![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2022/09/Lazarus-Chakwera-Kulamba-235x176.jpg)
Bungwe la Mulhako ladzudzulidwa posaitana a Chakwera ku mwambo wa chikhalidwe
Oyankhulapo pa nkhani zochitika mdziko muno adzudzula bungwe la Mulhako wa Alhomwe chifukwa chosaitana mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ku mwambo omwe ukuyembekezera kuchitika pa 9 October, 2022 kwa Chonde ku Mulanje. A… ...