Sindinakumaneko ndi a Chakwera – Kabambe
M'modzi mwa omwe akufuna kudzaimila kudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wa dziko lino kudzela ku chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) a Dalitso Kabambe ati iwo alibe maganizo aliwonse ogwirizana ndi mtsogoleri wa dziko… ...