Malawi ali patsogolo pankhani yoteteza Njovu
Bungwe la Elephant Protection Initiative (EPI) lati dziko la Malawi lachita bwino pa nkhani yoteteza njovu ndipo laposa maiko oposa 24 amchigawo cha Africa omwe ali pansi pa bungweli. Poyankhulapo pa za nkhaniyi ndi wailesi… ...