“Kaliati waputa mwana mulhomwe” – Ngolongoliwa
Mfumu yaikulu ya a Lhomwe mudziko muno Paramount Chief Ngolongoliwa yaopseza m’modzi mwa mamembala a United Transformation Movement (UTM) a Patricia Kaliati ponena kuti akhale osamala chifukwa aputa mwana mu Lhomwe. Chinatsitsa dzaye kuti njobvu… ...