Lakeshore road has been cut off in Salima

Msewu wa Lakeshore waduka

Tsopano mayendedwe akhala wovutirapo pa msewu wa M5 pamene madzi ochuluka adula msewuwu, omwe umatchedwanso kuti Lakeshore, kamba ka mvula yamphamvu yomwe yakhala ikugwa. Msewu umenewu waduka pa malo otchedwa Mwalawoyera kuchokera pa Salima Turn… ...