Fees must fall: CoM students to protest against fee hike

college of medicine
college of medicine
College of Medicine students against fee hike.

Students from College of Medicine (CoM) a constituent college of University of Malawi (UNIMA) have disclosed that they are next to be teargased as they plan to demonstrate against fees hike.

Being under one name, Unima students from CoM have disclosed that they are to take action in solidarity with other colleges.

Speaking in an interview with Malawi24, University of Malawi Students Union (UMSU) vice president Godfrey Pumbwa said CoM students are to hold the demonstrations soon.

“They will start very soon even maybe before going to school. However, I cannot specifically say that they will demonstrate but they have confirmed that a certain action will be taken to show their fury on the same,” said Pumbwa.

Unima students have been demonstrating against fees hike arguing that the adjustment has come when Malawians are sailing on seas of financial woes.

Godfrey Pumbwa
Godfrey Pumbwa confirmed of the looming demo.

The student demonstrations have been seen spreading like a disease with Chancellor College (Chanco) taking the ignition role to the protests against fees adjustment.

On Friday, Polytechnic students defied armed police officers who began patrolling the campus as early as 5am when they were notified about the protest in the evening.

Over 14 students were arrested as authorities claimed that the demonstrations were illegal saying that the students were not allowed to protest.

Two days after the Polytechnic fracas, students from Kamuzu College of Nursing could not hide their anger as they blocked the main road to the campus and Kamuzu Central Hospital with burning tyres on Monday to show their dissatisfaction with Unima council’s decision to adjust fees.

But despite the students’ anger, the council maintains that it will not to give in to the students’ demand on the fees hike matter.

Advertisement

133 Comments

 1. Ine ndimaona ngati kukhala pansiku ndi nzeru, koma ndazindikira kuti ndi kupusa kopambana, Zimene zanena mzakozo ndizo nzeru ukanakhala wina ukanayamikira mfundo yakeyo. Koma ulimdi mtima osafuna kumva zaena pozitenga ngati Madolo. Mmmmm, njira imene mumachitayi ya mademo it is not right ,u could have to choose the right way than against the Government through this Rubbish way. Inu ndi anthu amozi amene mukuwononga Malawiyu
  Nde mumati boma lizingoyang’ana pamene mukupanga zoipa . Pakufunika azikuthirani Utsi ngati mulomwe pokumba Mbewa kuuna. Mukuzolowera zopusa azigogoinu, Fuck off.

 2. Iyai lero sindifuna zokangana ndi munthu wokhala ndi misala mmutu, pepani sindine wabwano akulu , musandiveke uchimo mutsiku lalero, pepani a minister, Ulemu nthawi zina ndi bwino. Funani ena oti muzikangana nawo mutsiku lalero Osati ine. Pepani ndili busy kusukunura Marandi , nde musanditaitseko nthawi. Just Go and Fuck hard your sisters including your Mother. Ine kale zanga zinayera, mupange ZANU.

 3. Bambo vomerezani munathawa umphawi kwanu,ndipo mukugwira ntchito zakalavula gaga kwa mwenye uku mukutukwanidwa ndi angoni makirikiri,musayankhule mwano chifukwa munaithawira pa zenera.akayamba kukukhapani okulandirani ndiwomwe mukuwatukwanao.FEES MUST FALL,LAND FEE MUST FALL,HOSPITAL FEE MUST FALL,WALKING FEE MUST FALL,suka man!!

 4. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my deities, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before a month my body start developing my skin start coming up after 2month I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via whatsapp +2348162447651

 5. Nkhope yako siwoneka bwino, nde ukuti chani iwe , ngati akuyabwa ,uzingozikanda, U will translate yourself about it. Maderfucker.

 6. Koma iwe ndunya, suzimvera sisoni nkulukulu ngati iwe ndunya, ukulankhula monga amuna opusa ,yet u are a man, I think Ugalu ndiumene wachuluka, uzoonya wena inja, bcoz nikubonire ukuthi aunang’ondo , likhanda lako futhi alisebezi, uyanyera Wena imbuzi , likundu rwenurwo, mbwaa .

 7. Nawe onyansa nkhope ngati iwe uti chiyani ? Ngati ambwiyako anamenyedwapo kujoni kuno nde wamva kuti ndi aliyense ? Usandipase uhule oyankhula nsunu wako, wang’izwa ? Devil .

 8. Fees must fall anzanu amapanga izi dziko lawo muli ndalama zambiri migodi mbwe nanga inu dziko lanu longodalira kupempha ndi ulimi ee kaya

 9. And waPolice amene akapezekeyo nkofunika kumudziwitsitsa akatha kupanga zawozo zotumidwa ndi Peter yo ife tidzapange zanthu tikawapeza m’manyumba mwao kuphelatu,wapolice yense amene akapezekeyu tengani Photo and fufuzani office/station yomwe akuchokera ma information ake tikawapeza konko tikadziwa komwe amakhala,aphedwe agalu amenewa amangololera zili zonse

 10. I, THE PRESIDENT OF THIS COUNTRY, TELL YOU THAT I WILL NEVER BRING DOWN THE FEES BECAUSE NO GOVERNMENT HAS EVER SPONSERED MY STUDIES WHILE I WAS ABROAD. I ALSO TELL YOU THAT IN AMERICA THERE IS NOTHING LIKE ‘CUSTOMARY LAND’. THEREFORE, IT GOES WITHOUT SAYING THAT WHETHER YOU LIKE IT OR NOT I AM GOING TO ASSENT THE MALAWI’S CONTROVERSIAL LAND BILL. AMEN!

 11. Jamie Ndunya, Do you know the meaning of ur name? It means kunyera in khokhola language_ now just go to toilet and realise your waist matters Oky , idiot.

 12. Amene akuvomereza za fee hike wa idawabula mmimba Unima ndi a ku Ma technical nde ati kubwenzera kuwawitsa …kaya zawo zimenezo but izi sizingatiletse ife kupanga Mademo

 13. Anthu onsewo akukweza fees zambiri anaphunzitsidwa ndi Kamuzu zaulereko and with more benefits as Varsity Students .. Pano akupanga ndalama zambiri ndiponso ali ndi ma benefits mma university mu oti zambiri akuchitiridwa zaulere… Ma scheme mbweee… Ena akugwira mma Illovo umu .. Escom.. Admarc… Salary ndiya ndiiii koma anaphunzira yotchipa….
  Ngongolenso yomwe ankatwngayo sanabweze…
  Kodi zikagwere mwana wakwa Nsundwe ?….

 14. FEES MUST FALL ,…OMWE USUSAWE KAGWERE UKO,KAWAWA IWE ETI

 15. Hahaaaha umbuli ndiomwe mumacita inuyo kumalilira za ulele kuzolowera kuleledwa pa chilolo . unvrsty NDE chani??? Za kwerazakwera bxi ngati zavuta maganyu alipo usamaone ngati kupita Ku unvsty NDE kuti waphunzira za ziiii yendani muone maphunziro Ali ndi anzanu . sikuti oxe aku comenta APA sanapite Ku sukulu , tinapita ndi ndalama zathu osakhala kumalilira za boma,mukamamva uphawi ndimwe mukuchitawo . ANA ANJOKA

  1. Chitumbuwa #pro-fee Hike Moron, Khalani Chete, Tikudziwa Inu Ndi Anamageya Anyezi, Mithutha Ndiye Inu, Simukulabadira Nkomwe Za Mwana Wa Mlimi Wopeza 200 Sauzande Pachaka, Smukulabadira Za Mwana Wa Masiye Yemwe Akudalira Sukulu Yokha Kuti Adzakhale Ndi Ka Mpamba Kodzithandizira Iye Ndi Abale Ena, Ndikuona Mukulimva Kukoma Dzikoli Anzathu Odala Inu.

  2. Most of the students that go to public universities come from Mission schools and private secondary schools. In secondary school, annual fees ranges from 450,000MK to 600,000MK. Let gvt help the few poor students with loans. Otherwise demos do not reflect the true status of these kids. 400,000MK is less than annual secondary school fees.

  3. pepan guys enanu zikuoneka kut mwachuluka olemera chonde avereni chisoni osaukafe. ngati inuyo sinkhani makobili chonde pitani ma university akuja tilekereni aku Malawi athandizeko amphawife

 16. Iwesonawe ndi chitsiru eeti mmmm, chinzibambo ngati iwe kumantchula zakumwenzi, aaaa wangokula mutu koma nkati ndichimphanga chabe muli empty, zoti zakumwenzi anayamba ndi siteni yako b4 nsikana ukumunenayo sudziwa, blad fulu wako wamva iwe.

 17. Hehehehe utsilu ndiumene ukuwapangitsa zimenezo ndikuyakhula mopusa ,kupita Ku unvrsty ya boma sikusonyeza kuphunzira , mubwere mudzaone mapepara Ali ndi anzanu xizanuzo ngati mulibe ndalama lekani bxi osamangozolowera zopangiridwa

 18. Anthu enani Ku University simunapondeko komanso zikuoneka kuti mmakwanu palibe amene ali ndi tsogolo lokapondako.. I don’t blame u .. Chicken heads…. #yaza tiyeni nazo… #feesmustfall

  1. Wa chicken head ndiwe ukulira za ulere haaaaa ntchito yamakolo ako ndi chani???? Amkangobereka alibe pogwira???? Hahaaaha limbikirani mudzilipilire osamalirira zaeni . unvrsty hahaha tapita kusukulu anthufe ndi ndalama zathu.lekani kulilira za ulere

  2. hahaha spencer ndiwe zoba …… ine sindinapondeko ku ma unima anuwo kom i am educated …….. and you wil never be like me kampopa ngolo

 19. MWAITHA! ENA AMATI INU SIMUPANDA DEMONSTRATE. MORE FIRE! WANDISOKOSERA MKULINGA UTAVA.

 20. Achisomo inuyo ndikuphunzira kwanuko… Mukufuna kundiuza kuti chimene boma lakwezera fees simukuchidziwa? But if so… Munataya thawi school sinakupindulileni…. MIND YOUR LANGUAGE.

 21. koma inu kodi mukaphunzira ma salary anuwo magawa kwawina aliyense jst start working hard mupeze fees basi,,,,,what z ma demo?.

  1. or munditukwane l dont care koma the fact z or atani koma ngati fees yakwera yakwera basi the best way ndikungopeza njira yopezera feesyo

  2. koma jamie dont make m laugh wamva,,,,,athu aulesi inu ofuna kulemera pa dzanu ndi ma degree omadzangomwa nawo mowawo k400,000 ndi feesnso uko

  3. kkkkkk mbuli inu tangovomelezani chomwe inu muli …..ngati simunavaye varsity sivuto lathu ……komaso nkhaniyi its between varsity students, unima council and govt nde ndikudabwa nanu mahule onukha chikazi osasamba ngati inu kuti zakukhuzani bwanji???

  4. ifetu sizitinyasa koma mukutinyansa ndinu ndizochita zanuzo zongolowetsa phokoso dziko,,,,tikadandaule kulephera kwa inu chifukwa cha fees bola kuma admarc kuli chimanga inu kalimeni

  5. nsanje man yakupwetekani inuyo kalembeniso msce basi sizanuzo iyayi ntchito chigololo basi??? sizikupindulilani zimenezi olo pa fb muli pa sipakuthandizani….kuli edzitu….kkkk mahulewa kkkk

  6. simunati…zikunyasani kumene..mufuna tiphunzire modula kenaka tidzaphunzitse ana anu,kukupasa mankhwala ku chipatala,kuyendesa chuma cha dziko and many more???? kumaganiza ngat munthu osati zopoila mukunenazi… fees will fall by any means..tikalime??

  7. hahahaha cos ma parents anu ndi ma failure ndiye ndikhale hule,,,,watch ur mouth pls ngati kwanu muli ophunzira akulipilirani,,,y r u hating?, ndayakhula zakukhosi kwanga ndiye musanditukwane kodi mesa aliyense akuika maganizo ake ngati Muli anzeru mukanaukirana apa mbuli zokhazokha takumana ndithu komanso ngati mukuona kuti simukwanitsa tipatseni ife malow tilipira ndi dollar zampiru

  8. kafunse anakubereka cos ineyo pandekha am amom & amene anakubala iweyo atha kukuuza cos u r hurting ma feeling ukamanditchula hule muthu wamamuna iwe opanda umuthu mayakhulidwe y?,nkhani ya fees yomweyi unditukwane okubalayo akhudzidwe shame on u

 22. #patience Lita, pali mitundu ya ma demo yosiyanasiyana, ku comenta kwa anthu pa nkhani ngati izi ndiye ma demowo.

 23. osafuna kumva za ma-demo a”fees must fall” angosiya asamapange comment,,,,mukuganiza mitu yonse yaganiza zopanga ma-demo ingakhale yopanda nzeru?????,,,,ma allowance anachosa,nde mkumangokwezanso fees mosaganizira,,ma demo basi,,ufulu wa aliyense kupanga ma demo…ngat ma demo akukunyasani nanunso pangani anu boma likumvereni zanuzo!!!!

  1. Angakhale tikapita mubaibulo anthu amene amakuwa kuti yesu apachikidwe anali ambili kuyelekeza ndi anthu amene samagwilizana ndimaganizo opusa ngati amenewa… am just trying 2say kuti just bcoz mitu yambilimbili imeneyi yozitenga ngati ndiyozindikilayi yaganiza zopanga ma demo as u, sizikuyhandauza kuti ikupanga zanzelu, mademowo nde kupusako coz ther’z always a better way of soving issues than violence/demos. munjila ina mitu mukuinenayi mayi kaya ndinu bambo ndiyopusa!!

  2. inu wochenjera eti???,,haha,kupusa mooooo,,,,chifukwa munthu ali ku MCHS((ndalama mumalipila ndizochepa ndatha kukumvesani!!!!!!,,,,vuto sinuyo!,,,chisanzo mwapelekacho sichikumveka bwino coz ndichokhuza milungu(yesu) not Yesu Christu

  3. ku MCHS,phwanya+accomodation zaulere,mukufuna munene chani man inuyo???,,,,boma likukuwetani bwino osamangothokoza bwanji,,nde anzanu mumasangalala azivutika?????,,,,

 24. Am really tired of this now , everyday same zindaba, azikho zinye ? Kukuma wena inja , just give up, if ever you know that, you can’t manage ,than doing nonsense then kukagona kundende. Put it down ,finish and clear .

  1. ULIRA SUNATI! KAYA ACHITA CHOKUTUMA UWONANSO. KUNALI MA CADET A MCP, UDF, KOMA LERO ALIKUTI. KAYA UKUDYA MONEY CHIFUKWA CHA PROPAGANDA YA DPP, INGOTI PHEE UWONE. I DO NOT CARE ANY POLITICAL PARTY. WHAT I CARE IS JUSTICE. ULAMULIRO WA DZIKO SI UFUMU. MUTSIKA PAMIPANDOPO MUDZATIPEZA IFE AMPHAWI. DZIKO AMAYENDETSA NDI MULUNGU. NGATI MTSOGOLERI SAMVERA KULIRA KWA AMPHAWI, ALI PAFUPI KUTEREREKA.

  2. Akulu ndinu chitumbuwa chokazingika pamodzi ndi zitete za ku Thyolo. Zopusa, ngati muli ndi ndalama, just scroll down, say nothing, yes shut your proboscis. Mukukhala ngati simukudziwa kuti boma ili limakana negotiation/dialog pa nkhaniyi bwanji? #FEES MUST #FALL. Because you commented this trash, many can’t wait to watch a video of you ukukhapidwa/kuwotchedwa ndi petro ku Joniko, courtesy of ndalama ukunyadirazo! Have a heart please. Umalawi unakuchokerani ngati zitumbuwa zina za bomazi eti?

Comments are closed.