Joyce Banda responds to Mutharika ‘Do your work’

Advertisement
Joyce Banda

This time around the ex Malawi President Joyce Banda, has only chosen to take President Peter Mutharika to some background work she did in office, even despite Mutharika failing to recognize her at international conferences.

Peter Mutharika
Mutharika: Blames the past.

Mutharika is on record several times as having criticized Banda for among other things selling the country’s presidential jet and ‘spearheading’ the public looting of public resources, a scandal christened Cashgate.

Even in his recent address of the media on his United Nations General Assembly (UNGA) in New York, Mutharika who angrily turned down reports he took along with a whole lot of a village, claimed that he had found the country in a mess and that he is still trying to restore the lost glory he believes the country had before Banda became President.

Mutharika also stepped on Banda’s toes by saying that she had let donors stop assisting the country because of her negligence to stop corruption.

But Joyce Banda in reaction to Mutharika’s remarks that she is the cause of the economic woes that have clumped Malawi now, she has only managed to drill the Malawi leader on some core issues that need to be dealt with and not castigating her all time.

A statement which Banda presented to Council on Foreign Relations, who also hinted that she was not coming back to Malawi anytime soon because of political arrests that await her hinted that it remains paramount for Mutharika to do his job and not talk bad about her.

She maintained that Mutharika’s remarks gave a bad reflection of the work she did when she held the same post.

” President Mutharika failed to acknowledge that I am the first Head of State in Malawi to take bold steps to fight corruption and staunch theft of public resources. I publicly stated that there was a problem of theft and corruption since 2005 when the Integrated Financial Management Information System (IFMIS) was installed and rallied everyone to jump on board to deal with it once and for all. I personally and aggressively led the fight against theft, fraud and corruption.”

“When the European Union (EU) Head of Delegation, Alexander Baum, alerted me about loopholes in the Integrated Financial Management Information System (IFMIS), I announced on September 7, 2013 the introduction of measures to seal all IFMIS loopholes to root out theft, fraud and corruption. My government drew up a comprehensive work plan to deal with corruption and plunder of public resources. The plan was subject to regular review by a Cabinet Committee, which was headed by the Minister of Good Governance, Chris Daza.”

On igniting of audits to the corruption that hit the nation, Banda stated “My government initiated a forensic audit into Cashgate. I shall forever be grateful to the British Government for its provision of resources to enable us to engage an internationally-renowned audit firm, Baker Tilly, to conduct the forensic audit. The Baker Tilly audit report was released on October 30, 2014. It included the names of the people involved in Cashgate. It is a public document .”

As if this was not enough Banda, who lost to Mutharika in a disputed poll last year expressed concern that Mutharika does not show interest to expedite an audit into an alleged 577 billion Kwacha ‘Cashgate’ that occurred between 2009 and 2012 before she came into office.

Joyce Banda
Banda: Worried with Mutharika.

“Just like the British Government provided financial support for a forensic audit during my time, the German Government has committed money to facilitate a forensic audit by Price Waterhouse into this financial scandal. However, President Mutharika’s government has shown no interest to expedite the audit.”

“Recently, robbers broke into a German envoy’s house in (city) where documents containing information about the 577 billion Kwacha forensic audit were stolen. In the midst of the outcries, a senior Anti-Corruption Bureau (ACB) official, Issa Njaunju, was brutally murdered in early July 2015. Since that time, no concrete investigations have been carried out.” adds Banda’s statement.

There has been a verbal attacks on Banda from government to officials.

At some point, ex Minister of Information and Civic Education, Kondwani Nankhumwa publicly claimed that Banda ‘mysterious’ killed late President Bingu wa Mutharika for her to ascend to the post in 2012, two years before she lost the post.

Advertisement

346 Comments

 1. I know peter is losing focus on his work… Ameneyu pamene tafikapa timati walephera… Palibe chimene akuchita DPP ndi chipani chimodzi cimene chinadzaza ndi anthu oba ndalama za boma.. And ayamba kulimbana ndi amai for no reason instead kut adziona kut titani sono mukamalimbana ndi amayi plus family yake ku dziko zipindula chani?? Peter alibe nzelu zosogolela dziko iyeso akuziwa cilungamo cimenechi en iyeyo ndi amai amai ali nazo nzeru kusiyana ndi peter..he is dry as sahala desert sangalamule zikoli lizinka kuonongeka siku ndi siku apa mwasigner kut anyamata azikwatilana okhaokha,, sono iwe Getrude wakoyo utani naye? Ayambe iyeyo kukwatila mwamuna mzake and atiuze ngat amai ake ndi amuna.. Ndi munthu ochititsa manyazi nkudana chikhalidwe. Amai asiyeni koma gwirani ntchito mothandiza dziko

 2. Vuto la ku malawi timavotera ma president ombwambwana. Akalowa pampando zikayamba kuwavuta amayamba kunamizira mtsogoleri opuma. Mwachitsanzo, BAKILI ankati mavuto Ake ankadza chifukwa cha kamuzu, nayenso bingu ankati mavuto Ake ankadza chifukwa cha BAKILI. Nayenso Joyce ankati mavuto Ake ankadza chifukwa cha bingu. Uyunso anthu amati ndi professor odziwa zonseyi akutinamizanso kuti mavuto Ake akudza chifukwa cha Joyce. Hahaha!!! Kagwere Kutali Pitala ukuoneka kuti wangobalalika. Koma chimadabwitsa ndi atsogoleri athuwa nchakuti zabwino zonse zimene amapanga amati ndi mphamvu zawo ndipo zoipa zonse amanamizira otsutsa. Zopusa zenizeni izi ndipo palibe atakumvereni bambo Pitala Mutharika.

 3. Anthuwa ndi amodzi akuziwana ngati saziwana bwanji osawamanga amaiwo may be akuopa nawonso akazaba asazamangidwe that’s a point

 4. We r @ the crossroads. We need God to thunder in our desperate situation. APM shud read 2 chronicles 7 vs 14. Edgar Lungu is leading Zambians in prayer and fasting next month to seek God’s face. Koma ife kukhala ngati APM is an atheist.

 5. Yes that could be true that we are struggling economically bcoz of cashgate but as you mr president on the driving seat try to do something. This blame game wil not take us anywhere

 6. Bola nthawi yanu amayi. Pano amene akutisogolera ali ndi chuma kale ndiye akungotinyoza osaukafe. Akuti ntchito ya m’boma its charity moti ngati ndalama ikutichepela tisiye.

 7. Zoona mai,, apangedi zake Gwaladi ameneyu,, ngati zikumukanika asanamizile wina ai… 2years ya Joyce Banda anayesetsa kukhonza zinthu zimene anaononge mkulu wake Gwaladi ameneyu (Bingu) monga kusowa kwa mafuta, kusowa kwa ndalama zakunja komanso kusowa kwa ndalama mdziko muno….. ndiye nawe Pitala ngati ulidi professor ndipo ukuona kuti Joyce Banda analakwitsa zinthu m’Malawi muno, taonetsano u-professor wakowo pokhonza zinthu zimene ukuti anaonangazo osamangotisokosela ife,, ndalama nthawi ya amai zimaoneka koma nyani iwe wazibisanso, chilungamo chimenecho??!

 8. Kkkkk Tikumbutsane.Kuloza chala JB for this economic mess will lead us nowhere.No president in this country has ever left the palace in good ties with the donors.It has been the responsibility of the incoming president to convince the donors but why is APM failing to convince them?Cashgate dates back from 2005 but why just targeting 2013 suspects?You can foul malawians but you cant foul the donors.Leave JB alone.Malawians need answers from the sitting president not from the former president.

 9. Amaiwa anaba Zambiri kunjaku akukhala kamba ka ndalama sanakhalepo ndikale lose chocho inuyo amalawi ganizani akukha m’mahotel anaba zambiri Mzimai ndi wovuta ngakhalele mupite mubaibulo mupeza kuti miliyamu anaukira mose amene adamutulutsa ku Eygpt nawoso amayi anaukira Malemu bingu amene anatola kukhala runnimate muziona amawi Bwanji Jazbell adali mai woipa choncho akanakhala amaiwo anli pa chilongamo akanabwera ineyo ndikunetsa kuti ngati sabwera azitengela okha wakuba amathayekha amayowo anaba zambiri koma Mulungu a walanga mudzaona, kuonoga koonoga wina Mutukwana a Peter osalakwa tembelero lopanda malire

 10. Since multparty democracy we have never had a President who thought of a poor ordinally Malawian all the four Presidents – its only their family members & relatives who have enjoyed this countries resources; No matter how we critisize or praised these mediocre Leaders nothing will change: kwacha inali bwino nthawi ya Joice Banda koma vuto nzeru alibe- amayenda tsiku lililonse kugawa n’gombe zachiani? Abwere azafotokoze Escom inapsya bwanji? Ndikumudziwa awobera Mphwiyo? Zowona? Azungu anandiwuza kuti ndigulifse ndenge; Zowona? Amai bwinotu bwino, ngombe mumagawa zinja zapindula chiani; Mukabwera muzandipatse imodzi ndizapange kanyenya;

 11. If jb made mistakes just rectify them no need to be talking about jb every moment you encounter problems you are our president jb is out, and only you can be answerable if the situation gets out of hand, do your job sir

 12. zopusa basi” Joyce,Joice juice ndekuti chani???, dziko likupita kumathero ngakhale simungathe kulibweza ndipo silidzabwelelanso mpaka yesu adzabwera mukungolumana chonchi..

 13. Pita ndiokanika,ngati kuona kuti mabvuto acashgate amukulira atule pansi udindo.Mkulu wake Bingu anapeza mabvuto ambiri-mbiri aBakiri koma anatetsa for the first 5yrs sanazungulire mutu.Za mayi aleke kunena koma ayendetse dziko.Bvuto ndife amalawi kusankha mutchona.>Getrude akufuna mwana>Mugabe ndi tonde.

 14. Liv jb alone. Show malawians that u r indeed a prof by providing good leadership qualities nt pointing at jb’s past dids..otherwise malawians are sturving en millions are loosing thier lives bcz of shortages of proper medication in the hospitals en hunger too.dont waste much of ur tym looking at what joyce banda did as it has no any possitive impact to the development of this country juxt do ur work

 15. mnzanu yo ndikazi koma anali ndi nzeru komanso umunthu amatha kuyakha zanzeru osati nyasi zanuzo msiyeni apume ziwani pomwe mkulephera simumati mzakhoza malawi nangano mkuyasamula kukamwa ngati mvuu bwanji ? olo mutatani a DPP simungafikire joyce anali wanzeru ndipo mutathere kachipani ka wanthu ouma mutu

 16. To be fair Madam JB u tried ur best but Malwians could not see your good job..its now they are realising the fact…ndizakusowani mayi Banda coz utsogoleri wanu umamasangalasa

 17. Mama mukabwera azidzati mukumusokoneza ndiinu now mulikukaliyala wakabaza ndipitalayu know mama ndiinu anzeru munaona kuti mkuluyu sangayendetse bwino dzikoli kulichoka mchokhacho mungapange galimoto akakhala oyendetsa mngokaikitsa timaitsika or wen asokose umangodziwa palibe aludziwa big up J b

 18. Malawians only have big mouths of criticising other people when something is going wrong…when it comes to politics dont bring in your personal enermity to blame others as if it had been that its you could have made Malawi a better place for its citizens…….Joyce Banda left Malawi in shambles its true therefore dont blame peter for what he said….I know some likes peter and other Joyce but whos business. ..after all the whole world is deteriorating….Amalawi muzitha kuona zinthu at an angle of creation not destruction……

 19. Plz plz plz mr APM jamani ina,disc mwaikayi ndiyokandika sikutheka olo pang’ono..kod Bingu mesa naye zinamuvuta cz amasunga ma dollars kuchipinda ife mkumati dollar yavuta,kayelekera ma profit amapita ku account yake.so chingamukanike APM kupanga zomwezo ndi chani?remember tym ya Bingu kunasowa 100 chakut billion koma masten anaexexa.nde mkuluyu chikuvuta ndi chani.?kapena2 nanuxo mwayamba kumasunga kuchipinda ndalama za amalawi.GOD SEE EVERYTHIN WE DO,HE IS IN CONTROL OF ANYTHING.

 20. choka hure iwe utibwezere ndalama zathu panyapanko muthu oipa tima ngat iwe sinamuonepo ndakhuluirirat mwambi ot fit yayikazi ndiwolimba tima prease soly 4 dat

 21. Eeeeeee alekeni amayi aupeze komwe aliko vuto ndi Saulosi Chilima kutipweteka potibela mavoti. Udindo ogula ndi ndalama ndimomwe ukakhalila olo mu mpingo eee mwtiomjeza# MADALA mufa osadwala chifukwa cha madandulo athu. a Malawi anzanga maiko olemela president samasankha prophessor , vuto ndilakuti samamva zamunthu

 22. UNGA ndi imene yayambisa zonse. aBamusi mfera za eni pamodzi ndi inu a Viola. Maina a anthu onse taapeza ndipo tiyamba kutchula mmodzi mmodzi.

 23. why malawi why like daughters of lunkokobe who dress in colours to meet the blind suitor now happens to malawi why you give honour to somebody who didnt deserve your honour, waba ndan? take pastor to rule this country with bible more will hate him malawi will never change because of kwaachaaa still in the morning enjoying 2 pm dreams busy follow the leadership instead of going to work ,just look for a root cause and you will bring the solution peter is ok and joyce too its ok but we followers we are not ok and our ideas will bring no solution

 24. Time is the great doctor and failure is the far more great teacher than success. An eye 4 an eye is just going to liv the whole world blind.

 25. Time is the great doctor and failure is the far more great teacher than success. An eye 4 an eye is just going to liv the whole world blind.

 26. Time is the great doctor and failure is the far more great teacher than success. An eye 4 an eye is just going to liv the whole world blind.

 27. Chimene Anathawa Ndichan? Ife Pano Tikuvutika Ndinjala Wasatanic Nzake Uja Waku Nigerian Uja Mesa Anamuuza Kale Kut Yake Ndi 2yrz? Kapena Ali Pans Panyanja Ndamene Akupangitsa Kut Mvula Izitikokolora?

 28. Yes, #Mutharika should do his work and stop the blame game. That’s a sign he has failed so he criticising #JoyceBanda to blackmail Malawian citizens.

 29. Player odziwa kugoletsa zigoli salimbana ndi ma player anzake iye amangochinya nde madalawa asalimbane ndi munthu wina agwile ntchito tione kuti pakati paiwo ndi mai wo dolo ndani .kukhala mwamuna sichoopysezera ife ndamene tizayankhule mosaphysatila pano tikudikila zaka ziwili zithe nde ndizawaika pa skelo

 30. Mama JB You are my Heroe mbali yanu munachita ndipo tinayamika ubwino wanu tinauwona simunanyoze wogwila ntchito m’boma munampatsa kufuna kwake amalawi olimbika ndi omwe anayenda nanu mu ulamuliro wanu lelo takukumbukani pano amoyofe tikusilila omwe anafa..!!

 31. Pitala ndi chitsiru kwambiri, zinthu zikumukanika mapote ake angotchulabe za amayi, JB ndamene naulura za cash zimene zinkabisidwa ndi boma La DPP, ndye mavuto oti anayambitsa okha mu chaka cha 2005 , lero ndikumananmizira munthu amene anangozipeza ndikuzisiya, ndisaname munthu ameneyu munthu ameneyu akuzitosewetsa mtendere ife a malawi,

 32. Eeee mwayamba kuzuzula anthu, si munkavina ku Comesa inu, vinaninso2 lero Mr APM zakuvutani basi mwa inu Mphatso ya upresident mulibe ata and ife sizikutikhuza za mayiwo. Mayi munali bwino kwambiri palibe munthu okuuzani kuti mubwele kuno kumalawi pasakufuna kwanu enjoy wherever you are Mam JB. UYU WANYANAYO(APM)

 33. Inu munthu uyu JB, anasokoneza chimanga over 40 metric tones ,kod Amalawi mwaiwala? Inu a mabungwe omwe si a boma mumati ,tikaone pamene pavundila chimanga anakuonesani? Ndegeija anaigulisa nde amati agula zida za nkhondo nkhondoyake iti? JB amakonzeka kumenyana ndi ndani? Nde kwabwela cashgate, anathawa uyu ,lelo mukuti come back why? Stuput, in 2yrs kuwononga dzikoli nde pano likukonzedwa mukutokota why?

 34. Ngati pogwira pasowa maiko enawa akhoza kungotilandira inu osapeza cholowa. Share our country to others who can manage ..north> Tz&Zim, centra>ZIM & moshiko, south ndiye ndizachidziwikire moshiko

 35. Ena mwa omwe adapanganawo cashgate amatsindika kuti amai JB ndi mboni.Ngati adatchulidwa ndi umboni okwana kuti mayiwa ndi mbava.Oyipa athawa yekha.DDP oyeeee.2019 bomaaaaaaa

 36. He shud do his work indeed. JB inherited a very sory & collpsing state with no fuel, no forex, people quing for sugar, companies closing down, economy on its knees but she managed to turn around the economy to its glory. APM pliz dont tel us JB dis, donors dat, right from yo campaign u were against d idea of depending on donors 50 yrs afta independence. Dont give us lame execuses, jus deliver wat u promised d pipo period!

 37. I Support The Idea That Jb Is The Cause Of Economic Hardships Here In Mw She Is Going In Different Countries Kukakhomelera Kuti Asathandize Malawi.Moti Amene Muli Behind Jb Nonse Ndinu Amfiti.Peter Siwabwino Jb Siwabwino Bakili Sanali Wabwino Kamuzuso Sanalinso Wabwino Bingu Sadali Wabwino Mulungu Yekha Ndiye Angathane Ndi Zonsezi Komabe Kukhomelera Kwa Jb Ndi Ma 100 Inches .Chonde Amai Tikhululukireni Maiko Atithandize

 38. Mudzaziona its only bad carpenters that blame their tools. China chilichonse pano ikutha ndalama ndi civil service. Anzanuwa amalamula bwanji pali civil service. Akuluwa apeze china chokamba cause ku malawi sitidya ma blames kapena kukwiya ngati wagwidwa ufiti. Zilikoliko pa malawi. mutikwiya

 39. Osadanda ndalakhula ndi Zuma ati akhoza kogura dziko la Malawi akalowa parliament mu June muno nkhani yoyambirira ndimeneyo musadandaure ndinu ana Mose mupurumusidwa.

 40. APA vuto ndi cash gate ya madala Bing Peter must blame his brother for looting K577billion of which he is involved how is he going to arrest himself? the answer is no! what to do blame Joyce Banda. no donor Mr President and your govt will suffer until you resign or die like your brother am sorry to say this.

 41. Atabwelera ku malawi mayiyo chilichose chomwe azanene kwa peter mzanena kt ndi nsanje. Kupewa kuposa kuchiza joyce banda anachita bwino musiyen anjoye bas

 42. The only problm wit JB was cashgate!!.Bt with this old man mmmm! no!! its mor than wors!! i think there is a lack of leadershp in this “Anganga”!!Leadershp iz a God-given tarent. U can hv so many mendals in az far az edu is concerned bt if u were born not 2b a leader, u can force urself 2b a leader, bt nothing u can achve!! So, Peter u beter Step Down indeed!!! Ayeseko ena iwe walephera!!!!!!

 43. chisime chikatha madzi ndipamene chimaziwika ntchito zake.I remember this words during peter speach on burial ceremony of his late brother.wat iam trying to say mama jb while she was a leader mumanyoza amalawi but know u gave realised that she was ryt unlike petela

 44. eya akuyenela kumuzula #jb coz vuto anapeza zitavuta kale, nkhan ndi cshgate akanakhala kut ma mirion aja sanabedwe a pter akanakhala abwino koma #mbava zomwe zimangoseweletsa ndalama zija nde eee akutizuza ife osauka

  1. Ndale zopanda pake it’s nonsense , pangani zoti zikuthandizeni pa moyo wanu. Dziko la malawi ndilosaukabe pakana kale kale. Palibe munthu osalungama pa dziko mot resident aliyese amaba ndithu akut kudyelera udindo. Mukuchedwa malawi ndi ndale. Ndarama zomwe amatidula musonkho kwa ine phindu lake sindikuliona. Nthawi yoti tizipanga zatha kuti titukire moyo wathu bas. Poor government of malawi. God bless malawians with good rainfall.

 45. bwampini chikutumbwe uyu amayesa ngati kuyendetsa dziko mkuphunzitsa mkalasi

 46. amai zikhalani komweko ine ndikuona kuti simunakhalitse kunjako chifukwa pali anthu ena amakhala kumaiko aeni zaka zoposera 10 pamene inu ndichaka chimodzi. kapena munthu akakhalapo paupresdent ndikuchoka samaenera kuenda kapena kukakhala komwe akufuna? chitani manyazi

 47. chikundisekesa nchoti amayi omwewa ali president akachitisa msokhano samalephelapo kubramer the previous government kuti inasokoneza zinthu……apa nde zikumuwawa. Anyway blame game wont tek us anywhere, face the problem n deal with it if u got the guts!

 48. the tym sh got on powr zinthu sizimayenda bt she managed 2 contrl thnx bac 2 norml thou she made sme blandrs bt sh tryd anyway!and durin compain peter wz alwyz sayn akazawina azalongosola zinthu coz he knws tht joyc hv mesd up th economy! bt now instd of kukonza hs stl blamn aftr all hs mesn2!so funy!i thnk hs runn out of mind!ngati ali dolo osangolongosola zinthu bwanji!kkk mumalitenga lophweka muli patali kkkk remembr nt evrone can b a ledr kk

 49. Hey asanalowemo jb zinthu zinaipa koopsa moti timaona ngati tonse tifa kuzalowa jb after enaaja ataazimangirira zinthu zinayamba kuyenda kwabasi, ntthawi ya jb yes kunali cashgate kooma amavutika ndi ndani? Kwa enaaja kunalibe cashgate timavutika bwa? Awanso alowapo kulibe cashgate tikuvutika bwa? Alomwe opanda nzeru inu,, stupit zanu.. Bububu wanuyyu mchiphwisi chotheratu,, anthu akuvutika instead of solving the problem akungoimba nyimbo jb jb jb jb jb,, osangosova zintthu bwanji? Munkalowa mboma zinthu zikuyenda despite cashgate inu nde mwangolephereratu

 50. Peturo bwampini nduna zake bakili muluzi nonse a satanic stupid mbulitesi mbatata agonondo athembwerembwe agurukunyinda

 51. Mumaona ngat dziko ndlophweka kuliyendexa kkkk uxovenge…panga zadziko oxat zamun2

 52. Apulezidenti mukanakhala amnzeru mukanalimbana ndi dziko kuti lipite patsogolo kusiyana ndi kulimbana ndi JB koma popanda chothandiza dziko..si nthawi ya kampeni ino koma kukwanilitsa lonjezo komanso sindikutanthaudza kuti za cashgate zithele mmalele koma tiwone kaye komwe dziko lathu likupita chifukwa ndizomvetsa chisoni kulimbana kwanu tizivutika ndife okuvotelani..show us the future of our nation not just fighting this shows that u r a ruler and not a leader.

 53. Sinu nomwe mumankhweza changa wachabechabeyu,amayi anayesetsa ngakhale zithu anazipeza zili zovuta ngati ndimamuna awonekera pamenepa chimaphweka chili kwa nzako wava Pitala.

 54. But im suprised dziko likupita kuti abale??????? Lets not point our fingers to each other coz dziko lose lapasi things are not OK , its not Malawi only , maiko ambili ali ndingondo yosata ena akugwilisa ndalama yoti siyawo. We are the ones tinavhotela Peter now ndife tomwe tikuti siwabwino bola Mai Banda komaso amene muli patsogolo kutukwana Peter u are the ones mumatukwanaso Mai Banda. Aliyese heshe’s a problem wabwino muzamutenga kuti?????? You have to know this dziko lapasi things are not OK.

 55. amalawi ndinu anthu ovuta kuti zichitike chonchi ndichifukwa chanda sichi mmayu chanucho akanakha kut sanabe sizikana fika apa musa blemy muthalika pangan jb

 56. Palibenso yemwe azabwele nkuzasintha zinthu… ngati mumawelenga Buku Lopatulika linanena kale za nthawi yomwe tili until mwana wa Mulungu kubwela… Owelengawe khala!!!maso!

 57. LEADERS THINK AND TALK ABOUT THE SOLUTION FOLLOWERS THINK AND TALK ABOUT THE PROBLEMS….. WE CAN NOT CONSTRUCT A NEW MALAWI WTH PAST. SO THINK ABOUT SOLUTION TO OUR CHALLENGES NOT TALK ABOUT PROBLEMS.

 58. Mmmh, paja ng’ombe ya mkaka kuchta makani. Ask you why she escaped on her own land?? Oyipa athawa yekha, Abweretu nanga azimuyankha pitalayo pafupi, akutumbwira ku mayiko kwa eni! chikhale chan chimenecho ali ndi kwao abwere. Ndinthaw ya APM iyi. You r fond of reaptng that JB should cum & take over the leadership, mmmmh Ndan adamuvotera nkuwna?? Even the tym when she took the gvnment nobody cast a vote for her. Mind you!!”

 59. You must check Cashgate records from 2009 up to now everybody who is involve you must Confiscate his or her Property and sell them and put money in Government to start working we are tired with making noise you must take action now otherwise no more Aid in Malawi

  1. Apaseni ulemu masten pliz stop using tht word yoti hule on ha.and dnt 4get yesterday it was mothers day.ngati zakubowani nalembazo mungo dusapo osakomenta.Plz be civilized.

  2. Ulemu amapatsa mbava mupatseni ndinu Ulemu amene munkadya naye ndiganiza muli ndi makola ang’ombe iwe Pheshaj Msukwa ukulephera kupatsa Ulemu amako ukalilile wina kupatsa Ulemu mfiti kkkkk Lestimo Nyirenda wakuba salandila Ulemu ngati mukufuna kazigwadilani mbava yanuyo anthu omwe abale awo awona mavuto ndi gwape ameneyu samuonera kukondwa namaloko Ana aweni akuvutikira ma 10 % zonse ataika mnthumba galu wanu mukuti amaiyo

  3. Ulemu tikunena ndioti musamagwilise mau ngat hule kwa munthu wamayi.za cows mwanenazo man hmmm,am nt part of any chipani bt those were jst my views.stop taking it personal jst komenti with sober minds.

  4. Kod abwampini enanu mukuti chan…kod bingu sanabe 577billion koma kubwera Amai zinthu sizinasinthe panthawi yochepa…? Tinkavutika sugar, fuel etc all these zinakhazikika in 2 yrs, kodi ndalama zingati zasowa pa jb….kumazisata momwe ndale zikuyendera osat mwamva winawake wanena ndalama zabedwa basi mitu m’mwamba ngat khwangwala…au happy wth ths guy called pitala…? Amalawi open yo eyes

  5. Kod abwampini enanu mukuti chan…kod bingu sanabe 577billion koma kubwera Amai zinthu sizinasinthe panthawi yochepa…? Tinkavutika sugar, fuel etc all these zinakhazikika in 2 yrs, kodi ndalama zingati zasowa pa jb….kumazisata momwe ndale zikuyendera osat mwamva winawake wanena ndalama zabedwa basi mitu m’mwamba ngat khwangwala…au happy wth ths guy called pitala…? Amalawi open yo eyes

 60. Ndiye kuti inu mwalephera kulamulira? Why calling her to come back home? When did you notice cashgate? Before or after taking power? Remember you were using de same word ‘cashgate’ when campaigning.

 61. My dear Malawians refresh ur memory to the time JB started as president count the problems Malawi were in She managed to overcome them But what is the problem with APM .just involve God as Zambia otherwise we will see u more w……God Bless Malawi

 62. the devil is attacking us becoz amalawi timakanika kugwiriza ndi kupanga chinthu chimozi chooneka,koma aliyese akufuna akhale woposanzake pazochika as a result we can’t build abetter malawi.

 63. kodi joyce yo anatenga makey a ku state house?Msiyeni munthu apumule inu zilamulirani modekha.Vuto lolowa m’boma ndi mangawa ndi limeneli,kalikonse kangakuvute umayang’ana amene analipo.Amangwetu mwatani?

 64. Blaming blaming your kid for spilling the milk is stressing, find means to bring another packet on the table

 65. A good leader does not complain or play a blame game but to find solution. That’s a sign of weakness. Leave the woman alone and do your part. We think it is easy when it is someone else doing it and condemn more. It is your time Mr president.

 66. nkhan si ya cashgate, komano chifukwa chokula mtima #pitalayu mabungwe ndi maiko othandza asiya, lets talk of #NAC, zoona ndalama za zothandiza dzko akapangre #mulakho!! dats very unfair,,,

 67. jb never cried for spilt milk bt went straight in office and tackled de most critical issues affecting de ordinary malawians,its a gibberish&myopic thinking to say de current situation is based on what happened 2yrs back,,aaahhh,if she messed up,why cannt Apm&team claear de mess?clueless leadership,aaasaaaaa,busy boosting akuti ndi millionaire!!

 68. Long live Mutharika. why Joyce Banda left the country soon after loosing the presidential race? bwanji osabwera nkuzazilongosora yekha kut she had nothing to do with cashgate issue.

  1. Nanu a Felix tamayankhulani ngati mamuna, pena kumakhalako chete ngati mulibe chokamba. Joyce Banda abwere azadzilongosole yekha kwandani? Adzalongosole kt chani? Ndani yemwe wamufunsa kt alongosole ? Mutharika mmene ankatenga dziko anadziwa kale kt zinthu siziri bwino mmalawi & analonjeza kusintha zinthu that’s y anthu anamuvotera bcz anthu ankafuna change. Now it is the right tym 4 him to do his job as he promised. Zomangoblema previous government zi sizingatithandize

  2. Olakwa amathawa yekha hule amene uja ndi mbava koma chifukwa choti anyasa tulo too much nchifukwa chake mpaka lero sitimazindikira chilichonse. Ngati siwolakwa chimene akukanikira kubwelera kuno nchiyani? Wake up guys tamazimvetsetsani zinthuzi, that bitch is a devil a thief she must go to hell and ine pa 2yrs wayendetsa dzikoli phindu lake siniliwone. #teamdpp4ever#

  3. Kulibwino ndikhale mbuzi pachoonadi bt i cn nt praise a thief a big one. Dzikoli lili pamavuto azachuma chifukwa chadyera lamunthu mmodzi. Kusazindikira kwanu nkumene kukupangisani kut musazindikire kut munaberedwa wake up mweee! Musiyeni Peter alamulire kwama term ake awiri then muzizanena kut walephera. Amene akuwona kut Peter sakulamulira bho atuluke akakhale komwe kuli amayi ake okubawo kkkkk DPP WOYEEEEEE and sindikuwonapo chipani chozachotsa DPP m’boma mark my words

  4. hahaha u fools jst stay out of wat u dnt even hav a piece of mynd on smeting peter doesnt knw tha ghetto life thats he z doing a ting lyk everybody in malawi is a general manager of a certain organizations pitala yo sangokweza zinthu mwaukape chonch

  5. Palibe mtsogoleri wadziko angamasangalare mitengo yazinthu izingokwera mwadala dala ndibwino kumazimvetsetsa mmene zimayendera zinthuzi more si Peter yemwe amakweza mitengo yazinthu ndiinu nomwe amalonda. Pali tsiku lomwe president adalenvezapo kut kwezani mitengo yazinthu mmashop mwanumo? why we blame the president all the tym? Kuti tiwonetsetsenso ambiri akunyoza current government pano ndiwomwewo ankanyozanso nthawi ya PP vuto ndiloti sitidziwa chomwe tikufuna or italowa MCP m’boma muzizati bola DPP yomwe ija kkkkkkkk plastic minds

  6. Dpp inaba 577billion why only JB? Anthu opusa inu leave aside yo political parties and look at facts. Zokuba zawozo amadya okha inu busy kukangana

  7. Felix Mike Nkhoma ukukamba zoona a Malawi tili ndi vuto busy kumunena president inu mungakwanise kuyendetsa dziko pangani zinthu zothandiza dziko lanu.mukamachedwa ndikuyankhula zinthu kumangoonongeka DZUKA MALAWI DZUKA NDIKALE UNAYAMBA KUGONA nyc song

  8. Nanga 92bn cashgate ya DPP ndi Bingu,simukuichula bwanji,Nanga za 577bn,kuchokera 2009 mpaka 2013 nthawi ya mbava Bingu ndi zimene zapangisa a malawi kusaukisisa.Musabisale kwa JB.

  9. Nonse Mbuzi Zokhazokha Mukangana Chani Mulibe Ni Nsabwe Yomwe Nkumakangana Kamba Ka Chuma Cha Eni,zopusa Basi Muthalika,joyce Banda Onse Zitsilu Muwauze Onse Analephela Kmanso Akulephela Kuthandza A Malawi

  10. Ndani angasinthe zinthu mdziko pachaka chimodzi? Give the president more tym ikatha term yake ndie muzizanena kut walephera osati 2yrs yomwe siinathe mwayambapo kutokota zaziii. Ngakhale Ntawali akupempha more yrs to build a strong national team what more mtsogoleri wadziko? You think chaka chimodzi zinthu zingatheke? Mukamufunse munthu odwala malungo akamwa mankhwala a malungo matenda amawonjezekeleka mapeto ake amakhala bho kkkkkk topic yokoma iyi mweee hahaha I wish mtundu wanga tinakasukusura nkuchotsa maganizo ofoyira timakhala nawowa mitu imeneyo ikufuni formating kkkkkk

 69. JB restored things in a few months my Guy so why is it so hard for yo u to do what a woman did!! Pano all you know is JB this JB that.. shame on peter your such a useless president… JB ndi deal ase..God helps those who help themselves so as Malawi we say enough is enough achoke basi its the people’s will.

 70. Remember the moment JB was taking over the Gvnt a number of basic & other items were in scaress just because of uneligibility of APM’s late brother ‘s leadership,but within 3 months we had everything in place(sugar,fuel,foreign currency,medical drugs etc) but its now close to 2 yrs APM is failing to control the Govt & things are now worsening so why blaming the innocent blessed natural leader JB now ? Kkkkkkkklk lakukanika ambwana leadership sikuphunzila kokhai koma umunthu ndi mzeru zachibadwidwe zamkalasi its just a suppliment ,to my assessment since kamuzu Muluzi is the president malawi will ever had in a million of yrs seconded by JB at the moment enanu thats why achilimawo anakuthandizani ndi technokogy yawoyo akulu anu aja ndiye anachita kuikidwapo tonse tiku

 71. That’s the point mom J B he was luking to be a leader nw he hve to …….mommy said that ……DO YOUR WORK BOY

 72. mukuti better cashgate kodi mesa zonsezi zikuchitika cauze of cashgate yo aaaa i dont brame apm but joyce banda oky wat if joyce banda still apresident of malawi i mean nw kunakakhala bwanji kumalawi kuno? think before talking

  1. Ngat cashgateyo idaliko kalero i dont no wat i know is boma la JB lidagwidwa likuba ndalama & onse amene akuzengedwa mlandu pankhani yi amutchula JB kut she is involved! why not mention Kamuzu, Bakili, Bingu popeza nawonso adakhalira mpando womwewo. Wakuba ndiyemwe wapezeka ndikatunduyo. Jb munthu wakuBa.

  2. Ome, what a wasted sperm. Think before you speAK man, your talking nosense here .. Muwauze president anuwo kuti m’malo momangolira lira ngati mwana AKONZE zinthu. Mesa ankati azasintha zinthu. Ankatathauza kumamubwebweta JB ?

  3. guyz apm sakulakwisa kathu tangowonani zomwe wakumana nazo atango lowa boma kusefukila kwamaz ,cashgate,zenofobiya, njala ndemukuganiza kuti mungaziwe bwanji kuti muthu akutha kulamulira kapena ayi osama ngoyakhula zopanda madz kumaganiza kaye madolo

 73. Remember the moment JB was taking over the Gvnt a number of basic & other items were in scaress just because of uneligibility of APM’s late brother ‘s leadership,but within 3 months we had everything in place(sugar,fuel,foreign currency,medical drugs etc) but its now close to 2 yrs APM is failing to control the Govt & things are now worsening so why blaming the innocent blessed natural leader JB now ? Kkkkkkkklk lakukanika ambwana leadership sikuphunzila kokhai koma umunthu ndi mzeru zachibadwidwe zamkalasi its just a suppliment ,to my assessment since kamuzu Muluzi is the president malawi will ever had in a million of yrs seconded by JB at the moment enanu thats why achilimawo anakuthandizani ndi technokogy yawoyo akulu anu aja ndiye anachita kuikidwapo tonse tikudziwa.kkkkkkkkkkk usova siunati kwatsalatu 3 yrs.

  1. Paja anakutumiza kunja komwe uliko ndi Joyce Banda eti? Bootlicker …….Anakumanfa chidukwa choupitsiea mtown ya eni ake

 74. joyce banda is having a piece of mind abroad, atabwera kumalawi ndinu amene muzizati amusiye peter ndi nthawi yake…!! Keep on enjoying your peace powerful jb…!! God bless you

  1. Surely! jb has paved way for this moya to do business just as she is doing hers too.You know the saying that goes”a bad carpenter will always blame a tool for the job wrongly done”Ndi za amuna izi osati azibambo.Amangwetu mwachita bwanji? Jb is representing us well out there.

  2. Uncle kunena kuti business yanga yagwa chifukwa akuba anandibera sikulalwa.Ngati boma lamutalika likuti ife boma lathu lavutika chifukwa boma la Jb linaba ndalama sikulakwa.Ngati RSA akudalira donation ndiye Malawi angatani? kudandawula basi.

  3. Moyayu zamukanika asalimbane ndi amayi amene mpaka pano amalawi onse amulilabe mpaka pano. Mavoti mudaba aja ntchito yake mkukonza zinthu kuti amalawi akhale mumtendere. Tiye nazo ukweza manja wekha.

 75. This is sad continuing dwelling on the past is of no interest to Malawians neither is helpful to help the difficult life Malawians are currently facing. The problem is that we appear not to be learning from the past. Banda Hastings had good things and bad things, Muluzi had bad things and good things, mutharika senior had bad things and good things, Banda Joyce had bad things and good things: Therefore it appears every new leader who comes into power concentrates on bad things of the previous president. As a result Malawians are quickly blinded and loose the good things that the previous presidents have done. In this process we are loosing excellent resources in terms of knowledge skills and competence that Malawi needs to build on and improve the lives of ordinary people in Malawi and social economic development of the country. Though this is a deliberate strategy for each subsequent president to make them look good to the people by making them forget the good things the previous president did, is not helping malawi. My appeal to the current president of Malawi is concentrate and build on good things that Joyce did and improve on things that she was not doing well for the benefit of the country. You have had enough time to have good analysis. You need to start showing improvement on how you want to improve the country for the benefit of ordinary Malawians. Stop accusing others people will not be helped by such accusations. Spend your precious time on how to improve Malawi . Malawians are not stupid they will soon start comparing your activities as worse than those of your predecessor. Get on with your work. Thank you

 76. Mdala uyu wawonongeratu mayi muwuzeni zoona ameneyu asakunamizirireni anayamba ndi mkulu wake wopanda manoyu angomalizitsa zamukanika we need fresh blood a lesson to all of us youth

 77. foolish peter mthalika u have to step down..amai ruled for two years anthu tinati aononga koma bambowa mmnmmm zanyanya

 78. Iwould love if jb contest in 2019, iam one of her vote ndukuliran mayi ise am’boma tikadanda malipilo eeee mmava osati zinazi pls mama come back

  1. He is trash not president…. Hiring a plane nkutenga ma supporter 100 achipani chake kupita ku America kumudzudzula nkumadzichemelera za chuma ali nacho….. Eeeeish…. Malawi is indeed on fire…..

 79. Mayi banda if u know that u are innocent why can’t you come back home?you are the best thief in the world and a disgrace woman in malawi

  1. get yo dirty mutilated pussy out bitch….what is yo bizness if she comes or not…? Will she rule malawi if she comes…? Let mamma alone, she is have a peace of mind

  2. i think ur presdnt hs proven tht he is th best theif than mai banda only 4 one year waonesa kale nde kuthele zaka five bwa?boma ilo kkk

  3. APM anagula nyumba ku area 10 at 3 million so who is a big thief here, pano akutinamiza kuti mmene amabwera kudzalowa mboma ali wolemera kale then akufuna chani pa upulezidentipo zowonekera2 afuna azitibera bwanji osapita kukhakhala kundata kwa brother wake ndikumakadya ma million akunenawo kusakwanilitsidwa ndi dyela lomwe

 80. How is he going to do his job after u mess up everything u heartless woman? Now that u r enjoying poor malawians money u have gut to tell the prsdent wat to do. God ll punish u wherever u r,

 81. AMAYINSOTU POLOWA BOMALI ADAPEZA LITAVUNDA NDI ULAMULIRO WA BUNGU MALAWIANS JUST CANT STOP POINTING FINGERS AT EACH OTHER.

 82. u say joyce has made it worse in two yrs …i would say better….coz muthalika waonongelatu dziko

  1. Malawi anavunda nthawi ya bingu ija amagona kuma filling station it stabilised a bit nthawi ya joyce banda ya peter nde mbola

  2. open your eyes Misheck and leave the politics aside as you and me are not politicians and we benefit nothing from them..you will see the truth bro..

  3. #jona ur the 1 who shud open ur eyes, cant you see kut ma donors anachoka tym ya amai.if realy u say ur seeing then you must be dreaming.

 83. kunena zoona,kulephera kwa boma la this old man kufufuza za 577billion kukuwonetseratu kuti ndiwakuba koopsa. Bwanji osabweza 577billion kusiyana nkukweza fees m’ma university? bwanji mukulorera kuti anthu azimwalira chosecho mukusungira 577billion yamisokho? Ma donors sakufuna kubwerera osati chifukwa cha JB ayi koma coz of 577billion. Do ypu think donors are stupid enough kupereka ndalama yofufuzila 577billion inu nkungoyiponya uko nkumati akusekererani?

Comments are closed.