Two gays arrested while having sex in Malawi

Advertisement
Mchinji

Police in Malawi’s capital Lilongwe have arrested two men for allegedly having sexual intercourse, Malawi24 can report.

The two, Cuthbert Kulemela, 19, and Kelvin Gonani, 39, were reportedly netted when they were romping each other  at area 25 in the city.

crime (2)Speaking to local press, Kanengo Police spokesperson Ester Nkwanda said the incident happened on Monday after the two had been at a drinking joint.

“After the boozed, they agreed to go to the house of Gonani where they had sex, when Kulemela was leaving the house he met community policing members who asked him several questions on what had been transpiring inside the house,” said Nkwanda.

He then admitted to have been making love with his fellow man as the law enforcers still puzzled him on the matter.

Nkwanda further said in condemning the act, residents invaded Gonani’s house.

The two suspects are yet to appear in court to answer charges of sodomy.

Advertisement

308 Comments

 1. U can talk, express ur views or watever. . bt it wont work, even though these guys have been arrested, or even akanawapha as others are puting it, but this act will still remain because the word of God will nt b there in vain, The end of time is near.

 2. amalawi ndife opusa, tikulimbana ndikuti awamange anthu awiri amene anagwirizana kugonana kwa okha ndipo pa zomwe amapangazo palibe amene amulakwila,anthu ambiri akumalakwa,pali za cashgate,anthu ogwililira,okuba,kupha kumene ,oti akuonenga maufulu a anthu ena,boma bwanji lilimbane ndi zimenezi kusiyana ndi kulimbana ndi anthu awiri amene amagonana atagwirizana ndipo palibe amene zamukhudza? Nonsenu mukuti awamangenu ganizani mofatsa,ngati chili chilango akaonongeka okha,tiyeni amalawi tizitaya nthawi pa zinthu zoyenela zoti we are affected rather than on this useless issue of which none of us has been affected,o poor malawians thats why our country is still poor,we waste our time on useless things

 3. U Even Call It ‘Sex’ Kkkkk This Wedsite Has educated Savages. U Reporters Who Told U That Is Sex? Give Me The Source Of Ur Education.

  1. Because it’s usually men who are outspoken bigots and homophobes.

 4. uuuuuuuuuuuuuuuu shame!!…shame!! shame!!……GOD did not create ADAM & STEVE PEOPLE……and he wasn’t a fool to create ADAM & EVE.

 5. Gay Siumunthu Koma Chowamangila Ndichiysni Poti Apresident Anavomeleza Kuti Anthu Amasuke.Zauchitsilu Kwambili

 6. Just CONGRATULATIONS for being called to court to write your entraces olowela ku Maula Prison eeee mwasogolatu anzathu ku Lilongwe chitukuko chimenecho??? Koma akawamanga ali oyembekezela choncho chifukwa ayenelatu kuti apasana mimba a Nyapapi amenewo kkkkkkkk My Malawi

  1. True. It honestly doesn’t affect anyone and what a person chooses to do in there life as long as it doesn’t affect anyone else is none of our business. More people should realize this

 7. If both sides agreed to do so then there is no need to arrest them. When it comes to love, Humans are autonomous they should have a right to choose whom they love without forcing them to go for opposite sex, religion, race, tribe and etc …..

 8. Mulungu sanachepe nzeru polenga anthu awiri osiyana ndie inu nzeru zanu zachuluka kuposa achikulire’Mulungu’???? Umve pamaso pa mpulutsi wanu

 9. If this act is against our law both of them they have to face the reality…..& everyone knows that judgement is the hands of God & even in the Bible we have Ten comments which is law……& the law is there to protect from evildoers…..why don’t u ask yourself the simple question lyk why do we have institution lyk judicially? ……in addition to that why do we have Police ?

 10. anasiyanisa nyama ndi munthu kuti munthu akathe kumulemekeza ayehova koma pano munthu zimene apanga ai ndithu nyama zikumpana koma ayehova angoyang’ana ndipo chilango chili mkuza.

 11. Kodi mukamati atumidwa ndi azungu nde kuti chani?? Kumeneko kunali mzungu? Baibulo lomwe mukunyadira leroli anabweretsa ndani? Paja amalawi mumachangamuka mopusa zoti mmalawi kuno ma gays anali, aliko ndipo adzakhalako simukudziwa? Winawu ndi umbuli basi, kuno ku malawi mtundu wina uliwonse ma gay alipo even every family. Iam a gay and am proud of it with no regrets, osatinso zoti mzungu wandituma no bt ma feelings

 12. Bad reputation, wicked behaviour, the devil in action, let Jah alone fi take control ova dis madness.. If you kno’ de best forget de rest… Jah protec’ Malawi,,, Jah bless Malawi..

 13. Asiyeni ayamba kuvala mapamper pompano pompano kutatamuka kobibira.Kungotsokomola bibi kutulukiratu nthawi yomweyo.These swines!!??

 14. MULONGOSOLE BWNO CHMENE CHACHTIKA KUT MUZIWAKAIKA KUT KUMENE AKUCHOKAKO AMAKATAN.KOD MUMAMUFUNSA ALIYENSE PAMENE AKUCHOKA KWA NZAKE KUT AMAKATAN?MUSAMAFALITSE MBRI YAUSATANA NGAT IMENEYI CHONSECO NDZOPANGANA

 15. Malawi is a country that is built on principles of morality and the act of gay is an immoral of which we as malawians strongly oppose and our constitution clearly stipulates the penalties of sodomy. therefore, using human rights as a way of defending this two (gays) nuisance is unacceptable as our constitution and our society’s values view this as not a right but a bad behaviour that has to be eliminated at all cost.

 16. Don’t be stupid Malawians, don’t provoke Jehovah to anger; remember Sodom & Gomorrah. Why can’t we admire Mugabe? if anyone happen to listen to the stupidity of whites he is also more stupid.

 17. Mathanyula ?sichikuzola manyi chimbolocho? Imfe tikuwufila ndi masula pa Durban.sorry my fellow malawias let you change about what you ar doing

 18. Koma mmene amakomera munthu wankaz,zoona ungamalimbaneso ndi mwamuna nzako shame on dem,khaya kwa amene akufilayo koma ine i wil deal with critoris for ever.

 19. Watheba, tangowona makomenti onse uwone ngati wina alipo akusekerera zopusa ngati izi. Bwanji kodi amalawi. Ufulu? Ufulu wake uti? kkkkkk. Akaweluza ndi mulungu koma ndiudindo wathu kutsusa pomwe pakulakwika. Mulungu analanga sodom ndi gomorah kamba kanchitidwe ngati uwu.

 20. Whether we like it o nt za ma gay sizitha coz dats how the earth woz made, we jus have to play not to be 1 Of thoz foolishest pipo… Sory for the english

 21. After reading the link, I got alot of questions to ask and the story lack credibility! how can you word from a drunk person? What if they admitted it out of sheer arrogance to irritate the people who were nosing in their business? You mean two friendly male can’t go into a house together unless its intimate? I think the story has been cooked up to create a debate around the homosexual behaviour. I am totally against homosexuality but taking word from a person after a booze is unheard of.

  1. Kuledzera Si Defence Malingana Ndi Malamulo A Pa Malawi Pano.Ukanakhala Kuti Ndi Mlandu Oti Munthu Wapha Mzake Atalezera Sakanamangidw Kamba Koti Mlanduwo Waupalamula Ndi Kuuvomera Ataledzera??Pali Milandu Ina Anthu Amayamba Kuiganizira Kuti Aipange Asanaledzere Chifukwa Choti Ali Sobber Amakhala Ndi Manyazi Amakamwa Mowa Kuti Achotse Manyazi Aone Poyambira Izi Zimadziwika Bwino Potengera Zomwe Eni Opalamula Akuyankhula.Komanso Sindikukhulupilira Kuti Olo Munthu Atati Waledzera Mwamtundu Wanji Zingamubweletsere Chilakolako Chogona Ndi Mamuna Mzake All Over Sudden.Olo Woti Wasuta Chamba Akamati Wagwililira Amagwilira Mkazi Not Mamuna.Izi Zikusonyeza Kuti Chilakolako Chomwe Anali Nacho Anthu Awa Kwa Wina Ndi Mzake Ndichomwe Chimawafika Akakhala Sober.

  2. the goodness is that even if the have realy done it no one outsider has been affected,ngati apolice wo amamufunsitsa munthuyo kuti amatani nyumbamo amuna awiriwiri ndekuti apolice wo anali ndi nkhani kale komanxo apolice ntchito yawo ndikuteteza anthu osati kuziwa private life ya anthu coz watever was happening in the house between the two was part of ther privacy of which no one is suppose to know unless if the two wish to tell people,malawi has important issues to deal with rather about two males who people just think they were having sex coz the y havent affected anyone,lets deal with issues affecting the nation as a whole

  3. Prisca Chisomo Malombe if you read the link, you would understand why I got alot of questions to ask! the link says, and I quote: ‘they were netted while romping’ meaning they were caught while doing it, later in the story it says when one of the them came, he was asked what was he doing inside the house. Does this make sense to you? How can you ask someone of the crime you just witnessed? Being drunk is not a defence, yes! but can you bring a drunk person to testify in a court of law? If yes, in what ways, if no, why not?

 22. ine sindikuona vuto, anthu amenewa siza chirendo chifukwa dziko likusintha zoti amalawi adzavara ma legez ndikuvara kwa chilendo pano zinakhazi kika ngati chikharidwe chathu zomwe Mulungu akuletsa ndipo dzikori likutha sizitheka zimenezi zibwera ndithu zikhazikikanso ngati chikharidwe nw ma gay abwera ndi zinaso zoti zikhara mmaiko onse ndipo malawi alandiranso zimenezi ndiye kuwa siya vuto paribe chifukwa zibwerabe ndipo zikuchitika ambiri akupanga izi

 23. Kodi guys what’s wrong to say they have admitted,to be having sex mwina understanding yanga ndikuona ngati d grammar is correct.

  1. Pa Chizungu Cha Court Palibe Cholakwika Apa.Fans Ingokakamula.Ukapita Ku Chipatala Admitted Is Another Issue Different From That Of The Court.Zimangofunika Kuti Nthawi Zina Tikakhala Ndi Mpata Kumakamvera Nao Milandu Mmene Imakhalira Mma Court Mu.We Will Be Serprised One Day Poti Kuchimwa Kulibe Mwini.

 24. Englsh error-BURNT NT BURNED Ofcoz its Gadaga English.

 25. Kkkk u i was kind of confused ‘while having’ then ‘when kule was leaving the house.’ Anyway mayb english has burned me.

 26. Kodi ngati mukuti ndiufulu wao mkayesa Baibulo linatiuza kale za sodom ndi gomola nde ufulu umenewu ukuchokera kuti, komatu akuona zanse zimene tikuchitazi ndithu ndikunena Namalenga (Mulungu)

 27. Sad thing is that palibe dziko lomwe linamenyapo nkhondo yothetsa vuto la ma gay. This is a world issue not Malawian. There’s gays everywhere including in Muslim nations where they practice sharia law. It’s been there and it will always be there. Moral issues can be really hard to deal with and so may be Co- existence is the only best way otherwise it’s a battle that can never be won. Komanso ndife a khristu so why should we judge when we know the Bible teaches us about the coming of Jesus to judge us at the end of the day? Unless we don’t believe the Bible then we can take it in our own hands but the holy book doesn’t give us that authority either. Tiyeni tidzingolimbana ndi Mavuto athu a tsiku ndi tsiku tisataye nthawi ntchitoyi ndiyamwini wake mulengi. Tisayiwale tonse ndife ochimwa oyenela kuweluzidwanso

  1. Tantchula dziko la chisilam limodzi lonkha lomwe kuli Shallia law koma kulu zau satanic zanuzo? Eeeh sangayesele kupanga zimenezo kungoapeza akhoza kusinga pomwepo

  2. Tantchula dziko la chisilam limodzi lonkha lomwe kuli Shallia law koma kulu zau satanic zanuzo? Eeeh sangayesele kupanga zimenezo kungoapeza akhoza kusinga pomwepo

  3. True. Point yomwe ndikuthandauza apa ndiyakuti it’s a worst of time judging these guys cause as Christians we believe that we’ll all be judged some day so we don’t necessarily need to worry about a certain fella being gay. Nothing has stopped people from being gay, even sharia law hasn’t. Don’t forget there were already gays in Malawi even before aunt Tiwo emerged, an estimate of 10,000 isn’t a joke. There’s no shariah law in Uganda and Jamaica but people get killed for being gay there and believe me there might even be huge population of gay people in those countries than here in Malawi.

  4. but ithnk dis sin of gaysim anoyes God,,remember wat de bible z teling us abt sodom and gomora,,,dis indicates dat guyism z de worst of de worst sin in de world.

  5. anthu limbanani ndi umbava,umbanda,njala,umphawi osati anthu awiri atagwirizana anagonana palibe yemwe zamupanga affect,dont waste ur time in these issues coz even in those islamic countries gaysm is there,if it wasnt there sibwemzi akumapezabe anthu akupanga zimenezo,it is everywhere and no matter how hard we may condemn this it will still exist so it is just a waste of time,be wise enough,akuba akapezeka amaphedwa koma kubako sikutha

  6. Mukakamba za akuba alipo ambirimbiri ……koma amene agwidwa ndi amene amalandila chilango……Nyasi zawozo mu dziko lathu lino ayi adzikapangila mudziko lomwe amaloleza m’chitidwe onukhawo.

 28. Jst reffer it with the word of god n we wll knw the trueth n that trueth will set us free!!

 29. Amenewo azingo mphedwa asalitenge kupusa dziko angakhale opusa mulungu kulenga mamuna ndi mkazi inu mkumagonana amuna nokhanokha zopusa bas afe ndithu

 30. wa nzeru akhale tcheru masiku otsiliza ano , lapani siyani tchimo kuti patsiku lobwera ambuye adzakupezeni muli olungama

 31. 2 gays have errested while having sex in Malawi and thy have admited? Kkkkkkkkkkkkk yaaa thats malawi 24. Dont judge let them do what thy want only God is responsible for the judgement

 32. sanalengendwe muchfanzro cha zamoyo amenewo,zowona tma insect,worms,zweto nd nsomba kukhala nd nzeru kuzwana chachkaz nd chachmuna iwo wosaganiza?nchyan kod amalawi?

 33. do you arrest anthu ochitila mwano makolo awo? as far as I know lamulo lachisanu liti honor your parents .do you arrest pple that don’t follow sabbath? do you arrest pple who don’t honor God? stop being assholes and be fair

 34. Last days!!!mmene timazunira ti mabebi munthu nkumalimbana ndi tonde nzako,devils workshop

  1. zaziiiii ndizoonekeratu izii and that doesnt make any sense…tisamabisalire pamulungu tikafuna kuchita zoipa and think before you comment though there is silent freedom of commenting.

 35. Is that news?? Who cares.. Distracting Malawian..this has been there and people do more indoors…irrelevant news
  Work on poverty issues

 36. Amalawi Chimene Timatha Kulemba Ma Comment, Koma Kuti Tipange Action Timalephela. Ofunika Kuwawonesa Adzunguwo Kuti UFULU Sikugonana Amuna Otha Otha Or Akazi Otha Otha… Malawi Stand Up And Be Wise!
  God Bless

 37. tisamaiwale kt tcimo limatha kubwelesa matembellelo mziko m banja olo pamuthu tisamasekele zopusa alangidwe amenewo

 38. “‘If a man has sexual relations with a man as one does with a woman, both of them have done what is detestable. They are to be put to death; their blood will be on their own heads.

 39. i wish it iz a fear God nation,these things bwez kulibe komabe let it be happen as it is,,,koma to arrest them no problem thats wat God want(yehova amati sazalanga munthu asanadzudzile).ukapanda kumva walahii yembekezela moto wa suphur,,,mamuna nzako ali ndi chikoka cha mtundu wanji guys,cant you see beautiful ladies God give us.ooooo,,Lord Jesus pray for our country Malawi.

 40. i wish it iz a fear God nation,these things bwez kulibe komabe let it be happen as it is,,,koma to arrest them no problem thats wat God want(yehova amati sazalanga munthu asanadzudzile)

 41. Ndiye muwone kupusa kwa boma lathu madonors akalamula kuti amasulidwe amathanyulawo,muwona Peter Mutharika akulamula apolisi kuti awamasule ogonana amuna okhaokhawo chikhalirecho madonors sakulithandiza dziko lino.kupusa ngati angavomerezedi zimenezo.

  1. Ndizoonadi mzanga sunama tinakakhala timaopa mulungu bwezi zikuoneka macitidwe athu mzungu akagot no it means no if they say yes it remains yes it means tinakali muulamuliro wa msamunda wat was de different nw

 42. Mungowaboola pamimba ndikuwaika bomba mmimba. Afe imfa yowAwa ndithu anthu opusa, zidzichita kuoposa nkhuku kuganiza ? Sindinaone. tambala akukwera tambala nzake, afe ndithu

 43. Paja Malawi ndidziko loopa azungu osati loopa Mulungu, anthu amenewo akwapulidwe zikwapu 72 aliyese zopusazaozo azikapangila kwa zungukonko,Kabungwekalikose kasatanic kasalankhulepo kanthu ndi sa ve cso,cso mumangofuna bread basi foolish

  1. zisatikhudze ife,limbanani ndi milandu yeniyeni osati zoti amuna ena awiri atagwirizana awapezelela akugonana,musataye nthawi ndi za zii,musati malawi is a God fearing nation,koma aliyemse payekhapayekha aziopa God,anthu akuphedwa onsewa,ndalama zikubedwazi,anthu mukungosaukilasaukilabe,limbanani ndi zimenezo,zomwe zikukhudzani osati izi zomwe sizikukukhudzani,ngati chili chilango aliyense azaweruzidwa yekhayekha tizalangidwamso yekhayekha

  2. zisatikhudze ife,limbanani ndi milandu yeniyeni osati zoti amuna ena awiri atagwirizana awapezelela akugonana,musataye nthawi ndi za zii,musati malawi is a God fearing nation,koma aliyemse payekhapayekha aziopa God,anthu akuphedwa onsewa,ndalama zikubedwazi,anthu mukungosaukilasaukilabe,limbanani ndi zimenezo,zomwe zikukhudzani osati izi zomwe sizikukukhudzani,ngati chili chilango aliyense azaweruzidwa yekhayekha tizalangidwamso yekhayekha

 44. Uh amene sanachimwepo awagende ndi mwala, tonse ndife ochimwa koma sindikutanthauza kuti zomwe achitazo ndi zabwino, anthufe takhala pa mipando ya woweluza kuwawona iwo wochimwa pomwe nafeso ndife olephela.

 45. “The two suspects are yet to appear in court to answer charges of sodomy.”

  We need a lot more detail to this article! GoM has stated and documented as much that it is no longer interested in prosecuting consensual, same-sex acts.

  Have these two men been charged with any offences? Have they been detained, or are they out on police bail?

  “Nkwanda further said in condemning the act, residents invaded Gonani’s house.”

  Have these “residents” been charged with their illegal invasion of private property?

  1. Inu Akulu Lankhulan Mwazeru Inu Kuti Mubadwe Zinakhala Bwanji? Mukumtenga Mulungu Kukhala Opusa Polenga Mkaz Nd Mwamuna? Nde Apa Muzit Ndiufulu Wawo Kma Ndinu Amoyo?

  2. ufulu wawo chani? ndiwe chitsilu, mulungu analenga mwamuna ndi mkazi, musatchule zina la yehova pa izi mwanva??

  3. mbalame iwe kodi mayako kapena bambo akasankha kukhara gay iwe ukanabadwa? penapake taziganizani pochita coment

  4. they have their own good reasons of doing that,it may be good if u ask them,dont waste ur time on useless isues,they havent violeted any1’s rights,inu mukutukwananu mukungochimwa za zii,mukutaya nthawi yanu kuwatukwana anthu oti sanalakwile munthu,iwo ngati anagwirizana kupanga zimenezo inu chikukukhudzani ndichani? Gwiritsani ntchito nthawi yanu moyenela anthu amagonanawo sanalakwile munthu,enanu titati tikufufuzeni mwagona ndi akazi osiyanasiyana,mwataitsapo atsikana mimba,mwabapo,ena kupha kumene,do u think these are not sins? From these sins i’ve just mentioned and tchimo loti amuna awiri amagonana,which one should be condemned first coz these two guys sanalakwile munthu?

 46. Khalidwe Opusa Umenewo We Are Not Mamerecas So If U Live Them Free Which Means U Are Agreed With This Stupt Habit Amalawi Chiyani Chikuchitika Plz

 47. Amangidwe basi muona maiko akunja akulowererapo kutiona kusauka.nanu amabungwe ndinunso akulu akulu amipingo koma chifukwa cha ndalama mumasiya zintchito zamulungu kusata ndalama kodi pakati painu ndimulungu pakakhala chani!

 48. Why following them to their house? Hidden and closed door? We have more problems to solve I believe! The more we confront such behaviours the more we promote them to the public!

 49. i don’t want to hear any CSO/NGO saying amasulidwe.Mchitidwe Wauchitsiru Ngati Ife Sitikuufuna.Even Maiko Ena Akunja Asayankhulepo Pa Nkhaniyi Coz Kuno Sikwawo.Mind You “we are not gays in Africa”

Comments are closed.