President Peter Mutharika says he is surprised by calls from some human rights activists for him not to assent to the Land Bill.
In a statement through his press secretary Mgeme Kalirani, Mutharika said the bill was not forced down the throats of legislators in Parliament.
On Monday, Billy Mayaya who is a renowned human rights activist led a group of people who were demonstrating against the land bill.
Mayaya and his group said they are seeing no goodness of turning the bill into law saying people in the village are at the risk of losing their land to the government, hence no need for Mutharika to approve the bill.
During the demonstrations, Mayaya also argued that the bill has so many loopholes which need to be looked into and ironed out before taking effect.
However, the state president through his spokesperson said he has been taken aback by the calls from the activists.
The Malawi leader argued that the bill was brought to parliament and was passed by the members of the chamber.
He said this could not be reasonable enough considering that Mayaya is an individual and the law was passed in the bill by a group of people who are Members of Parliament.
Azipita kwawo ameneyo Ku malawiko sikwawo athamangisidwe ameneyo.
Kupusa kwako
Mavotavota enawa si abwino titengerepo phuziro
A Malawi musamangoombera mmanja zili zonse. Za malo izi even ma MP olamula omwewo sakugwirizana nazo. Ngati boma lilibe ndalama ife amphawi anthu wamba ndiye tizitenga kuti? Tikalephera kudula msonkho wawowo adzalanda malo athu. Kodi a Malawi chuma cha munthu wa ku Malawi ndichiyani kuposa malo. Boma limabwera komanso limapita. Samalani mudzaombera mfiti mmanja.
Iwe munthalika ofunika suicide bomb liyendepo basi, anthu pano akumachoka kumaiko akunja kubwera kwathu kuno kuzaona satana ati anasintha dzina kukhala APM
Ife tinanena kale olakwa anali mayi JB anakamugwira mkuluyu nthawi yokapereka zikalata zoimira kuzavota kuti amufufuze za green card basi nthawi nkudusa. Mwawona tsopano zimene akuchita munthu wakunjayu? Pano ndiye Muli tikanadziwa tikanaphika therere aaaaah gosh! Musova makamaka inuyo inu ndikunena inu inu aaaaa.
Akasaina ndichitsilu
President ? I ne ndiye zimandinyasa olo titakhala opanda president bolani
aaa! azowona
Kodi mfiti zonse zidafa kuMalawiko?..ali ndichani choopsa chokulepheresani kumutsogoza akapume atsatilaure ife!..zoona tizikhala mdziko lanthu ngati ma foreigners mmmm aMalawi Tiyeni tigwirane manja timchotse bwampini Ibu bubu!
Malawi sazatheka
WTF? Sindinaone boma lofuna kubela anthu ake ngati ili
Kodi ngati ife amthu akumuzi tilephele kulipila nsonkho malo athu ndiye boma ndikutilanda malowo kodi tikalima kuti chisanzo ziko la south africa silinapeleke mwayi kwa anthu anzikolo malo olima koma boma limamangila anthu nyumba komanso amalandila ndalama yogulila chakudya komanso dzimatenga nthawi kuti munthu nkumangilidwa nyumba malingana ndi vuto lazachuma ndiye fuso langa ndiloti kodi kwa anthu omwe tilephele kukhoma nsonkho ndiye boma ndikutenga pali madogosolo otani ofuna kuthandizila ife anthu ovutikafe? Zikomo
Aise peter muthalika usasainile utipweteka ife akavule luzi
Kwathu tikaphana!
koma satigulitsa kwa masaniki ameneyi .bwinotu kufuna chuma kusiya chikhalidwe chabwino
if he didnt see how his brother died ,continue to robe people
Achipatala mulipo kodi bvuto ili kuti lithe ndinu ,ntchito takupatsani gwirani ndithu mmadziwa zochita wanthu akulira APA ,zikomo!!
what iz the purpose of refrendam? apa pasavute ai khan tingopanga refrendam bas
Kkkkk tinanena voterani chakwera koma inu kusavaa taonani aa atupere zomwe akupanga at agenda for change kkkkkk aaaaaa aayoooo amalawi sadzava sitidzava
Kkkkk tinanena voterani chakwera koma inu kusavaa taonani aa atupere zomwe akupanga at agenda for change kkkkkk aaaaaa aayoooo amalawi sadzava sitidzava
Kkkkk tinanena voterani chakwera koma inu kusavaa taonani aa atupere zomwe akupanga at agenda for change kkkkkk aaaaaa aayoooo amalawi sadzava sitidzava
kalanga apumila kuti anganga
This bill is brilliant bullshit
Masiku omaliza
This typically means we are not citizens now. I was born Malawian can IMF or World bank change that? This nosense of land or whatsoever you call it, should stop!
Dziko la fodya ili, anthu ake ali kutsogolo ndi afodyaso, komanso anadya nyemba zambiri amayang’ana pafupi
dzikoli ndalilephela.palibe chabwino ndikuchiona.
nkhani imeneyi ndikaonetsetsa pali msampha owopsa zikuonekA kuti zikuchokela patali president akudzIwapo kanthu. IMF. UN ma bungwe amenewa ndi omwe akulimbikitsa zimenezi because presdent okonda Anthu ake sAnga pange zimenezi izi zikubwela pang’onopang’ono malingana ndi kukhazikitsidwa kwa new world order zambili zikubwela zowawa. Peter muntharika akudziwa zimenezi ngati ndikunama anditsutse ppanopo ndi mubweletsela zomwe anayankhula president John kennedy ndi presdent Dwight mu 1967 pa 27 apirl
Nthawi imene makolo amakolo awo amakolo awo ankapeza malo,kusosa chitedze kudula ndiku tchetcha chilikumwamba iwe kadzimphuno uli ku America galu president wankhaza chitsilu cha munthu,zipatala za gvnt pano nzolipira school nzolipira kwathu kuno ndalama kaya mukusetera kaya sizikuoneka nde mudziti tidzilipilaso malo athu omwe ma degree akumakupatsaniwo akungotaya pa mbutuma-apa ngati gaysm yavuta pezani njila ina yobwezelera komaso ngati Mulungu anakuthidzimula ndi floods last year this year mizimu ya eni malo ikunyonga satan iwe eti ndalamazo zidzipita kuti and zichokera kuti-tiona
kikkk eeesshhh onthu okwiya akuti sizomafusananso kuti did you read the bill pr ur just commenting .hahaaaa mzonwe tidavotera izi no wonder ma results a unofficial mpaka ambendera misozi.
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my deities, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before a month my body start developing my skin start coming up after 2month I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via whatsapp +2348162447651
The President Is Surprised??Tel Hm More Surprises Are Yet To Come,,this Is Just The Begginig!
Kuba poyera! Daylight robbery! Bwino bwino apa, wina wandale akufuna kuba apa. Tiyeni a Malawi tikhale tcheru!
The truth is Peter is now going mad.He has run out of ideas of bailling malawians out of poverty. He came to power without concrete polices,why punishing the poor like this?We thought we have the right man but tinangoyimbila mfiti mmanja.God help us,this man is a devil
TAKANA IFE A MALAWI ZA BILL IMENEYI. NGATI BOMA LIKUTSUTSA TIYENI TIPANGE REFERENDUM.
Kwathu kuno nkhota kota ai malo ndi athu makolo athu anavutka kutema kuti tpeze polima pomanga nyumba,samatemela chi pitalaaa cho mkamwa mopanda manomo ngati anaikamo matewela apite kwawo akawauze aphwako zmenezo ,amalawi tkanena anathila nsiizi taziona pano tkulila sopano tngopempha mulungu kut anve kulila kwathu
Ondiuza analipo koma mnkhutu mwanga,,mayoooo,,,,amalawi makani,lero tikulira koma dzana tinali ndi Bingu tinabangura,mmaona ngati uyu ndi mwana wa ndani?? kkkkkkk mupeze polekera
I don’t know how to run the nation. But my opinion is that this may be a good idea if you deeply understand it. Only that this may hinder the village people somehow somewhere
nde ikhalaso gud idea bwanji wth such hindrance?
kkk then it is not good.
I can’t foretell of what’s going to be done and what’s not going to be done. The government knows. My concern is of those who live in villages. I’m asserting nothing on this issue here
Muthalika I m angry with u FUCK U
ATTRIBUTES OF OUR LEADER: 1. ‘CONTACT AND DIALOGE’ DOES NOT EXIST IN HIS DICTIONARY. 2. HIS DECISIONS ARE FINAL. HE CANNOT APOLOGISE, WHICH WAS TYPICAL OF HIS LATE BROTHER. 3. HE LIKES TO ACT BEHIND THE SCENE. THE FEES HIKE AND THE LAND BILL ARE BOTH HIS INITIATIVES. HE PRETENDS TO BE INNOCENT YET HE IS A SNAKE IN THE GRASS. 4. HE DOES NOT KNOW THE MEANING OF POVERTY. I WONDER IF HE EVER HAD HIS SCHOOL HERE IN MALAWI.
Patrick Lobe… shutup ur mouth its bcz u don’t knw hw Malawians are suffuring according to my undestanding most Malawians their income z very low so if gvnmt stl overloading them where thy gonna run?
Malawi will still wave in a wind…
vaugalu vekha vekha matchona no zeru,
hey manyi ako pitara osalanda malo anga ndinasiya masara abho bho ambiri xo be care
To ruled a country is not easy, I remember Dr muluzi’s word,Eish mavuto achuluka bwana mukulephelatu apa,lets just say no more DPP bcz no one who will vote again
Guyz tigwilise ntchito nzelu,ndipo amalawi onse omwe tili koyenda mayiko osiyana siyana timaphuzilako zambili.choncho sangativute ayi,pamene abale athu kumuzi amangosatila.pa chifukwa chimenechi aliyense popita kumuzi atenge mfuti.mtundu wa mutharika ndi okhweka kupha,tikuvutika mayiko ayinwake chifukwa cha asasamba amenewa.akuwona ngati afika,akamufuse bingu ku nthata kuti zinakhala bwanji?chifukwa chosamva za azake.
This land bill is not Malawi government who need it. Its IMF and UN who wants it This is in line with New World Order. Don’t blame APM.Its our helping parterners.
Balaba Chigawenga Chimenechi
Zakezokha kuphiri LA ndalapa
Iwe Chakwera ndikuti usamuke ukalowe momwe akukhala mutharika takatundu take mutiponyere panjapo
Zimenezo mukapange kwanu osati ku mzmba zautsiru kufuna kudyera osauka titemana basi tiyambe kumenyana basi tilowetsapo masenga
Ine ndikuonakuti tilimbane ndikuti tidzaonana 2019 tikuchedwetsa nthawiyathu chifukwa adzabela chisankho chilima adachita kusiya ntchito yapamwamba,ndiye sangalole kukhala lova.anthuwa akutipha tisanamepoapa. Mulungu simunthu anakwanisabwanji kuchosa bingu atavuta,kulibwanji awa osapemphela ngati awa.tiyeni tipemphelekwambili kulilila dzikolathu mulungu amayankha,pls amalawi tiyeni tigwilane manja pakupemphela.aaaaaandaona ndipemphelo palibechosatheka.chachikulukulu,tileke kutsatila tizipani tatsopanoti kungonvakuti wina wayambitsachipani timangosapota sizabwino taziona,tikafuna kuvota tiyeni tibwelelekumbuyo, kuli mcp,udf zinazi aaatidzakhala mumphawi moyowathu onse.chonde amalawi anzanga tiyeni timenye nkhondo yamapemphelo osati yathupi.
Mungofuna kuti ananyonyowa azitokota yawo yausiilu
Nthawi zambiri ndimazimvera chisoni vote yanga kumandipatsa ukapolo.Anthu awa akamapanga campaign amati azikatinenera mavuto athu kwa président.Nde ndifunse kuti kodi land bill yi adawatuma ndi anthu or dd these people cald themselves members of parliament dd they visit their various constituency to ask for those who vote for them?.Mukapedzakuti chiwavotereni amangopita kukaombanitsa anthu mitu time is coming paja matsiku amathera kuchipinda don’t 4get that
Its game of numbers and self enrichment. Some opposition members of parliament opposed the bill but were outnumbered.
Moses mazoni anthu awa akutionjeza koma i realise kuti lakula ndidyera basi
Zinazi bwana zawonjeza inu mwazitenga kuti?
Koma ndiye zonse mukungoponya kwa anthu osaukatu!! ngati boma lilibe ndalama nanga anthu ndiye azizitenga kuti? iiiiii iyayiiii mukuwonjezatu!! Aphungu omwe akunenwdwa apawa omwe tidawasankhawa ndiye aaaaaa!!! muvuto okha okha akungovomereza zina zilizonse no wonder akumangokagona ku parliament
Dr Chakwera and MCP get ready to go in government in 2019.Zinazi zawonjeza.
chitsiru chamunthu ichi abale ziko lathu akulipitisa kuti kukamwa ngati nsomba yamlambako manyazi bwaa?
Wish him to die and put in hell
Mzimenezotu!
Last year ndinalima ndithu koma kamba ka climate change ndalephera kukolora, now pano ndikulephera kugura chimanga choti ndizidya ndizdya ndi ana anga kamba koti ndilibe pogwira @ kodi ndalama yoti ndilipire pa munda wanga pomwe ndikulephera kugura chimanga chot ndizidya @ iwe Mutharika usandilaure, Vuto loika anthu ophunzira kwambiri pampando ndilimeneli zoti kuli anthu ena chovala n’chimodzi sazidziwa kapena kuti sanazionepa @ Mutharika undilakwitsa ukanakhala pa fupi nkanakuthira Makofffffffi
Bwampini sadzatheka basi! Waliwonanga dziko ndipo akulionangabe
Kkkkkkk koma Bwampini ameneyu ndimutchera msampha wationjeza zedi
Some other comments are foolish. Mukulimbana ndi anthu oti zawo zinayera , koma uchitsiru winawu very difficult to understand, eish ! 2 much Gologolos in Malawi .lool ! Angiyazi kuthi kwenzakalni nomalanga ?
Bwanji osakasaka kuli chimanga azigawa kwa amphawi nkulu ameneyuso watani kodi iiiiiii apa ndie ayiii
A kak president
Musalire mudamsankha nokha musiyeni apange zimene akufuna mdziko lathu limeneli.
577billion kaliati Henry mussa chaponda
koma zoti ziko ndilosauka anthuwa akuziziwa ngati mpaka nkuonjeza kuti anthu osauka kulipira malo ali awo a demet zinu enafe tikafera kundende coz sinzalipira CHALO CHANE ningati agogo pasi. TWEE!!!!!!!!
Lembani zomveka mani school yakuvutani zomveka
They must find something else to do not oppressing the poor like this .
Angochokelatu zisanamivute mwana wamphaka ameneyu
Is none of my bizness because am tired to heard stories for this mother fucker President.why always he likes to talk shit,kaki things he must leave to rule us his nanyongo
Ine ubwino wake si mmalawi ndine munthu chabe
I think as a professor plz Mr President
That is not going to happen. (1) The goverment have’nt put infrustrature in some of the rural area and they want tax. What for? As far as i know the goverment must put good infrastracture eg good roads, health facilites, education etc. Then tax must go to pple who have big bussines and big houses/surbubs not ordinary pple. They must pay 5% the value of the house every year as rates like other countries. #No Tax #Step down mr President u have done enough damage . If we can vote now no one wil vote u.
Awa akufunika achokemo m’bomamu ndithu tioneko Tambala wakudayi mwina akhoza kutipulumutsa ku ng’anjo yamotoyi @ atcheya taonako zawo amiyi taonako zao tsopano tioneko kokolikoyi kuti apanga zotani ka inu mukuona bwanji anzanga??????
Ayi ife tikuona bwino ndi maso onse awiri opanda magalasi ndipo mwalankhulazo tazimvaso bwino kwabasi ndi makutu awili paja limozi timalikhalila.
Cry my beloved country
apa szofusaso mnthalika walephera kulamulira dzko
He must go to Hell even before his life lasts
Panafunika achoke posadikila mavoti chifukwa ndikale limenero
Kunena zoona guys ndikufusenikoni moti pamfundo imeneyi azapezekaso wina ovotera DPP? abale anzanga ndindani angasangalare kumalipila ndalama malo ake omwe @ this is foolish!!! tiyeni a Malawi tigwirane manja munthuyu watizolowera kwambiri
Kikikikiki
Mmmm. …kodi aid tinkalandira from foreign countries were coming from such initiatives in their countries. Now, no more budgetary support and Mw Presdnt / gvnt introduces financial supportive measures and we complain. If gvnt fails to deliver social services due to low income we will cry as well. Wat do my country wants… Paul Jonathan
A Malawi ake ati? Sadzakumbukila zimenezi akadzangopatsidwa t-shirt mu nthawi ya campaign.
Dzikoli mukuliseweretsa abwampini inu.Kale kuli aKamuzu kunalibe zotelezi.
Panyin pa amache ngat alipo
Kkkkkkkkkkkkk mmmmmmmmmm
Ngati ku thyolo kwanuko malo akutherani musapeze mpata woti mubele anzanu.Ife za bill imeneyi tikukana.Last time amalawi wonse anakana kuti musagulise MSB,koma chifukwa chakuzikonda kwanu munagulisa.Palibe chimene amalawi anatolapo chaphindu kuchokera ku ndalama za msb.Nde ngati mukukakamila pa nkhani ya za malo ife tikukana bill imeneyi.Aliyense agogo ake anamusiyila malo,ndiye inuyo ndi anzanu amene mukubvomera za bill imeneyi tikuti lamuloli mukalikhazikise kwanu ku thyolo,osati kwa anzanu.Anthu oyipa inu ofuna kumadyelana masuku pa mutu.Mwatibera kale 577 billion,simukukufanaso kumangana,mukungozembazemba pa nkhani iyi,nde pa za malo tikuti toto.Kwathu kokha nde ndawunjika maduka,dzakugendani chitani chabwana tiwone.
Anthu akuba awa.
Amene amayidziwa no ya bwampiniyu atandigayilako ndimulozatu ameneyu, kukhala President sindiye kuti nthaka ndi yako,ukafufuze komwe makolo ako ankalima and anthu amene ukawapeza pamalowo udzikawalipilitsa ukayelekeza kusamva,umva paja wakulu anati chosamva anachiphikira limodzi m’masamba, ukamafa mumayamba ndi nkutu kugontha……
Mbuzi yimeyi tingoyilodza.
Thawi yafika kuti apresedent akumane ndizowawa
It looks lik alot of pipo r just commenting without knowing de content in de bill and how important it is to de pipo of Malawi. Pls b4 commenting go through de bill then comment.
Iwe ndambuyakowo nonse mbuzi
pansana pako
Pa Facebook pano munthu uth kumacheza ndi amisala. How can normal pipo think of insulting some1 they dot know? Am nt blaming u.
Pa Facebook pano munthu uth kumacheza ndi amisala. How can normal pipo think of insulting some1 they dot know? Am nt blaming u.
chosamva anachiphikira mmasamba
YU ONLY REALSE THE COST IMPACT OF A DECISON AT A TIME WEN YO LEFT INNER PART OF LIFE TWISTS YU- EMPEROR NERO…………………………………………………………………….from the look of things it seems p.m is yet to realise the inna part twist of the forgon decision on land bill stay tuned as yu ruin the remedy
Mwapwiya zeru zolamulira alibe km ntchito yake kunyengesa ponyera mathanyura
Akonza Chilima posachedwapa izi. Ingodekhani mukhe madzi. Wakumva wamva…
akukwanani mcthonayu zanu izo ndi ameki anuwo
Osadanda ndikudikila cardiac arrest apange mature bobo iyeyo musiyeni apita ayisiya bill imeneyi
dats y dziko linampasa dzina loti{ Bwampini}chifkwa amaganiza ngati mwana now dziko likusowa ndindalama imene anthu akatenga kuti ndalama zolipira Malo awo? akuluwa ndiopusa mwina tikanasakha opanda nzeru akanakumbukira mavuto awathu
When the students of unima come up with the term munthuology I understand that their were referring it to this lack of humanity president of Malawi (APM) the most educated savege
Ndicifukwa cake amango tchulidwa kt ndi ibu saganiza ngati munthu km ngati bwampini…. Anthu apumire pati?watinso anthu asiye kudya nsima km azidya mbewa ndi dzombe zoona?.
Nzika ya chi Malawi INA iliyonse,chuma chache ndi nthakayi, dothi lathu,
Lamuli limenelo a President mwakhala apo, munafunsana chabe ndi nduna zanuzo zokha mwina a Malawi eni ache nthaka?
Ubwino kwa a Malawi ndi kuipa pa billuyo a Malawi one munauzapo?
Mwabisila chiani mkate kwa billuyo?
Kwanu Ku Thyolo ndi Mulanje pa miyezi itatu yadutsayo munaona zomwe anthu akumeneko amafuna kuchita kufuna kulanda ma Esiteti?
Pali nkhani zina kuti zitheke osathamangira mamba koruna mapindu a inu nokha ndi chipani chanucho ayi, itanani ma fumu akulu mudziko akuthandizeni nzeru pa billuyo.
Akamuzu kukana multi Party anayamba ndi kale, koma potsimikizira ubwino anaitanitsa Referendamu, nkhani inayankhidwa, azanunso angelezi kuchoka my EU, anaitanitsa Referendamu,
Kodi inu nzeru zodelera mafumu adzikolo mupita nao Pataki utsogoleri wanuwo?
Ndi mafumuwo anagwetsa Kamuzu Mr. President, nanunso ngakhale mutapanga katangale wotani wamavoti simungawine.
Mwayamba mafumu a mumidzi akulu ma TA, masub TA ma GVH, muitha a DPP,
1.Kwawo ndi ku estate ya tea alibe malo nde sangadandaule ndi bill iyi 2.Iye ndi nzika ya ku America kuno nkodzangolamulira musaiwale green card ija 3.Ndalama za misonkho amalo zizilowa mmatumba aiye ndi anzake 4.za umphawi wa anthu iye sizikumukhudza 5.Alibe polobulemu ananena kale musaiwale 6.Amene alephere kukhomera msonkho munda wake ukhala mopezamo zitchetche ananena zija zomwe zithandizire food diversity 7.Zokamba za mafumu iye sangamve mzake ndi Gwanda Chakuamba awakutumula makofi akapusa Koma ndikudziwa kuti kuli Bon Kalindo, this time tiyenda miyendo m’mwamba apolisi akonzekere! Another July 20 is coming soon!
This government mmene akubela ku road traffic ku migration pakufunika madomo
Opitala opitala inu wat kind of person ar u? zona anthu azikudandaulani each & evryday koma osasinthu ai ndithu ukanakhala mbuzi ndikanangokupha ndikukupanga kanyenya nw cz ndiwe munthu zosatheka! anyway let’s jst put evrythin in Gods hands osaukafe taberedwa kokwanira
Saamvamkunkhu ndiye ameneyu. Amamva zake zokha anavoteredwa basi.
Pls read de bill b4 u comment
kodi anachokera kuti munthu?
Mwapwiya nzeru zolamulira alibe koma nzeru zamkalasi basi
This thing called land bill stated by his brother… mwai imfa ija….
This will b bad 4 the poor
How? Did u read de bill or u r just hearing it from this post?
We knew that he is behind it
Mutharika! assent to the bill at your own risk. We will respond in 2019 in style. This is broad day theft
Ndawerenga that’s good devepment malo azipangidwa recognized as personal property osati malo onse akhale m’manja mwa a president and we are going to acquire loans from banks using our land as corrateral
Kodi mwapangana zogukitsa dzikoli kenako muthawe?
Guys, munthu Yu atigulitsa ndithu.
Chifukwa palibe cha nzeru akuchita iyai.
Thats sh**t why u want to rob poor people
Did u read de bill or u r just comment?
Enock, or whatever they call you…keep quiet ok??
kikkk eeesshhh onthu okwiya akuti sizomafusananso kuti did you read the bill pr ur just commenting .hahaaaa mzonwe tidavotera izi no wonder ma results a unofficial mpaka ambendera misozi.
Tidziwona
you are saying Muthalika is still silent on this @Martin…. why is he silent on this disgusting move..??.
Malawi24 Source Unreliable,am So Kin Lookng 4wad The Mata Hence Ther’s No Comment 4rm Apm,hw One Reporter Post This Lambo?
Am just crying for my poor Malawi, pls Jesus Christ come and take over from these cruel and shameless leaders who r robbing from poor Malawians daily
TOTAL FOOLISHNESS! THE PRESIDENT HAS THE MANDATE TO APPROVE OF IT OR NOT. HENCE SHOULD WE SAY THAT EVERY RUBBISH PASSED BY THE PARLIAMENT SHOULD BE ASSENTED BY THE PRESIDENT?
Even the one who brought this bill in that chamber didnt think well. And these members we chosen to stand for us are helpless.
President mapwiya muthalika
nonsense zanuzo apa ai
Bodza Anena Liti Zimenezo? Apm Still Silent On Land Bill,dont Cheat Pple
rockless,
Ha ha ha mapwiya!!!