‘Come home and prove your innocence’, Joyce Banda told

Advertisement

She continues to claim that the current regime wants to arrest her and has not yet provided her retirement package, but ex Malawi President Joyce Banda is being called upon to come back from her ‘self-imposed exile’ to clear her image on her feared involvement in the Cashgate scandal.

Banda has continuously  hinted that she is  not coming back to Malawi anytime soon because of political arrests that await her hinted that it remains paramount for President Peter Mutharika to do his job and not talk bad about her.

Christopher Mzomera Ngwira
Ngwira: Says Banda need to come back home.

But this time around vocal northern region provincial chairperson, Christopher Nzomera Ngwira who was behind a move that ousted Banda for Khumbo Kachali before it got rescinded wants the President to come to face her critics.

Banda has been now implicated three times by Cashgate convicts as having been the one who championed the scandal which dented her image during her era; a regime she gave away to Mutharika in a disputed poll last year.

When speaking to Zodiak’s Maganizo Mazeze on Sunday, Ngwira argued that despite the fact that the Peoples Party (PP) needs her to lead the party, it is something of paramount importance that Banda come back home to clear the mess her name has worn.

”You see, Banda is innocent. She personally told me that she never took part in any of the acclaimed theft. She asked me and the other officials to concentrate on the work.”said Ngwira before rendering a coy question on whether that response was enough to vindicate the ex Malawi President.

However, Banda is still not coming to Malawi as she cliams that the Mutharika led government intends to politically haunt her, something which the ruling Democratic Progressive Party (DPP) led government has played down.

Recently, Mutharika said claims made by Banda that she was not been given her retirement package were insincere and aims at denting his image toward donors.

Joyce Banda
Banda: Being asked to come back home.

“I wish to inform the public that numerous claims purportedly made by the former President Dr Joyce Banda that she is failing to return to Malawi because she is being denied retirement benefits, including accommodation and security, are insincere.”

“Government has duly provided to Banda the requirements of a retired President as stipulated by the President’s (Salaries and Benefits) Act,” reads part of the post.

On Banda’s gratuity, Mutharika said the former president has already received a tax free lump sum amounting to K30 million comprising MK12 million and MK18 million as gratuity in her capacity as former vice president and former president, respectively.

However, Mutharika admitted that the former president is yet to start receiving her monthly pension which he says is currently being processed by the Director of Pensions at the Accountant General’s office.

According to Mutharika, Banda was also offered several houses to choose from in some affluent neighborhoods of the capital city but she rejected most of them.

Mutharika also said Banda has been provided with seven police officers in accordance with the President’s (Salaries and Benefits) Act.

The battle between the two did not just end in the elections, it surely rages on.

Advertisement

166 Comments

 1. Kkkkkkk panopa aliyese akumazi dyetsa ekha sithawi yolimbana ndi ndale kapena ulamulilo ai ndibwino kumalimbana ndi bible bola tikapulumuke. Chifukwa aliyeye tikati tizivota tikumadyeledwa masuku pa mutu akumabwela ndi nzelu zao ngati athu anzelu cholinga awine aleme le basi ndiye agaluwa tatopa nao ndibwino azikakhala pa mzela ku ma vota okha basi bola ulamulilo wa bakili unali onama koma timalandila zithu ma bridge amamangidwa mokwana minseu koma pano aaaaaa manyazi ine mpaka ndidzafa or iven ana naga adzafelamo koma sadsa ponya voti ndibwi kumalimbana ndi kutamanda chauta basi

 2. Kodi simumadya mmakwanu chifukwa mnthuyu ali kunja? Musatisokose ndi zimenezo wangwiroso ndiye uti pamenepa akadzabwera tidzamva

 3. nose boma la peter panyapanu msandsazse mwava ho! zosusa inu 577bn mkusya kut musyen muthu wamay azdyelera kumene alko pete ndalama umangothela kukwatla mabodegad akowo chslu iwe agu choka!

 4. KODI NGATI SADABE AKUTHAWACHANI.MUSAMAYEREKEZE NDI MULUZI.PACHISENA TIMATINBO OIPA AMBATHAMANGA YEKHA.AMANGIDWE AMAI ,MOSATENGERA CHIPANI OR NDALE

 5. malawians r hardworking pipo.how can a villager get K20 pin for jst a bag of fertilizer?tell me how can a villager work hard 2 makesure he gets the reqired medical treatment @ the hosp? its the duty of the government.pipo r doin their part bt govnt is failing them.

 6. akabwera,mankhwala nzipatala apezeka?njala itha?umphawi utha?nvula igwa bwino?fetereza atsika?mitengo yazinthu itsika? we dont want JB in malawi.first tell us pipo involved in 570bn cash gate. dont be selective.once MCP comes into power u will all payback without secretive.mzlswisns dont want JB.malawians nid food,good health and better life not wat DPP is offering now.ndakwiya nawe kwabasi!

 7. akabwera,mankhwala nzipatala apezeka?njala itha?umphawi utha?nvula igwa bwino?fetereza atsika?mitengo yazinthu itsika? we dont want JB in malawi.first tell us pipo involved in 570bn cash gate. dont be selective.once MCP comes into power u will all payback without secretive.mzlswisns dont want JB.malawians nid food,good health and better life not wat DPP is offering now.ndakwiya nawe kwabasi!

  1. malawians r hardworking pipo.how can a villager get K20 pin for jst a bag of fertilizer?tell me how can a villager work hard 2 makesure he gets the reqired medical treatment @ the hosp? its the duty of the government.pipo r doin their part bt govnt is failing them.

 8. Anthu apanda nzeru kumalawi achuluka dziko silidzatukuka, chifukwa sitimafuna kuona pomwe panayambitsa vuto, moti pa ma presdent onse uyu wayesetsa, onse ankathandizidwa, koma mankhwala ankasowabe, miseu anayilephela, koma uyu sakuthandizidwa ndiye mukuuembekezela kuti achite zoposa onsewa, kahule kanuko ndikomwe kanaononga dziko, kuteleku kakupabgila uhule komwe aliko, abwele adzalandileko chilango, adzakamukwele anyamata ku kaidiko.

 9. Za zii bax, muluzi was not arrested why JB?after all there is no real evidene if she is behind the cashgate scandle,mr president have u forgotten how ur brother spoiled the economy of this country,busy basi ndikumavomeleza zonena za ma donors kuti you should drop charges against that stupid so called gay couple..koma busy kusokoneza zinthu mdziko muno ndi kulimbana ndi jb basi,muyambe mwachotsa chitsotso cha mdiso lanu..asiyeni amayi azikhala pa easy komwe aliko!

 10. Mukungovutikanaye jb tilinayekuno ku rasten berg akudyazake inumuzingosaukabe kuvutika mkumamunena.mwaiwalakuti imadyapomwe aimangilila? Leloinu mwadyapakulu zakuvutanitu..jb alindimaziko ake musiyeni.

 11. Nthawi yoikira kumbuyo wandale aliyense ndilibe.kuti ndipeze chilichonse pa moyo wanga nkuyenera ndi thamangethamange ndekha.No any politician in Malawi iz clean.

 12. Anthu enanu ndiye nzeru mulibe, kodi mwayamba lero kumva zaumbava m’boma? Ndi anthu angati akhala akuba ndalama zaboma koma wosamangidwa? Poti zimatengela kusaphunzila nthawi zina, poti ukakhala wosawona umafuna wokulondolera njira. Zaziii! Tangobwera pano pa capetown nanu muzafune chanuchanu chuma wosati zamkhutuzo.

 13. Uyambe wachosa chisoso mdiso lako ndiye uzichosa chanzako zaka ziwiri anaba zingati mai mukamakamba yamai mkukwiisa mutundu wa malawi zikomo

 14. One word for those who are against the decion to come and answer the charges…Ine am failing to describe them…help me pliz ..are these pipo malawians or mozambicans??help me pliz

 15. Kodi iyeyu BWAMPINIYU sayimbidwa mlandu limodzi ndi a JOLOJI CHAPONDA?Mmalilira mpando waupulezidenti ndiumenewotu basi kungokhalira kulozana dzala mwanya nalo boma asaa mbuziii inu sizinachitikepo kuti anthu akhale zakazaka osalembedwa ntchito mpaka kugulitsa zipatala kuvomereza u GAY ndiye wabwino ndani pamenepa khalani ndichibwampini chanucho ife ayi walaura dziko ameneyi shupiti

 16. Msiyeni mayi akhale ndi mtendere. Ndalama zinapita. Konzani zinthu zimene zikusowa pano

 17. amalawi tikazasiya kupondelezana ,katangale,kuba, zithu zizasitha kma apo ayi mmmm tizingovitikabe. komano amalawi mutalingalira bwinobwino ,kugeja bobo,boma ili linangotengerapo m’pata kukwangula zinasala zija.chifkwa boma kunena zoona silingakhale opanda ndalama? vuto ndiloti amalawi ife timapanga ndale molakwika ,eti ndale pachili chonse dziko silingayende bwinobwino. kmano apa titasitha mbali bwanj ? apolice athu ali namba wanu pa afrika katangale ndi ziphuphu ofufuza anafufuza kale ,manyaz bwanj boma lamalawi. nkaka ndi uchi pano udaora unayamba kutuluka phusi,,,,,dzaka 51 palibepo chositha.

 18. oh my God,wud u pliz grant her long lyf so d@ whatever she is running away from must face her, amen.”Amayi bwerani mudzaone mbava zinzanu mmene zikubera,osati zanu zija zotengera mmakatoni zija,ahhhhh

 19. She must come and answer the cashgate scandle.Is this woman a Malawian?

 20. Dziko la Malawi silipita pa tsogolo kamba koti tikasankha atsogoleri . Mmalo mochita chitukuko amakhala kutanganidwa ndi kumanga anzao ponena kuti anasakadza ndalama za boma. Koma ndi kungotaya nthawi chabe mmalo mopanga chitukuko. Mayiko ena anzathu odala sasakaniza nthawi, ya kampeni ndi nthawi ya kampeni ikadusa amalimbana ndi chitukuko nkaonatu mayikowa ali okwela pa chuma. Muluzi anamanga Kamuzu nkhani yake ati anasakaza chuma cha boma. Bingu anamanga Muluzi nkhani yake ati anaononga chuma cha boma. Lero Peter akusakasa Joyce Hilda Ntila Banda nkhani yake ati anaonga chuma. Izi zimangoononga chuma chathu pa zithu zopanga pake kamba koti mumalipira maloya oti ndiolemela kale pomwe nzipatala mulibe mankhwala. Izi ndi zomvesa chisoni komanso zodandaulisa, pomwe atsogoleri a ndalewa amafuna kuonela abwino pa nthawi yomwe akulamulira. Pakazapezeka ntsogoleri osalimbana ndi amene wasithana naye mpando, ameneyo azakhala hero wa malawi chifukwa izi zizakhala zoyamba kuchitika mumbili ya dziko lathu

 21. Winawe ukukondwa chifukwa choti wavomera ndipakamwa pako kuti satana akugwiritse ntchito kaya zanu izo ife athu ndi maso,pajatu mukamatukwana mumalandira makobiri kuchokera kwa afiti anzanuwo shame!! ndatitu shame!!

 22. Kodi munthu kuti Abe ndalama koma mankhwa ndimafuta agalimoti zipatala azipezeka, aphunzitsi ndi ogwila ntchito zachipatala alembedwe ntchito, magesi aziyaka , fertilizer agulitsidwe munthawi yakekomanso mtengo wosika, mwachidule zofunikila Kwa amalawi zizipezeka ndikuti muthuyo asamabe koma zifukwa ndatchulazi zisamachitike,pamenepa wabwino ndi uti? Chifukwa akanakhala wabwino bwenzi zithu zikuyenda Maya.

 23. 2 yrs only kuchita ma scandle oposa zaka zake zobadwa? We are tired of singing the very same song,, abwere,abwere, who is JB? MSCE certificate yomweyi atinyadire nayo? We need professors only NOT PROFESSORS BY THE NAME but only those with PROFESSORIAL QUALIFICATIONS i.e, Professor Arthur Peter Mutharika. Afune asafune abweratu mayiyu. Iyaaaaaa, tshwiiii!!!! retirement! What for? nyumba 10 zonse zija adamupatsa kuti asankhe zija zosamusangalatsa? Akhale kukamwa kwakeko mwina kungamusangalatse!!

 24. 2 yrs only kuchita ma scandle oposa zaka zake zobadwa? We are tired of singing the very same song,, abwere,abwere, who is JB? MSCE certificate yomweyi atinyadire nayo? We need professors only NOT PROFESSORS BY THE NAME but only those with PROFESSORIAL QUALIFICATIONS i.e, Professor Arthur Peter Mutharika. Afune asafune abweratu mayiyu. Iyaaaaaa, tshwiiii!!!! retirement! What for? nyumba 10 zonse zija adamupatsa kuti asankhe zija zosamusangalatsa? Akhale kukamwa kwakeko mwina kungamusangalatse!!

 25. While you are talking like that” i like her leadership as second from muluzi” accusation is helpless to poor malawians.just maintain the economic crisis and enough drugs in the public hospitals you will see we will start loving u as vision leader

 26. While you are talking like that” i like her leadership as second from muluzi” accusation is helpless to poor malawians.just maintain the economic crisis and enough drugs in the public hospitals you will see we will start loving u as vision leader

 27. akumuikera kumbuyo ngamene anadya nao cashgate money, kutoluku inu cmuziwa zimezi? mapresident onse.mbuyomo amaba koma sizinaonekere chifukwa they were very clever, ndipo madoners sakadasiya kuthandiza. koma kuba kongoba ngati makosweku. kukhala ngati kuti mwini nyumba wazimisa malights, ndiye iwo amasuke.

 28. akumuikera kumbuyo ngamene anadya nao cashgate money, kutoluku inu cmuziwa zimezi? mapresident onse.mbuyomo amaba koma sizinaonekere chifukwa they were very clever, ndipo madoners sakadasiya kuthandiza. koma kuba kongoba ngati makosweku. kukhala ngati kuti mwini nyumba wazimisa malights, ndiye iwo amasuke.

 29. SHE DOESNT EVEN QUALIFY TO GET RETIREMENT PACKAGE BECAUSE SHE RECEIVED LOTS OF MONEY FROM CASHGATE MORE THAN HER RETIREMENT PACKAGE

 30. Mayiyu ndiwakuba kwambili abwere tikumufuna adzabweze ndalama zathu Zitsilu. zina zikumuyikila kumbuyo mayi wakuba ngati ameneyo kodi chimakhala chamba chani Nose mukumuyikila kumbuyo panya panu Agalu nonse

 31. Mayiyu ndiwakuba kwambili abwere tikumufuna adzabweze ndalama zathu Zitsilu. zina zikumuyikila kumbuyo mayi wakuba ngati ameneyo kodi chimakhala chamba chani Nose mukumuyikila kumbuyo panya panu Agalu nonse

 32. Mziikila kumbuyo mnthu wanzelu osat ameneyu,,,inde palibe wachilungamo pandale uyuyu anaonjeza,, ndlama zimene anaba ndizanu ndye mzimuika kumbuyo? Iiiii inu mwaiwala amakutailani himanga ngakhale pamene anataya sipakuziwika,, mmmmm munadya zambiri eti?

 33. Mziikila kumbuyo mnthu wanzelu osat ameneyu,,,inde palibe wachilungamo pandale uyuyu anaonjeza,, ndlama zimene anaba ndizanu ndye mzimuika kumbuyo? Iiiii inu mwaiwala amakutailani himanga ngakhale pamene anataya sipakuziwika,, mmmmm munadya zambiri eti?

 34. Okuba tilipo ambiri koma kutsagwidwa,so we must punish yemwe wagwidwa kuti ena atengerepo lesson.Akabwera ndidzaimba kuti:waba wekha! Utsalire!!

 35. Mayi musabwere kuno dziko lija layipa ndipo mlomwe uja mmm watizuza misomkho pali ponse mpaka ma condom.Avomeranso mathanyula kkkk koma malawi uja wanukhaa.

 36. Panyapanu nonse amene mukut Jb abwere, nd ndrama zngat zomwe galu wanuyi wadya? nchimwene wake anatenga ndrama zngat popta kundata kwakeko? apa wagulitsaso ma tractor ndrama zake zapta kut? musiyen mzmayi akhale nd mtendere wake osat za kunkholo mukunenazo mwanva? Njala kumudzi muzipatala anthu akudya kamodz, mankhwala kulibe, nanga magetsi mutiuza chan? pezan manyumba muzchta umathanyula mwasankhawo, dzimitu dzanu!!!!

  1. Yu a just shameless idiot, yu dont have anything sensible to say,do yu know de reason why there is no medicine in the Hospital, why electricity is On n Off? Ndichifukwa ma Donors analeka kupeleka thandizo kumalawi chifukwa cha Cashgate wamva then who caused it? Osamangotukwana apai,ulibe nzelu ndi umunthu chifukwa choonesa umbuli ndi kutukwana wapindulanji? Ozindikira akaona anthu ngati inu amati onani chitsiru sichidziwa kusova vuto mmalo mokonza zinthu chimangotukwana,osamangotsutsa zilizonse coz yu hate the one who’s ruling n his party,yu must understand wat he’s saying.

  2. Nthawi ya Bingu ndiye kuti magetsi sankazima pumbwa iwe? there is no any sensibility in peter he has education without wisdom and vision,why u are just pointing on JB have you forgoten about Bingu who died with bags of money in his room,pliz u should think before u reply to the comments of ur friends,remember that this is the worst president than ever b4,you are behind him because u are dating with him

  3. Point of collection Chirwa Watson Chitete is dating your father why yu 4gate fast,I want insult a small boy like yu when he insult me I just flog him.

  4. u idot zoti boma ili likuphula njerwa zamoto zomwe linasiya boma la pp sudziwa ndiwe mlendo mziko muno eti? Ukanena zoti muzipatala mankhwala mulibe ndimmesa mukumabamo mkumagulitsa?zoti munthawi yamakoyo mitembo yokwana 50 anaikwilira dzenje limodzi kamba ka kusayenda kwa zinthu muzipatala kukhala ngati kuno kuli nkhondo waila?iwe ndi mbuzi mmutumo mwazadza mamina okhaokha

  5. Iwe yo garu ndi mako JB yooooo ine Mlohmwe in Botswana or utani or ulalate fotseki ndi makoyo as she land @ any airport she wl be arrested…..tel her to come u wl c w@ Ndata means…uxazayambirexo mau ako wa udzasowa wamva….u a 2 young

  6. Palibe Zotukwana Apa. Jb Kaya Abwera Kaya Sabwera It Can’t Change Immediate Calamities We’re Facing. Cashgate Was There Since 1994. Tingozolowera. Tafa Tatha.

  7. Kodi Jb Ndi Amako Sakukudziwanso Mbuzi Mano Kunsi Ngati Pamalawi Pali Mavuto Galu Wake Ndi Ameneyu Abwere Ngati Akudziwa Kuti Alibe Vuto And Ngati Akusowa Mtendere Zonse Umbava Wake

  8. This Stupid idiot if not that he was abeneficiary of JB….then one of his relative is onthe payrole of this Hilda..Unfortunatel u want us to dance to ur sympanthy.kkkkk..Utukwana Utopa bt tell ur anganga U~She will be arrested…come what may!..Muzikatukanira ku Makwapala prison….shame on u cochroach!

  9. Hehehehehe….. Tiyeni nazoni guyz. Kwa munthu amakhala ku Malawi kuno, ndikukhulupilila kuti akudziwa kuti ma donors anathawa in 2013 pomwe chipani chija chimati nzimayi azitakata, kukhala nzimayi sichifukwa ali president. Komanso nthawi imene ija nkuti anthu ogwira m’boma akumagwidwa ndi ma million in cars and homes, who was den president ? So, budget ya Malawi relies on donors, nde how can u expect kuti mankhwala apezeka ku hospa ?

  10. man fuck u, stop insulting the late, intime of bingu kunalibe njala, mankhwala analipo muma hosp, only thing that went wrong was fuel coz of sme political propagandas, mutharika bingu invested alot for your ass to be at a better place, you can call lilongwe and blantyre a city coz of sme strong policy and development that bingu did, college of medicine in lilongwe, must, new kcn, zina ukuzidziwa wekha, malawi became second fastest growing economy in the time of mutharika, malawi even began donating food to other countries , your hate to the dead man is your curse, if we had him by today, malawi couldnt have been hopeless, and nw u expect peter just correct all jbs trash at once? does he have super powers to command all the problems to go away? learn to be cooperative and stop hating, else quit

  11. man fuck u, stop insulting the late, intime of bingu kunalibe njala, mankhwala analipo muma hosp, only thing that went wrong was fuel coz of sme political propagandas, mutharika bingu invested alot for your ass to be at a better place, you can call lilongwe and blantyre a city coz of sme strong policy and development that bingu did, college of medicine in lilongwe, must, new kcn, zina ukuzidziwa wekha, malawi became second fastest growing economy in the time of mutharika, malawi even began donating food to other countries , your hate to the dead man is your curse, if we had him by today, malawi couldnt have been hopeless, and nw u expect peter just correct all jbs trash at once? does he have super powers to command all the problems to go away? learn to be cooperative and stop hating, else quit

 37. kaya muzimubakira koma honestly mai u ngwakuba kuposa mapulesident onse akhalapo pampando kumalawi ndi akuziwa chomwe chikumulepheletsa kubwera kumalawi kuno akuziwa kuti anaputa zingwe, koma zotsamuyeratu zoti ndi muntgu wamkazi anta ndi khalidwet lonyasa ngati limenero shame to her and her followers .

 38. This is a song now for evrybody to sing.Why cant the govt stand up n do the right thing to arrest her if she is a suspect of cashgate.We have interpol wat is the use of it?

 39. Apa nde walasa bwanawe kumalawi kwachuluka mavuto,thats why ife amalawi tili anthu ovutika kaamba koti pakamwa too much mmalo moti tidzilimbana ndi ndalama muli buzy kumangitsa anthu zaziii!chabwino munthu waba and inu mwamudziwa ndiye mukuganiza kuti ndalamazo angabweze?money its satan,adalephera malume akawiri aja bwa,pano adapuma nkupita kunja,,,……mbava yaimuna

 40. Kodi ku DPP yapitayo ayamba liti kufufuza poti nawonso anaba ndalama zankhanikhani,afufuzeni kayo alipowo akuwandikiraniwo ndipamene ataziwe kuti simukucheza kupanda apo kaya…..

 41. inu olomutayankhura amalawi palibe angakumvereni takharani chete tinayamba kulira lijasilero zilimbikirani maganyuwo mphoto yanu ilikumwamba uremerero wapaziko lapansi ndiwakanthawi kochepa zanziko nzosara izi tinazipeza tizazisiya izi

 42. AMAI NDI AMISALA BWANJI ANGOZUNGULIRA DZIKO LAPANSI NGATI ALIBE KWAWO.NANGA MUNTHU AMENEYU ANGAKHALE NSOGOLERI?AKUOPA MILANDU NDEKUTI MAIYU NDIMBALADI,BWANJI SAKUIKA MATAKO PANSI

 43. Mmalo momalimbana ndi umphawi ukutikwatilawu mulibe olo ndi manyazi omwe kumatisokosera za cashgate? zinapita zinatha ndiponso sikuti olo mutani ndlamazo zibwezedwa, kodi mmesa ndlamazo anayamba kususa ndi Achimwene ajawa kenakonso ujayi?? Ndiye mmayiyu wangosilizila chabe tiyeni tiyambe kumanga achakulu aja kenakonso uyuyu tikamfukule ku Ndata ko timuzenge mlandu wandlama nkuzamalizira Amayiwa bwaa?

  1. Sizimenezonso koma chilungamo a Malawife sitimachizowa ndlama zinayamba kutafunidwa ulamuliro wa bwana Muluzi, kenako Bingu kumalizila mmayiyu ndiamene wagwidwa, nthawi yomangolozana zala kuti uyu anaba inapita kulibwino tizingoyang’ana za mavuto achakudya tili nawowa, ndlama zinadyedwa anagwidwawo ndiang’onoang’ono akuluakulu sangagwidwe coz ndiye ingakhale chain mwinaso Achikulire athuwa atha kukhuzidwa nawo

  2. Amuna wakuba ndiamene wagwidwa, its true amalawi tkuvutika, so mukufuna ACB isiye ntchto yake ikayambe kusaka mankhwala nzipatala?

  3. Ndiye nanga osangopita konko nkukawamanga bwanji? Ife tizingokhalira kumva za cashgate pomwe chenicheni mpaka lero sichikuziwika moreover kuli INTERPOL bwanji osakamuvumbulusa ngati ampeza olakwa?

 44. Angobwera,ndi tsiku limodzi lokha limene akagone ku maula m’mawa wake adzakhala akucheza ndi adzukulu kunyumba maloya akulimba nazo

 45. Amene amaikira kumbuyo mai uyu ndimunthu omvesa chisoni ndiso opanda nzeru, iyeyu akuzuzinsa anthu ambirimbiri chifukwa cha cashgate,akhale osalakwa akukanika bwanji kubwera azazibakile kuti ndosalakwa.

  1. AWA ALIPOWA NDIYE AKUBA MAPETO KUYAMBI KU AREA MAKOPONI KULIMA MU NSEU AKUCHITA KULEMBA NDI MALEMU OMWE KODI KUBA KUPOSE APA DPP ONSE NDI MBAVA TIONETSANA 2O19

 46. Amalawi anthu akufa ndinjala mzipatala mankhwala mulibe ndemuzi JB kdi ndiyekha wanzeru angayendetse boma,mayesa munavotera ujeni ujeni mumati ndani.We shuld not be cheatd dat Money wz stolen by last regme y y malawi.92 BLN BWANJI wen she coming thngs were worse wth de current regime now wachoka bck in truck Dpp ful of criminals lies

 47. Kwakwakwakwa 😀 😀 😀 Pls Mama don’t come back home, the liars are calling you back say big nooo if they are failing to fulfil what they promised us during campaign tym do you think they can treat you well??? Mhhh no, dont try to take this people us ur doctors no they are butchers they want you in custody. Even there leader uses bible wrongly so if he dont respect God he can respect you hehehe kwakwakwa pls tell dem mwaremba mmadzi kharani ndi dziko mwaloredza umathanyuralo so the one will get angry from Mr ibu to Idi Amini kwakwakwa #Ghettoboyyy

 48. Bwelera kunyumbaaa tizakulandilaa,umphawi siumaphaa,malilo kudula singing Tomas Chibade song.mama just come home but remember when your coming bring kathumba ka ufa njala kuno yafikapo,your succesor don’t know where you used to buy maize.I strongly believe that you’re innocent but he wants to arrest you for political reasons

 49. Ngati mukumfuna pa joni mpafupi pitani mukampeza,munthuyu simugona naye tulo,sangabwere chifukwa choti wina wanena kuti abwere,azabwera 2019 !! matter closed.

 50. Oipa athawa EKHA!!zikanyelekana kumene aliko azatipeza and azIfikira pa unyolo.. Mayi wantundu wanji obela amphawi,?Mpake samagwilizana ndi Malemu Bingu anamuona azithokoza Ma NGO,s anapeza mwai olamura dziko.

Comments are closed.