![gabadinho mhango](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2020/02/gabadinho-mhango-235x176.jpg)
Gaba wakalamba? Mtsutso wakula pa masamba amchezo
Pabuka m'tsutso pa masamba amchezo potsatira zomwe wayankhula mphunzitsi wa timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino a Patrick Mabedi omwe akuti Gabadinho Mhango wasiyidwa kutimuyi chifukwa osewelayu akukula. Lachiwiri Mabedi wauza nyumba zina… ...