Malawi Police in Ntchisi district have arrested four people including an Admarc official and a police officer on suspicion that they connived to steal 100 bags of subsidy fertilizer and hand them to a vendor who had bribed the four with a sum of K375,000.
Ntchisi Police Public Relations Officer Gladson M’bumpha identified the suspects as driver Dalitso Chafikila, 36, Admarc unit marketing officer for Msumba Admarc George Kambwiri, 56, police officer at VIP branch in Lilongwe, Sub-inspector Stephen Katundu, and the vendor Chikondi Kalulu, 34.
M’bumpha said that the Admarc manager for Ntchisi and Dowa, Yasinta Nora Jere, reported to police after realizing that a motor vehicle registration number BU 3009 belonging to Apita investment which was carrying 300 bags subsidy fertilizer meant for Mzandu and Nsinda Admarc depots was diverted to Msumba Admarc depot where it only offloaded 200 bags of fertilizer.
The suspects then took the remaining 100 bags to the vendor’s shop where they offloaded them.
According to M’bumpha, the vendor gave the Admarc official K175,000, the truck driver K130,000, the police officer K50,000 and an assistant driver K20,000.
Member of Parliament for the area Honourable Kalima alerted Admarc officials who started their own investigations and discovered the discrepancy.
The Admarc officials reported the matter to police who arrested the four after investigations and Kambwiri admitted to have been involved in the bribery.
Chafikila hails from Chizuka village T/A Mtema in Lilongwe, George Kambwiri from Nankhako village T/A Mtema in Lilongwe and Chikondi Kalulu hails from, Ndendere village T/A Chikho in Ntchisi.
Anthu oipa kwabasi, they have to face the music bad habit. Why do you have to take all the poor have
Let’s wait and see.This is Malawi. Only the poorers will servl the Jail
Mbuzi za wanthu, K375, 000 matumba 100 kupusa kwake kwa mtundu wanji katundu wa K2,000 000 kukangopereka basi, olo titamusiya pa 10000 per bag ndiye kuti ndi 1,000 000.
shiiiii ali pa relationship ndi apolice muzingowona wedding ring yo.
It happens nde dziko limenel
Fetreza wina anandgulitsa ine dzana .andbwezele ndlama zanga azatenge fert wawo!!!
ndiye anthu ngatiamenewa chilangochawo ndichotani tawonakuti avaladi zibangirizo? Mufatsepo apo .
Osandinamiza kuti ku mmwera kulibe chinyengo koma ndikudabwa sindikunva nkhani zokhuza katangale kummwera.
We remembered dr ngwanzi bingu as ant corruption
In lilongwe kwa mgona akapeza wakuba amamuotcha pano anthu amaba koma amadziwa kut akapezeka aotchedwa iwoso aotchedwe ena aphunzire
Ndilo ziko kusiya ndi ku gwila Mwana …….. Komanso ….mukuchedwa ndi mijedu bwanji tiyeni tikakumane………komweko
Achikondi mwazionatu mudatizuza ko khuwi Admark apa ndie mwalowa wamu maula basi
Achita bwino kuwamanga kut ena atengele phunziro
Aphedwebasi chifukwa alibe chisoni komanso matha alibe olonso manyazi njee musungilanji mbuzi za anthu ngati izi.zopanda chisoni ndi anthu osauka.marabishiiii
Oh dear!
Ndondomeko ya fertiliser otsika mtengo sikupindulira amphawi ayi.
Inu Amaudindo Gwilani Ntchito Yanu Zimakhala Zowawa Nkhani Mmene Zalengezedwelamu Mukampeza Munthu Amutaya Pazifukwa Zosaveka Bwino Itini Polengeza Zimaoneka Ngati Wapalamula Zenizeni Pothela Pake Munthu Oteloyo Amachita Matama Kuti Wa Ndalama Sa Mangidwa Koma Amphayi.
Nkhani ya mzana inu mukulemba lero tinamva kale izi malawi 2f mumakonda kukamba zinthu zoti ma medias onse zawakwana yet bwenzi muli oyambilira.
I like handcuffs !
Mavendor akugulitsa fert.K26000 per bag,chonsecho akumabanso.Anthu oipa kwambiri amenewa
DALITSO TIKUSOWANI KUNO KU NAMBUMA KUBAKO UNACHITA BWINO ZANGOVUTA POTI AKUGWIRA.
Malawi will remain poor bcz of this habit. It’s not strange thing “Ngati liyamba kholo kukodza pamphasa kulibwanji mwana wam’nyumbamo angatuluke panja?” Apa Malawi uja wakodzeledwa m’maso ndi Satana sangatheso kuona kutsogolo ndipo wathimbilira alibeso colour mbili yake yanyasilatu ndinkhani zopandapake ngati zimenezi.
Kwa ma Kape onse obera anthu ovutika!
Ma Kapee onse obela anthu ovutikaa!
How many Admarc Official arrested ? mmmmm is getting worse now juxt kill them once
Those r greedy pigs.they 2b wit the community.
Ta omberani
Subsidy fertlizer is free anthu mukuba kumakagulitsa anthu akumalawi ndiovuta mukatelo muziti Boma silikupeleka fertlizer
Koma Ku ntchisi mwanyanyatu tizingova zakumeneko.
Mvula yayamba kubwera bwino mukubanso ferti… kodi amalawi mumafuna chan? anthu adzisowanso chothira m’minda choncho njala ingathe? tadzikulani kma adzikukwizingani choncho sitingakumveleninso chisoni mukujaira.
Malawi good at stealing from head to toe.Evil!
Thats why poor pple will remain poor while the rich r’keeping Billions in there Accounts!its amazing nw 2hear Minster of Finance saying dat our ECONOMY need #GOD,whats the conection btn money ‘n’GOD?haaa’u mst b,jocking!Anthu inu mwangokhala ma udindo jst 2enrich urself not 2solve our Country Prblm
Bola ngati ndalama yakwanira no matter kuti awangulisira ma vendor
ACB guyz were here in Ntchisi yesterday ,hope nkhaniyi chilungamo chake chioneka!!!!
Malawi wavuta aliyense afuna kulemela basi
Pa malawi satana safalikira ndipo akugwira ntchito yake
Is what bible said that it will happen in last times
Well done!
Job well done for the apprehending of these culprits.Bad practice like this does derail national development,thereafter,some pple begin to point fingers at govt yet they are spoiling themselves.
Ziphuphu zagona ku police,nanga mpaka kuba fertilizer?
They should face the law
Aphedwe amenewo,akufuna kupha myandamyanda yawanthu ndi njala.zinthu zachinyengo zafalikira kwambiri mmalawi muno bz of policemen.
Umbava ku malawi sudzatha
Uphawi wavuta tengani khasu mupite kumunda
Enanu musathe mawu inunso mudzagwidwa tsiku lina,moto upita kwasala udzu
Amangidwe anthu akubawo, km apolice agwire ntchito mopanda chinyengo. (chilungamo patsogolo ndalama pambuyo)
Basi akalowe
Size ya mtaun
Ofunika kuwa Charger zaka 36 aliyense
Survival Of The Fittest,,imadya Apo Aimangilira
why doing this? pliz God have mercy!!
Life is hard here in malawi, evryone is trying to be suvivor-of-the-fittest
Ampeza pole amenewo
Mangani mfiti izo.