![Lazarus Chakwera](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/06/Lazarus-Chakwera-1-235x176.jpg)
A Chakwera akana kuwapaka kukwera mitengo kwa katundu
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati mitengo ya zinthu mdziko muno imapitilira kukwera kwambiri chifukwa boma linagulitsa makampani a boma omwe amatha kuchititsa kuti dziko lidzipeza ndalama zambiri kuti katundu adzikhala ndi mitengo… ...