
Ngozi zogwa mwadzidzi zikulikwirabe miyoyo chaka chilichonse – DODMA
Chiwerengero cha anthu amene akutsikira kuli chete kamba ka ngozi zogwa mwa dzidzi chikunkira chikwerelakwelerabe m'dziko muno. Nthambi ya boma yoona za ngozi zogwa mwadzidzi ya Department of Disaster Management Affairs (DODMA) yati mwezi wa… ...