Up to 15 people have been arrested in connection with the fights that broke up at Likuni Roman Catholic Parish in Lilongwe on Sunday, Malawi Police say.
Malawi24 had reported yesterday that infightings over concerns some grouping withing the church had over the Parish Priest and the main church executive, whom they accused of no cooperation.
However other reports claim that the men behind the row are not Roman Catholic faithfuls who sources claim only wanted to dent the church’s image by causing rows at the church’s main choir.
While information on the main cause of the rows which saw exchange of blows in and outside the church- and also the forcing of the priest to stop the Eucharist celebration remains sketchy, the church has not made any statements at the moment.
According to Lilongwe police Public relations officer, Kingsley Dandaula the arrested are remanded at Lilongwe Police Station and that they will be charged today with conduct likely to cause breach of peace as they appear in court today.
(MORE TO FOLLOW)
Abale bwanji mkunyazinsa mpingo? Anakupasani mphamvu yoweruza wolakwa ndani? Mwakwanisa kale kukhululukila wokulakwilani 70×7?? Tikanena kuti nanunso mugwire yakalavula gaga ndie kuti takwitsa? Ngati munaona kunyansidwa ndi wansembe munasiyilanji kusapitako ku mpingoko? Dziwani kuti mwapalamulawu ndi mlandu uli ndi maputala,masekisheni, ndinso mapinakodi mubuku la milandu yoweruzila mkhoti. Apolisi angokunjatani zonse mukamva ku khoti. No mercy with u.
zochitika masiki omaliza
Ambuye Yesu nawo anakwapula anthu omwe amapanga malonda ntchalitchi..kwapulani zilombo!
Ambuye Yesu nawo anakwapula anthu omwe amapanga malonda ntchalitchi..kwapulani zilombo!
Redson Mbewe ukanamudziwa iye sibwezi ukunena choncho ndakudandaulila mphwanga moto uwopeni ponyozesa mtumwi wa mlungu tiyeni tuzinyozanani tokhatokha koma tisafike ponyoza dzina lantumiki odalisika ngati Muham’madi (ntnmdz M zki) chifukwa moto olusa kwambili

Mukanawasiya atibulane, Zampingo izi.
mpingo ulionse anthu aswanapo kkkkkkkk ndiye sizachilendo anyani sasekana zikundu
mpingo ulionse anthu aswanapo kkkkkkkk ndiye sizachilendo anyani sasekana zikundu
Kuteleku Satana Amakodwa Akaona Ana Amulungu Akukangana Mchifukwa Ambiri Mukulemba Mfundo less Cbola Akatolikafe Mwat Tamenyana Km Enanu Mpaka Kuchosana Moyo Zamulungu Zomwezi? Vuto Limaphweka Likakhala Kwamzako Bt U Mst KNo Dat No One Z Perfect Only God Z Nde Shame To U Devil Coz Katoloka Ilipo Ndipo Izakhalapo.
Ndewu opephera nanga osapephera makalati ake akhala bwanji?bad image
Cash ndiovuta.masika a chakachino sapelekedwa basi chifukwa mwatichotsa zambili
Kutha kwaziko
akhristu nde mwationjeza2 mpanka karate mmyumba yamulungu?eeee zovu…zedi
Sionse amanena ambuye ambuye akalowa ufumu wa mulungu km akucita cifuniro cake.Ndie anthu ambiri amakhala nawo maonekedwe acipembedzo km mphamvu yake anaikana, ndie amene tikuwaona akumenyana mkacisiwa.Musafatse mmasiku osiliza ano.
Ithink 666 has born at Likuni catholic
zikuyenela kupephera kwakuya
zikuyenela kupephera kwakuya
Nanu apolice chinyengo mwaonjenza, zikakhala zoti opalamula ndi bwana nkhan Imatha ngati kavuluvulu koma akakhala osauka opalamulayo eeeeeeeeee.Plz investigate & bring to book those who murdered NRC student.
mwawonjeza acatholic bwanji kungokambirana koma mpaka kupindira shat oky..kkkkk….kkkkk.
mukakhala inua boko haramu musalowelele zainu timaziwakt mabomba mipeni mwaiwalakuti kumzuzu apolis anapeza mfutimu mzikiti ndi chiwadachanu mumachipembezachiji muhamad satanawanuuja zupusa zazi
ziko la pansi chitsoni ndi anthu ake ntchiyani ichi?
mwayamba kunyamula ma weti nkachisi wamulungu dziwani kuti tchimo silichepa,apa nde satana anayendadi ndi miyendo dela limeneli,kusiya kupemphela kuyamba zakayesala?
Kkkkk , sabata yatha anatibulanaso kuzimba a ccap, zuloso kulilongwe , eish! Mipingo yalowa bussiness tsopano aliyense afuna ka change,
eee bola kungosamala coz everybody did,do/does,wil do so something wch z dismay 2 GOD,bola angotisamalirako aphuzitsi aku LIBOSS
eee bola kungosamala coz everybody did,do/does,wil do so something wch z dismay 2 GOD,bola angotisamalirako aphuzitsi aku LIBOSS
Such is earthly life,full of destruction instead of building
Vuto laakatolika kupita ku church mutamwa,opemphera amamenyana?
LAST DAYS!!!!!
masiku otsiliza munthu azadzikonda yekha
Akatolika mukuchitisa manyazi.mmakanizana kukalandila ukalestia,muli apereke mtulo ndiizo kkkkkkk hiyaa!
akakhala asilamu eeeee kukanaipa lero ndizimeneZi mutipo bwa. kkkkk nde pamenepa agwe mumpingo ndani omenenyedwa ndi omenyana omwe kkkkk
Munene kuti zikanachitika ku Livingstonia Synod, koma kunali kufulu mitundu ndi mawonekedwe. Chomodzimodzi, Nkhoma Synod inakhazikisa mpingo ku Mzuzu ndi Mzimba, koma ndi akuzipemphelera mwa bata chifukwa palibe akuwanyoza. Kuli ziii. Ndikukuthokozani my fellow civilized people of the north
akakhala asilamu eeeee kukanaipa lero ndizimeneZi mutipo bwa. kkkkk nde pamenepa agwe mumpingo ndani omenenyedwa ndi omenyana omwe kkkkk
osadabwa,ntchito za vinyo zimenezo anamwa ochuluka,kuledzela mkacuisi ndizimenezo mwayamba kutibulana ,musamati vinyo muziti mowa fotseki .mwayamba kuona ngati bar malo opempherela.asatanainu.
Bwanji akulu zampingo wakatolika zisakuchimwitseni pangani zampingo wanu
anachenjeletsana ukalistia?
Listen,Jesus said,MATTHEW.24:15.When you see the abomination of desolation spoken of by the Prophet Daniel,standing in the holy place(let the reader understand)THESE ARE SIGNS OF THE END OF THE AGE.watch and pray hard.
Munthu wina aliyense ali ndi ntima wake wake ndiye kusemphana maganizo kumatha kuchitika pa malo ena aliwonse.koma kuti nkhani ikatero ndiye timangophatikiza kuti a ROMAN CATHOLIC onse ndi oyipa komwe ndi kulakwisa,Muwone nkhani ngati imeneyi ikanachitikira pa nzikiti ndiye kuti ife ASILAM ndiye tikanatukwanidwa kumene,eg Pali mayiko amene akumenyana okhaokha pa zifukwa za ndale m’mayiko mwawo koma chifukwa ndi mayiko a chisilamu ndiye timangonyozedwa tonse,kamba ka umbuli was anthu onyozawo.
Salam Salam Sheirk Zowona
zowona kumakhala kusazindikira,tiyeni tizingowapemphelera kuti mulungu akadziwitse chowonadi.
zowona kumakhala kusazindikira,tiyeni tizingowapemphelera kuti mulungu akadziwitse chowonadi.
Nafuma chitchalichi chinu kkkkkkkkk,koma uyu amakhala ku italy mulungu wanu atipo bwanji
Akuchitire chifundo Mulungu amene umampembezayo wamva
ndiwachifundo nthawi zonse
ndiwachifundo nthawi zonse
Sizachilendo izi tingomvome leza kuti nthawi yayandikila
Sizachilendo izi tiyenela kumvomeleza kuti nthawi yayandikila tingoti Amen
Nyumbayi siya atate anu, ndiya atate anga, lero nyumba ya atate anga mwayisandutsa mokwapulana
Too bad
Nyasa Times says its DPP. Lol ma page ena kaya
even if akadaphana remember wi r pipo nt angels! D only sin dat cant b 4gven mkunyoza mzimu woyera!!! Repent & cum bak 2 Jesus! R C C 4ever
amenewo ndi mchere osukuluka kungowakwapula mapama basi atipitsira chritianity
Koma zibakera zake zowawatu mmmmm holly ghost firw
But as a church ,it would have avoided de fight a a a not up to that extent.
Aphinana chopereka?
Born a Catholic,,,,Raised a Catholic,,,,and Will DIE a Catholic,,,,, No matter what…… In those days there was one Christian Church the So called Roman Catholic before reformation. But due to some misleading by some of the leaders, there came out reformation. what I want to say is that disagreements will always be wherever there is a group but as Chrisian we aren’t shaken and ran away. We pray tha God should grant His Holy Spirit to re-unite the scattered/lost ships. But that isn’t so to the protestants, when they meet a small/big problem in the congregation they scatter and there is no turning back. They go search for another church or introduce their’s where they’ll follow their rules. Catholic church of the universal was there,,is there,,and will be there 4eva. I pray for union, wisdom and patience in My Church. Mongokumbutsana mpingo sulakwitsa koma anthu amumpingowo ndi amene amalakwitsa. I never blame religion even to judge someone or religion. Let God be God.
Ndipo anthu amene akunyozawa asiyeni siakatolika ayi
Catholic church
Catholic school
Catholic hospital
Palibe church ⛪ lothandiza anthu ngati limeneli.
Ngati pali mavuto zokambirana zitha.
Amen.
Muwauze kuti oooooonse amene amapembeza mumpingo u agwa mumpingooo ndawagwetsa ine
kodi anali ndi mfuti kapena mabomba ngati anzathu aja?
totaly means there z no Holy Spirit guidance in that church.zoipa zikamachitika mu church ndibwino kumazuzulana mwa mtendere.anay way bible linanena kale za masiku otsiliza sizachilendo izi
Mtima wanu usavutike yang,anani kumwamba,pakuti nthawi yakwaniritsidwa.
Kikikiki koma kumeneko
That’s bad
hehede,uluu koma ndiye dziko likupita kumapetodi eti kale ndeu ya m church imasowa koma lero mwezi sungathe osamva zot akhristu atibulana uku.kaya zanu izo.
Horible Tragidy… #Jesus Christ Is Coming Soon.
Si Za Chilendo Komanso Tisamanamizane Ngat Mmidzimu Muli Mbava Zimapitanso Ku Church Ndie Sikut Tikati Ku Church Ndie Kut Kumakhala Olungama Okha Okha Ai! Afiti, Asatanic Ndi Ena Oipa Amapita K6a Pot Ndi Nyumba Ya Mulungu Aliense Amabisa Zofooka Zake Kuiwala Kut Mulungu Akutiona Ndie Tisayankhulepo Zambiri Apa Coz Nkhan Yake Ndi Yaitali Ndipo Ya Pa Chiweniweni Ma Demo Sachitika Popanda Vuto Ai Komanso Wa Msembe Ndi Munthu Amalakwa Ngat Munthu Wina Aliense Koma Apa Zinaonjeza So If We Say Church Is Just Un Instrument Of Salvation Meaning Chipulumuso Ndi Wekha Ngat One Of The Instrument Is Weak Use Ur Brain 2do The Job Of Salvation Ndiponso Kulikonse Nkhan Ya Ndalama Ndi Yovuta Guyz Or Even In Church , &ma Church Ambiri Akubadwawa Its Becoz Of Money “Dyera” Ndie Sizodabwitsa Izi Kungot Maliro Amfumu Amatchuka Than Munthu Wamba
Cathoric si kristu
Chifanizo chayani ichi?
koma akatolika kukonda ndeu
Ukunamatu iwe akatolika sakonda ndeu ayi.
kkkkk kumenyana mu church
last days no doubt ready for something big
If machurch leaders akutero…mafollowers apangeno chani??..is christianity being depicted pamenepa??????
I want to give a testimony on how I get cured from HIV/AIDS. As I was browsing through the internet on how to get cured, I saw a lady testimony praising DR Williams I never believe it before until I tried it and it really work for me am very happy right now may God bless him. this is an opportunity for you to get cured contact him via [email protected]….. and also you can contact on whatsapp number +2348143143878 THESE ARE THE DISEASE Dr.DR WILLIAMS CAN CURED. HERPES. HIV/AIDS. CANCER. LOVE SPELL VIRUS.

No all who says the Lord,Lord shall enter the kingdom of heaven
No all who says the Lord,Lord shall enter the kingdom of heaven
No all who says the Lord,Lord shall enter the kingdom of heaven
ngati eni ake aziweruza okha ife ndetitani? bauti yoyambika mkati mwapemphero mumapenyanabwanji? kkkk

Let’s pray for them

mukuti atani?

what was the cause plz? follow it then judge later.
what was the cause plz? follow it then judge later.
what was the cause plz? follow it then judge later.
What were they fighting for ?
What were they fighting for ?
What were they fighting for ?
Eric Malungah, Winnah Cancheepootoo, Nathan Chitseko, Welos Amos Bruno, Timothy Njolo Imbwah zosabwino
pamenepa ndiye pampita pathu anyamata alikuni boys sec scull popita kunsika

Nyumba ya atate anga mwayesa malo ochitilamo malonda
Mkantho wa ambuye ndiumenewo musadabwe
***AFalisi osadulidwa ajah amenewo iwe iwe iwe iwe iwe iwe iwe iwe ilipo palibe ilipo palibe iwe iwe iwe iwe iwe iwe
EEEE, KOMA ADAKAKHALA ASLAM WEEK YOSE INO TIKAMANGOMVA ZA BOKO HARAM, AL-SHABAB. AL-QIDAH, POMWE MAGULU MUKUWANENAWO NDI AKHONDO CHABE SI ACHISLAM AI. NDI ANTHU OMENYELA UFULU. LELO NDI IZI ZAGWA PAMPHUNO.
Luckly Iam a follower of Christ,not Papa Benidict..
Ndiwe omvesa chisoni wanena za Papa ndani apa
Mmmmm dziko lapansi
Malawi ukupita kuti ?
What happen? Guys osamafulumira kuweruza
Masiku omaliza
nde bolaso mpingo wathu wa satanic nanga mkumati wanuwo ngoyela??? kkkkkkkk ma fight amwene
#Lucius banda can u pls tell me why ur church members are fighting ?
osamufusa peter mutharika bwanji?Paja ndiwa katolika
osamufusa peter mutharika bwanji?Paja ndiwa katolika
osamufusa peter mutharika bwanji?Paja ndiwa katolika
Komanso Mpingo Si Wa Lucius Banda Ai! Ndipo Iyeyo Ndi Wa Ku Balaka Mukadamufunsa Za St Lewis MottFot Parish Akadakuyankhan Koma Za Kulikun Zikumukhuzapo Chani? Tamaganizan Enanu Plz?
Hahahaha ndafuna lucius yo inuyo fusan ptr yo,Iwe happy tapita uko usanditopetse ndiwe lucius iweyo?
Kkkkkkkk Vanesa Wapenga Ndie Ukadalemba Ku Inbox Ya Luciusyo Nanga Amaika Pa Wall Umati Akuyankhe Ndan Lucias Azikhala Busy Pa Fb? Zot Kuli Watsapp Siukudziwa Dzipatule Wekha Ndipo Uziike Grade Ya Iwe Ndi Luciasyo Kkkkkkkk Pepan Sisikkkk Mukufuna Soldier Hahahahahahaha
Aah opusaso iwet ndikamufune soldier kut watan?zamanyi et,mwina mayako ndamene amamufuna mxiew!
selfish,jealous,greedy and self-centered.
Thats how u are Zulu,thanks for letting me know
shaaaa! m’mpingo mpaka zigogodo? nde kwa anthu osapemphela ndi zikwanjetu.
Muzisiyanitsa Kwa Opemphela Ndi Osapemphela Awatu Amapanga Ma Demo Coz Ansembe Aku Likun Anafika Po Bowa Mpaka Kumawaletsa Anthu A Chinsapo 1&2 Kut Asamakapemphere Ku Likun Instead Azipita Ku St Denis Chonsecho Likun Idamangidwa Ndi Anthu A Ma Area Ndatchulawa Mutakhala Inu Mungakondwe Komanso Kudya Ndalama Za Mpingo Poti Ndi Ansembe Tizingowasiya? Ai Kwa Osapemphera Zochita Zao Sizingamveke Even Pa Radio Ndipo Kukonza Zinthu Sometimes Zina Zimaonongeka
yes, dats true koma akanakambilana mwantendele mpaka mafaiti? mpaka ena kumangidwa? mulungu amtaya kuti, mpaka ziwoneselo mmpingo? very shameful.
Shameful Indeed,Holly Gods fire!!!!!.
Why church of to day
kkkk kuyenera kunali zibakera zauzimu kumeneku
Apolisi amanga zigawenga 15 zachi khiristu zomwezimamenyana dzulo mutchalichi ku Likuni
amakangana vinyo?
Kodi za Mulungu amamangananso? Nanga bwanji aja amaba chopeka aja sitimawamangisa
Kukongoku ndikumene kwaambitsa
Yesaya 21v 11
Ndinthawi yanu ziswanani!
mwatichititsa manyazi a catholic anzanu bwanji
Mwafufuza bwino mwayamba kuweluza