Njala yavuta Ku Machinga, anthu akudya chitedze
Phungu wa dera la Machinga Likwenu, a Bright Msaka, wadandaula kuti anthu ena m'boma la Machinga akudya chitedze pomwe njala yafika posauzana m'bomali. A Msaka analakhula izi Lolemba Ku Nyumba ya Malamulo. Malingana ndi a… ...