A Roman Catholic Father has been arrested after he was found performing sexual acts on a 17 year-old girl.
Dedza Police spokesperson Edward Kabango has identified the Father as 60-year-old Andrew Timpuza who is based at Mtendere Parish.
He said the Catholic priest was caught red-handed at Malawi College of Forestry campus with the girl who is in Standard 4.
“He packed his car in the bush and was found touching the private parts of the little girl in readiness for sex.
“He was attempting to have sex with the girl but was disturbed by the forest guards who found him while romancing the minor,” Kabango added.
The Father has since been charged with indecent assault and he will appear in court soon.
He hails from Nkutu Village, Traditional Authority Kamenyagwaza in Dedza district.
ZIMANDIKHUDZA KUVA NYASI ZA ATSOGOLERI OPUSA CHONCHI,KODI SIZE ZAKO ZA 60’S SUMAZIONA?,UKUFUNA IFE ANA POZAKWATILA MWANAYO TIZASAMBILE ZIMATENDA ZAKOZO?,A BOMA/MABUNGWE OSAMUTAYA AMENEYU OFUNIKA AZAKHALESO MFULU ATAKWANITSA ZAKA 74 (60+14=74) ADAYAMBA KALE ZIMENEZI,inu mukadabisalanu vulilatuni mikazo yanu mwalephela ntchito ya MULUNGU
Mpingo Catholic Ukuyenela Kukoza Pamenepa.Kukwatira Si Uchimo Ai.Uchimo ndi Umene Ukuchitikawu.Mukuyenela Kukoza Panepa.Simukuona Kut Mbiri Ya Mpingo Ikuwonongeka Chifukwa Cha Anthu Osakwatira Ngat Amenewa?
Why can’t he resign and join us the non celibates
Kunyenga timanyenga koma kukwatira ayi
Too bad
Devil Be Out Ov The Father
Devil Be Out Ov The Father
Ma church enawa ine iyayi, posachedwapa mumapanga njira ya mtanda lero mukugwililira mwana kapena ndie UkALISTIA uja m’matisokosera nawo uja??(if another priest found plz send him here bcoz he need deliverance).
Kitkitkitkitkit mwandiona Ine ndakomemta nawo????
AKATOLIKA NONSE MANYAZ BWANJ APA?ZAMANYAZ NDTHU
Good news oyes !!
Kwavomerezedwa ndi mulungu kut ngat mwaziona kut mwakula pezani mkazi kapena mwamuna oti mukwatirane naye.Sono zosakwatirazi anakutumani ndani?Taonani sopano mukugwa mu uchimo,analemba pati?Thats wy Iam amuslim coz chimaendera malamulo amene mulungu anaika.
Koma Ku Malawi Mmmmmmmmmmm
Sizoona
Komano zaka 17 std 4 zangochepa ndi zaka koma maiwo ndi mai ndithu
Komano zaka 17 std 4 zangochepa ndi zaka koma maiwo ndi mai ndithu
Mentally Challengd
Yaaa that’s true nature can not be controlled
wow, a 17 yr old still in std 4? or may b you wanted to say form 4? ok. believe in God not people
Kkkkkkkkkkk..
Komabe tisaweluzane apa inde afr awonekela nanga inu ndi ine zosaoneka zija bwanji?For He who said don’t still said don’t commit ,,, ,,,,.Tonse mngochimwa tikauyankha wobisika uja.
Komatu adafuna okha kukhala father ndiye lero zakhala bwanji father kufuna kudyanso?
kkkkkkk(GOD)
Amafuna asnthe oil aaaa!
Its part of Satanism
Tsono chokumangira ndi chiyan ngat wampha munthu kapena wagwirira mesa zinali zogwirizana, za ziiiii
Nothing to say
Kod mmayesa inalowa
nayeso ndi munthu mulekeni
Kkkkkkkk Mahule osewa? W@ a shame!
Nobody can cheat nature. Urge is difficult to control let them marry gbam. Pope will hear this
Naye amazipepesa
Go on,that’s just behind the scene
mmm the and of world
Do not judge
Azingokwatira, kusokoneza chilengedwe ka
Vuto lakusakwatira ndilimenero,its like kumakana kudya ……osamangikwatira bwanji….u cant compete with nature,accept the truth kuti everyone need a partner
This is sodomy and Gomorah pagan (non Christian )
Is this true? Shame.
Kkkkkkkkkkk kachikenatu kameneko mwandikumbusa Wizey mkweza lamba zakulilongwe mwina pano ayimba part 2
17yrs in standard 4???,,,pali zoona zankhani pamenepa?,,I don’t think so.
Kkkkkk koma Mulungu akatiranga abale nanga mukapitiraji kusukulu ya usmbe
Mukwatirani basi
Everbody Iz A Sinner, I Cannot Change My Belief Coz Of These Stupid Comments, Alwayz A Catholic Christian Until Forever. Im Lovin It.
aika malamulo oti sangathe kuwasata,osakwata bwanj?
That’s news papers of malawi posting nonsense on public, look so much many scandals in world but u can here these nonsense all is about kuyalutsa mpingo.lets talk developed things here not as such.
Because he was a priest too much talking, has been could be a political people we couldn’t talk like that, , malawian people!
genesis 1v27) mateyo 19 v4-5) 1 akolito 7v2-3-28) 1 timoteyo 4v1-2-3) asembe kale analiko amakwatila luka 1v5-6
Mukumapangitsatu manyazi mpingo wanu ingoyambani kukwatira basi muzikhala ndi mkazi wanuwanu chifukwa mukumasokoneza ma banja a eni ndi ndalama za choperekazo.
all men(biblical term for people)have lusts and weaknesses. being a man of God and catholic priest doesn’t make him inhumane or saint.all we need is to strengthen and pray for him,yet allow the law to take its course.
Zizindikilo zakutha kwaziko izi
I don’t believe it.
Allow them to merry rather than this.Ngakhale bible limanena,”kunali kwa bwino osakwatila koma koma chifukwa cha chilakolako akuyenera kukwatira”Malamulo ampingowu salibwino
Oky! NDE why?
aliyensealindikufookakwake,baibulo linati musaweruze kuweruzandikwamwini,
standard 4 but 17 years? be serious
Good news
Priest naexo ndimunthu alindizofooka zake
Shame may God send him to hell
Ngati simunachimewepo mponyeni miyala
Nayenso ndimunthu akuyenera kupanga baxi
Hahahahaha..ndi munthu yes but he vowed never to do DAT ..
Zinangovuta these pipo amayenera azikwatira basi
Kkkk zimangovutadi Poti amalonjeza okha kti sazakwatira
Eya ka..now they are not able to keep their vows akunyozetsa mpingo ena uwapeza kuti akudwala matendawa kumati awa anakawatenga kuti matenda..mulungu akuwalanga awa
Kkkk ait ait Amazemba koma Akayamba kudwala kumatidi bwanji zachokera kti izi
Palibe cholakwika
Zabodza izi musatipusitse
Sindikumvetsa, can a 17 year old girl kukhala in standard 4. Let’s b serious in our professional
Pope anatulutsa maganizop abwino kut anthuwa azikwatila!!! Ndi anthu abwino ndiithu koma vuto ndi lokhalo bas….!
My fellow catholics just amend your Constitution and Let the Priest get Married!!
e ndibwino kungokwatira
Amwene amene safuna kumene kuja ndindani?
Azikwatila
Ife tikusowa mabanja bcoz of these devil people
17 in std 4 …… I like that 1
Let him be judged by the law
! That has nothing to do with church coz its personal
Sheeeee apa yalakwatu iyi….
So she was in std1 when she was 13years old? What will a 17year old girl be doing in std7?
Aaaaaah,
Timadziwa kale za iwo ngati ndi munthu ma feeling amamupeza baxi taona ana ansembe ife pali nkhaninso apa?
komatu amalawi24 nthawi zina mumasowa zolemba,cholinga chanu ndi kungofuna kunyozetsa mpingo wa cathoric basi,stupid.
Catholic fo ever,wachimwa ndi iyeyo ,osati onse komaso ngati mukunena zoona potinso atolankhaninu mmawonjezera maka mukaona kuti walakwa ndi otchuka.
Ndikhale mbuli pa nkhaniyi!
Why do u call them fathers? I don’t think one can be a father yet he has never tasted “the fruit ” or being in marriage. With such name FATHER he has to father children in the bush .No wonder!
we call God our father has he himself tested marriege?
We are in there. Catholic for ever more
Athu amenewa kungowachosa mumpingo musakhalenso amsembe amatinamiza Wzimeo s
”Nkwabwino kukhala osakwatira koma ngati simungathe.. KWATIRANI kuopa mungagwe mmayeselo..” Akatolika, tikayenda mmakwalalamu ana a anthu amenewa ali mitanga mitanga, Akatolika chonde masukani.. Wansembe yemwe sakwanitsa Uyekha muloleni akwatire..! Zikomo
Mmmm koma bembeke! zochititsa manyazi .koma timadziwa kuti zikachitika timavela wanthuwanthu .from kapenuka village.A Gondwe timakunyadilani.
Kodi zoti mwamuna asakwatire anayambisa ndi mulungu??? Kapena yesu kapena anazitola kwa masatanic aja aWorld population Reduce.
Mutiuzira kwa mbuli imeneyo kuti akafuna mulungu kutero sakadalenga mkazi adam anakwanira.
Ndipo makolo ake akadachita zimenezo iyeyo akanabadwa??
Very stupid minded, stupid religion plan, I hope not gods command but Satanism is what amongst u ppl
Ndi anthu oti Ali ndi ma degree koma eish can’t think what is right or wrong
Only god knows best how to deal with u..
Yes anakwatira?
r u a xtian or a muslim? if u r the former then u must be uneducated xtian… maybe du u read and interprete well the bible? if u do then u wudnt hav spoken these primitive words of urs
It’s just human weakness, don’t blame all priests for a wrong done by an individual priest
Imeneyo nde yosavuta @..?CHAPONDA sakumangdwa buanj..?komaso apolice nde mwafka penapake2,,DPP ikukugwrtsan ntchto ng@ ndnu agalu2,,
Our priest of nowadays where are you leading us to? Its shame on you!
Mabasa eZANU PF aya.
1. Alphonso Plaxedes of Dzivarasekwa, Harare was killed on 10
June 2003.
2. Andoche Julius, a farm foreman was shot and killed on 20 April
2000 by Zanu PFmilitia.
3. Bakari Besta was beaten to death by Zanu PF youths at Stodart
Farm in Shamva on16 May 2008.
4. Bakacheza Joshua, an MDC driver was abducted by State
security agents in Masasa, Harare on 25 June 2008. His
decomposing body was on 5 July 2008 in Beatrice.
5. Banda (Mr.) of Shamva was killed on 24 April 2008.
6. Bashitiwayo Moses died after he was assaulted by Zanu PF
youths in April 2008.
7. Botha William was murdered by purported war veterans on 23
July 2000 inMarondera.
8. Newman Bhebhe was murdered in February 2002 in Nkayi,
Matebeleland North.
9. Solomon Bote was beaten to death by Zanu PF youths at
Musikavanhu Village inMakoni on 17 April 2008.
10. Butao Peter Tom died after he was severely assaulted by Zanu
PF militia in Mudzi North constituency on 28 April 2008.
11. Bvekera Kennias of Ward 7 Clearwater area, Chipinge was killed
by Zanu PF militialed by one Chikumba on 13 June 2008.
12. Bvumburai Paul of Shamva was murdered by Zanu PF youths in
2002.
13. Chabuka Method was beaten to death by Zanu PF youths in
Makoni on 6 July 2008.
14. Chacha Augustus, an MDC activist, was found dead in a dam in
Shurugwi on 10December 2001 after he had been abducted by
Zanu PF youths.
15. Chakwenya Tinashe was murdered in Marondera on 4 April
2000.
16. Chakwenya John was beaten to death by Zanu PF supporters on
2 July 2001 in Epworth, Harare.
17. Chaitama Nicholas an MDC supporter and farm worker was
murdered in Kariba on 25
April 2000. He was abducted with eight other MDC members by a
Zanu PF mob ledby Rex Chikwana which took them to Charara
Estate. The ZANU (PF) militia. His bodywas later found dumped in
Nyamhunga Township.
18. Chakwenya Tinashe was murdered in Marondera on 4 April
2000.
19. Chambati Milton, an MDC member, was murdered on 23
December 2001 in Magunje.
20. Chaparira Abia died after being tortured by Zanu PF youths and
purported war
veterans.
21. Chapuranga Lemani an MDC activist was shot dead on 19
November 2001 in Marondera West, Mashonaland East.
22. Chatunga Richard an MDC activist, died on Sunday 27 January
2002 in Buhera from injuries sustained after being attacked by Zanu
PF thugs.
23. Chibika Tatenda, an MDC supporter died on 17 April 2008 after
a purported war veteran, Richard Makoni shot him at Chibeta
Business Centre in Mutoko.
24. Chipiro Dadirayi an MDC activist from Chikowore Village in
Mhondoro-Ngezi, died on 5 June 2008 after being attacked by Zanu
PF youths. They cut off her hands and feet before burning her alive
inside her house. A vehicle owned by Bright Matonga, a Zanu PF
MP in the constituency was used in the brutal attack.
25. Chemvura Lameck, a University of Zimbabwe student, died on
24 November 2001 in Manicaland.
26. Cheu Shepherd a headmaster in Mutoko was abducted on 3
June 2008 by a Zanu PF
and later found dead with one eye and genitals missing.
27. Chibvamudeve Nikoniari an MDC activist was murdered on 21
September 2002 in Mashonaland West.
28. Chidzidzi Nancy was shot dead by CIO operatives on 31 May
2008 in Rusape.
29. Chigaga Chrispen Chimusoro died on 5 July 2008 after being
brutally attacked by Zanu PF members in Mhondoro.
30. Chigagura Zeke was fatally assaulted by people chanting Zanu
PF slogans at the Kahobo Business Centre and dumped his dead
body in front of the house of the MDC candidate’s campaign
manager.
31. Chihuri Taurai was shot by CIO operatives on 31 May 2008 in
Mutoko.
32. Chijeke Chrispen an MDC supporter died on 20 July 2000 in
Gokwe after being assaulted by a Zanu PF mob.53
33. Chiutsi Chrispen an MDC activist was murdered at his home by
armed Zanu PF thugs in Mutoko North on 27 June 2008.
34. Chitsa Crispin was assaulted by known Zanu PF youths in
Gokwe on 27 April 2000.
35. Chikomba Simbarashe – a high school teacher – at Zuka
Secondary, Masvingo was abducted by Zanu PF youths on 14 June
2008 and later found dead on 19 June 2008.
36. Chikova Simba a teacher was abducted from his school in Zaka
by Zanu PF youths and beaten to death on 13 June 2008.
37. Chimbarara Shemmy a farm worker died on 8 February 2004 in
Chimanimani, Manicaland after being assaulted by Zanu PF youths.
38. Chikwenya Richard Dzokurasa an MDC activist died after being
assaulted by Zanu PF youths on 1 May 2001 in Buhera, Manicaland
province.
39. Chiminya Tichaona died on 14 April 2000 near Murambinda
Growth Point in Buhera North. The vehicle he was travelling in was
petrol bombed by a Zanu PF mob led by a CIO operative Joseph
Mwale.
40. Chiwara Laban an MDC activist was killed by Zanu PF militia
on 7 May 2000 in Harare.
41. Chingombe Darlington was beaten to death by Zanu PF militia
in Chirumanzu, Midlands
Let who has no sin cast the first stone
Satana alibe zikomo amamutuma munthu kukachimwa yemweyonso mkutuma anthu ena amuwone kochimwa komweko kkkkk Mutimvere ambuyeeeeee!
Abakha mwaonela chani chitosi cha wa Nsembe. .
Ingokwatilani zamkutu zimene mukuchita katolika zazii bible lake liti?limene limaletsa kukwatila
Mmmmmh
Atsikana Ambiri Amayamba Dala Anthu Ndicholinga Chofuna Ndalama,,, Zaka 17 Ndiwoganiza Ameneyo Akanawakana A Father Sakanapezeka Nawo Ku Forest-ko Koma Naenso Amawafuna.
Koma nde anarimba ntmatumwana wazaka 17? Iye 60 kusyana nd 43 aaah asungidwe bas
Anatopa
Those feet look like a white person
Them can’t fight nature
kapena mwina amam’chotsa ziwanda? Shame a man of God
Ohh
Did He Use A Condom?
Ha ha ha ha
KKKKKKKKKK AMAZITENGA NGATI IWOWO NDI ZITSULO ZANJANJI .
Zoona Munthu Wamupingo Angapange Izi
Kma tikalangidwa ndithu
Kod alibe chani
He z human after all
For we all sinned and fall short of God’s glory, do not judge for we all shall be judged
Sometimes kumadzifunsa kuti why cant you just get married and by way serving under this beast wont help anything
Nkamoyo kabwerere kumudzi kkkkkk
Amene sanachimwepo ayambe kumuponya miyala wansembeyu
Glory to JESUS CHRIST, here it’s not about sexual, it’s about who was doing it?
Apostle Paul said, if you can’t excise self control get married don’t die with desire, here three things happened, one he is a priest, two the girl is young and last the spirit of lust was upon him.
Solution, Pray for him so that the spirit of lust will not go to other priest, satana is laughing right now. A true believers understand this, Pray, Pray and Pray!!!
For him I believe he can still get married to his sized woman osati makanda. She is the future and has been manipulated by him, we Pray wisdom to young girls to say noooo to madalas
Thats why i abandoned the c church long time ago.aaaaaa!full of lies
kkkkkk its not the church but him
Very Shameful and bad.,
Osaononga mbiri ya mpingo muzitchula dzina la munthu wamva iwe
Mmmmmmm whats that now to bad
Mind you Priest Fathers,GOD is WATCHING you.Read John 8
Azingokwatira awa!
yense sanachimwepo ayambe kuweluza
Kkkkkkkkk nde mwati mesa sakwatila madada amenewa anafuwulidwa kkkkkkk
Kill badi
ma siku ano 17 years ndi wankuru. how can a 17 year old girl be in standard 4?
Put him away and get rid of his church affiliation. Here, he’d have to register as a sex offender too
asamatinamize amenewa ndiasataniki.
We also have cases where married pastors are caught in sex scandals .I think its wise to let God decide the fate of our beloved men of God…stop ridiculous comments on our faith…pray for them rather
In whatever a person does in secret,,,,God is watching,,,,thus why there is a sayng lyk ‘walls have eyes’ let us just becareful wth our deeds! lord have mercy on him!
Kkkk zala zili tang’atang’a kumva shuga
osamangokwatira bwanji? tatopa ndikumva zopusazi. mulungu angakhale wopanda mzeru kulenga mamuna ndi mkazi??? SHAME!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
I am a proud catholic.
For the sake of our minors, the church, community and country, I suggest putting him away for awhile.
So embarrassing and sad!
He is a human being, he did what we are here for, as long it was not rape, it will be Catholic internal matters.
Actually Ebrahim, your comment is carrying no weight.
– no, we are not here (us humans) for sexual crimes
– obviously, this is not rape however, it is a crime punishable by State law
– yes, the Catholic Church will have its own disciplinary hearing on this however, the State (government law) is in the leading role here!
I remind u too that the girl z 16 fully protected by our laws Ebrahim Jamal
Q
Kkkkk
What does the “Public” Affairs Committee (PAC) say about this? Father Mlomole, can you address the Nation?.
wachita upgrade uyu pajatu amakonda kuchita zadama ndi anyamata achichepere.
No sens
Watch out azimayi amene mmati a father !a father MUPHIKIDWA! Zilombo izi.
Indecent assault without a complainant? Strange!!
ndy mfanayo mwat ndiwa 17 years komaso ali mu standard 4? i cant buy this.
Mmmmm
BODZA
Zaziiiiiiii,miyendo imeneyi ndiya wansembe?mwasowa zolemba eti stupid kkkkkkk amene walemba zimenezi asayambilenso kulemba zimenezi
Aliska mwachitika uli na? Mtitilengesa hakweeee!
Walakwa chani??? Amugwililira??? Ngati sanagwililire nzabhobho….men cheat
Chipongwe
you will see some pathetic people typing ‘proud to be a RC’. I don’t know when they will stop this
17yrs girl in std 4
Pali kusiyana pakati pa #CHIPEMBEDZO ndi #CHIKHRISTU ndiye,amene wagwidwayu ndi #wachipembedzo Osati wa #CHIKHRISTU !
17years old girl….standard 4?….oky?…with 60years old grany….oky following…….may the good Lord grant us his loving mercies n forgive us
ansembe amakhala ndi chilakolako koma alibiletu nkazi koma azibusa ndi ma sherkh alindiakazi mbwembwe akugwidwanso mchiwelewele.
17 years standard 4 lol eish
He is not the only one almost all priests do have sex…nyele imabvutitsa azibambo mukuzidziwa zimene ndikulankula
Pepani baba munazanga njito yolakwika,bazi itayeni mukwatire nangazi mwazegula baba!!!!!!
Amsembe achikatolika nyere
Zabodza apa ayi chithuzi mwaika apa cha ma cartoon, komanso timaiwala kut wansembe ndi munthu inu mumasiya akazi anu ene kunamiza amuna anu kukakhala ndi zibwenzi za mseli koma chonsechi muli pa banja
Nzoonz, nkhaniyi yalembedwa mapeji angapo. Dzina lake liri pompo. Tamavomerezani zinazi what matters most is the Bizzare news not the photo. Mumafuna achite kuwajambula Ali mbulanda? Muzaona nkhani INA yokhuza kuzimangilira amangoika kacartoon chabe. Nzoona izi
Ine ndekha ayayi zankutu zanu zo ayi kamban zina
the name is andrew timpuza
mmmmmmmm,hhhhh.Chilengedwe ndichovuta
Zoona koma ena akusiya zawo
Nawonso ndi anthu
Ndichifukwa nawonso amagwada pansi kumapemphera,,,,,amadziwa kuti iwonso ndiolephera pamaso amulungu…..pangani zanu abale
Khokhoko u r right ndi munthu ali ndi zofooka zake tisatengelepo advantage pa ma weaknesses a wansembe pamene ife timachimwa every time kumaonetsa ngat ndife oyera . Amene sada chimwe ndi amene ayambe kupeleka comment
Aloleni anthu wa adzikwatira abale.
Amenewo ndi amene agwidwa.Nanga amene sanagwidwe? Jahenna will be fo church leaders if not taken care of.Check this out.
Zandikumbusa post inayake yomwe Sheilkh Dinala Chabulika adazuzula Pac, komatu akhristu kunali kunyoza chisilamu kut pasa maina osiyana siyana ngat kut iyeyo ndiye chisilamucho. Apa ndakondwa pot palibe nsilamu yemwe wanyoza. Tiyen asilamu azanga tipitilize nkhalidwe umeneu. Otinyozawo asiyen chocho tizaonana tsiku la qiyama
shame
Azimayi ambiri akusowa banja coz of these ppl…osangoyamba kukwatira bwanji aaaa
Ma devil amenewa sadzatheka
Catholic is simply a wickedness of human soul.
Zoona mbeta zambiriri bwanji osatengabwa size take. Muthu wamulungu anata
kkkkk anati akutengeni mukanavomera!!! kapena tinene kuti mukanakwanisa kumufewesa kubedi?afafuna katheteka kuti afewe.
A Ngoma mukuona ngat chomwe chingalepheretse kuwafewetsa ndi chiyani
Hahahaha pastor
Andugi aiphula..
Kodi osamangokwatira bwanji?mchilengedwetu ichi kkkkkkkk
hypocrisy at its best
Amachapa ndodo yake inachuluka madeya paja zosadula
Bizarre!Malawian Roman Catholic *Priest Father Andrew Timpuza Caught Pants Down.*
*Wonders Shall Never End, the Police in Dedza district are keeping behind bars a Roman Catholic Priest for indecent assault.*
*Dedza Police Station Public Relations Officer, Sub Inspector Edward Kabango identified the suspect as Father Andrew Timpuza of Mtendere Parish in the district.*
*Kabango said that the priest was caught red-handed at Malawi College of Forestry Campus touching private parts of 17-year-old girl.*
*“He parked his car at the bush and started touching private parts of the little girl getting ready for sex,” confirmed Edward Kabango.*
*According to Kabango, the suspect Timpuza has pleaded guilty to the charge saying that he wanted to have sex with the little girl but he was disturbed by forest guards.*
*The Suspect Father Andrew Timpuza, 60, who hails from Nkutu Village in the area Of Traditional Authority Kamenyagwaza in Dedza district will appear in court soon to answer indecent assault charge.*
What is an indecent assault really?
Good question Ebrahim, Google it.
Charge Him Fairy And Accordingly To Story Iz
Charge Him Fairy And Accordingly To Story Iz
Mmmmm! mulungu awakhulurukile pa zomwe achta, bcz azibusa ambiri masiku ano ndichoncho kmaso chikhristu ndmtima wamunthu osati ma yin form amene tmawawona mu mipingo ayi!!!
Masiku osiliza athu azalekerera ndye osadadwa izi ndi zizindikiro ananena kale muthu wanzeru angosiya machismo ake omwe akuchita ndikukonza njira yake tikati tiyambe kuweruzana pansi pano ndye tichedwa guys.cz masikwano ansembe,azibusa,mashelkh,mabanja akuyaluka osanama.tiyeneni titemnenuke mitima.
Amapasa ulimbitso kaye
Palibe malemba akuletsa kukwatira .Tate woyera ndi yehova musamanene kuti ansembe ndi woyera.
From whom r we going to take an example? Thanks Mr priest for demostrating the reality, we know that action speaks louder than words.
Idiot!!
KKKKKK chizungu chake mwat performing? Koma nanu a fazala mukutichititsa manyaz bwanj…ndye kut azimay onsewa a size yanu simukuwaona et? Kkkkkk nafuma tchalitchi linu
amafuna adye ndi maunda omwe
Kkkkkk edson
It would be better if anyone could be like me except these chains but in order to avoid falling into sins everyone must have one partner…….. The Apostle Paul*.For a man not to marry is not God’ s commandment rather its a church rule.
When Jesus ascended there was one religion called (Pentecost christianity) and the 12 disciples they were split world wide to spread Gospel and they meet once a year. Now One apostle he was preching in Rome and that He was bought with money and he introduce his religion under Roman empire. therefore there were apostles in the west and East regions. The true religion is not from Roman Empire because he was bought with money and its where Roman Cathoric was born.
not correct
yemwe sanachimwepo amunene priest
Kulibe wambeu tisayankhule zambiri apa,ngakhale awa mukuti abusa kaya a Profeti nkhani zake zokhazokhazo,opusa ndi awo akumavulira ansembewo,anavula yekha ameneyo nzogwirizana,anawo daily akumanyengedwa ndi anthu ngakhale akuluakulu aboma akuzichita koma ndalama ndi yomwe imawayankhulira,enanu uhule thoooooo ndiye muziti chani apa iyaaaa lets talk developmental issues here!!!!
Mawu bwana!
Thats why christianity is a free religion you can create a church and put your house ordres unto the followers. I wonder when will many realise that they are following man’s orders not that of God . Imagine the world without whites lies
Kunyozetsa ntchito za apostle Paul uku kkkkkkkkkk
guyz amvetsetsen anthuwa amalumbira kt sadzakwatira osati sadzagonana ndi mkazi.
Kodi amene anakuuza kuti chikhristu ndisakwatila ndani aroma ndinu anthu omvetsa chisoni nanga pamenepa palinso umsembe apa caus bola munamakhala ndi njira zophera chilakolako for ever mkumati ndine wamsembe bola koma kupita kumsembe uli wa mphumphu limenero ndibodza caus mmene ndimadziwila ine mamuna akati akufuna mkazi ndi matendanso apadera ndichifukwa chache ena osaupeza amagwilira chitsanzo olo nyama ngati agalu amalolera kuyenda tsiku lonse kuti mwina angaupeze kumedwa mkati koma osabwelera ndiye inu amsembe ndinu wotembeleledwa kwambiri chimdala cha za 70 chakuti kutenga kamwana ka 17 satana ofunika akalape kundende akatsogolere misa kumaula
is the guy under police custody, I mean is he locked up?
Plz Avoid Arguing To One Another,coz Knowingly God Say’s ‘ I Knew Wile U Were On Your Mother’s Womb That U Ar A sinner ‘ So Its Normal Evn If The Followers Of Boko Harham(muslims
Let him rote in jail
Nature things
Not a surprise to me
chinyongeni chimenecho chikunyozetsa chikhristu,chinatani kusankha kukhala bar man
tangoyambani kukwatira agalu inu m.mm zilako lako ndi mwana yomwe ..chomcho azikazi anuwake mukamawapemphera zimatani
Father man must marry the girl o
Timati kwatilani koma ati ife timapilira analemba pati kuti kukwatira ndi chipsinjo Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk nde Apa wayaluka ndi ndani Si mpingo wanu kkkkkkkkkk Roman Catholic mother of all false churches musova ife mulungu anatilengela akazi ndipo tikunjoya mosabisala stress free
akaweruza yekha ambuye patsikulo
I will apply to the court to suspend this demonic church
Njira….ya Ntanda…kkkkkk…..
hahahaha arrested? umangodziwiratu kuti nkhani yabodza iyo
Nawoso ndi anthu amadya
NDI KHALIDWE LAWO OSANGOKWATIRA BWANJI? AKAZI ONSEWA
Amene sanapangeko tchimo ayambe kumugenda zimayiyu!
azingo kwatirana osanamizanapo apa kuti ndi ansembe pamene machimo ali bwebwebwe ndizimenezo zauulika
ndi munthu nae amamwa water ngati u
Nature
No one is holly
Nature
Ameneyo nde mkatolika amene ndimamuziwa
That 17 year old girl is in standard 4 or form 4? Iam lost
sikoyenela kukhala ngati Bakha 0samba pamwamba mkat ayi sichikhristu chimenechi.
palibe olungama apa ….
Nkaziyo Amangidwenso Achimwa Onse.anthuwo adagwirizana osati olakwa ndimmodzi ayi,chifukwa choti asemphana chichewa ndiye amangidwe??,law enforcers y?
We are all prone to errors, lets help each other & b salt & light in our communities, blame game can’t help pray 4 him instead.
Palibe chifukwa chomumangira apa ndipo ameneso wamanga mzakeyo mumufufuze nayeso ali ndi zofooka zake.Palibe mngelo padziko lapansi.Mukufuna alape pamaso panu mmene mwamumangamo
Ngani mwayambayi akufunika serious kazidyanani
Wamsembe naye amavaso njala dats y amadyaso nsima,alekelanji kupana?
Kkkkk chilengedwe shaaa!!!!!
Bola akanangopanga chigololo basi, kma Defilement mmmmmm,anyway
Kkkkkkk ,palibe ntchimo lonyadilisa but wansembeyu walakwisa osamuikira kumbuyo aaaaa
Usaweluze zako ife ndife ndani kuti tiweluze don’t forget we all God,s children.
do not following what jesus was doing nthawi ija inali yina & tili m’mibadwa yina palibe wopanda zilakolako pa dziko la pansi kwatirani ndikupiliza utsembe wanuwo ndikulalikira muchowona Aaaaaaaaaa A Roman catholic mwatani. panopa titati tikhazikitse kagulu kuti kafufuze za ma kaya mumati father, mother, sister, brother mumva zambiri Eeeeeeeeh! Kaya.
bt sizikutanthauza kt ife tizisekerera zimenezo,the sin has no excuse my brother
some sins are given ndichaziwikile kuti munthu at a certain time azakwatira azakwatiwa si tchimo ayi, nanga anzathuwa?
who tod u dat priests do not hav sexual feelings? du u mean kt jesus didnt hav sexual feelings? i pity ur poor and uncivilised comment and u inclusive….
is sexual a scandal #precious ndizimene ndimakama thus why ndimanena kuti palibe amene alibe feelings pa dziko la pansi and why this priest wakhala mutu wa nkhani mu nkhaniyi u have to understand be4 commenting WHO IS A PRIEST when we go to ROMAN CATHOLIC?
Celibacy must be abolished from lmmediate effect,zikutichititsa manyazi Ife.The canon law yakhalitsa.
Romans 3:10
ndani m’modzi mwa inu sanachimweko kuti muweruze zimenezi?palibe zachilendo apa coz mipingo yambiri azibusa apangapo izi koma kungoti ku catholic asembe eni eni anakondadi kutumikira mulungu samapanga izi mpaka ukalamba wawo koma enawa oti ntchito zikuwasowa ku malawi kuno emakajoina ku catholic kuti azikapezako zosawa zawo osati kutumikira mulungu kwenikweni ayi koma ntchito zinawasowa ndiye asembe enieni alipo ozigwira ndiye tisaweruzane ngati tonse sitipanga
Mapaziwo ndi nkhaniyo sizikugwilizana
17 years in std 4 hahahaha r u serious olo ukungofuna kutsangalatsa osatira page yakoyi
Reform your rules and regulations so that you can allow priests to marry as anglicans do
Nkhani yabwinobwino ija yafika potiwonetsa chithunzi cha mapazi anayi,awiri ayang’ana kumwamba,awiri ena ayang’ana pansi,mmm,zandiwopsa
Nanga mukat sakwata kkkk
zonse ndi nthawi
miracles nowadays,
Kodi enenu simunalumbire pomanga ukwati wanu!ndipo mumachita chigololo,ana Ali mbweee mmakwalalamu,nde chadabwitsa chani?tikadziyesa opanda tchimo tidzinyenga chabe aliyense Ali ndi kufooka kwake.monga mzimayi wogwidwa MDI chigololo Ambuye Yesu anati yemwe sanachimwepo ayambe kugenda mayiyu!zili kwa inu mungotengapo nsambi chabe.
abro ndibwino kungosiya ntchito yamulunguyo ndikumapanga zimene mukuzichemererazo,mwaiwala kt mulungu ndiwasanje eti
Kuchemelera uhule Gloria? Shame on you!
Grolia Sukunamal Ndipo Anthu Ambiri Tikaona Kut Nzathu Wachita Tchimo Loti Anthu Adziwa Timakamba Zambirix Taiwala Kut Zathu Zisanaonekere Poyera.Wotch Out!
Zikomo gloria! Wayakhula momveka ndithu
Koma awawa analumbira kuti samanyenga . Daswhy faz ikutokota
Munamiza ndani mwana wa std 4 zoona? Manyazi bwaaa!
Komatu a Roma ndi a silamu ndi amozi amangowona kukangana. onse chimene amapembeza iwo samachiziwa.
Kulibwno kukhala sngle kapena ai. Kma cfkw cha dama tkhale nd mkaz modz. Palibe angazfanizle nd Yesu kma awa amafuna kutero nde ndi zmenezo.
ukwati uliwose odalisa ku mosque or church kumakhala kulumbiri. open our eyes wider so that we should not only see kulumbira kwa ma priest as a unique one. between 9 and 3 each there so many prostitutes being facked in almost all corners of malawi. most working men patronise the prostitutes and most of them went through ukwati wodalitsa meaning analumbira. its interesting some people value kulumbira kwa priest so different from kulumbira kwa pa ukwati wodalitse. stop pretending
Nkhani ili apa sikusakwatira ayi, kodi simunamvepo kuti abusa agwidwa ndi mai wa chigwilizano, onseo ali pabanja? Lakhala tchimo loposa chifukwa analumbira kusakwatira kenaka nkupezeka ndi mtsikana wosakwatiwanso? Onsewa ndi machimo ndiponso akuchita izi mu mpingo.
Kkkkkk anatopa ndikupukusa with soap
Ndinanena Mzikwatira Koma Kusamva,Kukanakhala Kuti Abambo Awo Sanakwatire Bwenzi Iwo Aliko
shiiiiii !!!!!,keep quit ndi munthu wa mulungu uyu don’t coment
Nawoso Akatolika Akunyanya Osakwatila
ZABODZA, AMAPEKA TINKHAN TAUTSILUT NDIYAN KODI
Mahule a chabe chabe awa…zachita bwino Hule modzi akukalowa..la 40 lamkwanilira..kkkkkkk.
These guys are just pretending ,God new that a man will need a woman…so does a woman.#God knows best.
kkkkkk yalakwa
A katolika.vomerezani basi kuti ma priest anu azikwatira.Papa ananena koma munamutsutsa kuti amenewo ndi maganizo ake.
So what’s news about that? Have you not done that ever since?
17 Years Walakwitsa Chani Wadya Basi Musiyeni Amulanga Ndi Ma Roman Okhaokha Osati Boma, Mtulutseni Amkwatire Basi
Mumaziyambilanji ngati mudziwa kuti simungalimbe kunyere zamgonagona… Get a lesson nigger
Paja analumbiratu kuti sazakwatila not kuti sazanyenga ofunika timvese bwino. Palibe nkhani apa. Palibe yemwe angakhare osanyena if anabadwa mwa umuna wabwino. But anthuwa analumbira kuti sazakwatila osati saznyenga. Palibe chachilendo apa
Thanx
Catholics are pretenders…kumabisalira mu zoovala zili zima devils …Tabangokwatirani basi. priest priest za ziiiii. Anthu awa amachuka ndi kugona ndi ana achimuna mathanyula plus kugona ndi ana achikazi amene amanamizira kuwathandiza. stupid people. si yekhayu ayi..onsewa mukwaona avala avalawa amapanga zomwezo. SHAME!!!
iwenso shupiti zako mngelowe
kkkk Zakuwawanitu man…paja mumatenga ngati angelo anu..sorry.
Kkkkkkk no comment
iwe ndiye olungama?mukamayankhula muziganiza
ndiwe opusa
akunena zoona osayamba kukwatira bwanji ngati zilako lako zikumavuta ..kapena muwauza mayi Maria akupemphereni lol
Kauzeni azingokwatira basi..si zauhule akumapangazo..
Kokokoko!! Zinvele mtolo,kungo marry basi nkhani yatha,siyana ndikuziika pamyezo wa nkhunda pomwe ndinu a nkhwangwala, ooo! Sorry maningi
ine ndinavapo ndekha muchurch yacathoric priest akunena kt,ena mukumakanika kupereka muno popeza mumaganiza kt tikamakumana m’mabottle store mumaona ngat tikumwera ndalama zanu,ifetu timamwera zathu,chodabwisa the congregation laughed ine eeeee,and ndinasiira pompo kupitako bcz ndinaona kt sizauzimu
you are talking my ccta..
this is not about Catholics
Shame!
Let God b the Judge. u cant say catholics as if all the catholics ar priests. We all seek the kingdom of God thats y we all go to church others to mosque just to learn the scriptures through the pastors,priests,sheikhs. it doesnt mean kut onsewa siochimwa. ndiochimwa ngat ife tomwe and remember, machimo onse timachita ar all of the same level pamaso pa mulungu palibe zokut ili ndi tchimo laling’ ono or lalikulu. with yo comment zikungooneselatu kut u really hate catholics for no reason bt wether u want or not, they were,they ar and they will b there so stop hating and lungamisa njila yako instead of following other ppos congregation nkumasaka kut alakwisa chan.
A catholic nonse ndi a gulukunyinda iiiih sorry
and it seems like u r a Muslim. hw about I remind u about the islamic state. hw about boko haram and many more others. killing millions of innocent in the name of islam. look at hw innocent ppo ar dying in syria,nigeria, pakistan, somalia, Egypt. Its A shame to kill millions of ppo in the name of ALLAH
and u call it Holy war. WTF
Iwe Highlands Tangopita kwa ma the so called priests akowo ukawauze kuti apangitse chinkhoswe basi. Aaaa man, ma engine awo ali hot hot u priest sangaukwanitse. malo mwake ndi izi..kuyaluka.
Kkkkkk chilungamo chinayandikana ndi mwano
APA nkhani ndi ntchimo,koma so catholic yokha u are saying much bcz they don’t marry,one where lam mbusa Wa mpingo wins anagwiririra mwana Wa 13yrs anamangidwa but sizikulakhulidwa choncho,do u mean anacita zabwino bcz amakwatira?its all about sin,the devil is ruling let us pray for them and ourselves bcz kumwambako kulije gehena LA ubusa or LA munthu wamba.mulungu awakhululukire ndikuwatsogolera kuti akwanitse maitanidwe,chikhumbokhumbo Ali nacho chotumikira iye namalenga
zaziiiiiiiiii zopanda mchere
kkkkkk They will start getting married ? lol…Is it the same God who will allow them to marry ? MAN MADE LAWS ARE UNSTABLE ..they added, now they want to remove it..This religion is really a big joke..
just like islam
until u stop killing ppo,then mungathe kumaloza zala anthu ena
No Islam is very stable my friend..we don’t have that childish things in Islam..it is only in Christianity mainly Catholics..
Paja mumakwatira akazi 6 aimbwa inu. The rotten priest doesn’t destroy the faith of the Catholics. We remain in faith because salvation is divine and it has nothing to do with marital status of a person. I know there are some sensible moslems than this stupid niggar.
bola kukwatirako..koma kumangopanga uhule nde zichani..In Islam it is allowed to marry only up to 4..maximum..but your priests are having more than 5 zibwenzi..ana achimuna ndi achikazi omwe plus azikazi a ma church members. this is not religion my friend.
Paja muhammad anatenga kazaka 6 et?
am telling u buddy, am proud to b a Catholic. what ever u say wont change my spritual faith. and we all praise one God. ndichifukwa mukungophana inu chisilamu muzina la mulungu. its a shame kut the whole world everyday ar listening nkhan zoipa zokhuza inu achipembezo chachisilamu especially for killing innocent ppo. look @ gadaff, he was killing,torturing innocent ppo in the name of chipembezo, look at osama, he was doing the same thing. look at terrorism is all about muslim buddies. thats what u kno best, killing ppo in the name of Allah nkumaganiza kut mukaziphulisa bomba mukapha anthu ambili mukatelo mukalowa muufumu wakumwamba mng’oooooo. u r going to hell brethren. the hell fire is waiting for u and God will deny u kut sananene kut muzimpha anthu muzina la iye….
Out of topic che blemo
Ansembewa abale akanangowalola kuti azikwatila basi.
anthu achifwamba inu. ku syria c hw ppo ar dyng. nkhondo yosatha yazaka zaka. ku Egypt.israel.nigeria.somalia
Sorry nkhaniy ndimayankha kuseliku
Ngati pali muthu ofoila ndiye ndi wa nsembe mmene likomera banja iye mkumakhala osakwatira ndikumapanga chigololo mozemba ndiye akuzembera ndani a roma changamukani
Asilam Musatiweluze Ayi, Komanso Who Do U think u r in the presence of God haa holy? you fuckin terorist. no place in heaven for all ant jesus
Musanene zambiri tchmo wapangalo ndlake sanapangre anthu kapena akhristu amene amawatumikira, zmenezo ndi za iye ndi mulungu wake amene amamuzembera nkumakachta chgololoyo.
Kkkkkk kaya zawo izo
Kod zot amsembe asamakwatile mu bible zili pat?
God have Mercy on yu. We are there we shall be there & we will die in there.
Proudly Catholic church for ever more
Daud
Church is a pillar and foundation of the truth. Timothy 3:15
They did not say Bible is pillar and foundation of the truth, No
So u were supposed to know.what is church?
Palibepo cholakwa apa
Walakwitsanji iyeso ndi munthu. Apolice omwe amumanga usiku wapitawu amapanga zomwezo zango siyana ndi ntchito zomwe akugwira.
mumpatse milandu iwiri wina okana kukwatila,,,,,mabanja akusowa chifukwa cha anthu amenewa
A mishe can u share with me how u write in colors?
Ansembe kupatsa manyazi kwake, iya
Koma nkhalan serious a Malawi 24 17 years akakhale standard 4 inuso mbudzi zaanthu eeti
This is the main challenge for Catholic priests. They have children all over and yet they dont want to marry. This is away of running away from responsibilitues of a biological farther. Spare us of your trash.
Why dere punishing themselves?Maybe da competing with Jesus christ bcz he didn’t married?
U preach and u have to have good carriber as father of words, but anyway you are human anyone can sin let us pray the God father to have mercy on us sinners
Kkkkkkkkk
amalawamuchere kuti wadzuna
Kkkkkkkkk its tym 4r secret issues be on public
Mine, 9 years old is in std 5.
Kkkkkk ndani safuna kuusumana.
Nzimene amatha zimenezo! Inuyo simmadziwa nthawi yonseyi?
she left in std 4 lst yr. she was say it wz 2nd tym.
Are those he’s feet?
……& hers
??????????
Nanga inu Becky Emmah Sitima what sort of rubbish is this?
Tikati tilimbemachimo tizinyengatokha
zapa tchire zimakoma mbewa…kkk
r u serious?
she z 16 yrs old. i asked her at dz hspt went she ws tested at vct. last dy gays. lets pray.
Muloma amayesa zida
17yrs? let them settle down n’ get married!!
Hahahahahaha
every one have feelingz there iz no way to controll when iz calling iz ahuman being
17 years in standard 4???
Remember he also hav feelingz
Ayi asamakwatire chifukwa kuu nsembe sachita kukukakamiza ayi
Boko halaam
Izi ndi zomwe anthu awa amapanga nthawi zonse nchifukwa chake Papa anayankhula kuti ansembe ayambe kukwatira ngakhale ma bishop a mdziko muno anakana kufuna kudziwonetsa olungama kwambiri nkumanena kuti zimenezi sizingachitike.
17 yrs ndiwankulu, paja munati zaka 16 akhoza kulowa mbanja
Amatelo aziti ndi olephera amenewa magulu a pack.
Is he arrested because of doing sex with a girl or being Priest?
The girl is underage
Lets Not Pretend Scandals Should Not Be Attatched To Particular Church,, They Can Happen To Any One
Lets Not Pretend Scandals Should Not Be Attatched To Particular Church,, They Can Happen To Any One
No no no…Catholic priests say they can stay without women…that’s why it is a scandal..if this happened to any other man it wouldn’t be a big story worthy attracting everyone’s attention.
Kķkkk akatolika
Amango Znyenga Ku Funa Ku Fanana Nay Yesu Bola Azkwatila
vuto lake lomatengera zithu ngati zinabwerela iwowo, priest? chigololo ndi chokoma ichi
Aliyense amakhala ndi chilako lako guys tisamunyoze munthuyu chifukwa kuti zake zaululika! Nanga akanachita chani zinthu zitavuta? ???
Zamanyazi!
Nature pa ntchito yake
Watch out for part two
Shame, But Plz Allow Them 2 Get Married Filling Is Nature
Straight
Do we have married be who committee aduttery? committing a a sexually related sin has nothing to do with one being married or not. use our brains to reason. hav a wide look on what makes someone to misbehave the way the said priest has acted. there are married people commiting the same sin. wake up.
17 years girl standard 2 ¿? comeon Guy’s
zma last #dayx.
.
akadatani munthu wamulungu?…its #nature!!!
kkkk kudya nkhosa lol..
Aroma mwapezeka
papa john paul must hear this
Aroma Diana a satan
mbwenu muwazomelezge kuti watorenge wanyithu awa
Shame on that priest,but alot more are doing the same kungoti samagwidwa.