![United Transformation Movement (UTM)](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/UTM-235x176.webp)
Kupilira kwa UTM mu mgwirizano kukanakhala kwa Mazunzo – Chaima
Katswiri pa ndale mdziko muno, a George Chaima, ati panali kuthekera koti UTM ipitilire ndi mgwirizano wa Tonse monga momwe anadekhera mtsogoleri wa chipanichi a Saulos Chilima koma ati UTM ikanapilira mozunzika. Poyankhula mu pologalamu… ...