Kuli kanthu kokanthula ndichala: Chakwera ndi Chilima avulana pambalambanda
Pamene masiku akuthera kuchitseko kuthamangira ku chisankho chapatatu mu Meyi muno, awiri mwa anthu omwe akuzapikisana pa mpando wa mtsogoleri wa dziko atosana zala m’maso. Lolemba sabata ino, mtsogoleri wa chipani cha United Transformation Movement… ...