![Ayra Starr is a Nigerian Musician with over a million followers on social media. Her songs include Rush and Sability](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/10/Ayra-Starr-235x176.jpg)
Nanga Ayra Starr simukumunena bwa? Queen Sheba adandaula zakutozedwa pa mavalidwe ake
Oyimba Racheal Muyepa yemwe amadziwika kwambiri ndi dzina loti Queen Sheba wati ndiodabwa kuti a Malawi sakuyankhula kanthu za mavalidwe a oyimba wa ku Nigeria Ayra Starr yemwe anali m’dziko muno, ponena kuti anakakhala iye… ...