MP Felix Jumbe has more ideas for Malawi: change the national anthem


Felix Jumbe

Member of Parliament (MP) for Salima Central Felix Jumbe has asked government to change the country’s national anthem saying some words should be replaced with positive words.

Writing on his Facebook account, Jumbe said the Malawi national anthem needs reconstituting by removing the words hunger, diseases, and envy. According to Jumbe, a state that is defined by such words in its national anthem cannot develop.

Felix Jumbe
Felix Jumbe suggests alterations to the national anthem.

“A state defined by hunger, disease and envy has no future,” wrote Jumbe.

He further said that these unpleasant words used in Malawi’s national anthem make the country’s citizens to be locked to the ground.

“No creativity, innovation, patriotism, statehoodism, no shared common purpose and full of infighting scrambling for the little resources and the business of people is running government and not engaging in economic activities.

“Our creativity is envy aimed at damaging one another. We are a people who get more excited with failure than success,” he said.

Jumbe expressed hope that replacing the three words in the national anthem would reengineer the minds of Malawians.

The current Malawi national anthem was composed by Paul Sauka who died in 1990.

The anthem was adopted in 1964 as a result of a competition.

627 thoughts on “MP Felix Jumbe has more ideas for Malawi: change the national anthem

 1. a jumbe pajaso chamba chaku salima ndi moto musaiwale osamasuta kwambili mukamakalowa mu paliament bola muzingolimbikila kudya msombazo tinakuuzani kale Ganja sikuyanjani koma kusmva abambo inu!!!!!

 2. Ngakhalewanene zakumalotozakezi chiwinileni sanabwereko kudzanenazazeru kwaokuno tinaiwalakuti tilindi MP oky! isinthidwe tiziimba MULUNGU dalitsani JUMBE kkkkkkkk akanasuta akadanenazoveka koma anachitachakumwa zachisoni!

 3. Fuck you Jumbe who the hell think you are? to change national Anthem. You think changing national anthem, will bring development in city or local community. and I think that you’re also the one who bring ideas of R2000 notes. one thing I can tell you is if you want to be famous than ever go in the Forest kill yourself,, by the way #Suck_my_Dick_son_of_bitch

 4. Jumbe or jumbo This is shit from Your mapwalapilila ithink u bought a certificate thats why u are dom not Free uare Ediot wasting Money and Time for My lovely Malawi

 5. Chisilu iwe wadya manyi eti? Ngat wasowa chochta usatikwanepo apaa wamva! Country is experienc lots problems, instead of u stupid anthu amanyi pakhosi kubwela nd gud ideas 4 country development eeeee usayelekeze kutelo . KATAWASEN UKOOOO…!

 6. The Malawi National anthem is a prayer for the nation and it stands. We don`t need crooked ideas on that. Fight for the better salaries in civil service and not your names when in parliament………..

 7. kkkkkkkkkk koma dzikoli guys atsogoleri ake saganiza mwavaa? ? kaya ndi ganja kaya iwe zoona utakhala kwanuko mmalo momakwatana ndi nkaz wako uli basi ndisinthe national Artherm? galu iweti mbuzi.

 8. Nde zachamba zimenezo, sangamaganize mfundo zothetsera umphawi mdziko muno koma kumangokamba zambwelera baxi. Stupid idiot ayesere kupanga zakanundu zakezoo aone

 9. Andale A Kumalawi Amapita Ku Parliament Kungofuna Ma Allowance Basi,mmalo Monena Mfundo Zenizeni Zotukula Malawi,nd Salima Central Busy Kumanena Zinthu Zopusa Ngati Ana,shame On Salima Central!!!

 10. Zikanamakhala kuti zimatheka kuonana ndi god nkanapita ndikapemphe akutengeni agalu inu.kulibe wabwino nzeru zenu nximodzi,simulangixana.pompano mwaononga more millions.bingus tym munaonongaso ndalama za flag,apamwayambaso

 11. This anthem is a prayer for our Land if we want to run away from God’s presence do as u wish and then u will see the results of changing it think and see it If it is worthy or not b4 u tell people.

 12. pachitumbo pamako jumbe end khope ngati kunyini kwamako cz ulibe zeru ngati zeru zatha kwabwino uzikachindana ndi akazako or apo ayi uzikakhula manyi a prsnt wako wava

 13. If jumbe is going lost is much better to you jumbe to go and seek guidance and councillors for your stupid ideas, why bothering the country instead of working hand in hand to make sure that needy people are having shelter and other necessary. Mmmmm mukamupeza atengeledwe Ku mental changu misala yakeyo isanafike poti angathe kumvula nayo zamanyazi

 14. mmalo mopeleka ulemu kwa malemu waluso yemwe anapeka nyimboyi wina amvekele ndidzaisintha. zankutu basi ndipo asadzayelekeze

 15. Kuvutika kwathu simukukuona mkumakalimbana ndi zazii useless boy, unalikuti mthawi ya Kamuzu osapanga zimenezo kalulu iwe eti

 16. Mumalo muyowoye vithu vakuwovwira boma njara njikulu or panji ndarama tipangechi kuti yiwe nankhongono mwamuyowoya chithu chaziii chitima chikulu chomene ajumbe mavoti nginu yayi kumbuka wanthu winu yikoma njara National anthem yilije chifukwa ninyimbo yamutundu wa amalawi not chipani

 17. aaaaa..malo mobwela ndimzelu zoti tithesemavuto kumalawi kuno…mukukamba zosintha nyimbo…koma anthu inu mwandikayikisa bac…amalawi simuzatheka …ngakhale tisinthe nation athem mkuyikapo nyimbo za Davido..kkkkk..palibe chomwe chisinthe…

 18. AJumbe muyaluka nazotu mukufuna kutchuka siyani ndale muyambe kuimba moti nyimbo yafuko lathu idalakwika pati mukulimbana ndinyimbo mmalo molimbana ndi chitukuko mdera lanu zaziiiiiii.

 19. Izi nde zopusa.MUNTHU WAM’KULU KUMAGANIZA NGATI MWANA OKWAWA.all god bless our land of malawi. nde chavuta apa ndichani

 20. Hon think twice,a chair(muluzi former head of state) was the champion posintha mayina and the like but he didn’t reach that far mpaka nyimbo ya pfuko? Pliz think twice we respect you hon.

 21. Jumbe ndiwe wausili zithele kusalima komweko ayi uzipitsa kunyumba yaboma nyimboyo inayamba iweyo ulimimba mwamako ndiye iwe ukati isithedwa fuck you mbuzi iwe

 22. Jumbe you must start go to church antharwise uyamba kugona ndi ana ako omwe, ndakuona ndiwe mbuli!!! Mudzimu, wht kind man u don’t know anothing stop nu-sense funk you.

 23. Sometimes it’s very wise to be silent if you do not have anything beneficial to contribute to Malawians in the August house. What will the idea of changing the national anthem benefit the poor masses abwana? So you mean you don’t know the problems which need your urgent attention when you are there. Magetsi akuzimazimawa simukuona, njalayi simukuiwona, kulipira ogwira ntchito mboma pa 38…….the list is endless zonse simukuona koma kusintha national anthem ndiye problem ya anthu anakuvoterani? Shame on you honourable.

 24. He is completely lost you grew up singing this National Anthem, so please can you just mind your own business, go and seak medical help

 25. Ndiye misala yanji akuiyambayo aJumbe ;dziko lasauka mu zambiri ilo ,iwo ali fundo koma yosintha nacionale anthem

 26. Kusowa chochita eeti mmalo molimbana kutukula dziko mukugwila zinthu zoti anthu ena anazipangakale bwanji? Ngati zilinzelu pangani zanu zozwizitsa nanuso mukhale mu history yadziko kuti munapanga zinthu osagwila zoti anthu ena anapanga kale ayi

 27. Ooo..mufuna mubenso money za ife ma tax payer?nzeru zanu zokuba baba..kusintha kwa national anthem kuonongesa ndalama zoti tikanatha kugulira chimanga..nonsense

 28. kkkkkkk kd unasuta chakunkhotakota kapena cha ku Salima konko chamba chake?Nyimboyo upeka ndiwe kapena mkazi wako?Uyivetsetse bwinobwino nyimbo ija.Kapena ukufuna mukhare zokambamo zokuti anakuchotsa ku MCP?

 29. muja umalilira upresident wa chipani umafuna kuti ukadzakhala mtsogoleri wa dziko udzayambe kuchita zimenezi zopusa

 30. Let us sing Jumbe’s new song. Gonjetsani adani onse, Escom waterboard. Luzitsani mitima yathu, kuti tipilire tisakagende kkkkk

 31. Kumakhara kuziona kukura mkabudura kapena chan akukupusisayo akupwetekesa aise kulitu ophudzira kuposa iwe iweso ndiye ndan masende

 32. I now get to undertand that one of those politicians who needs a brain Doctor is you Che Dyumbe coz there must be a health problem upstares.Jumbe who told you that our lovely nation arnthem needs to be changed?aai wena man futseki

 33. Don’t try to change the Malawi National Anthem instead pls Mr Jumbe sort out the problems in your constuency we are tired with rooten ideas as you are,no more vote for you Jumbe

 34. Ndipo ngati kuli constituency yomvetsa chisoni ndi ya galu ameneyu Jumbeyu ,Ku chitchire kosowaor kogula fanta or ma units eishii baba jumbe takakonzani kwanu kuja anthu amoloketa mmabafa chifukwa chisowa mlatho NDE mudzaone za nyimbozi pambuyo.shame on you!

 35. Chokapo apo asaaa anthu akuvutika ndi njala chifukwa cha drought ndi floods nde iwe ngati mtsogoleri uzikalankhula za kusintha nyimbo kusowa zolankhula etiii Idiot

 36. u want to be changed where? Why not thinking of changing Malawi’s country Mr Jumbe its better to restart talking of federal system rather than changing of national anthem!!!!!!

 37. If you have been told to get promotion of satanism let our beloved country with national anthem not victimized on your fucken speech

 38. Imeneyi mfundo? Iwe wasuta kumene et? Osakamba za kuchepesa mavuto a mdziko, mkumangobwebweta, utakhuta ndi ndalama za misonkho yathu.

 39. Stupid and Idiot why consuming your time in such way, seems like we are directed by fools, you must follow our prority first idiot, hunger then that u think to change. fuck u

 40. If you wnt to be famous kachindile mkaziwako pa msika was nsalima wava !I will never respect u idiot! M’malo molimbana ndi njala kuti tiyithabwanji mziko lathu latendele!and u came with manyi idea!

 41. If u think dat u r a best compose don’t waste ur tym,meet werge de producer to work upon ur songs u have composed and listen with ur wife u MBUZI bwanji

 42. Iwe aMalawi salimwakale muja ayi akulodzapo apa angosiya zimenezo, kulibwino kulimbana ndi mavutowa basi ya K2000 mogwilana kuti itsike kufika pakale.

 43. mulungu dali tsani malawi mu sunge mtendere gonjetsani adani onse njala nthenda nsanje luzitsani mitima yathu kuti tisaope mdalitse mtsogoleri nafe NDI MAI MALAWI! wht a great song

 44. Zafodya ayi takana ngati mwatopa ndikudya ndalama zikutisowa anthu akumudzi muzingo pita Ku chimbudzi mwava nyasi takana,munasitha mbendela pano mukuti national anthem.NDE mukasitha zitathauza chani? Mukana badwa kale kuti national anthem mupange compose ndinuyo anzeli,chitani manyazi a jumbe

 45. Iwe Jumbe nzeru zako za manyizo uwone nazo kopita galu wachabechabe zopusa basi, machende ako + abambo ako chitsiru iwe Jumbe

 46. Ayisinthedi njala, Chaka nchaka, tikukhalira njala muno, matennda ndiamenewa sakutha mudziko muno, nsanje Nde si nkhani muno mumalawi, ndinali ndimaganizo omwewo a MP

 47. Iweyo uli maso psuu mmagalasi akowo tidziti anthu akwanuko amene anakuvotelawo anakutuma zimenezo school imachotsadi umbuli kusiya uchitsilu amene akutumawo wawuze kuti amalawi akana.

 48. I just blame the way the reporter has written the article. It is crystal clear that the article is starkly incomplete basing on the inconsistencies it elicit. Henceforth, it is a huge misnomer to blame jumbe according to this ameuterish reporting.

 49. So we must change it and bless malawi how are we to be blessed while we are lazy, kukhalira kupempha, and hatred toomucch to each other akufuna pa udindo wa president akhalepo okha okha, , yisinthike basi i support you.

 50. Educated fool is more foolish than uneducated one, mbuzi ya munthu on high position, ndie tikasintha national anthem sithandiza chani for the development of the country????

 51. Its true we must change the NATIONAL anthem why there is hunger always we face hunger… Jelousy have nsanje too much we MALAWIAN and greedy, there is fear we MALAWIAN we fear too much as a result we are coward , eg we fail even to reveal the sickness of the president.

 52. National Amthem Idapangidwa Iwe Usadabadwe Ndie Wakhuta Bonya Wako Uko Wat Tisinthe? Iwe Siudziwa Kut Ndi Pemphero Limeneli

 53. one with full stomach talks nonsense to empty it forgetting that someone needs. their help.shame on you jumbe.come to your senses MP’s .Malawi is declining while you watch.

 54. Uku timati kuganiza mopusa!! kodi akati mtsogoleli wa chitukuko ndikusintha nyimbo? aaa mukuwononga osati kukonza.kapena mufuna kupezapo mwayi wa cashgate ? kapena mukapeka yanu mukuona ngati mudzasupidwa? amalawi sitingasupe chosavina ayi.mwachoka pokambilana zotaya mimba osafusa maganizo aanthu ndipo mahule anakondwa nayo bill imeneyi.ndiye mukufuna kubweletsa bill ina ma mp owononga dziko inu.(malawi okongola mbendela yokongola court of army yokongolaso)nde ena akufuna kunyasitsa koma jumbe ndi amalawi kapena mfolena? jumbe ngati ukufuna kusintha chinthu m’malawi tenga nyanja uike m’malile amalawi & zambia.mwina tanzania asowe chochita.

 55. There is sense in what he is saying… people remember what you learn when you are Young that’s what stick in your mind…think about language you learn the language of where you are raised as a sibling…so is the instinct of the National Anthem ..we grow by it and we become it..then if it’s a negative Anthem like Ours which talks more about (kundandaula,njala,nthenda,nsanje)and many other things what they planted in Us …it’s the same things ..so if these come to Us as challenges we Say we are used to them …as a result we can’t fight them they already defeated us in our minds…Go World Wide and check which country has a n Anthem like Ours ..their Anthem they talk about happiness or God and it ends there…for me am on the side of Jumbe there is something in what he is saying…For those who don’t think deeply are the ones who are criticising this Man… it’s not about Politics here these are Ethics.

 56. Ajumbe ndale zonsezi mumapangazi koma nzeru mulibe zoona mukufuna gwamba/ gwalad ati pangile compose nyimbo ina ya fuko lathu.

 57. Ajumbe ndale zonsezi mumapangazi koma nzeru mulibe zoona mukufuna gwamba/ gwalad ati pangile compose nyimbo ina ya fuko lathu.

 58. Wayamba misala ameneyo maiko one atizungulira amayamikira ndipo amalephela kupeka yawo, amangotsintha zilankhulo,ndiye ife nyimbo yathu IJA imakamba za nzeru ,atukule dela lake ngati Ali ndi vision

 59. Chizeleza cha jumbe,chibekete chawaka,chinthu chawaka,mbuzi iwe,sumu yafuko kuona nge akapanga ninyoko panya wuso,magalasi nge kujima kumigodi,chindele eti,waka chimulomo fwizu uko,ndivo mwizira ku dpp ivo,vibanthu vinyakhe vujioneshelathu undele wawo!!!!!WE SAY NO TO CHANGE OUR NATIONAL ANTHEM,STUPID!!!!

 60. Aaaaaa aaaaaa come on guys…..these politicians they think like mad people that’s why our country is suffering……..even a child can’t think of this nonsense

 61. mmmm uyundimunthu modzi okhomelela coz ana amunthu wanyimbo lmeyo munawathandizapo chani as a nation palibe luso la bambo awo muzikhala ndiumunthu ngati anthu obeleka no benefit koma munthu uja anaganiza shame to malawi tapangani yanu timve kkkkkkk osamachepsa zanzanu ana ake palibe amapezapo chonsecho ku xool mwaimbaimba koma ndi zoona ananezo nsanje kwa basi amalawi mumangofuna ana anu azisangalala koma tsiku lizafika tidzaonana pa mtengo wa kachere ka zinyopolani kaye ndi ana anuwo

 62. Kumeneku ndiye kuwaputa anthu ali pheeee wakhuta chani kapena???zausilu bs m’malo molimbana ndinjala wakutumayo akupwetekesa mphwanga.

 63. If you have nothing to say just remain silent the whole of you , is this what the electorates told you to say in parliament?.

 64. No wonder you are fired from #MCP.You are one of senseless MP & I don`t know how the people from your Constituency will react.Have you finished developing your area?Instead of talking of hunger in your area you are busy talking shit.

 65. A Jumbe, tangopanga za udindo wanu ona kuti chakudya chilipo chokwana dziko, inu nyimboyi siili mwa nyimbo ngati zomwe mumavela nyumba mwanu ayi iyi ndi pemphero, ngati mwasowa chochita mungokhala mudziwabela anthu misokho yawo osati kutitukwanitsa ife a salima Central ayi, mwandichititsa manyaziii!!!

 66. look at him he is finished though he doesn’t know it yet. so u didnt show up at masintha simply because you were busy thinking bout this garbage. malawi yonse yaziwa lero kuti your mentally incapacitated. pepani anthu a ku salima povotera manyaka amunthu ngati awa.

 67. Ajumbe don’t be jealousy, there is only one man who composed the Malawi national anthem and this is no other man than the late Michael Sauka who was jailonh from Mthumba Village Traditional Authority Sawali in Balaka District in case you did not know. He is the heroes of the nation although he died poor. Now you want to take advantage in order to get fame, that’s not on my man. However I would say you have never composed any song in your life and you have never been a musician , You are a politician let it remain like that,don’t confuse people with your silly ideas. Bring ways of eradicating poverty in Malawi

 68. MR JUMBE,CHANGIN DE NAT.ANTHEM IZ NOTHIN,KOMA ZIJA MUCHITA NDI KUPANGA ZOLIMBIKITSA,KUCHULUKITSA NDI KULIMA CHIMANGA AND OTHER CROPS DIVERSIFULLY.

 69. Stupidity is when you are in central region mainly in salima and you are locked off from MCP and you don’t know what to do and you start thinking of joining DPP but your sense tells you that you will not inherit your seat in 2019 and then with your confused mind you start doing what MR jumbe is just doing now….iam not surprised..this man is totally confused.

 70. Akudana ndi Kutchula Mulungu, alipo wamunamiza mwina mzungu kaya ndani uko. He is like other American who want to remove “in God we trust” from the US dollar because of their disbelief in God. Koma ufufuze kuti ndi angati anapikisana ndi Mulungu nkupambana. Pali zambiri zoyenera kusintha ngakhale mnyumba mwakomo zoposa national Anthem. Even socks zako ukuyenera kusintha!

 71. to change the national anthem or the price of maize? nchisirunso eti, anthuwa akakhala mmwamba saona pansi, mukukhutatu a JUMBE eti?

 72. Vry stup man who are u whr do u cme frm ukasithe songs fm ur church just eat cash gate money and fuk u 2 to the end of ths year

 73. Who r u aftr o kunena kut isinthidwe national anthem????? Pangani zina Mr jumbe ngati fundo mlibe tangomveserani zolankhula za anzanu Ku parliament, oryt? Hop u get m well

 74. Greetings to you all, am Juliana Maurice by name i am here today giving a life testimony on how i was cured from HIV Virus, i have been stocked in bondage with this virus for 7 years now, i have tried different means to get this sickness out of my
  body and i also heard there was no cure to the HIV DISEASE, all the possible ways i tried to get heal did not work out for
  me, but i do have the faith that i was going to be healed one day. as i was a strong believer in God and also in miracles,
  One day as i was on the internet i came across some amazing testimonies concerning how Dr Abuu has cured different people from various sickness with his Herbal Medicine, i was touched and i decided to contact Dr Abuu, with that i had the courage and i contacted Dr Abuu, i told him about my illment , He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with him, he finally prepared the medicine which he sent to me and he also gave me prescriptions on how to take them, My good friends after taking the medicine for some days i started to experience changes in me and from there, I noticed the HIV Virus was no longer in my body as he ask me to visit the hospital after 28days which i did, as i have also gone for test, Today i am fit and healthy to live life again and i am completely cured from HIV virus. I am so happy for the good work of Dr Abuu in my life, Friends if you are having any type of disease problem kindly email him on: [email protected] or whatsapp him on: +23408066454364. Am sharing to save lives, please share to
  save some lives

 75. Koma iwe jumbe ndiwe nungu went weni ukufuna kusintha national anthem, wawira kuti national anthem inayikidwa iwe usana badwe, komanso, kodi anthu aku salima ngati anakusankhira zimenezo, anakusankhira kuti uzikawanenera mavuto amene anthu akukomana navo kusalimako ngati masukulu, miseu zipatala milatho ndizina zotero,ndikhulupilira upange likasa pazimene ndakuuzazi don’t speak fucken stupid things in parliament ok! Take a note

 76. Kamudzutseni Saukila mwini wake anapanga compose national anthem imenei ku balaka anagona iyeko kut aisinthe ikhale mmene mufunilamo. or else pangani yanu munthu wankulu

 77. Was the composer Paul Sauka or Michael Sauka? Tamalembani zoona mudzifufuza monga aatolankhani. Osamangothamangira kutulutsa nkhani ili ndi zolakwika musokoneza anthu. National anthem ndiyofunika kuonjeza adani ena monga dyera,ziphuphu,katangale(umbava wa mbomawu) chifukwa nthawi imeneyo zinali zochepa ndizosaonekera mwina.

 78. I sing this song since i was born, n now this stupit u call him piss of shit jumbe he must go n wash his brain or u don’t blong to Malawi n myb its time we ask umbdsman to dig a lot about this guy. This mother fucker must leave malawi . other thing take him to the doctor for brain check something is wrong piss of us.

 79. Not on our priority list.can we do more to get this country out of chained camities we are going through. A good ideancrancy is the only way out.

 80. Kkkkk zovuta kuvetsa, iwe jumbe kodi national anthem ya Malawi ili ndi ma verse angati? Bwanji osangotenga stanza 2or3. Vuto lovotela educated savage ndi limenero. Nzako bingu anasinthaso flag pamene zithu sizimayenda dziko, what is wrong with Malawian readers.

 81. Jumbe Kale Ndimayesa Kuti Ndiwe Munthu Aaaaaaaaaa Chitsiru Cheni Cheni Moti Umafuna U MP Cholinga Udzasinthe Nyimbo Yafuko Aaaaaaaa Pajadi Xool Imangochotsako Umbuli Uchitsiru Umakhala Chikhalireni Mpaka M`Manda Wooooooooo!! A DPP tengani jumbe akhale wanu!Dzina Loti JUMBE Anthu Ake Eishiiii Mbola Zeni Zeni

 82. Mwangothamangira kutsutsa akuluakulu akanatiimbira tiimve kaye yakeyo ndipo tikanafusanso kuti mwaganiza bwanji kusinthaku akamaliza kufotokoza ndipamene titsutsane naye mwatan a Malawi tinene njala imeneyo?

 83. National Anthem iri ndivuto lanj kapena ndiimene ikubweresa mavutowa mdziko muno? Ofunika amufuxe bho pot amati wamisala adawona nkhondo paja2 kkkkkkkk.

 84. iwe national anthem olo atakhala kuti anayimba ndi nkasa itipindulira chani mukaisintha, do you think it will end hunger and blackouts ,nchifukwa chani mukakhuta kondowole mumapita ku parliamenti kumakanena zinthu za mmutu mwanu when you can talk about important things that matter to us,for example why are we having water ploblems in salima when there is the lake here? i think we need o change constitution as well to say andalewa akafika zaka zakuti azipatsidwa pension you know amasunduka ana nkuyamba kumaganiza ngati mwana wanga oyamba

 85. Ngat ndale zavuta bansi kuvomereza Jumbe ,,uku mukupitaku ndimisala bansi kkkk mukufuna kubanso ndalama apa mwatikwana shupt uuze anthu amene anakuvotera asangalara nazo

 86. Some people can be stupid in mind hey….how can someone think about that and skipping current economic crisis in country which is very serious problem. I think it could be better off if he suggested that his salary should be reduced by 30%……..it’s a high time for him to look into a big picture & stop this nonsense

 87. Eish kumalawi! why God made Malawi? The so called leaders are just useless, we have more problems to solve than debating rubbish. after all who are to change that? Mwayamba liti ndale zokhoza? go to your constituency and make progress! #recyled politicians.

 88. wait until u be in power then u shall do ur mind nt nw ukufuna kupepera kwakoko upake ndani? as an MW of ur area wat meesures hv put to hlp ur ppo 4rm ur this disaster? nthng bt yet but u r bleming ppo hu r try. or are ppo hum u present sent u to say that or u&ur family?. if u r old kumakalima ngat a Tembo NDI Chimunthu nt ur bush…..T

 89. I don’t see any problem with our national anthem to be changed because firstly it mentions about God to give us peace and development for the country.

 90. Jumbe ur vry stupid, salima central anakusankha ukapemphe chitukuko, now u busy wth national anthem, mmmmmm this is ridiculous

 91. Osamanyoza komwe mwachoka, munali ndani inu kupanda nyimbo imene ija?? doesnt u mind dat this song still guide Malawi fans?? kusowa chochita bac?? utha kumakanda mapwalawo……..

 92. M’malo mopempha boma kuti likhazikise tsiku lokumbukuira munthu amene analemba nyimbo ya mtundu wathu akabwele ndi nzelu yoplayi zoona? Wakhuta zigege jumbe kkkkkkkk

 93. At first i respected this man alot i even reached to apoint that this if he wishes to stand as a presidential candidate i would cast my vote on him but with this nonses i have put him on my black list ooh death take this jumbe out of us plzzzzzzz

 94. Malo mokonza ziko mukulimba ndi nyimbo fuck you Jumbe ur kak u dont know what the meang of that song thats whay ur talking shit now fuck u filx fockon shit jumbe

 95. Chabwino tingoyerekeza kuti Pepho lanu MR Jumbe lavomerezedwa nde a Malawi akupephaniso inu nomwe Mr Jumbe kut pekani nyimbo ina yomwe iziyimira Fuko La Malawi koma mau ena musachotsemo like..Mulungu Dalitsani Malawi..Gonjetsani Njala,Nthenda komaso nsanje mau amenewa okha akhale Mr Jumbe ndikuperewera nzeru kwanuko mungaipeke bwanji nyimbo imeneyo ?? mxiew anthu ena mumafunika #Gun straight, sunachilaweko chipolopolo thats y u r busy talkng that Nonsense…

 96. If you are running out of ideas just shut your mouth. Bcoz I don’t see any harm in our national anthem. It educates,protects and unites us all.What more u want?Mr Jumbe

 97. No smoke without fire things are going changing eg last national frag,paper money K500,K1000 and now K2000 next but people especaly poor are sing’ing the national anthem while rich people want to sing their prosperity song Eishii leaders are enjoying with money of nation.

 98. che fellix jumbe,,,maso ali tong’ooo mmagalasi ngti zanzeru uchitsilu mmutu uli thooooo…komma kumalawi guyz skudzatheka..kuteloko salima central amenewa. ndi a MP anu? kkkkkk ungoyamba kuimba fellix

 99. Mwina a 24nu simunamvese bwino guys munthu wanzeru angadendekere mutu olemera 10kgs nkumaganiza zambwererazi kkkkk nyasaland

 100. Mwina a 24nu simunamvese bwino guys munthu wanzeru angadendekere mutu olemera 10kgs nkumaganiza zambwererazi kkkkk nyasaland

 101. A Jumbe chimene mukufuna makamaka ndichani, magetsa sazimaso, athu asiya kuba ndalama boma , katundu sazikwela daily ngati mene ziri leromu, kodi anthu asiya kugona ndi njala penapake fodyayu tizizimitsila tikasuta zosadabwitsa panja ndikuchimake kwa mbwelela muliko

 102. Kodi mukuona kuti chifukwa choti muli Ku parliament tonse ndife zitsiru amzeru ndinu kusithako kutipindulira chani a Malawi osakamba za nzeru ife tikuvitika

 103. Koma aMalawi sitixatheka muzamba yotani j.c.e munasiitsa ija sidakwane timva mwasintha kamuzu central nkukhala Peter hospital

 104. Moti Musinthe Zinthu Zoti Anthu Atha Kupindula Nazo,mukufu Kusintha Nyimbo Ngatikuti Akamaimba Amakhuta Or Imabweletsa Chitukuko.Mwandikhumudwitsa Bwanji Mr.

 105. Chomwe ndimaona ku Malawi kuli anthu otengera pan’gong’o ndale amangofuna kutchuka basi. Guys dziko momwe lilimu nkumalimbana ndi national anthem koma, opusa apa ndi anthu omwe amakuikani mmipandowo. Eeesh cholinga chokhalira phungu sakuchidziwa kapena mwina anakhuta kwambiri kapena misalatu iyi

 106. This country don’t deserve people like you jumbe.we need positive mind people to lead us.what change will bring when we change our nation arthem,how will we remember our heros?Gusbag.

 107. Koma a Jumbe ali ndi mkazi? Ngati a Jumbe ali ndi banja adziyamba a funsa kwa akazao kuti ku parliament ndikanene chani, chifukwa zaonetseratu kuti uyu jumbe payekha ngopanda nzeru

 108. OOO GOD BLESS OUR LAND OF MW ….NDIYE IWE UKUTI CHANI??? Agogo ako anayimba yomweyo ndiye iwe ungakhale wanzeru kuposa iwowo agogo akowo empty tin always make noise

 109. Zopusa eti,ufuna ayike national anthem ya Satanic, u go to hell we love our song,ngati adakuchotsa Ku khala MP wa MCP its coz of uchitsiriwo

 110. Self destruction…ndiye if voted to be MCP president ndiye ungasithe zambiri,thought of voting for MCP koma ummmmmmmmmmmmmmm…Zandiopsya….is better to stuck with my mapwiya

 111. Well I agree, Mr Jumbe is actually right. The thing is we unconsciously give energy to those negative words listed as we sing the National Anthem and at the end we attract them that’s how a human mind works Period! Agree or don’t buh it won’t make no difference juss like how gravity still holds down anything to the ground whether it does or don’t believe in it. That’s my opinion
  #EverybodyWantsChangeBuhNobodyWannaChange

  1. Uyahlanya wena moron. In this song there is no negative words,if you listen that song logically you will find that its a prayer. Have you ever try to listen the National Anthem of England which says thatGod bless The Queen unlike ours says God bless the Land of Malawi .#Jumbe_must_4

  2. I agree with peter that Mr patient kaya ndi patience whatsoever you call yourself should go back to the national anthem ,understand it well ,you will see that there’s no any negative word. You need not to back up everything just because Jumbe is now DPP you think he can’t come up with nonsense.

  3. Guys I made my point why am supporting it and calling me a moron or whatever name you like it won’t make any sense you need to make your point too. Only if you understand the power of words we can argue till forever. Go back to the basics know the power of words then come back here. If you saying there are no negative words in the song you are attempting me to ask you what are negative words. And please am not saying this cus Jumbe is DPP or what I literally don’t care bout that and who said DPP members can’t come up with nonsense anyways

 112. Surprisingly he is not mentioning about corruption which is rampant in the DPP led government and perpetrators are well shielded by the state itself.

 113. Mukakambirane zoyitanitsa alimi achizungu adzatsegule minda kuti njala ithe mmalawi osati zosintha nyimbo yafuko,,kotere mavuto onse alimmalawimo ajumbe kumaganiza zosintha nyimbo?? kkkkkkkk koma ajumbe mpatali

 114. ajumbe ngt mwasuwa khani kulibwino kumagona ndikucheza ndi ana ako bas no kukamba khani zopusa malo molimba ndi mavuto uzinena zopusa ngt zimenezo

 115. Fuck u Honourable Jumbe ,munasowa cholankhula mu august house? Osalankhula za chimanga chomwe chakwera mtengochi bwanji?even anthu akwanu(kumudzi)akulephera kugula pa mtengo okwerawu osawapemphera kubomako kuti asise mtengo bwanji ?

 116. We as Malawians we regret for the changing of Nyasaland to Malawi. Indeed we are on flames of fire. Greedy of the authorities they are lusty for money, Worthy and fame. Politics of Malawi only inspires to aspire the term of office before expire.

 117. Apapa choyambilila tingoti machende anu nose komaso ajumbewo mapwaka awo mboliyawo kwa amene aposita komaso mamvuzi awo kwa amene ankhale ajukomenta pafika ziko lathu la malawi bola tingogawanapo chifufukwa zafikapa ndipamapwala enieni

 118. si ma prophets a masikuanowa othirana nazo doom mthupi? National anthem izathetsa bwanji mavuto athu wa? The words hunger, diseases, and envy are meant to solve those problems amongst the population and removing the words from the anthem does not in itself remove these problems from the people.

 119. I respect his opinion but to me its pure stupidity. The country is having serious problems and a Malawian to think of changing the frag is senseless and unlogic. The same was the frag change which costed millions of tax payers money.

 120. Iweo jumbe udapangapo chan or ukupangapo chan pothandizilira kutukula dziko? chimutu chosecho kumaganiza zopusa ngat zimenez? u r jast a big empty hed lyk a tin dat orwez meks noiz i notin!! U SO STUPID!! wat cn malawians gain 4rm chengin t? das the athem buy tobaco wa alim? daz t plan 4 educaxon? daz t contro helth secta? SHUT UP U IDIOT!!

 121. iwe jumbe, kodi zimenezi ndizimene anthu akwanu anakutuma kuti ukawanenere kupaliamentiko? m’malo mokamba zothandiza anthu akudera kwako kumakamba zaziiiiiiiii ngati zimeneziii??? “u mp wakukanika utule mpansi tisankhe munthu wanzeru osati mbuzi…ai.

 122. That’s meaningless Mr. Jumbe, why don’t u ask about the prize of maize to be deducted more than national athem. Soap ina imangokula koma ili yo salimba eeeti!

  1. Ndpo abro jst lmagne lyeyu akudya wanthu anamuikapo akufa cos of Njala …lnstead to find other ways to fight against it koma lyeyu ati amveke…stupid mp

 123. Hahahaha plz find something worthy for country…talk about oil in lake Malawi, opening govt big farms, mines etc not the sh*t you talking…

 124. koma iwe ndi mbuzi ya munthu Jumbe wamva! koma iwe uthenga uli munyimbo imeneja uchotsapo mawu ake ati? ngati ukufuna peka kungwe wako udzikaimbila ku chinamwali.

 125. In this life of nowadays I have seen every body wants to be a Hero of which it can’t be like that. God have mercy on our mother country Malawi.

  1. Does he really understand what the national anthem say? Instead of dealing with really issues he’s opening a pandora box? Those lines he’s mentioning ask God to protect us from those vises. Is that wrong? Komatu penapake tikakhuta ndibwino kumakasonja uko. Asaaa

 126. Like really? ? That coming from a full member of parliament? ?
  Its not the nation anthem that keeps Malawi undeveloped! !
  Its the leadership style and not the national anthem.
  Is that all what Mr. Felix Jumbe can offer as an MP and get allowances and salary for such thinking? ? This is robbing a tax payer of his / her hard earned money.
  No wonder people jump into politics for quick easy money

 127. national anthem is gud only that we say God bless the land which he does but we dont know hw to extract the blessings from the land atleast we shud b saying God bless Malawi as america says God bless america so that blessings shud b falling on our heads then on the land we cn change

  1. kkkkk koma awa ndimagulu aja samakhala pa assembly ku xul sadziwa kuti national anthem ija mumatchilidwa kuti God bless our land of malawi? hahaaha

 128. Stupid Idea from another stupid MP, which negative words we should replace with positive ones?…..whatever was mentioned in that song is true. Nonsese, you should discuss that with your family , instead of discussing of spreading maize to the villagers who are struggling with hunger there!

 129. Zauchisilu ife sitimafuna, zoti mukakhuta-khuta muzibwela ndi mfundo zanu zofoilazo malo mwachitukuko ife takana, ana tizizawauza kuti chani ? Kufuna kuonanga tsogolo laana kumeneko, kapena ulibenso anawo,

 130. Sharp! Bwana MP Jumbe.Ine ndapeka kale NGUNGWE yomwe ilowe mmalo mwa National Anthem.Indeed old things need to be revised.

 131. That means MR MICHEAL SAUKA he was ignorance to copmpose the great national anthem like mulungu dalisani malawi ngati ajumbe akufuna kutchuka pa ndale akafune kopangira zatulo zawozo!!

 132. Hope jumbe doesn’t understand the meaning of this song,
  Put down each and every enemy, hunger,diseases and envy!
  I will change it like,
  Put down each and every enemy, Felix,jumbe, and diseases,,
  Mr jumber u must go to church and have deliverance,

  1. He is a fool somehow kkkkkkk are those words negative? Some people will never develop our country, its very unfortunate that they are leaders . Instead of talking good things that can give hope to people he is thinking of changing national anthem hahhah

 133. All these are idiots and gufies who dont deserve to be listened at all. You steal the government money and start talking stupid stuff which doesent have any thing to do with ordinary malawians at large

 134. This nkholokolo has run out of ideas. It’s mind-boggling. Will Malawians benefit anything from the proposed change? The NA is a true reflection of Malawi. Envent your own things to be famous. Don’t rely on modifications. OBANDA, NTCHISI

 135. Nthawi zina zake munthu ukasowa chonena !! Kukhala chete ndibwino kusiyana ndikuzika pa map kuziwitsa amalawi za #UCHITSIRU wako kuyambira kumutu mpaka kumapazi!!! Kunyazisa banja lako lonse// ndi achibale!!!! Kupusa kwako jumbe takuona bas khala pansi anzako akambe zanzeru apa mxiewwww

 136. Fuck you Jumbe!! Just keep fucking your wife ten time per night and you will see she will change the way you do it. Give Malawians food not that slippery mind ed of yours

 137. MBUZI YA MUNTHU TIKUFA NDI NJALA IFE, KUSINTHA ANTHEM KUTIPINDULILA CHANI? KAMBANI ZANJALA BASI MP WAUTSILU

 138. Fuck you Jumbe! What change will it bring to the development of the country? No wonder the country is going down everyday bcoz of brainless stupid people like u in high leadership positions.

  1. Kholoko imeneyi ikuti iri ideas to change Mw? Utchisi bwake ameneyu. Awafunse anzake mwano achitawu ngati adzapondenso ku parliament, kunali aHeatherwick pano ankateronso, ukamfunse mzakoyo poti ali komwe walowerako akuuza. Ndipo ali ndi nkhani yoti adzatiuze, zitsamba zikumubisazi zikadzauma xamalloance ndi kweni ma 500,000 opita ku Malasia koma osapita.000 dz

 139. iweyo jumbe nyimbo omenei unakhala ukuimba kuchokela uli stand 1 mpakana ku form 1 to form 4 nde yaipp lero?ndimaona ngati udziti ukufuna ukawauze ma MP anzakoo kuti bwanji bill ya section 65 ija mukaikambilaneso chifukwa ambilinu mwasiasia dzipani dzanu mkupita kuzipani zinaaaa

 140. Za national anthem zo ayi… we are satisfied ndi mmene yilili……panopo mziko muno muli mavuto ambiri oti ma MP inu mukambirane ndikupeza mayankho a mavutowo than spending tym pa za anthem zo czitithandiza……..

 141. Should we believe that the said negative words are putting a CURSE on mother Malawi? Should we say the positive words being envisaged by honourable Jumbe will be a magic cure for the socioeconomic ills such as corruption, diseases, njala, electricity, water, shortage of medicine+ trained personnel in our hospitals, poor education system, scarcity of portable water, insecurity (as pples lives and property are being lost to armed robbers) etc. Having positive words like “a God fearing nation” has been part of Malawi. However, the situation remains pathetic. We still have a long way to go.
  In my opinion, i would call for a change of MIND SET. Everyone should shoulder the responsibility of taking Malawi out of the dungeon of poverty. However, this can only bare fruits if there is POLITICAL will. Our leaders ought to adopt the approach taken by the president of Tanzania (am not assuming that his shoe fits all)….but it is an example worth emulation. Too much resources in form of financial resources are being shared among the FEW PEOPLE at the social ladder…the gap between the haves and have nots is so wide. They should forego some of the laxurious life and channel such resources towards improving the service delivery and production.

 142. koma misala yoyambika utavala suti + mazenela imankhala yachiwewe eeti aaaaaaaa basi kungokhuta RaRi + Chopichila basi ndikumakamba za ziiiii !!! iweyo ndiye Zeru kwambili eeti ? ngati ukufuna kupeka nyimbo ukampeze GwaladI muzikayimba zanu ndikumagulisa patsika wava .

 143. Che Felekesi Jumbe mupedze china chotchukilapo, maganizo mukuganizawo ndiopusa ndipo palibe chilichonse chomwe ife anthu akudela kwanu tingapindulepo

 144. why cant he move a motion to replace this negative Escom with a much more Positive escom, thats the change Malawi needs at the moment.

 145. its how you spend your time in parliament,instead of talking sensible ideas,you are busy saying goverment must change national anthem…go and wipe your ass…or you must tell us what’s the positive words and sing to us

  1. He is a fool ……how can a fully grown up person think like this? Kkkkkkkkkk how come people vote for this guy….the country is struggling and he is thinking like this.

 146. That dude has nothing to say in parliament, its better to go home and sleep rather than speaking nonsense

 147. Koma ma mp enawa shame.magetsi kulibe chajudya cha dura ,ntchito kulibe.ma college ndi otsekedwa ,dzipatala mulibe mankhala .koma tchito ikhale ya national athem?kamwana kakang,ono ka juliana lunguzi kadzikuposani maganizidwe abambo akulukulu shame

 148. Bwana, anthu adera lanu pokusankhani sanakusankhireni zimenezi, mukupangawu ndi uchisiru, pangani zomwe munalonjeza dera lanu , maganizo mwapeleka apawa ndiupusa ndipo ogwesa ziko, musazalankhulenso zopanda pakezi, amen

 149. Zaziiiii pali nzeru pamenepo???? M’malo mokamba zacitukuko akutaya ntawi ndi nyimbo ya mtundu waziko ayi antuni kkkkkk

 150. Agulugufe Inu Kumeneko Kufuna Kuoneka Pa map Kapena Kufunira Amalawi Kulumidwa Poimba Nyimbo Yabwino Ija?Kkkk Uhu Uhu aaasa!

 151. Ukuganiza Zosatheka Mphwanga!Nyimbo imeneyi singazasithe Or Mpang”ono pomwe!iwe wabadwa waiyipeza Nde ukasithe iwe?Anthu Osewa bwanjino Samaganiza Zositha? Ukunama!!

 152. Then jumbe should convince the president to again change the syllabus of our kindergartners education cause its eminent from change and not mmutu moti kolaption ili thooo. I school u jumbe that the first thing u need to do is to stop corruption in malawi then the kountry can develop and not changing words ayi but action.we all know kuti munkasokoneza ku mcp mutapatsidwa ndalama ndi cholinga choti mupeze business ya mbewu zija mumagulitsa. Shame on u all recycled politiking whores

 153. Lol mufuna mudziwike kodi a jumbe? Pitani ku dipipi akupatseni u minister.

 154. Lol mufuna mudziwike kodi a jumbe? Pitani ku dipipi akupatseni u minister.

 155. maganizo amenewa angothera pa Facebook pakepo osati boma ligwire zimenezi. musayiwale kusintha kwa lake nyasa kubwera lake malawi kunabweretsa kuti mayiko oyandikana asavomereze kusintha. pano akuti lake ndi yawo . ndiye kusintha kwa national anthem kupangitsa kusokoneza kumene tikuchokera. kodi iyeyu wawona ku nthenda anje kaduka zatha pamalawi? bwanji osamangopitiliza ndale zakozo ndi dipipi yakoyo. kagwere ku dipipi kwakoko jumbe.

Comments are closed.