I am not Satanist – Skeffa

Advertisement
Skeffa Chimoto

Malawian Musician Skeffa Chimoto has denied social media reports which said the music icon confessed in a program on one of the local radio stations that he has been introduced to Satanism by another local musician.

In an interview with Malawi24, Chimoto said the rumors are coming from jealous people who do not wish him well and want to tarnish his good reputation. “I didn’t want to say anything because I don’t normally fight back when something bad but false is being rumored about me,” said the Lilongwe based artist.

He emphasized that the story is fallacious and he has never been on any radio on the issue.

Skeffa Chimoto
Chimoto: People want to tarnish my image.

“The truth is that I haven’t been to any radio station in the past ten months or so. The last radio program I had was at Galaxy FM in Lilongwe and it was a phone in program during the time of floods last year when musicians organized a show at Lilongwe golf club and I was one of the artists that were chosen to promote the show. So everything you are hearing is totally fake,” he said.

He further challenged people to go to the alleged radio station in order to prove if he really granted interview.

“You can go to that radio and ask them if I once had such a radio programme at their station. I know that when some people somewhere hate me, there are also many other people that love my work and I pray to God that He reminds them that it is a sin to tarnish an innocent person’s image,” said the Chinamuluma Chakuda hit maker..

He then told his fans that they should not worry about anything because he is still healthier and is planning to leave for Zimbabwe after celebrating his wife’s birthday where he will be recording some songs for his forthcoming album.

Advertisement

555 Comments

 1. Skeffa osadandaula chako si chawo chawo si chako mulungu wakudakitsa ndithawi yako nawonso nthawi yawo idzafika,a malawi mukamakhala ndi moyo wa nsanje nzanu akachita bwino mulungu sadzakupatsani m’dalitso wanu chifukwa cha moyo oipawo

 2. Nkhawa Nje Skeffa,okha Atsutsika Ndi Nyimbo Ya Zamabodza Nenereni Ine.Iwetu Skeffa Umakwana & Nyimbo Zako Zimatipasa Chilimbikitso.May God Bless U Abundantly.

 3. Pali anthu ena sakondwera mnzawo akamachita bwino, God will continue to bless you so that they should be put to shame, all we know is that Skeffa amatiyimbira bwino

 4. Eeeee ! Eeeee ! Abale! Abale! munthu akalemera satanic? asauka za Mulungu kodi ? Aliyense alindi nthawi yake yake imene Mulungu amachitira zoziziswa. Mukamati satanic zanu !inu agwiro mu makwanilitsa malamulo khuni ?

 5. Eeeee ! Eeeee ! Abale! Abale! munthu akalemera satanic? asauka za Mulungu kodi ? Aliyense alindi nthawi yake yake imene Mulungu amachitira zoziziswa. Mukamati satanic zanu !inu agwiro mu makwanilitsa malamulo khuni ?

 6. Eeeee ! Eeeee ! Abale! Abale! munthu akalemera satanic? asauka za Mulungu kodi ? Aliyense alindi nthawi yake yake imene Mulungu amachitira zoziziswa. Mukamati satanic zanu !inu agwiro mu makwanilitsa malamulo khuni ?

 7. Eeeee ! Eeeee ! Abale! Abale! munthu akalemera satanic? asauka za Mulungu kodi ? Aliyense alindi nthawi yake yake imene Mulungu amachitira zoziziswa. Mukamati satanic zanu !inu agwiro mu makwanilitsa malamulo khuni ?

 8. Eeeee ! Eeeee ! Abale! Abale! munthu akalemera satanic? asauka za Mulungu kodi ? Aliyense alindi nthawi yake yake imene Mulungu amachitira zoziziswa. Mukamati satanic zanu !inu agwiro mu makwanilitsa malamulo khuni ?

 9. Eeeee ! Eeeee ! Abale! Abale! munthu akalemera satanic? asauka za Mulungu kodi ? Aliyense alindi nthawi yake yake imene Mulungu amachitira zoziziswa. Mukamati satanic zanu !inu agwiro mu makwanilitsa malamulo khuni ?

 10. Mr. Chimoto, you know yourself your background so don’t mind about somebody’s speech. Adabadwila banja losauka…………..should be your label. We are looking forward for forth album. I wish you all the best. GOD BE WITH YOU.

 11. Thats why Bushiri ananena kuti Malawi has evil spirits ya nsanje ndichifukwa zambiri zikutivuta……. nyimbo za skefa zilingati za west life sizima fifwa nde muthuyu anadalitsika coz alinso ndiumuthu kuposa zitsiru zinazi

 12. Thats why Bushiri ananena kuti Malawi has evil spirits ya nsanje ndichifukwa zambiri zikutivuta……. nyimbo za skefa zilingati za west life sizima fifwa nde muthuyu anafalitsika coz alinso ndiumuthu kuposa zitsiru zinazi

 13. Bora iwe zako zikuyenda asiye azichedwa ndimabozawo ngat iwo analemera ndi satanic ndiye zawo zimenezo maplan kusiyana

 14. Vuto ndalama zake sizithera mahule ndimowa koma zitukuko ndie munthuyu ngati akutukika tifunseni Ife tikuuzani ….ngati ndinsanje ikuphulikilani mukhaula

 15. Uyuyekha musiyeni…ngati ndichiwanda amalawi muyaluka nacho….satanism yanu mukumamupaka wina wapheeee!……tsiku Lina mudzayaluka take care

 16. eeeee kaya zonse ndi choice yake.onsewa maganizo chabe choona chili ndi mwiniwake sikefayo pansi pa ntima.but we like your sound brother.and mupitilize kutikwapulila sound like momwe mukuchitilam

 17. zazi basi mukamuike munthu mu bunge loipa ngati limene lija zausilu basi zachamba eti ngati mwasowa chokamba muzingokhala basi leave him pliz munthu zisamuyendere basi mwati ndiwa satanic zichepe ndithu amalawi amene mukufalitsa nkhani imeneyi

 18. zazi basi mukamuike munthu mu bunge loipa ngati limene lija zausilu basi zachamba eti ngati mwasowa chokamba muzingokhala basi leave him pliz munthu zisamuyendere basi mwati ndiwa satanic zichepe ndithu amalawi amene mukufalitsa nkhani imeneyi

 19. skeffa,dats how life goes on..dat culd b a sign of ur prosperity..i wish de raws culd wrk on dis…

 20. Sanje siyabwino ukasauka mumati fiti ukalemela satanic sono tipange chani kuti muyamike .Tikuziwa ndinu nokhanokha oyimba siife kwathu nkuyamika

 21. Dziko lonse lapansi umbuli uli ku malawi munthu akamachit bwino kumbali yake zavuta the end its satanck tamulekani CHIMOTO APITILIZE lunso lake limene mulungu adamupatsa fuck them the one who say this sheet mbuli kusafuni azanu kuti azidyako bwino Malawi sitha

 22. kumuyipitsila mbiri sibwino choncho,asakugwetse mphwayi umayimba bwino ngakhale pa SA amakukonda ndi nyimbo zako zomwe.

 23. zamabodza nenereni skefa mbiri yake ipitsani koma mudzaleka….last week inali nkhani ya mtumiki wa mulungu prophet mbale kuti wasanduka njoka chifukwa cha nsanje….skefa ndi deal no matter wat..amphawi ambiri akalowa ku gehena kamba ka nsanje zomwe akuchita pa skefa ndi prophet mbale

 24. Musiyeni skeffa, ngati maxenera amadalitso amutsegukira vuto ndichani anthunu makaa_maka? Mwangodxanxidwa ndixiwanda xamabodxa eti? Ishhhhhh mulungu akukhululukireni popexa comwe mukulankhhula cmukucidxiwa mitu yanu mwamvaaaaaaaaaaa?

 25. zinazina2 iz kmabe ndichocho nde amalawiwo kumawazolowela kukongola kwake anayimba kale akachuluka anjilu uzyamika chauta pot kaduka skangaze popanda chpambano

 26. Malemba Amat Utsaweruze, Uwone Kut Pamene Ukumuloza Mzako Ndizala Dzingat Dzaloza Iwe Mwini, Zingoonetsa Kut Tsatansm Ndiwe..!!

 27. Malemba Amat Utsaweruze, Uwone Kut Pamene Ukumuloza Mzako Ndizala Dzingat Dzaloza Iwe Mwini, Zingoonetsa Kut Tsatansm Ndiwe..!!

 28. u people dnt judge,wait 4 GOD’s judgement!! siinu mulungu ai,siyani kunyogodola ena chifukwa muzikhumudwabe mulungu akuwakweza pena!

 29. u people dnt judge,wait 4 GOD’s judgement!! siinu mulungu ai,siyani kunyogodola ena chifukwa muzikhumudwabe mulungu akuwakweza pena!

 30. sindikufuna kumuyimba nawo mlandu skeffa pa nkhani yopanda umboni……komanso sindingamuyikile kumbuyo 100% chifukwa muntima mwake sindinalowemo….I. prefer to stay newtrol over this issue…..nevertheless..nsanje ndi mulili owophya

 31. sindikufuna kumuyimba nawo mlandu skeffa pa nkhani yopanda umboni……komanso sindingamuyikile kumbuyo 100% chifukwa muntima mwake sindinalowemo….I. prefer to stay newtrol over this issue…..nevertheless..nsanje ndi mulili owophya

 32. kma abale skeffa yekha nde musamuipese..mukuleka kunena achina Gwamba and Armstrong mukulimbana ndi munthu wosalakwayi.eeeee a Malawi sitizatheka nsanje ndyomwe inakula,just coz mayimbidwe ake akupta patsogolo nde basi mwati mumufooketse?Mulungu sangalore zmenezo kuti zmuchitikire kwa mtumiki wake woonayo u have to know that kmanso matsoka ndi matwmberero adze kwa inu oipanu.mmalo mopanga focus pa lyf yanu mukulimbana ndi wina oti zake zikumuyendera mukuchedwa guys..

 33. kma abale skeffa yekha nde musamuipese..mukuleka kunena achina Gwamba and Armstrong mukulimbana ndi munthu wosalakwayi.eeeee a Malawi sitizatheka nsanje ndyomwe inakula,just coz mayimbidwe ake akupta patsogolo nde basi mwati mumufooketse?Mulungu sangalore zmenezo kuti zmuchitikire kwa mtumiki wake woonayo u have to know that kmanso matsoka ndi matwmberero adze kwa inu oipanu.mmalo mopanga focus pa lyf yanu mukulimbana ndi wina oti zake zikumuyendera mukuchedwa guys..

 34. yemwe mulungu anamudalisaaaa!,,,,palibe!!!!!omutemberela siyani kunyogodola enaaa…….muzakhumudwa chauta sayang’ana samayang’ana khooooooooope akafuna kudalisa!_______________________________________________________for all the gud things that God did to #Skeffa thinkng that he can join Santanism “God for bit” may God have mercy to all the LIE composers……..ame!

 35. yemwe mulungu anamudalisaaaa!,,,,palibe!!!!!omutemberela siyani kunyogodola enaaa…….muzakhumudwa chauta sayang’ana samayang’ana khooooooooope akafuna kudalisa!_______________________________________________________for all the gud things that God did to #Skeffa thinkng that he can join Santanism “God for bit” may God have mercy to all the LIE composers……..ame!

 36. Ku malawi. Zinthu zikamakuyendera ndiwe wa satanic. Uka kalamba ndiwe mfiti.

 37. wh@ u shuld knw zimene mukunenazi u hv made him 2 b motivated much 2 another high level ndy knw kt u hv a big gap bwtn u n him n sufikira komwe,stay wit ua gossip without knwing kt ukumupangisa iyeyo alemere koposa lero ,#jahcountinue blessin u #skeffa

 38. wh@ u shuld knw zimene mukunenazi u hv made him 2 b motivated much 2 another high level ndy knw kt u hv a big gap bwtn u n him n sufikira komwe,stay wit ua gossip without knwing kt ukumupangisa iyeyo alemere koposa lero ,#jahcountinue blessin u #skeffa

 39. Kuipamtima amalawi ngati njoka ya mphiri ufiti oyamwila ndiovuta kutha dziko lija ndilopusa chimodzimodzi mwana akamakula osanyetsedwa amakhala chitsilu

 40. palibe munthu angakhale Osanenedwa poadziko unless suli moyoo,, Skeffa me lov yo songs, and evn yo character. don’t giv up, keep going. no matter hw pple talk worry not dear its part of life..

 41. Aliyense amaziziwa akakhala yekha chomwe ali ndimulungu wake ma Radio station ku Malawi achuluka zowauza anthu zikunsowa ndibwino kutseka ndikutsegula Tea Room

 42. I think Satanism is for Malawians who are doing better in life kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk. I give this issue to God to judge but for me and my family I will save the Lord without kulozana zala!!

 43. Why not suing the radio station that aired the fallacious interview then,,,,?????? lol

 44. Zamabodza nenelen lne mbiri yanga yipisani lne wonyogodola ndinyogodolen lne koma muzaleka.lne nkhondo sindimenya ndekha andimenyera nkhondo ndi ambuye lne mwini wake ndili chete. Musiyen skeefa anakuyimbiran kale

 45. By his sweat he is doing well, when he was not doing fine u pple were quiet, the man laboured for his wealth, leave him alone, let him enjoy what God has provided for him in peace.

 46. We malawians why do u give satan authority and good things go and read ur bibles well and you will get the answers riches are for Gods children he said silver and gold are mines says the Lord and yet when someone who believes in God gets rich you say wa satanic…kkkk! mumandivetsa chisoni u shall remain poor if u give satan the good things of life…..we are heads not tails,…Skeffa worry not move on with your life let the true satanists talk coz ngati sakuziwa a satanic ndiomwe akukunenawo maboza ndiake asatana.

 47. Eee! Gyz pafuka usi pali moto chilungamo akuchidziwa iye ndi Mulungu wake, lets talk about this, munthu ukalemera ndipamene Mulungu amakupasa mayeso coz a time that u become a lich nsatana amakhala ali pambalipa kutheka munthu kukhala wabwino at first & then ndlama zija zimayambano kukulamula Mulungu umakhala ukumuiwala pang’ono pang’ono, Gyz tisanamizane kuimba ndi chida chimodzi chomwe nsatana amagwiritsa ntchito pofuna kumuitanila munthu kumpingo wake,just emagin kumene kumachitikira show kumapezeka zonyasa zambiri ,Mowa,Mahule, zibwezi Ndewu,kusuta Chamba,kuvala kosalongotsoka.zambiri zonyasa zimakhala zikuchitika kumeneko. Nde ngati amaimba nyimbo zauzimu mukuganiza kuti Mulungu angapezeke malo otelewo? Kodi Mulungu mumamutenga ngati ndani? Nankha Yesuyo anaphunzitsa zimenezi? You Gyz Muchenjele nsatana akukugwiritsan ntchito koma inu simukudziwa ntchito za nsatana zimawoneka ngati zabwino koma pamapeto pake mukalowanazo ku GAHENA, Mulungu wapatukana ndi zimenezo,muzipemphela kwambiri ino sinthawi yomapita kumashow kapena kapena malo ena aliwose kumene Mulungu waletsa. Osamangot amaimba za Yesu amatisuntha ameneyu koma chonsecho simukupemphela kumangokhali kukonda zoimba Yesu akakukanani poyelayela Yesu sanabwele ndi Gitala kapena Keyboad mkumaimba iye anabwela ndi Umodzi wa Mulungu. Komanso mu Baibulo mulibe vers lokhuzana ndi kuimba.NSATANA AKUGWIRABE NTCHITO MPAKA TSIKU LACHIWELUDZILO, anyamata nda atsikana azimai nda azibambo musamale mutha kukalowa KUMOTO WAUKALI ZEDI

 48. Nde chimene kugaziwe satana waonekela paliponse kufuna kukwanilitsa ntchito zake zonyasa kufuna kugwetsa ana ake amulungu chenjelani satani mtanda wake basi wa yehova

 49. Zisakukhuzeni zachuma cha skeffa. Kodi muli ndigawo pa chuma chake?pangani zanu, mukungokhalira ma rider ndkachasu pamene anzanu akugwra ntchto molimbika choncho kuchta bwino kulakwa? Nsanje imadza kamba kaulesi. Gwirani ntchito molimbika nanu mufika ngati skeffayo.

 50. Zisakukhuzeni zachuma cha skeffa. Kodi muli ndigawo pa chuma chake?pangani zanu, mukungokhalira ma rider ndkachasu pamene anzanu akugwra ntchto molimbika choncho kuchta bwino kulakwa? Nsanje imadza kamba kaulesi. Gwirani ntchito molimbika nanu mufika ngati skeffayo.

 51. Kod Munthu Chabwino Chilichonse Chomwe Alinacho Nde Bas Ndiwasatanik? Lucius Banda, Skefa,,,,,,bushiri,, Salanje,,, Pompano Mumvanso Akut Gwalad Koma Malawi Mpake Tikungosaukabe!

 52. Kod Munthu Chabwino Chilichonse Chomwe Alinacho Nde Bas Ndiwasatanik? Lucius Banda, Skefa,,,,,,bushiri,, Salanje,,, Pompano Mumvanso Akut Gwalad Koma Malawi Mpake Tikungosaukabe!

 53. Akamakuona ukulimbikira ntchito mkumabweza komanso mkumasinga mumtimwa mwawo amamva kupweteka kodi akufuna akhale ngati ndani?Skeffa usafooke anthu olephera ndichoncho,,Mulungu alinawe

 54. Akamakuona ukulimbikira ntchito mkumabweza komanso mkumasinga mumtimwa mwawo amamva kupweteka kodi akufuna akhale ngati ndani?Skeffa usafooke anthu olephera ndichoncho,,Mulungu alinawe

 55. ine ndimakonda nyimbo ya kaunda.
  kunena zaena, kunena zaena poti chala sichiloza mwini, wayambitsa zimenezoyo akuyenera kukhala hule mfiti kapena mbabva kkkkkkk akambe zake timve nawo kkkkk

 56. Amalawi malo mothana ndiamene Wavomeleza guy MMalawi muno kuti timuphe ,mukulimbana ndi m’bale wathu skeffa walakwa chani?asatanic simukuwawona?skeffa dont worry akumenyela khondo ndiambuye ife tili pambuyo pako,akuyambisa zonsezi ndioyimba azako be

 57. zamaboza nneneleni ine mbiri yanga ipitsani inu onyongodola ndinyogodoleni koma muzaleka singing ……………….uuuuuuuuuuuu

 58. Pali anthu ena samakodwa azawo akama chita bwino…………. Skeffa mind ur busness don’t what stupt people sayin:D:D:D:D:D:D ;(;(;(;(

 59. Anthu kujohn amangoremera kulibe kutosana chala kuti uyu ndiwasatanic ayi, kumakhala ngati moyo wazungu kodi chumachi munthu wakuda sichimamukhala opanda matsenga?????muyakhe anthu akajaynu, Eish….. Zandinyasa.

 60. U can’t put gd man down, dziwan kut simungapindure ndi mtima wa sanjewo komaso ukamalimbana ndi munthu yemwe Yawe anamudalitsa ndy kut ikulimbana ndi Iye, nanga ndiwe ndan kut ukalimbane ndi Namalenga?

 61. ine kudabw and i ddnt beliv anthu ansanjewa, skeffa which skeffa ,ambuye akhululukile onse olimbana nae,,,,,,,, amalawi muzipeka zina not kuwapekela anzanu zinthu zoipa ngat zimenezo ,,,,,,,,,,,, koma ndie mwampasa nyimbo ndi mutu wa album yomwe ikubwelayi ndie mumvesaso simunati anthu oipa.

 62. You can listen for hours and hours to lovely voice of the skefa chimoto.he is the most talented of music has ever had ndiye mukamati ndi satanic ife timangoseka kuti haa zichedwani zanu akusogolo komatso nafeso tikumukonda i lv y sk

 63. I know some musicians join illuminate /satanism to have protection and become very famous as well but Skeffas back ground is very good i dont think he can dare to do that. Some of us expect him to finish his music art as a gospel musician not these claims.

 64. sungandichotse,zonse ndi chabe koma yesuyo!dont judge 4 u too u shall b judged!musiyeni muthu ayimbe mmene akuziwira,koma amayitha!

  1. ZOONA JEALOUSY DOESNT PAY WHEN JESUS SAY YES NOBODY CAN SAY NO!

 65. “In Malawi we have a problem, when someone is succeeding in life we try to pull that person, I think that’s an evil spirit of jealousy and we need deliverance

 66. KUUNIKA KUKAFIKA PAMALO, MDIMA UMADANDAULA.
  (zamabodza nenereni…mbiri yanga…ipitsireni ine!…onyogodora…ndinyogodoreni ine koma mudzatopa!)

 67. In JESUS NAME LETS BE HONESTLY AND FRANKLY SPEAKING GOD GOTE MORE THAN U CAN IMAGINE.
  GOD IS STRAIGHT seek u shall find .

 68. Skeffa can write, produce the tune, create the beat, he works very hard, he has a voice and OVERALL he is a singer! No doubt he has alot of haters but he will survive.

 69. Skeffa can write, produce the tune, create the beat, he works very hard, he has a voice and OVERALL he is a singer! No doubt he has alot of haters but he will survive.

 70. akudziwa yekha chilungamo gyz nde enanu musadzivute….. wanenayo wawonapo chiyani…fiti zimadziwana zokha usiku kokatamba nde kaya……???

 71. Amalawi ndichotcho basi inu bwanji osalowa kuti inuso mulemele alimbaliyake vonelezani skeffa tikudikila iwe pa( cape maclear)

 72. Just bcoz he is succesful in hz music industry then he is associated wth satanic occult.you fellow malawians ought to b serious sometimes.

 73. Munthu wankulu osakhumudwa za inu timaziwa ndi ife Mulungu apitilize kukudalisanibe nsanje ndiyomwe yakula God bless u Skeffa

 74. zamaboza…..neneleni ine, mbiliyanga ipetseni. …inu. .onyogodola ndinyogodoleni ine. ..koma muzalekaaaa. ……singing. …..mumakwana madala. ..kip it up. ….level. ..we are waiting more from you Mr chimoto! !

 75. Mnena zanuzo mlephela mulungu sangagonje ndi satana satana amagonja ndi mulungu inumkhalila zomwezo anthu apusa inu kungonena zaazanu bas skaffa more fire nena zina ukuwalephela

 76. not every black is ur friend,,#nor every white is ur enermy,,#skeffa wil stil entertaining malawi in music industry 4 eva & eva.#ali mbali yako!!

 77. Kodi aMalawi munakhala bwanji? Aliyense akalemera ndekuti ndi satanic? Mukufuna enafe tiziwopa kulemerako chifukwa choti wina wake atinena kuti ndife asatanic? Zanu izo, tayani nthawi yanu kumakamba za anthu ena. Anzanu tizilemera.

 78. siufuka popanda moto…….kale lonseri bwanji anthu samanena akanene rero ndekuti kenakake kalipo kuweruza ndi kwake kwamulungu……ine ndikufuna mthunzi chonde musadure ntengo wangawo

 79. Anthu ena akamanena kuti malawi wachuluka ndi anthu Anthu ansanje mkumakana,ndi anthu angati omwe ankhala akuimba nyimbo zokhuza nsanje,vic marley adaimbanso nyimbo yokhuza msanje,chonde amalawi tiyeni tisinthe mkhalidwe lonyatsali.

 80. Tikalimbikira miseche tichedwapo tiyeni tipange zoti ifenso ena ake pena pake atidziwe ulesi supindula kupemphapempha ndi tchimo loposa .

 81. But why malawians are like this. ppl work hard to get sucsess when they do you say satanic if they don’t get sucsess you call them failers or lazy! Wat is it you want ppl to do now?

 82. munthu sumamukaikila munthu chinthu choti iweyo sunapangepo amene wayambisa nkhani iyi iye ndintchito yake nd he/she think that momwe ndadutsa muja mzangayu akudutsa momo shame zabwino zonse zimachokela kwa mulungu zoipa zonse zimakutsata malingana ndi.khalidwe lako munthu,mulungu amapeleka kwa amene wamfuna stop jearous guys ask for help m’mene amaimbila bwino skeffa kumalenela ndie anthu tizifusa kuti how come

 83. kumalaw nditelo gat lwe ukutel osayambaso lweyo bwaj kukhalila zopusa basi mukaone abamu yoyamba kenak muziyakhul zopusaz mwav

 84. No smoke without fire. Bwanji sanatchule Gwaladi, olo mkasa…. komabe the truth lies in urself… anyway Istill love ur songs.. osamakhumba too much… Osamangowaona chonchi olemerawa sagona! listen to Luciuos song..

 85. only God knws hw perfect he z dnt judge and people osamuikila ku mbuyo coz u oso hve alot to ansr to God.zione wekha kaye bwnji Allani Chirwa angopereka zimimba kma muziti ndi Ebennezer Galu Wamunthu

 86. aaa amalawi kuzimuka kwambiri! ukapezeka nditimakobiri basi wasatanic! hede! yabwera mochedwa satanic ndi a skeffa omwe! this is kkkkkkkiest!

 87. Ikudalitseni kopotsa achimoto. We love u nothing can Chenge us.

 88. Amalawi koma kunyenga ana azaka zitatu. Tidzafa tili osauka mpaka kalekale. Tikangowona munthu wachita bwino basi wasatanic, m’malo molimbikira kuti tifanefane naye mwina njalazi ndikumazivera mayiko ena ayi. Satanic ya ambuyako SKEFA DNT WRY M WItH U

 89. Skeffa no worry wekhanso unaimba kale ZAMABODZA NENELENI INE MBIRI YANGA IPITSANI INE ONYOGODOLA NDINYOGODOLENI INE KOMA MUDZATOPA,so don’t mind them iweyo ulibe problem.

 90. Wy Malawi bas kukweza ntchito za satana kunyansidwa ndi zabwino zochita ena bwanj amalawi? keep on skeffa don’t mind that fucken rumours we like you

 91. If many people has born with the heart of jelousy hw they can make someone to be somewhere. Bull sheet zopusa kwambiri. If u hv the heart of jealousy and ngati zakunyasani mupite mukakolope nyanja as he already said. Ngati mukufuna kumukopa ku satananic wakukanilani. Aliyese amadziwika ndi ntchito zake. Skeffa amaimba and aliyense akudziwa zoti amayimba. I love him very much. Ndiiye mumakondwa munthu akamaonda mumakwiya munthu akamanenepa. Walemera mwakwiya zakunyasa . Amene mukufunawo palibe chomwe akupanga. Pita pa tsogolo wakwathu ku Nkk. Am proud of you

 92. only God knws coz palibe yemwe angavomere kuti ndiwa satanic aliyense amafuna kukhala wabwino.as for me i lov his songs. makhalidwe ake i dont care

 93. Koma Amalawi Ili Ndiye Jelasi Laufiti Nawo,kamati Kupata Kwamwana akulu Sakodwa Ndizowona Di,walakwa Chani Munthu Asatukuke Mwati Wasatanic,mphamvu Zaulesi Imeneyo Alesi Nonse Mukasowa Zochita Muzingozikanda ,mlungu Sijames Mumafuna Skeffa Azituwa Kufana Ndinu Oti Kukacha Mumangoziwongola,guys Munthu Ndiwovuta Thats y Anamupangila Mfuti Plus Yake Mkumpangila Bomba,

 94. Ndibodza Sangapange Za Usatana Kaya Mwina,koma Skefa Anagwetsa Kholingo Ndi Mai Joice Banda Mwa Mtima Bii Ngat Angatukuke Mwina Ndalama Zake Zachoka Kumeneko Sinanga Nyimbo Mumamubelaso Inuyo Kut Chan?Musamale Ndikulodzani Pano Walemela Muzit Satanic Et?

 95. Hahahahaha Malawi!!! Munthuyu Skeffa alibe mulandu ulionse. Koma kuti tapeza kuti iyeyu amati akapeza kandalama amadya kena nkusunga mmalo mwake wakatamuka palibepo za satanic apa. Enanu tapeza kuti mukapeza ka ndalama kamapita ku Mahule, ndi Malaida. Kodi choncho mungalemele? Ulesi umadzetsa nsanje

 96. eeeeshiiii amalawi tinatani muthu asatchuke walowa satanic. mulungu akamudalisa ndichuma.mumati ndiwasatanic. kod ngat munamuwona muthu akuvutika. mumafuna azikhala opephampaka kale mulungu si BETHER Amasitha nyengo. yowawa kukhala yokoma@

  SINDIZASIYA KUMUKONDA. NDIZAMUKONDA MPAKA KALE CHIFUKWA NYIMBO ZA ADAWA. ZIMANDISHA THOKOMELA KWASI

 97. Malo mokapepha nzeru kut mwina next time mufanane naye mwayamba kumupekela nkhani zoipa. Skeffa tmakukonda asiye asatanawo azingokanda iwe ukupita patsogolo.

 98. HE|SHE WASTING TIME 4USELES THING LIKE THAT.SKEFFA DONT WORY ITS UR ECOURAGEMENT KEEP IT UP MORE MUSIC,ICAN SAY DONT TIRESOME OK.

 99. Aliyese opanga zoipa ndi satanist yaa a member of satanisim moti simuziw but dont point fingers pamene iwesoso zangozaza mmaso. Panga zako kodi watani leave skeffa alon

 100. zoti ndiwe wasatanic kapena ayi,ife sitkuziwa zoona zake akuziwa ndi Mulungu ndi mwiniwake skeffayo!tiyeni tkhale buli tizaonana poweluza.

 101. Koma munthu aaaaaa,ine wandikanika zoganiza zake.Kodi ndiye munthu asapange bwino? I think munthu amene wayambisa nkhani usatanikiwo yiye akuwufuna komanso ali ndimasomphenya wozakhala satanic. Shame on you devil!!! Lesten Alimbali yanga ya Skeffa ndipaneme ungapeze mayankho abho azomwe ukunenazo.GOD BLESS GOOD WISHERS TO SKEFFA.

 102. Of course I support Dan Lu n Saint ( Yami) But Skeffa ni Moooo Fire……the Malawianz which I know, they are alweyz Full of Jealousy….Leave Skeffa az he izzzzz, Skeffa no sizeeee……..

 103. Annie matumbi sananame kuti munthu ndiovuta kuposa nyama zonse za kuthengo! Skeffa never mind these nosense keep going on what you do coz god gave you that talent

 104. They have seen ability in u, but dont care them they have nothing to do thus why the’re trying to pull you down. I respect ur talent & believe comes from Almighty God

 105. VUTO LA MALAWI ANTHU AMBIRI AKULA MOVUTIKA ZA CHINGUZU AZIWONA POSACHEDWA NDIYENSO A MALAWI ALI NDI NSANJE NGATI YA NKHUNDA YOBADWA NAYO AMENE AKUTI ULI NDI EVIL SPIRIT NDIWOWO ALI NDI MA EVIL SPIRIT KODI A MALAWI SADZIWA KUTI MULUNGU AMAPELEKA MWAYI WOSIYANASIYANA KWA MUNTHU ALIYENSE

 106. Insted of dealing with mathanyula behaviour now your busy dealing with those people who are wellbeing in their financial status through their hard working spirits…..Mukhala choncho chifukwa man wa sound amakwapula mopanda malire ndipo azaposa pomwe alipa inu phee muone!!!

 107. eeeee ayi a Malawi simudzatheka ndinu okanika ndithu Piksy – Nthuzi sinaname poti zanu zikukanika mwayamba kuloza zala anzanu…. kaya mwina mukudziwana

 108. Guys lets nt put bad image to our celleblity, munthu asalemere walakwisa,mufuna munthu azikhalabe momuja? Mopephapepha thats nt gud zandibowa.plz!plz! Work hard Allah shall provide u anything u dream of, uuuukoo,,,..

 109. Amalawi Kunena za Ena #1. Mabodza akula. Pastor changed to a snake linalinso Lie. Kodi ndi chani chikuchitika mxm.

 110. paja kumalawi ndichoncho munthu usachite bwino or kulemera ati ndiwe wasatanic!! kod mtima wotelewu malawi angatukuke? abale tiyeni tisinthe nthaw yonenana inatha…

 111. People are like that if a song or a singer sings beautifully and the music is making pple happy they say u are a satanist

 112. Kkkkk Mukuchedwa kulimbana nd Skeffa Mzanu uyu Akulimbkra ulesi bas osamakalima thonje uko bwanj?? or Zipwete Mzanu Kunja angopita daily uyu ngat ku Nsanje hahahaha Malawians!!! Why?? Live him

 113. Vuto la a Malawi ndi nsanje pamene tawona kuti mzathu akuchita bwino,koma tidziwe kuti nsanje sipindula.

 114. I thnk skeffa is a christian,and i believe that,b4 he sing a song first he neeldown n pray to god,then start dreaming a song,aftr that start wright a song,then cune the voic everythng put in condition,thats why skeffa is a hot musician in malawi,if you listen n followng nicly he song,you will be conected with god,evn in your country shall never ever be war,just freedom n peace.but the weeked people are hate ds,plz stop jelous insteed of work hard that god wll bless you2

 115. SKEFFA dairy timaona news akaimba kwakuti,iyayi koma uku sichina ayi kulimbikila basi ndiye zikamayenda basi Nsanje kuphatikiza ufiti mkumapeka bodzo..Skeffa ndiyenkhayo timukonda palibe wina so mlekeni mulingu waloza iye ku mpumzitsa mtundu wake!!…mwa iye tinyadila …..Kip Burning munthu wa mulingu!…

 116. Munthu wochita zabwino anthu sachedwa kumupekera nkhani, ndizimenezotu Skeffa usafokere angofuna kukubwezera m’mbuyo tipemphe Mulungu atithandize amalawi tisinthe mkhalidwe wa nsanje.

 117. Guys amalawi jerasi si umuna inuyo amene mukuti ndi wa satanic inuyo ndiye asatana chifukwa mumafuna kuipitsa mbiri ya munthu uyu kodi simunave kuti chanu si changa inu mukufuna usatanic wanu mupatse skeffa hesh mind ur busness Malawian jaracy

 118. Tandipatsirani mbazukayo ndiwaphulitse onse akufalisa dzina lonyasalo kwamunthu wamkulu pamaimbidwe khokhokhokhokho chipere

 119. Kkk ignorance is a problem. This kind behavior we wil end up embrancing satanist without recognising who they are & running away from men of God claiming they are satanist! So watchout, my fellow Malawians,lets stop being childish.

 120. Zitha kukhala zoona nanga mbuyo monsemu samamveka ndi mbiri zimenezo bwanji???? Zithanso kukhala za bodza paja a Malawi mkukhala kwawo;ka ndalama kawo amathera mowa ndazimayi komanso sagwira ntchito aliyonse yomwe ingawabweretsere ndalama pomwe nzawoyu ali ndi zochita zambiri komanso sound yake ndiyanyatwa;iwo akumangosintha akazi alipheee mutukuka bwanji??? #MULUNGU ndamene akuziwa za zimenezo ine ndilibe umboni wokuti mkuluyu ngwa sataniki kapena ayi kotero sindinganene zambiri pa nkhaniyi

 121. M’alo moti mudzilimbikile panokha busy ndi kulonda munthu, Koma ngati khalidwe lidzikhala lotelo umphawi ukubandula moipa. No wonder lots of shallow minded people dies poor!

 122. Sibwino choncho mukufuna azivala sanza kugona kanyumba kosalongosoka azipemphesa aaah musiyeni anjoye ndindalama zake kod mesa ndioimba uyu ndintchito kaya kod mwatani koma mukuchedwa ndikuweruza anzanu iwo zikuwayendera

 123. Muchezera yoloza zala azanu akutukuka dziko lake lomweli cmunaveko mau oti kapolo azasanduka fulu chachilendo ndi chani.

 124. Koma mumutha chifukwa munthuyu sound amakwapula saizi kukana.Apanso mwachita bwino ukulu wamulungu waonekera mumafuna azituwa, kodi simunamvere akuti anamuuza kuti kamene wakapeza. akasunge bwino ngati mbewu osati chokolola. shame the devil

  1. No wonder 3/4 of ppo from Malawi r lazzy in thinking,how can one think so low like that,illitracy is another contributing factor,We hunt for money & not money hunt for u,wake up Malawi

  2. Shame on u davie plz plz ntundu wanga zuka malawi kodi sukuziwa zomwe mulungu amapanga skeffa wake ndiyemweyo ukumuziwa yemweuja lelo mulungu wamukweza let god be god pa skeffa

  3. Amalawi amasangalala ukamapempheza kwa iwo azikulalatila, ufiti basi ndichifukwa chake tikukanika kutukula ziko lathu lomwe.

 125. czoona munthu ndiwaluso basi muchezera kuloza zala azanu akutukuka dziko lako lomweli simunaveko kuti kapolo azasanduka fulu chachilendo ndi chani.

 126. Peace be to God and to U Skeffa, some people are busy talking bad things about u. They want to push u down which is not good anymore. Keep the fire burning, they dont know they are pushing up instead of pushing u down.

 127. iknw skeffah lusoli ndilake si satanic.kuimba anayamba kalekale ali ndi luso ndi mwayi so plz plz plz malawi dont tanish his image respect yourself.ilove skeffah olo mutati munampeza akutamba sindingatsike ilove him.

 128. today i travel on foot.. but after some years i will be rich.. people will say am satanic.. thats malawians.. but today i dont sleep enough finding the way to prosper in life…

 129. Amalawi yatkulir ndinsanje bas,wina akangpit pasogol bas taymbap kudeseran mayin,mmmmm guyz tien ticepes kaduka kt malaw apte pasogol.

 130. VUTO LA KUMALAWI KUNO NDI LIMENERO.MUNTHU ASACHITE BWINO WAYAMBA SATANIC,KODI AMAKANIZA?MESA A SATANIC WO AKUFUNA ANTHU,OSAKALOWA BWANJI?SI BWINO KUYIPITSIRANA MBIRI MULIBE CONCRETE EVIDENCE.

  1. maybe they think that satan is richier than God.they think God has no resources to bless someone with.its a shame really.

Comments are closed.