![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2021/10/Vehicle-set-on-fire-235x176.jpg)
Anthu okwiya atentha tchalichi
Mapemphero anasokonekera dzulo pa mpingo wa Headstone Prophetic Ministry International ku Chileka mu mzinda wa Blantyre pamene anthu omwe akuwaganizira kuti ndi a gulewamkulu atentha tchalitchi. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Chileka a… ...