Opposition Malawi Congress Party (MCP) members invaded the party’s headquarters in Blantyre where they exchanged blows with top officials, Malawi24 has learnt.
MCP executive committee member for the Southern region, Samuel Kaphuka, confirmed the development adding that some members have been injured in the process.
“I was there, people came and invaded our office, and everyone was running away for his or her life. But for the meantime allow me not to say much as we are yet to investigate on the matter,” said Kaphuka.
Meanwhile the number of officials believed to have been injured is not yet known.
Thanks wa Mutharika Artaxerxes for your likeness on my comment.
Chakwela pa nyaaa pako
Pa mtumbo pako
Mbuzi ya muthu
Zomwe umamenyesela mtundu wanga ndi chain
Mutu kukula ngati basi
Ma suit ngati anapachika pa mtengo
Wanva kape iwe
Nde wins ati nyo nyo pano
Ask Gwanda Chakuamba & JZU Tembo they did in 1976.
Kkkkk koma
kutha ngati makatani kkkk
Kodi inu MAKADET a DPP, anyamata azikwanje mwasowa chochita eti? Nchifukwa chake mukukanika kulamulira dzikoli; kukacha chaphindu chomwe mukudziwa nditukwana MCP basi. MCP ndi dilu!! 2019 boma!!!!
Wow
Malawians as a Ctry nid tu change especially da leaders cos pple at grassruts are suffering.
das being naive as leaders of da oplosiition, in any way if dea is a concern dey suld hav tabled it to da concerned authority. Africans let stop bing ebackword otherwse we sal continiously be underminded by great ctries, we betta unite for prosperity and dev for da next generation tu come thanx.
Inuso mukut chan apa DPP Z MOVIN forward kupita patsogolo ndiku2ukwana atolankhaniko en wat z DPP AFTER 0? Nonses
zambikah bandah 2019 bomaaaaaaaa
no coment
Che Kaphuka sopano ati ndi ma youth a MCP kkkkkkkkk
Ha!ha!ha!,the madala party.
Hahahahaha chipani chamagazi ichi. Sichizathekanso kkkkk boko haram yeniyeni iyi.
ndiye?? ? mzachilendo anthu kumenyana?? za ziiiii pezan zina zotiuza
musationongere mbiri makape inu
Chipani chopanda mtsogoleri
Zomenyana lero ,zakalekae,anausawichiiiiii?
Mwati ayuth amakumbukila chikale, koma alipo anamumanga nyakula? Kkkkk midala asiyileni achinyamata ayendetse chipani cha MCP, kunali thawisa wako angakutsomphole
Hahaha mwapanga evolve from MCP to FCP, haaa #fighting #congres #party phanani tichepetse population..ndipo enanu mukuzitcha a MCP ndinu amalawi koma? Kapen makolo anu sanakuuzeni history? Mulekeretu zimenezo.
Kkkkk zonyadisa kwambiri kumawongola manja.
MCP kukumbutsira chikale panthawi ya macard mikwapulo mix nyakula
Magogo Chakwara Party (MCP) mwatikwana tangomwalirani tipume ife ma yuthi tili nga ndi UDF & DPP basi
Kikikikiki.. Why gentlemen? Where is contact and dialogue? Where are the four cornerstones? So mother party might not have changed iron stick treatment of anthu owukila? Kikikikikikiki
nkhaniyo nde wailemba zako za tobacco koma bola aphwasulana basi anazolowera kumenya anthu pa misonkhano kupha achina sangala, matenje, chiwanga, a gadama ndi ena nde piano akudabwa zomwe akuchita anzawo ALI aaaaaaaaa tizingomenyana tokhatokha Master Chakwera ALI ku parliament kusokonezako naenso kukamba zopanda nzeru kuti sha chipani cha magazi Mulungu amachifulatiradi eti, komaso yese osasusana ndi MCP wapha nawo a chiwanga sangala matenje ndi gadama just to mention but afew monga baibulo linena kuti wosasusana nafe ngwogwirizana nafe.
Anthuwa sianasinthe ndipo sadzasintha
Kkkkk, if u kick and blow one another, what will u do to Malawians if we giv u a chance to rule us? Won’t u start a civil war?
Azatitibula tonse.
Iwe bakili ukuona zotsatira za sukulu yako yaulele?shame on u son of a maggot,kamuzu told u,but u were 2 selfish to listen.
Atolankhani a ku Nyasalande mmmmmmmmmmmmm
akumenya anthu ndi a DPP mzina la MCP.
Kikikikiki eeeh!,komandee ndemanga zikuperekedwaaapa iiii!
Ma guys a MCP akupulana ku BT,mfazi mukulesanu kaya ife taona akuthyapana
Munaonelapo film ya ROBOT ya chichewa?kodi CHIPI amafana ndi president wa chipani chiti?
Kwaaaaacha! Kwacha!!!!!! Kumenyana ndi ufulu!!! m’mtendere!!!!
koma amapanga ndewuwo nga mcp kapena nga chipani chinachi kunamizila mcp
Mbuli za anthu
which is which?
ndizimene anazolowela mbuzi zanthu adazolowela kuvutika mtendere saufuna
Amaphunzitsana Kumanga Nyakula Agalu Amenewa(mdokote Style) Ndiye Anaukirana Wina Itamuwawa.
Mwasowa zolemba eti,lilongwe yake iti en akuluakulu ake ati? Za ziiii
kkkkkkkkkkk koma kumenko
VIVA MCP,2019 Govt!
Muchenjele m24 mumangidwa mwanva
Zabodza zmenezo, amamenyana ma member a MCP Kapena anthu amene anakhala pa office ya MCP?
Keep on fighting mcp while dpp iz going foward
A Dpp amenewo
mukaponyelanenso ku ng’ona!
Akuphanilana galimoto ya chakwela kkkkkkkkk kkk
Anazolowera kumenya mzika za dziko lino pano ayamba kukunthana wokhawokha.
Zabodza sizisowa! Mutu wankhani ndi nkhani zikusiyana bwanji? Malo amene ukunenawo pamakhala onenelela mabasi obwera ku lilongwe komaso pali mashop,kodi pamene pali office aliyense okhalapo amagwira ntchito mu office? Komaso nkhaniyi mmalema ngati wina amakuthamangitsani ndinudi atola nkhani enieni kapena mudatulukila pawindo bwanji. Shame on you!!!!
Vuto siolemba koma iweyo. Suziwa kuti malo onseaja ndi a MCP ndipo enao amangopanga rent? Upite ukaonesese bwinolomwe analemba kuti MCP headquarters
Ndale zapa Malawi,nokhanokho mumenyelananji?tiyeni mugwilane manja. MCP ndipani chachikulu .zikapitilila chomchi,aaa kaya.
Koma chipani ichi chili ndi magazi m’manjadi eti? mpaka kusinthana zibonyongo nokhanokha! Nanga kuti muzalamulire nde kuti muzatha mtundu wonse wa a Malawitu!…mapazi anu anyani a MCP!
Malawi24 you jus write news jus to get the attention not zopindulira a Malawi. Which Blantyre is that one?
WWE at MCP headquarter in BT Chakwela join Authality and muthalika thnks if it is gud to join authority. Monday raw night is DDP tag team agains Man of god + man of politics #chakwela and referee Atupele mwana wa Muluzi
exchanging of blows eee fighting party
Malawi 24 tchende lanu kuno kumwera kulibe mcp. Kmaso ukusiyanitsa bwanj mitu yakhan. Pathako panu.
Imeneyo ndiye mcp imene ndimadziwa. Nyau minded party kkkkkkkk
guyz tingodya tambala wakuda uja bas ine mundisileko matumbo
20 19 mcp bomaaa
Mcp ndi chomcho,atsala chakwera amuzula mutu posachedwapa
Hahahahaaha ndim’mene ziyera kukhalira basi, Sinanga cholinga chawo mkufuna maudindo basi ndiye sizodabwitsa kuwaona akusinthana zigogodo.
Anthu azimenyana mu banja ndiye mukanene mundale.. Amene anayambitsa ndi Alomwe amene ali mu MCP. Alomwe sianthu anzeru ndaonela Ibu.
mmmh mwasiya ndale mwayamba kunyoza mitundu sopano
Zisakuwaweni mwamva amene wanena kuti achewa ndi nyau walankhula bwino? Zopusa basi.
kumangot mchewa kutichani stupit…alomwe takuziwani kamba ka Bingu..ma hule ambiri ndi alomwe,opemphapempha alomwe,,mbava alomwe zopusa basi,,akamat malaw ndiosauka ife timangot alomwe zitsiru koposa ndi bwampini….
www@nyau style.com kumeneku mutha kupezako mbili zabwino za mcp
Patrick mutu wako wamva.
Sizachilendo izi poti nthawi ija ankapanga zomwezi kumenya osusananawo.
Zabodza2 izi
Nyau za mcp mukumenyerana chani? Chipani cha anthu amagazi mmanja.
khoswe iweso ukut chani ngat wasowa zochita itana mkaz wako
Usowatu mphwanga, ukulimbana ndi ma cadet?
Mizimu Yalusa Kuli Chilala Cha Magazi.Mwazi Oti Apelekere Nsembe Ngati Wa A China Solobala Sakuupeza.You Can Even Look At Their Leader He Is Spiritualy Affected Lol!
Then who will save malawi? you yourselves are fighting! what if u come into power? malawians decide.
ku south kulibe mcp koma dpp ndi udf kkkk komanso pp pang`ono
ichi ndiye chibwana sopano
yep,which one? kkk
Mizimu ya GADAMA,MATENJE,SANGALA ndi ena itakwiya kumaphwasulana nokha uwuu! Iwe wa ZBS bwanji sulemba rept sabata ino?
Mizimu ya GADAMA,MATENJE,SANGALA ndi ena itakwiya kumaphwasulana nokha uwuu! Iwe wa ZBS bwanji sulemba rept sabata ino?
Muhahahhahaha kukumbutsira chikale????
Malawi24 Journalists Go Back To School Before It Is Too Late. What You Are Writing Its A Total Trash!
Hehede Bwanji Manyazi Ndi Mabodzawo
chithothoka ngt makatani ,black chicken wil die soon
kkkkkkkkkkkkkkklkkk iwe ndye wandimaliza
Kummwera Kwake Kuti??Kulibe Chipani Cha Dzina Mukutchulalo Kuno.Sinnamveko.
Tanena zowona iwe!
Kkkkkkkkkkkk Ndiye choncho mukazatenga boma tizizangopanga exchange ma blows tu
Mbuz agalu anyan inu pathako panu malawi 24…. MCP Woyeeeee 2019 boma Dr chakwera boma hon richard msowoya vice
kikikikikikiki ikafika 2019 muzizati mcp 2024 boma hahahahahahahaha koma muli mmavuta aphwanga
Mcp Izingokhala Yosusa Chonch!Singatenge Boma!Blv Me,
Akulu-akulu ndeu ndaona ine dzulo ku office ya mcp ku bt, siyachibwana. Mpaka pano sindikubvetsa, anthu amamenyana ndi dzipika komaso kugendana ndi maduka a jerwa
MCP???????
Kaphuka will kill the party he iz not true mcp member he is there for desperate because he tried all partys
Kkkkkk WWE at MCP headquarters.
ngakhale mwapanga edit boza ndi bozabe basi, taonani bozanso lina ndilokuti ku BT is headquarters ya MCP
ngakhale mwapanga edit boza ndi bozabe basi
Propaganda yanu siithekapotu apa…long live MCP
amalawi tamakulani muthupi ndi mumzimu
Tsopano ikumveka aipanga adit.
Iwe ukakhuta uzingosewelesa zakumusizo:::::osati kumakamba za mighty mcp
wher dd it happen llz or btz? poor reportin
kkkkk youthwik mix nyakula stars,.muphana munya!!
Cheni cheni ndichiti #Blantyre or #Lilongwe :p
zabodza ndichoncho. Malo a Heading ndi news akusiyana bwanji??
Sibodzayi its true coz I was there mmene amabanduranamo. Vuto atola nkhani penapake sakumadziwa chomwe akulemba. Zin2 zi zachitikira mu Blantyre momuno.
Nyasatimes yalembanso nkhaniyi. Ndizoona amaswanadi.
ok? Koma azilemba nanga waona you are saying zachitika ku bt iwo alemba lilongwe
Inconsistencies in the news make me to doubt its validity. the heading reads: MCP members fight in Blantyre, and the story says: Opposition Malawi Congress Party (MCP) members invaded the party’s headquarters in Lilongwe where they exchanged blows with top officials. Which is which Blantyre of Lilongwe?
Za ziii
mungopwetekana za ziii!akudya ndalama atsogoleri anu,akuendera magalimoto odula inu muli vwiii!zitsilu
kambani zomveka a Dpp inu
http://free.facebook.com/l.php?u=http%3A%2F%2Fmalawi24.com%2F2015%2F11%2F12%2Fmcp-members-exchange-blows%2F&h=uAQFDGK27&enc=AZNEPD8SOwFoPDbZr0UFmBz3UiUjVWS2ZlIQbouQDLBlVMWQU4EtKeINd5R295cjNoUtPazil1roCXO6Vt0dQC3w_8zk3rH4M5OqjmpOpbkUV1pU1-7khh9MMMuRdVVxx8LP7APQEHh9_SzhGehQicDAlYQhUi64hqOTnGwbFUUK7w&s=1
lumanani agalu!
Mcp Members Fight In Blantyre,,,,,,,,,, Invaded Party Headquaters In Lilongwe,, Which Is Which??
Ine ndudabwa, basi mwina nkhaniyi yachitikira mlengalenga.
Ma Report Aboza Samasowa Amwene
Flames ayikanila kumenya Cecafa. Few dys later, flame imenya ndi Sudan mu game yoyamba ya Cecafa. Ungodziwilatu kuti sakudziwa kuti zinthu zikuyenda bwanji. They just write hearsays!
They Just Want To Keep Their Page Alive Basi Nde Amangolemba Zilizonse
zachitikira kumwamba izi
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk fightng mcp
nanga nchaniso?
Heheheee! Koma kumeneko,,,,,u r failing to run ur own party how will u b able to run a big country like mw,,,aishoshe aione!kkk
Muphana Simunati