkkkkkkk.
Pa chitonga tititi nkhukoliyera kooo adaa tisabise APA koma kunena choona this is child abuse, kaya mkana paka mawa koma malemba angawa sasintha ndikuti child abuse
Many of these people are jeolous love is between the two of u congrants my former IG.
Akayanjana alekeni kkkkkkkkk
Mukhito sapepesa kkkk that was a speech made by the late Bingu during that time!! I knw this man Mukhitho!! But for the past yrs where was he???? Why having a wedding this time??? That’s child abuse cz the woman is too smaller than him and can be in prison for 14 yrs !! That’s part of difilement
Palibe chodabwitsa, Mukhitho ndi waPolice paja.
Ayuneco munthu wakwatila mwana wake uyu
Kodi Bambowa sakuwapeza akazi amisinkhu yawo? Komanso mkaziyu waonjeza, bwanji walolera mwamuna Wa nsinkhu Wa a Tate ake? Zomvetsa chisoni
Mukhito sapepesa, academic freedom ,wedding freedom
Who cares!!
So sad
Sapepesa nthawi yonseyi anali single kodi eti
Kkkkkkk got divorced in his earlier marriage
Kkkkkkkk Ok I was wondering kuti kukula konsekuja sapepesa
I don’t see any problem!! The lady has followed her heart desires…. Komaso tanyamata takwathu kuno too much kuchulukidwa mtsikana atani ?? Iyaaa olo ndili ine sindingamafere size yanga ngati palibe zolongosoka more over 58 is the new sexy!!!!
Wawoneka kale iwe komano vuto ndirakut a bambowo sangamakukwanise chifukwa Mafuta mu thank anachepamo
Waitha umazi yeti.
The lady has followed the money you are very right
Congrants Mr Mukhito zikumupweteka akagwere mwamuna sakalamba
Kanwana ngati kameneko kungofuna pogona ndichakudya eti dyera ana amasiku ano
Hello young lady! How do you expect to get anything from that old Madala with Obesity not other than Money? If you want 3 to 5 then go on your way.
And mmene ndikuwawonela madalawa akutupilana@ kunenepa komaliza.
Lithanso pompano, akwatilanso wina, Shameless whore.
size kukana section……………. girls abuse mukhito nooooooo 0/100
Ngati akazi enawo sanamange nawo ukwati vuto palibe
Bola wawa belekela ana sichoncho?
I hate such kind of a comment.
Munthu ngat watenga mkazi osamanga naye ukwati olo mutakhala zaka 40 chimenecho ndi chibwenzi olo mubelekelane ana ndizachikunja zimenezo kuma ngati anadalitsa banjalo ndye Ku catholic sama Lola kumangisa ukwati ndi mkazi wina ,komano inuyo ngati muli ndi umboni oti anamangitsapo ukwati mkumusiya mkazi yo mkutengaso wina ndye kaneneni kwa bishop kuti wansembe wanu wapanga za chinyengo
Anawa akukanikana ndi size yawo chifukwa cha mbongo wise achinyamata mfemfwe alibe thatswhy tu madalamadala akumadya mwafresh,mafanawa dyera
Mmmmm, muthu uyo anakwatilana ndikale, 2000 if nt a mistake only tht angopanga ukwat,
Definately your a liar! go to the link you will get everything. In 2000 she was 10 years old, so how on earth someone got into marriage in such age?
Peter Dennis Mandevu link ikuchedwesani
Dyela ndi ndalama atsikana .People with age gap of 32 years, what can they have in common ?
He might be even older than her father .
SHAME!!
Kkkkkkk
MUKHITO mngosalakwa,,,kukwatirakwatira mkwake,,,chatsala mkut anawa ampatse matenda bas,,vuto nd atskana akumalaw kuno,,akukwatiwa amuna okalamba kale kut azalandre petion yake,,,mpaka mkaz nkhope kumankhwima @ kudikira kt adzakwatirane nd msilikali,,kaya wapolice,,sakusiyanitsa dolla nd banja…
Marry some more have more kids bro
Osangokwatilana mwachinsinsi bwanji?koma akulu akulu ena aboma ndi mbuzi
Koma Ho!
Kuluyu zokwatila kwatila zimamukonda nanga pa four times
Ku kwatira kosatopa nako kkkkkkk chaka chamawanso mumva kuti wakwatira wina , tinakadyabe ukwati wa munthu wakulu mpaka yesu azabwere basi
All the best
When you’ve done abad thing people talks, when its a good thing …they still talk badly!
What the hell is wrong with people?
Mukhito sapepesa
Ali ngati mwana wake .koma akazi enawa alibe mantha.
Nkazi ameneyi ali after money basi dats y walolela kukwatila nkhalambayi ali ndi chilinga
Za ukwati ndi zapansi pano kumwamba kulibe ukwati. Iwe sungwana anthu asakukhumudwitse pali mwambi woti chikuni chachikulu ndiye chimasunga moto lol
Lol I never knew that you’ve been in Heven? would you tell us please more about heven apart from weeding?
Gold diggers, koma nde akazi okonda ndalama avulidwa chaka chake ndi chino, ndipo avulidwa sanati…..
Kkkkkkkkkkk koma yes.
“Mukhito sapepesa pazonse” musiyeni ameneyo
Kkkkk….. koma Ana amasukwano kupanda matha sibambo anu amenewa
Kodi akatolika mumalora mitala ?
Sitimalora thus y mukuona kut ukwatio sanadalise Ku Catholic Church
Koma adakali member wa cathoric?
Ayi . Self ex-communication.
Am also a Roman catholic member. As far as our church is concerning, munthu samaloledwa kupanga ukwati wina pamene mkazi wako woyamba alipo unless akhale kuti anamwalira. Ndiye inu mukuti mkaziyu ndiwanamba 3??????
Ishmael Zinali Kale Zomwe Ukunenadzo Inenso Ndi Wachikatolika Koma Panopa Zikutheka Kuthetsa Banja Loti Munamanga Ukwati Nkukakwatiranso Wina Amene Akufuna Umboni Wonse Pitani Mu January Parish Mu Archedioces Of Blantyre Ku Thyolo Mukazipeza Zimenezi Zikuchitika Osamangonamidzanana Pano Ayi.Amukhitho Sanalakwitse Thats How Life Goes
kwathu kuno kulibe zimenezo, mwina zikuchitika kumwera unless woyambayo amwalire we call it zayenda mwachinyengo last month azanu anakanira kudalisa kuno
Ngati mkazi woyambayo sanamange naye ukwati,chimenecho ndichigololo/ukwati osadziwika pa church,koma ngati anamanga ku church ndiye pamakhaladi vuto,bible izi ndiye sili chotsera
wansembe adamanga ukwati umenewo simkatolika!
Wamsembeyo asiye ntchito basi
Pipo pipo siyireni kake munthu hahaha
Akathetsa banja coz of chigololo zimatheka
Koma zikumveka kuti mkazi ameneyu ndi wanamba 3 ndiye kuti awiri enawo amapanga nawo chigololo???
Nzodabwitsa Zimenezo? Nzowonadi Kt Akatolika Mkaz Akachita Chigololo Banja Lithe Thats True,amene Atsutsa Anditsutse,
Kkkkkkk Odi Uko
kkkkkkkkkkkk koma ndiyeee
Mkazi samachepa mamunaso sakalamba mau akutelo. bola chikondi basi.
Congrats..!
Mkaziyo akungofuna kumunyambitila ndalama mkuluyo
Smile u r on the camera
Blesser bless the girl ndalamazo adya ndisize zake.
58-26=32 eeeeeh bola akanakhala 58-32 kkkkkk
MMMM komabe man. Katenga iyeko nde ndikafresh pamene mbwiye nsana wayamba nyamakazi, axikakwanisa kundalama Koma sangaka kwanise kuzilako lako, nde poti aganyu tilipo igwiridwa basi kakakaka
Mkazi wake wakale Ali keti.cimene munga ziwe mkazi.wako woya ndi amene Amakhala kuti wavutika.nawe nthawi yayitali Akulu ngati amenewo sanachite bwino Abwelele kwa fest Lady wawo
Mukudziwa chifukwa chimene anasiyilana ndi awo mukuti ndi oyambawo..?
Mkuluyu kunyenganyenga,i know this man,mkazi wake woyamba ndi mayi ndithu wa ulemu wake waku namitete
kkkkkk
This young lady she is a gold digger trust me
Kkkkk Dintle via Scandal
Guys osamayankhura za chopongwe mzanu wapeza basi. Enanu olo ndi ukwati omwe simudapangepo chibadwire mudangotengana ngati nkhuku
Bambo ngati ameneyu angakhale mzathu
Kaya Ukwati Kaya Kukwatirana Ngati Nkhuku Palibe Vuto Kma Bola Mbanja Lanu Mukumvesetsana,ena Ukwati Lero Mawa Banja Latha Nde Chbwno Ndichiti
So wat kutengana ngt nkhuku..banj ndi banj nmbac wava kap iwe…la nkhukulo ndiloxo limalimba..ulibe zeru …
Oh anthu ndiye aombele manja four times
Ndipo chosangalatsa ndichani udalitsawo ukutha
Olo chinkhoswe cha mnyumba cha budget ya k3500 chidakukanikaninso Lol
kkkkkkkkkkkkkk koma ada chi_#Henderson mchokula mtima kkkkkkk
Kkkkkkkkk.
5th Wife?
Syz yanga2 iyi
Why is he on Whatsapp, when he has a brand spanking new wife….lol…
Kanyerere pa Bread iiiii kaya paja amati mkazi wooonde nde amakhala papakulu kkkk zanu izo
Sugardad
Alim’maluzi awa,afuna apezepo cholowa.
Kankazi kolimba mtima kkkkk kafuna kadye nawo za cashgate.
Funso Langa Ine Ndi Lakuti Ali Ndi Akazi Angati And Akwatitsa Kangati Obwanawa ?
Ameneyu ngwachitatu aged 26
Serious? Koma guys.
Ngakhale akanakwana 10, nanga sikuthetsa umbeta akazi padziko lapasi ndi ambili zedi adzipezako maukwati.
Zikubwera mochedwa
mmmmmm bodza werengani nkhaniyo akut mkaz uyu ndiwa # 5
Koma Ndie Zausilutu . Kudzimva Ndalama Kumeneko ?
Ofoyila, adyela, aziphuphu, ndi amene akulola kudalisawo chifukwa akuziwa lemba.
MARRIAGE FOR MONEY
Ur In-law
Kkk
Makonda makonda paja buluzi anakonda khonde…
Kikkkk Mukhito weds eti? anyway zabwino zonse, kumakapepesa koma m’banjamo
Anthu akulu akulu kumangowononga ana basi
Longosi mwanakazi uyu nimwana yayi. She is in her early 40s. Akawa limoza na ankhazi wane ku Chayamba Secondary in 1996.
mmmm Rachel bodza
Mwamvatu bwana Omega Bema ,when commenting atleast have little information of what you are commenting. And kuononga mukunenako in what way
Futsek!!!! Pamenepo ndiye timve ziti? Link ikuti ali ndi zaka 26 , and iwe #Rachael_Junior_Gausi ukuti she is in her early 40’s . which is which?
Iwe Peter Dennis Mandevu khulupililani zomwe mtima wanu ukufuna. Mkazi ameneyu ndi Chance Mwale analemba form 4 pa Chayamba Secondary School ku Kasungu muchaka cha 1996, kuchoka 96 kufika 2017 padusa zaka 21. Sovani masamu pamenepa.
Zimene wanena Racheal Gausi jonior zowona primary anali pa Raiply bambo ake anali driver kwawo ku Engutwinl i no her simwana amenewo ndipo anakwatilana kalekale