The Anti-Corruption Bureau (ACB) is yet to discard six cashgate buses which are stationed at Police headquarters in the capital city Lilongwe.
The Marcoporo buses are valued at K520 million and their procurement was facilitated by former chief tourism officer in the ministry of tourism, Leonard Kalonga.
Last year, the court convicted Kalonga on his own plea of guilty for stealing K3.7 billion ($6.3 million).
After the conviction, ACB deputy director general Reyneck Matemba said they plan to dispose the six 65-seater buses.
“With respect to the buses, we know that something must be done, they have been with Malawi all along now we think the office of the Director of Public Prosecution can help to shed more light on the process,” said Matemba.
He further said ACB will also involve the ministry of justice to insure transparency.
However, the state is yet to remove a restriction notice on the sale of the buses.
This means that the condition of the buses will continue deteriorating and they will be sold at a low price.
Izi simuotcha?
these buses should be allocated to Chanco, Poly, Mzuni,Luanar, Must and Kamuzu college of medicine and deduct from their allocations
Pliz jst donate to unima unlike kuononga ngati kumeneku
Mungo ziotcha
Bus ziwiri zilembedwe malawi police zinaso ziwiri zilembedwe malawi deface force zinaso ziwili pelekani kwa azachipatala chifukwa ndalamazo anaba za boma ndiye ma bus amenewo apelekedwe ku ma dempartiment aboma pathambi zitatu Malawi Hearth malawi Police ndi M D F
Amenewa si anga kkk koma mayi uja
Osangowaotcha Bwanji Ma Bus-wo.
Za ziii!!! Zotentha akanakamugwira Jb kuti atifotokozere chomwe watithawila kutisiya tikuvutika. Iye ali ndi mabilion a cash gate osati mabus a mamilion mungogwila matemba mashage nsomba yaikulu mnyanja
Zimenez zikufunika kut boma lingo otcha ngat mmene anapangra ndi nyanga za njovu zija kut ena atengelepo phunziro
Eeh! koma!
Aaa cifukwa ciani kugulusa mabasi ndi sanve izo musaiwale kuti zithu zakuba timaotcha ndiye judge ameneyu akuti chani ife tonse tiyembekezela mabasi folo kuotchedwa za halamu izo plz. To be continued
Azembesaso izo bwanji ziyambe kuyenda. Mwin wake ndan yemwe anagula.
=oooooo?
Ndalama zake tigawane
akagulitsa ndiye ndalama zipita kuti why osango wagawa ku ma department a boma
Apasine.a Malawi azikwera koma azipeleka kandalama kochepa
Hahaha kaya zanu zimenezo
Yea,ma bus amenewo akanapereka ku ma department a boma osati kugulitsa,akufuna adye ndalama etiii?
Ma bus amenewo mwiniwake ndani?
Why don’t u share diz buses to M D F,MALAWI POLICE, AND MIINISTRY OF HEALTHY. Koma bvuto ndi kufuna kususa basitu sife anatu muzidziwa zimenezo…
LOOKS FOWERD ITS NOT BETTER TO COAMPLEGHN ABOUT THIS PALIBE CHOMWE MWACHITAPO PAMENEPOPO MWASIYE BASI NANKHA NTHAWI IYONSEYI TIZITI SIMUMAONA MA BUS WA
Pa Malawi kumangoulula zinthu chisawawa ngati mmene mukuchitira a MW 24, anzanu akumapita osadwala.
Gvt yakonzeka fodya gate
YOU MUST SELL THOSE BUSES AND PUT THAT MONEY IN GOVERNMENT TO START BUYING MEDICINES IN HOSPITALS AND FOOD FOR THE POOR WAKE UP MALAWI
Mukungoonona nthawi m malo molimbana ndi zotukula ziko izo zidapita kale
Magalimoto angawa musamale bwino ndidzawafuna
Ztisunga iz? Mpaka bus kumaola?
Mwini wake sanapezekenso.
Kodi mawilibalawa mwapeza popanda eniwake.
MUNGOYIKA PANSEO AMALAWI NDIKUPEZA NTCHITO KUTHAMANGA NAWO
Bola kugulisa ndalama zigwire ntchito zina zaboma…….