Akukana a Malawi kudyela suwiti mpepala: ochepa okha akutchena
Sikuti ndi yodula kwambiri jumboyo, imathekanso kupezeka yaulere koma a Malawi ochulukilapo ndithu akumayizemba. Malinga ndi kafukufuku, zadziwika kuti a Malawi sakugwilitsa ntchito kwambiri chitetezo pokasamba. Angolowa ndi mutu basi. Itchoke itchoke. Pa mwambo omwe… ...